Kungani tikiti – watelo Chilima

Advertisement

Wachiwili kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima walangiza atsogoleri a mpingo kuti asangodalila pemphero, azichilimika pa zochita zawo.

A Chilima amene anali mlendo olemekezeka pa mwambo wa maphunzilo a utsogoleri pakati pa atsogoleri a mipingo anauza atsogoleriwo kuti pemphero lopanda ntchito ndi lopanda ntchito.

“Pali nkhani ya Mnyamata amene anakhala akupemphela kuti awine bet. Masana ndi madzulo ali Ambuye ndithandizeni ndiwine bet. Anachita kubwela a sisteri kuzamuuza kuti sungapambane ngati sukugula tikiti la bet,” anatelo Chilima.

Advertisement