
Kulibe za CAF kwa nyerere, pezani zina zochita basi
Aiopela kutali. Olo asanaugunde mpira ndi komwe azitaya. Za CAF zija sanali maloto koma zilubwe. Pano mukamuona mzanu wa nyerere, musayambitse ya CAF mudana, ingokambani ya Super League. Masiku atangotsala pang'ono kuti nyerere zikaponde ku… ...