
Njala yafika posauzana ku Balaka
Anthu ena a midzi ya group village head Kabiyo ku Ulongwe m'boma la Balaka, ati njala yafika posawuzana pomwe ati Chimanga akugula kapu K900 pomwe chigoba K9000. Malinga ndi ulendo omwe Malawi24 inali nawo Lolemba,… ...