A Malawi apemphedwa kukhala anthu olola ndi omasuka pa nkhani za njuga. Malinga ndi wamkulu wa mu unduna wa zamalonda, a Elsie Tembo, a Malawi sakuyenela kuona njuga ngati chinthu choipa.
A Tembo ananena izi mu mzinda wa Lilongwe pamene amatsegulila malo ochitilapo njuga otchedwa Marina Casino.
“Anthu akuyenela kumvetsa kuti njuga si chinthu choipa, chinthu chilichonse chili ndi ubwino ndi kuipa kwake. Nayo njuga ili motelo,” anatelo a Tembo.
Iwo anaonjezelanso kunenapo kuti anthu akamasewela njuga akuyenela kukhala omvetsetsa ndi oleza mtima.
“Anthu azidziwa kuti awa ndi masewela, utha kupambana kapena kugonja.”
chenjerani anthu inu.sizonyadila izi zitchito zasatana ndizimene akuyendetsa anthuwa
Nditchimo njuga.boma lathu likupita kuti abale.owerenga akhale maso.amen.
Zaulendo uno by mwanache
Zautsilu
Dirty funny
Nde lolaninso chamba kuti chizipezeka paliponsetu kkkkk
Nonse amene mumakambirana nkhani yimeneyo ndinu mbanzi zawanthu mwava komanso nonse m’bomamo ndinu agalu awatho
Chamba koma kuba
ndezachamba suja mumaletsa viganda, mwayamba kulolezanjuga ndechambaso tiyambe kulimba
Kkkkkk Malawi waonongeka
Mbuli za anthudi zimenezieti? Kukalimbikisa khalidwe lachabe koma abale dziko lathu likunka kt makamaka! Last week amakambilana at nkhani zololeza abortion koma zooona? Lelo akubwelesaso ina akt boma lanyong’ola kt amalawi aziyenda juga, our country is damage by stupid leaders
malawi wakeyo.soon timva zoti alola anthu kuti aziba momwe angafunire
Mhhhh!!! Kukadakhala kuti kuli mwayi, osinthanitsa kutenga Wa moyo munthu nkukamuika kumanda nkukatenga wakufa kuti akhale ndimoyo chinali bola kukasiya Pitarayu nkukatenga Bigu chifukwa bolani ada ajawo ankakana za chifinezi ,osati INJA uyu/ ( Galu uyu )
Kkkkkkkkk ndinali ndisansione nkhaniyi Mwati Boma kupempha Amalawi kuti ayambe kukonda njuga? kkkkkk Mukamamva kuti uchitsilu wa Anthu akulu akulu ndiumeneu basi kufatsa nkufatsa amvekele Amalawi azikonda njuga asaaaaaaa!!! mukauze akwanu zopusazo mwamva kuganiza uku nde bolanso Mwana anganize zanzerutu Mbuzi za wathu
Komanso muloleze kut munthu akaba asamangidwe boma la alomweeee zaziiii
Pansana pake galu ameneo
Kkkk what is happening to my home country? Tell us what is wrong to reach that extent
No wonder Multiculture @ its best lol
Ndili panseu ine.kamachesi wakaona ndani?
Mawa ndi game number pansi pa kapu.
Chaaa kosowa chonena et
Ndithu????
that’s a great idea…nthawi yonseyi mumatani…….
Gambling is in many ways but we dont know. Insurance, medical scheme, game betting,(indirect gambling). Look at NICO, MASM, TNM-kulosera tnm league games.
Ayitha pano tizimenya njuga no cheuche
That’s stupid ! Build Casinos so people can be gambling with open hearts .
ngati uli umphaw pa malawi ndie wafika pazawoneni
Kusowa sochitakupariament,uuu,komakumalawi abale,safika pamathero
Achakwela taziuzeni zitsiluzo zmalemba pankhani ya juga malo makambilana zazeru kumakhala bisy ndizamanyi basi
BOLANSO NSABWE ILI BWINO IKAONA CHALA IMALUMPHA NKUTHAWA.KOMA MUNTHU AKUZIKUMBILA YEKHA ZENJE.
Malawi nde ameneyo kulesa frozy kuloleza mowa,akuti odwala achuluka mzipatala ndichfukwa chomwa frozy,imfa zuuchulukaz akuyambixa ndi frozy,akut ma driver akamwa akumalezera mchifukwa chake ngoz zikuchuluka.Akut amuna tokhatokha tizikwatirana,akazixo okhaokha,akuti mimba titha kumatenga nkumazichotsa momwe tikufunira,lero akuti tizipanga njuga ndipo tilemera khasu tipachike.what a nation?malawi.no wonder mvula ikungogwa yoononga mphezi ndi izi zikutikanthazi.uchimo wachuluka.Mmera ku admarc akugulixa modula ngat ndi gold,katundu wazinthu akungokwera koma malipiro ndiomwe aja.Zafikapa nyasaland tizimutanthauzira mchichewa kut dera lonyasa muzochitika osat nyanjaland.
Zomwe kale anthu timaziopa kut nditchimo pamaso pa Mulungu pano kumufusa munthu umva malamulo amalawi akulora kutero..Gambling,,Abortion,,Amuna kapena akazi kukwatilana okhaokha,Sex out side mariage..kuvala mosazilemekeza makamaka atsikana pano unva zili mu fashion komaso malamulo zonvetsa chisoni..zithu zoti anthu simungakhale carbinet ndikumakambirana coz ndizochita kuonetseratu kut siziloledwa kwa Mulungu kutero koma umva akut aphungu anyumba yamalamuro akukambirana mfundo yoti pakhale chilorezo choyenda njuga mwaufulu aaaaa koma zoona imeneyo ikhale nkhani yokakambirana mavuto onse ali kumalawi ndikumakaonjezeraso mfundo zina zobweretsa minyama pamoyo wa aanthu.. yes malamulo anuwo akulora kutero komano nanga malamulo a Mulungu akuloraso kutero ?? nanga chabwino ndichani kusiya zomwe Mulungu akuletsa ndikutsatira zomwe malamulo apadziko akulora ?? afta 2yrs ndikukutsimikizirani muzanva akut kwamene akufuna ku joiner Satanic malamuloso akulora kutero bolani dziko lathuli likhale ndichithandizo chokwanira so bad… God forgive us..
zomangana palibeso njuga patsogolo
Mmmm kkkkkk mulowelelepo ambuye.
Ndiye oyenda juga azilipila nsonkho? kapena for free?
Za kumindima zayambaa kuoneka shame
Amene walamulayo aziwapatsaso athu ndalama yoyendela njugayo cz athu akusowa chakudya angakapange njuga yachani aaaaa sheme
Atchalitchi ali kuti amatchenso za njuga…..
Munthu asewera njunga ku Cassino ngati Salary ukulephera kukwanitsa kugula zofunika gi ve better salaries muone ngati sitizipita kukapanga Poker
Koma ziko lafikapo
Kamano inu amene mukupanga mfundo zopanda phiduzi mukuganiza bwanji? Jugayo iwapanga anthu kuvutika kuposela mene akuvutikikamu wina azibesa ndalama yogulila chakudya
Shame
zautsiru basi…umbavatu….umenewo….koma mau a Mulungu mumawatsatadi…kapena inu mwaposter zakumtima kwanu..pofuna kuona ma comment ochuluka….mukuzitenga kuti zimenezi….am vry sorry…
Stupid ngati mulibe chokamba ingokhalani pheee
kkkkkkkk
Kkkkkkkkk sure!! Koma zoopsa
yaaa kwasala muloleza kuti alibino azigulisidwa mwasowa chochita dziko lakukanikani
Adatilodzayo ndi Mfitidi,,,,,, “muzichita njuga kenaka mulemera”
Koma!?
Za ziiii ngati 1 tambala
Tingolemba Mzungu akhale president wathu coz iye amangofuna kupanga mbiri basi osati kuba. I think more things can change.
My God
Kulinso nsonkho kodi?
Mmmmmmmmm mmm kaya zidze pano zatonse
create good jobs, encourage us to work hard & stop encouraging pple to indulge in acts of theft & laziness,
Hahahahaa uku ndikuima mitu kwa anthu ena
Gambling z better to sell ganja
though tli osauk we all obey GOD so ths is a god fealing country hw come the pple in it might indudge thm selves in that sin,,shame malaw
Zitsilu.
Zopusa anthu otembereredwa inu
dziwisani kaye apolice kuopa belo
Zizindikiro zonse zamu bible zosonyeza kutha kwadziko Malawi yamalizamo. Abale ndi alongo mulekelanji kulapa machimo anu?
Juga imayambitsa kuba
.
Ha ha ha……mpaka njuga eti….mwawonjezera pa chamba kkkkkkk
Kumeneko ndiye kulimbikitsa mchitidwe wawumbava apolice gwirani ntchito yanu pamenepa m’malawi muno mulibe lamulo losewera njuga aboma mwatani kodi ngati mwasowa zokamba ingokhalani
Yeah its truth other countries lys south africa likes gambling
Kkkkkkkk, nazooo
Pantumbo pake ameneyo kwa december ino npaka december ya chaka chamawa mumakambilana fundo zopoila bwanji kumipandoko pankholo panu nose ku phatikiza ndinduna zose zamu dziko lino mukufuna muti onongele ana mudziko muno zoyambitsa chisokonezo muno ayi muzikapangila kwina manyi amenewo
Kusewela Njuga Ukaweluka Kumunda Wa Chamba!!! Malawi Wa Dpp Amene’yo!!!
Anthu opanda zeru
Za ziiii zikuonesa poyelayela kuti president wathu saziwa kuyipa kwa njuga mupaka lelo iyi ndiye mbuzi yamunthu akuvomeleza kuti anthu akuba achuluke mudziko lathu
Tiyeni tizisewera pa kati pa lamba guyz.iyi ndi njuga ya bwino kkkkk
Kumeneku timati Boma likusowa chochita ku wathu ake..
Misonkho yonse tikupangayi mukufunanso wa njuga nde ma hulenso ayamba kukhomeratu
We letting devil rule us n when things go bad we blame God. Ana anjoka inu
Where these dirty people are taking Malawi to? Misleading and Misuse.
Mavuto. Angokula. Basi. Mwalephera. Lolani. Mulungu. Alamulire. . taona. Anthu. Akukhala. Pa. Rent. Cz. Analandidwa. Nyumba. Ndi. Anrhu. Ajuga. Anzawo. Ubwino. Uli. Pati. Apa?
Akuti God fearing nation
OH!!!! What a stupid development!!!!!!
Kenako adzalipeleka dzikoli mmanja mwa zambia,mozambique ndi tanzania kuti aligawane . Chifukwano uku ndiye kusowa kolowela . Let us wait and see.
Uchtsiru umenewo! ndi zmene mukumakambirana ku parliament mukakhuta? shame on you! what malawians should benefit from gambling? a china adzachotse parliament yawo dzitsirudzi dzikusowa kosewerera dzkakhuta shooter!
Kkkkk
U dnt even knw wat ur talking abt.
seems lyk u r de one hu dont know…..#bester’s 100%
I knw wat am talkng about coz even in e bble gamblng is a sin before God!
That awkward moment when you try to look wise by commenting something… Only to realise you just made a fool of yourself because your comment was total bullcrap……lmfao
Aaaaa guys,, bac muli busy kupanga reply ma comment anxanu monyoxa chonchi?? Kodi mesa aliyense akupereka maganixo ake? Musapange xa ena mbuxi inu. Aliyese atokote xake mwamva?
Sapemphela Tembo akadakhakuti Bible amalidziwa akadadziwa kuti njuga ndiyoletsedwa Bible ndipo inatembeleledwa anthawi imene amkapanga mayele zovala za yesu
Njuga ndi uchimo-chifukwa zinthu izi zimachita involve kuba komanso kupha.Ndiye boma povomereza avomereza zonsezo GOD PLZ ABIDE WITH LAND OF MALAWI
Asowatu malonda opanga tsopano ndiye tingolowa Ku njunga kkkkkk Malawi alibe chochita atsogoleli nawoso mutu yangosonekera mabvuto achuluka.Dziko ngati lavuta tiyeni tiwapatse mwayi azungu athu aja tidawathangitsa kuti mwina tingawoneko kuwala ngati mmene azathu akujoyela mmayiko awo pali mzungu sipanama ife anthu akuda aaaaa mbola kudzikundikila too much
Hili ni shirika lisilo la kiserikali (NGO) lenye Makao makuu yake nchini UFILIPINO na sasa limefungua ofisi zake nchini Tanzania. Shirika linalilojihusisha na utoaji misaada kwa:
(1) Watoto yatima
(2) Wajane
(3) Watu wenye changamoto mbalimbali za kiuchumi
Hivyo shirika kwa sasa linatafuta mabalozi/ wawakilishi popote pale nchini Tanzania ambao watalipwa na shirika kwa mshahara mzuri. Kwa maelezo zaidi tembelea.
OFFICE: kivulini, Mlimani city Dar es salaam.
WEBSITE: http://www.helpinghandsinternational.biz
CONTACT: +255 677 898 941, +255 655 216 136, +255 767 216 136 or
+255 621 892634.
USITUME MESEJI HAZITOJIBIWA.
Wote mnakaribishwa HELPING HANDS INTERNATIONAL.
HELP US TO HELP OTHERS.
http://www.helpinghandsinternational.biz
Apeter abalalika akutiso aliyese osuta fodya azita chamba opezeka akusuta Embasy azimangidwa koma ku Malawi eeeesh!!!!!
Where is malawi heading to?? One day our leaders will sell us to the foreigners mwachinsisi
Kkkkkkkkk aboma zawavuta apa
Dzulo munati adzimai azitaya mimba lero mukulimbikisa azibambo za junga kwenikweni mukufuna chani anamajekete inu kwamalawi
Boma la pitala or peter kkkkkkkk opitala woyeeee
Oh yeah! suprise! suprise! where have you been all along? so onse amene anamangidwa coz of gambling atulutsidwe….mu ndende right?
Serious
Dzowona Mpakana Juga Mulungu Dalitsani Malawi
eshiii kom inu mbunzi zina eti kupanda manyazi ndikusowa mzimu kumati “kayendani njuga”what is njuga?aonereni akhakhatha,atombolombo agulukunyinda simudzathekaso ananchidwe inu
Mutineeresera mbava bas
Zamanyazi dziko lavutadi ili mmmm only god knows
malawi ukupita kuti tsopano lwee!? apa ndiyet undisiya lne,
Wachiwona ndani mmene azimayi ankadyetsera ndalama yokagula chimanga ku admarc muja mukufuna ayambirenso? Mwachitika nasi uli tanyinu? Imwi mutchaya cha mbwenu isi titchayengi, hinya ukavu ngwidu ndatchayapu cha.
Malawi
Nanga kuyenda juga ndi tchimo
Kkkkkkkkkk
Haram
Malawi was moto kkkkkkk
Zaziiiiii
Ooo! ! ! Shame
Mwayamba kulimbikisa anthu kuba eti
Akusow zonena bwanji osakamba nkhawi yot anth asangalale zazii mbozi
Ooooh NO this is a really corupt goernment, DPP umbava wanu mkufuna ukhale palipose eti? njuga zimayambisa kuba kumeneko nde kupepela koma pitala ndi boma lake awa nde akanikilathu kuyendesa dziko eish
mmmm!!!!Dziko latha basi
Kkkkkk njunga yake mukuona ngati yachisawawa eti kkkk siyomwe mukuganizayo ndi lotto anthu a mwayi amatha kuyalura mphasa ndianthu kkkkk
Koma ndi njuga basi!! kutha ma plan kumeneko
Sikutha mapulani poti sukuziwa kuti in developed countries they like it so much…
Man lotto kuno ku MLW inakhazikitsidwa kale kale ndipo Juga akunenedwayo nde wachisawawayo
Kkkkkk sanganene zimenezo iwe kkkk akunena legal gambling which is lottery
DPP is satanic
Is that ur plan guys its better to lieve if ur tired to work Gvmnt ndizimene mukumakambilana kumeneko mwasowa zochita eti mbuli za anthu inu dzika lalowa satanic baSi
Njunga? Or juga?
kkkkkkkmkkkk! zochitika Ku Malawi sungazivese paka pamenepaaaaaa
A frnd of mine he started gambling at very young stage now he is just robing people.
Musasokeze dziko lathuli..Ngati kwakukondani kuno mutha kumapita kwanu ku USA…
Chakula apa ndi usatana zowona zake ndizakuti aliyese wandale ndi satana coz malamulo omwe amatipatsa amakhala ochokera kupasi kwanyanja mkumatulukila kumtunda ndiye sizachilendo dziko kuti lithe pakufunika zizizndikilo zomwe mwini wake namalenga analosera zichitike ndiye izizi ndizochepA zenizeni zikubwera koma tsoka ndiiyemwe akukwanilitsa zizindikilo za kutha kwadziko ndiye alinditsoka kenako atipatsa ufulu oyendano maliseche azimayife
Koma mulungu ngati adalanga kapena kukwiila Sodom ndi gomolla zifukwa zoti mulungu atikwiile zakwana ndipo tikapanda ku sintha mulankhulide,zochitazathu mulungu achita nafe
Yes I agree with that
Koma ngati kuli kukula kwa ufulu next kuzakhala kuuza anthu aziphana
Ndiye ose ogulisa chamba,okuba ndimahule apasidwe ufulu atuluseso andende ose popesa zifukwa zomwe anawamangila pano siuchimoso
kkkkkkkkkkkkkkk.atsogoleri akumalawi oganiza ngati galu ot atasaza nthawi yomweyo ndikumadya MASAZI AKE. kkkkkkkkkkk WHICH BENEFITY CAN WE GET TO GAMBLING WE US ANATION?KKKKKKKK. ndathedwa zeru. inu cheni cheni chomwe akufuna anthu awa ndichani?
Kkkkkk mwina ibweretsa forex. Koma yaaa failed state indeed
Kma Achawa abaleeee,,,Njuga ndiye chani?
Gambling is a bad habit coz it tain someone it stealing people things.
Njuga toto
To be objective , nation can’t develop cos to gumbling or njuga
Zachisoni ndithu anthu anga akuongeka chifukwa chakusadziwa akanadziwa Tembo sakanalankha
Mmmhmmmhm….. amalawi!
Siye kulima?
#ufulu tidauvomera tokha kuyesa zizakhala better koma …!
Kkkkkkkk kkkkkkkk kkkkkkkk kkkkkkkk kkkkkkkk kkkkkkk
Gambling is, has been, and will always be there just that there hasn’t been more promoters of responsible gambling. It’s a game actually but it is a sin on religious grounds. Nonetheless, people play that game responsibly even irresponsibly.
You are right mr Timothy,only other pple dont knw the meaning of “gambling” Come to South Africa,pple make millions of rands–lotto,casinoes!
That’s for sure dude
Bodza ili, mukapezeka mukusewera bawo ya dola ndi mlandu..pa malawi..
Kodi Ku Malawi kuli casino? Chifukwa ndikuona ngati olo olemba nkhaniyi sakuzindikira chomwe boma likunena.
When nations fall into the hands of fools,…nothing works!!!
Ndthud braz smuknamay!
Hehehehehe koma yaah
Vomerezani Chamba chizilimidwa tikokere ndalama yakunja tilibe osati za manyizo abwampini inu iyaaaaa
Kuphuzira sikupita school kokha ayi!ndiye ameneyo muwaphuzitse kuti njuga imaletsedya
Kkkkkkkk fwiiiii
thats y athu akuthawa mziko.
Malawi 0% behaviour we hav gone crazzy eshi! too bad.
Hmm amalawi anzanga zikatere ndichiyani?
Eeeeeeeh MALAWI kwachaa, wasanduka kwadaaa, ambuye musalolere kt ana anu tiyende muchionongeko ,tichotseleni ziwanda zomwe zikufuna kuononga dzikori ,kutenga tchito zakumidima kubweletsa poyerah achite manyanzi dyerekezi ameneyi muonetseleni ukulu wanu ndipo ndi pemphero langa ndi pembedzelo kt oipao achite manyazi..AMEN
Luck enough I know that gambling is sin before God so this you better cheat to those who are cheatable #freedomof speech #democraxy
Owerenga khala maso.
Owerenga khala maso.
mulungu akhulukire dziko la Malawi chifukwa cholowetsa uchimo mdziko lawo.
Hahahaaa tchova tchova flower, corner,queen led hahaaa stupid propaganda
Kodi mesa kuyenda njuga ndi mlandu…azimayi okonda ziganda alimbike zedi….kkkk
Hahahahaha! Kmande zafkapotu mmmh….
Aaah! Aaah! Heee!? surely the thunder that will strike Elsie Tembo is doing some push ups. Mpaka njuga.?
Malawi wapitadi basi mpaka pamenapa,mmalo molimbikira kupemphera kuti Mulungu atichotsere mavuto tili naowa,ndimmene mukwaudza anthu kuti adzichimwabe,kapena malemba simunawaone
Kkkkkkkkkkkkkkk
unkolo ,,,muti kulimbikila kupephela kuti asiye ,mmmmmh i think its good but if somene knows its better just to leave that bad thing,,,panopa zomangoyang’anana basi.
unkolo ,,,muti kulimbikila kupephela kuti asiye ,mmmmmh i think its good but if somene knows its better just to leave that bad thing,,,panopa zomangoyang’anana basi.
Kulimbikila kupemphera mumalo moti azikazisaka.
mmmmm mbale taenda mu maiko aza2mu muone kae, palibe cholakwika apa
kuno kumalawi zinthu zikutipeza mochedwa nkuona chilichose timaona ngati dziko likutha kkkk,,,,kumangoti ambuye alowelelepo zilizose,,,,,,,kkkkkkkk tamaendani abale osamangoti machimo zilizose,,,,
Koma inu simukudziwa kuti ndi tchimo,inuyo mungalimbikitse ana qnu kumachita zinthu zosayenera?
ndi khalidwe loyipa osati tchimo ,
Gambling can never make economy come right. No!
Ngati nzeru zachepa chifukwa cha kukula tipaseni ife dzikoli tiyendatsa bwino ndithu njuga ndiyolesedwa angakha mma holy books,inu muli ku njuga panopa?musasokoneze mitundu ya anthu ngati mwasochela ,sokelani nokha amene pemphani kwa Chauta nzeru musanayankhula kuopa kuti mungaonongeke komanso kuonongesa anthu ena
o allah pls hlp me 2stay away 4rm ds foolish leadership
The government and it’s leaders have gone crazy.
kodi Malawi ukupita kut mmmm ma last days timva zinthu koma iwe Tembo mutu wako umagwira bwino koma ndipo ndiwe opusa wava ufuna kut umbanda ukule et
God Fearing Nation? Where It Is Ok To Indulge In One Sin And And Not Ok In Another
Ndiye tikati atsogoleri athu ndi amene akuononga dzikoli tikunama? amalawi tiyeni tipemphere kwambiri chifukwa oyenera kumanga Malawi ndio akumasula Aaaaaa! Shame Malawi!
Za ziiiii
Malawi wawonongeka basi…
Kkkkkkk tiyeni nazo
kkk boma ili nde lilibho
sinful nation
The late kamuzu anati chuma chili muntha koma lero chuma chili my njuga lol kkkkkkkk my Malawi.
zopusa zokha zokha chamba eti.
So funny
Mmm hhii malawi wanga ineee!!!
It is not our culture, pliz mutionongela ana.
mmmm ayi tinaphunzira ku school subject ya lifeskills kuti juga ndiyoipa
kkkkkkkkkkkkk kenako muloleza chamba kugulisa palipose akazi ambili akhala opanda mabanja amalawi tikupitakuti
Inu a24 bodza y?
Iwe sbodza its true!!!! udztsata current affairz….za dzko lako zmenezo.analankhula pamene amatsakulira Cassino.
Kkkkkkkkkkkk uyu ndi ganja weni weni
Mayoooooooo!!!!!dziko langa lija ine!
Kkkkkkkkkkkkk.Malawi tsopano!!
Allih Allih Hashm Manjolo Imed Hashm Bernado Tenmay Million PE LE TE Ben Son
Chamba basi kkkkkk
F**k govt
kkkkkkk, wow
Boza limenelo