Following the firing of Grezelder Jeffrey from the Democratic Progressive Party (DPP), the party has now appointed Alfred Gangata as its vice president for the central region. This has been revealed today Monday, 26 February,… ...
Articles By Archangel Nzangaya
Unduna wa zachilengedwe ndi kusintha kwa nyengo mogwirizana ndi nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo, ati sabata ino madera ambiri m'dziko muno kugwa mvula ya mphamvu ndipo akuti pali chiopsezo cha madzi osefukira m’madera… ...
The Leadership Institute for Transparency and Accountability (LITA) says it is worrisome that the Malawi Congress Party (MCP) is strategically set for anarchy and one party state, and has since urged the party to stop… ...
…akuti “a Malondera analemba zigawenga” Ya pa chiweniweni: phungu wa chipani cha MCP ku Dedza, a Willard Gwengwe omwe bokosi la maliro lomwe anagula lakanidwa mochititsa manyazi, aloza chala phungu nzawo wa chipanichi a Steven… ...
Pomwe kudzigulira mavoti pa chisankho cha chaka cha mawa kuli mkati, m’mawa wa Lachinayi kunali “taonani taonani, zilikotu ziliko” mu mzinda wa Lilongwe pomwe aphungu awiri a chipani cha Malawi Congress (MCP) aliyese anagula bokosi… ...
The Malawi Minister of Finance, Honourable Simplex Chithyola Banda, will today Friday, 23rd February, 2024 present the 2024/25 National Budget Statement. Chithyola Banda is expected to present the 2024/25 budget statement at 2:00 PM in… ...
Wa polisi wa zaka 41 ku Ulongwe m’boma la Machinga ali m'manja mwa apolisi anzake kamba kakuba lamya ya m’manja ya mlonda wina. Malingana ndi lipoti lochokera pa polisi ya Liwonde m’boma la Machinga, omangidwawa… ...
The Ministry of Natural Resources and Climate Change through the Department of Forestry has condemned attacks on Liwonde Forest Reserve officers by charcoal producers during routine forestry patrol. On Saturday morning, 17th February, 2024, some… ...
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus McCarthy Chakwera watsimikizira mtundu wa a Malawi kuti palibe ngakhale munthu m’modzi yemwe amwalire chifukwa cha njala yomwe yafika posauzana m'madera ambiri m'dziko muno. A Chakwera amayankhula izi Lachitatu… ...
Members of Parliament will not meet today for continuation of 2024/2025 budget deliberations following the death of Assistant Clerk of Parliament Lawson Chitseko who died after knocking off on Wednesday. This is according to a… ...
A study which is one of the two drug trials being carried by scientists at Kamuzu University of Health Sciences (KUHeS) to establish shorter Tuberculosis (TB) treatment regimens, is progressing well. According to Dr Hussein… ...
Mzibambo wa zaka 47 munzinda wa Lilongwe wathilidwa dzingwe kamba kopezeka ndi ngaka (pangolin), pomwe awiri enaso munzinda omwewu awanjata chifukwa chopezeka ndi nyanga za njovu. Izi ndi malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya… ...
In a move to improve and expand secondary education, the Malawi Government through the Ministry of Education says it has recruited 2,681 secondary school teachers and promoted 2,259 teachers. This is contained in a press… ...
Driemo’s ‘Trailer’, which is now an anthem in Malawi, has become the first video in the country to hit two million views on YouTube in just a month. On 15th January, 2024, Driemo who was… ...
As climate change is increasingly exacerbating droughts, flooding and inconsistent rainfall, a call has gone out to the younger generation to take a leading role in caring for the environment so as to mitigate the… ...