Bwalo la ndege la Chileka ligwetsedwa mwezi wa mawa
Bwalo la ndege la Chileka ligwetsedwa mwezi wa mawa kuti pamangidwe lina latsopano. Nduna yoona zamtengatenga Jacob Hara yatsimikiza kuti ntchito yogwetsa bwaloli iyamba mwezi wa mawa. Iwo anati chifukwa chakuti bwaloli lakhalitsa, sipakufunikanso kungolikonza… ...