CDEDI yakonza zionetsero

Limodzi mwa mabungwe omenyera ufulu m'dziko muno la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) lati lipangitsa zionetsero sabata lamawa kaamba kakunyalanyaza kwa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pa nkhani zofunika. Malingana… ...