Lutepo wants K1 Billion for sex report

Advertisement
Oswald Lutepo

…I am not having sex

Cashgate convict Oswald Lutepo is ready to knock on the doors of the courts again, in demand of a staggering one billion Malawi Kwacha.

Oswald Lutepo
Lutepo demands K1 billion

According to information that Malawi24 has, Lutepo has sued Times Group over a publication it made which indicated that he is accessing the essentials of his wife while in the cooler.

According to a report in The Sunday Times of 5 June, 2016, Lutepo has been having conjugal visits while at Chichiri prison.

However Lutepo has refuted the reports and through his lawyers he has written Times demanding a compensation of K1,000,000,000.

“We do not believe that prisoners have no rights to their reputation. We therefore have instructions to claim from you the sum of One Billion Malawi Kwacha being damages for libel on the footing of aggravated damage” lawyers for the cashgate convict wrote to Sunday Times.

Lutepo claims that the report aim to cast him in bad light and affect his chances of getting a parole or appealing his case.

“We find the publication of your article repugnant to journalistic ethics as Mr. Lutepo was not contacted for his side of the story” added the lawyers.

Lutepo was sentenced to 11 years over his role in the Cashgate scandal. At the time he was being sentenced, it was said that he was disabled.

Advertisement

214 Comments

  1. Ife sitikufuna kuti banja la Mr lutepo lithe ngati muja zinakhalira kwa president Nelson Mandela chifukwa samapasa mupata kundende kuti acheze ndi mkazi wake wine matikizera Mandela.

  2. anthu oipa ngati inu ndiosafunika mudziko anthu opanda chitukuko ongoyang’ana zanu zokha osalabada za anzanu mmesa munkaziesa madolo tiyeni tione udolo wanu kuti ulipati pano mukuchita kulakalaka bonya anthu opanda nzeru

  3. Galu iwe watha ndalama zamisonkho yathu,mamkhwala mkumasowa kuchipatala iwe ana ako akuphuzira kunja kugona pa mkeka wolukidwa ndimijavi.
    Shut-up ur mouth!!

  4. komaso apa tilembe chichewa aliyese amve mvemveve. akuti akufuna 1billion Mtima wakuba. akadalinawo akutchura ndalama zomwe mmasomwake ankaziona ku captal hill. akufuna abeso mwanjira imeneyi bwanji. osanenapo 100 000 koma billion ndimbavadi munthuyi.

  5. Kkkk ndalama ndalama zachani suzivela chisoni wekha ndimene ulili usovatu ife ndie tingoliwuza bomalo kuti lingowonjezelapo zakazo mwina ena atengelepo phunziro malawi wanga pano sakukoma kamba ka anthu ngati inu eish!

  6. Ngati anakwanisa kuba ndalama zankhaninkhani,kungamuvute pati kugona ndi mkazi wake ku ndende,pakuti kundende nakoso ndiye kwawo kwa katangale.

  7. Palibe ndalama zomaononga pa nkhani zopusa ngati izi. Nthandizani anthu ovutika osati nkhumbayi. Kuba eti! Wazolowela kuba iwe!

  8. This issue borders on what is known as DEFAMATION. Lutepo has a right to claim sth from the paper that published this story. Courts do NOT only hear criminal Matters; there is infact a wide range of cases such as tort, contract, constitutional etc. this one falls under tort. as for the amount being claimed, thats sth pple may debate. but its a valid claim from a Legal point of view. Even prisoners have rights. They do not cease to be human by virtue of being in prison

  9. A prisoner has no rights. Rights for what ? Your rights were forfeited .Even if we can call you names you cannot do anything. Mbava ngati inu ofunika death sentence. Matama eti.

  10. Nanga wadya ndani kumenekuku? Nanga wadya ndani zimenezizi? Usakane iwe tavomera…tanena iwe tandiuze….. Ukununkhira …..wadya iwe.. Powered by #Blakjak

  11. all u foolish, all dat u do z bushit, realy au burn u lyk bush, u gat evils i wil cal u bushri, zachamba bax u only steal our makobidi, ofunika fire u all oxatxo holidy,

  12. Zachabe-chabe zapansi pano iziii hmmmm…! mbava zokhazokha kulangana. Enawa nde sakusolora? Ka2ndu akungokwela tsiku ndi tsiku mankhwala akusowa, nde misokho ya2yo ikupita kut?

  13. Musayitaye mbuzi imeneyo ndiposo muyipatse FOYA itchene osati suit ngati ili panyumba pake kapena ngati apita ku Office

  14. Amalawi Tikhala Moyo Ovutika Kamba Kamenewa Apolice Munthu Akaba Ndagwidwa Nakhala Kundende Sayenela Kukhala Musuti Ngati Achoka Kunyumba Yamalamulo Mupatseni Foya Yawhite Mnkaidi Ameneyo Akazake Ndiwakwatila Chifukwa Atopa Mthupi Muyabwa Nyele Zachulukila NgaKhale Akudya Ndalama Zakuba

  15. Tsoka kwa iwe lutepo poti unaba zocheza anzako anaba zambiri koma akulamulilabe sanamangedwe.Pepa nkhaniyo osadandaula nayo poti njala inakupweteka kwambiri poti naweso ndwe mmalawi ngakhale uli mndende komabe uli ndiufula osuna usagwe ulesi onse amene akukutukwana apa ndi aja akutha ndi madzi kumusiku nde ali paululu chimangaso chinapita

  16. Lutepo is talking like this knowing that, he thoroughly washed his propeler and deleted all evidence. otherwise he was suporsed to be examined, if he really climbed his wife kundendeko. next time madam ake akadzabweranso mudzamutengere akaidi ena adzamuthandize kudya katunduyo njala ndi imodzi.

  17. Koma lutepo pantuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuundu wanu pali anthu akulu sunalangidwe eti

  18. mmmmm Lutepo nkhuli ndi ndalama. Iwedi ndiwe mbava koma stranded thief. A lawyer anuwo sakukuthandiza. Ndiye ngati times ingakupatse ndalama zimenezi, iwe upereka 100 trilion kuMtundu wa aMalawi coz mavuto tikukumana nawo ifewa mngosasimbika and u are main prayer to these problems. Vuto lanu aLutepo ndinu opusa, mmangovomera zilizonse mwanamizidwa. Now this ur lawyer wants to get rich pokugwiritsaninso ntchito. nanga olo atakupatsani ndalamazo mukadyera kundendeko? Za mkhutu ukuyankhulazo. We want INFORMATION into the parliament. zopusazi zithe.

  19. Kkkk Ukatibela Zolembela Ndi Zolembela Page Tikakufuxa Umatilipitsa Chimanga Chokazinga ,lero Uziona Ndimaona Ngati Unasintha

  20. How stupid is Lutepo?.Most of the times he sounds as if he is got no brain at all.Whos stupid person is gonna give you that money?.For what proper reason?.What tribe is this man belongs to?.We don’t want such idiots in Malawi you better die,foolish!!!!!!.

  21. Koma olembaso ndizitsilu chowakhudza ndichan munthu akacheza ndimkaziwake basi nyoooo? Aaaaa manyazi mulibe muzizilemba inu nokhamukagonana ndi ndiakazi/amuna anu

  22. Ndikamuona galu ameneyu mtima wanga umawawa havy munthu wakupha anthu wosalakwa chisilu chamunthu ndalama yachani osamangonyengana bwanji zopusa basi.

  23. Kodi mesa anasiya kuyenda ndikuyankhula munthuyu mmene ankamupatsa sentence yake? Mpaka kumamuyendetsa pa wheelchair Kkkkkk koma uyu ndi bulutu bwanji

  24. uwawuze amako akupatse ndalama ukufunayo, iwe chitsilukwete etii ukuwona ngati ife amalawi timakuwonela kukondwa shupiti zako.

  25. Muli ndi nzeru ngati chitete man ngati ineyo modzi wa chinyamata sindimasangalala ndi anthu obera anthu osauka ngati inu kuphunzira kosekuja mukaphunzira zobera anthu osauka BASI pake mai Malawi akuchedwa kutukuka chifukwa cha mbuzi ngati inuyo kadziko kakang’ono kungokhala ndi atsogoleri mbava BASI tikanayenera kutukuka pakale APA zikusiyana chani ndi ulamuliro wazungu omwe john chilebwe akawuona ngati sunalibwino tizingopalasa malo amodzi BASI stupid……………..

  26. Koma guyz a mkuluyi alibe chisoni malawi mmene wachulukilidwa mavutomo ndiye mkumati amupase ndalama mmm komadi zamatsiku otsiliza idzi kukonda ndalama

  27. Iwe wopusa eti ukuwona ngati tikukondwa nazo? Mesa mmene unkadya dalamazo umawona ngati ndiwe sha sha ; bulshit mbuzi ya mwana ; anthu akuvutika mdziko kusowa chakudya ; mankhwala nzipatala iwe ndalama ukungosewelesa ndi zibwenzi kuti chan??? Ndikadayandikana nawe nkadakuswa khofi crc ; mbuzi ya munthu shit!

  28. Lutepo ma plan amenewa bwanji? kodi ukufuna uzingolemerabe wekha basi, ku tchajilatu ndalama mulandu usanakambidwe choncho ungavomeleze kuluza galu iwe. mapulani ako opusawo taleka kaye, nanenso mwina ndione kuzizira iwe ndithu unamuchinda wekha nkaziyo lero ndiye ukukana iwe panyopako kwabasi 1billion yangayo usiyiletu ndisamvenso.

  29. koma ngati sananyengedi amulipire coz olemba ma newspaper adzazoloweraso ngati mmene anazolowerera lutepo kuba misonkho komabe 1 billion yachuluka akanati ka 20 grand kogulira soap adzikachapira white white uja

  30. koma ngati sananyengedi amulipire coz olemba ma newspaper adzazoloweraso ngati mmene anazolowerera lutepo kuba misonkho komabe 1 billion yachuluka akanati ka 20 grand kogulira soap adzikachapira white white uja

  31. koma ngati sananyengedi amulipire coz olemba ma newspaper adzazoloweraso ngati mmene anazolowerera lutepo kuba misonkho komabe 1 billion yachuluka akanati ka 20 grand kogulira soap adzikachapira white white uja

  32. Bwanji bro u want 2 be a comedian kumeneko chani?,Ngati munapeza mwai onyengao ingothozani mulungu cas kutsogoloku akuswani yakumbuyo kumeneko,Chifukwa akazanu akhala atatopa kubweletsa golozi so akhala atapeza kena ka short time,Inu Pheeeee kumeneko mpaka 11 yrs yathuyo ithe,

  33. atangot chi 1billion khatcha ku account ya lutepo pa airtel money kkkk or bushiri sangakupase coz ndiwe mbava.koma man mwasowatu kumatiyenderako matama eti?

  34. koma iwe anakulanga anapita ndithu . kodi 1 billion imaoneka bwanji cos i want my money kkkkkkk usova peter adakwiya akapuku nonse muli mmadzi

  35. Prisoner nayenso ndi munthu, nchifukwa chake ku ndende kumapedzeka conjugal rooms.

  36. akakupatsa udzandiitane uzandichinde nane mwina udzandigaireko 10 million round imodzi yokha.Ndiye mkazi wakoo umamchindira pa wheel chair pompo?

  37. akakupatsa udzandiitane uzandichinde nane mwina udzandigaireko 10 million round imodzi yokha.Ndiye mkazi wakoo umamchindira pa wheel chair pompo?

  38. .. ndalama zake ziti.. wapanga chani chanzeru pa dziko pa to be claiming such a large amount of cash, banging his wi-fi? lol som pple tho!

  39. Tamuvekani whitewhite ameneyu,,,mukuchta kumulora kupha suit chonchi???? chnasolola misonkho yathu chmenechi,,, akut chinafka pakut lunch kumakadyera pa JONNEZ kuchokera ku Malawi pa Ndege tachioneni ukhaula kumeneko

  40. kkkkk 1 billion? kudzolowera ķugwira ndalama zitalizitali ñgati kale eti ñdie ukuiwona ngati 1 billion ndi 1ķwacha tazingosevàni kumeñeko

  41. kkkkkkk uyu ndi galu wakubadi eti. Anakuuza ndani kuti munthu akakulakwira umatchaja wekha chindapusa ndani? Akuwonjezele zaka zina 30 basi uthere kundende komko galu wakuba iwe.

    1. He z right. Mulandu wa defamation tikamapanga claim for damage timanena ndalama yomwe ukufuna. But its not automatic the court decides or either u negotiate out of court

    2. Iyeyo ngati ali uncle ako umuuzeso kuti mapwala ake. Awonjezele wina mlandu kuti alemele akugawileko ndalamazo wamva.

    3. tiwonge anthu ukuwatukwanawa ndiwolemera a ndalama zikuluzikulu ukuwuputawo ndi mulandu.tsamba walembalo ukhoza kudzakhala umboni nawonsotu ali ndi foni ndipo its easy kuti akupeze ndiye man kumaganizira kaye.

Comments are closed.