Musawamvele achule omwe akukuletsani kuyenda – a Matola awuza Chakwera

Nduna yoona zamphavu yamagetsi a Ibrahim Matola awuza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti asamvele achule omwe akufuna kuti a Chakwera asiye kuyendayenda, ndipo a Matola ati dziko lino likuyenda bwino. A Matola amayankhula izi Lolemba pa 6 June ku Golomoti m’boma la Dedza komwe mtsogoleri wa dziko linoyu amakhazikitsa ntchito yapanga mphamvu … Continue reading Musawamvele achule omwe akukuletsani kuyenda – a Matola awuza Chakwera