Apolisi pa Jenda akukanika kumanga mwana wa amfumu

Anthu a kwa Inkosi Khosolo ku Mzimba adzudzula apolisi a pa Jenda ponena kuti akulephera kumanga bambo wina yemwe anakwatira mwana wazaka 15. Anthu akuganiza kuti apolisi akukanika kumanga bamboyo popeza ndi mwana wa a Inkosi Khosolo. Nkhaniyi inavumbuluka ndi mabungwe womenyera maufulu a ana m’bomali. Mabungwewo anachita chotheka kukamuchotsako mwanayo kubanjako koma chodabwitsa ndichakuti … Continue reading Apolisi pa Jenda akukanika kumanga mwana wa amfumu