A Nankhumwa ati boma lichotse misonkho pa mafuta a galimoto

Mtsogoleri wotsutsa boma a Kondwani Nankhumwa alangiza boma kuti lichotse ina mwa misonkho yomwe inayikidwa pa mafuta a galimoto ponena kuti ndiyomwe ikupangitsa kuti mafutawa akhale okwera mtengo kwambiri. A Nankhumwa amayankhula izi atayendera ina mwa misika yamumzinda wa Blantyre komwe ati amafuna akaone m’mene kukwera kwa mafuta agalimoto kwakhudzira anthu ochita malonda. Ina mwa … Continue reading A Nankhumwa ati boma lichotse misonkho pa mafuta a galimoto