Mr Jokes apepesa poselewura a Mutharika
M’modzi mwa akatswiri ochita zisudzo mdziko muno Andrea Thonyiwa amene amadziwika ndi dzina loti Mr Jokes, wapepesa kwaotsatira chipani chotsutsa cha DPP kaamba ka kanema yemwe anatulutsa oselewura momwe amayankhulira a Peter Mutharika. Mukanema yemwe… ...