Wife of Wanderers defender Namwera dies


Takondwa Jambo Namwera

Mighty Be Forward Wanderers long serving defender Foster Namwera has lost his wife.

Takondwa Jambo Namwera
Takondwa Jambo Namwera : No more

According to information sourced by this publication, Namwera’s wife Takondwa Jambo Namwera has passed on today.

The 32-year-old was until her death working for National Bank of Malawi in Blantyre. Meanwhile, former Wanderers defender Moses Chavula has condoled his ex-teammate.

“My heartfelt condolence to you Foster for the loss of your wife, may the good Lord comfort you in this trying times and let the soul of Takondwa rest in peace,” Chavula wrote on Facebook.

100 thoughts on “Wife of Wanderers defender Namwera dies

 1. May her Saul rest in peace and may Almighty God comfort you my brother from another mother

 2. Ine ndikukudabwani inu anthu amene mukupanga like uthenga wa chisoniwu! Munthutu ukapanga like chinthu ndiye kuti chinthucho wachikonda kapena kuti chakusangalasa! Ndiye inu zoona kumwalira kwa mkazi wa mzanu kukukusangalasani???

  1. As long as fb likes are concerned mean that you have noted the issue, you’ve seen it. If you like something on fb, it doesnt mean that you are really happy with it, rather it shows you have got it, you have seen it, you have noted it.

  2. A Ching’amba ife ngendeyo sikweni kweni komano kupanga like chinthu ndiye kuti mwachikonda basi olo tingalisinthe tanthauzolo motani kumano sibwino kupanga like uthenga wa maliro thus all

  3. Ooooh koma debate imeneyinso ndiye yachematu! Kaya kungoti kumvesesa ndikovuta! Komano apa tingoti technology vs chikhalidwe! Komano pa chikhalidwe chathu ife a Malawi palibepo amene amasangalara ndi maliro ndiye chikhalidwe cha chizungu chomapanga like mauthenga a maliro ndikuonadi ngati ndi ife a Malawi ndiyosagwira

  4. Ine ndimaona ngati like ndiye kuti chinthucho chatisangalasa ndiye ayi mwandiphunzisa basi kuti ngati tapanga like ndiye kuti tikumva #chisoni! Ubwino wake kuphunzira si m’class mokha

  5. PALI react amwene

   React pamakhala love, like , sad Ndi wow.

   Ndiye enafe timadina sad but still it pops up on a like button

  6. Like amathandauza mosiyana it means wawerenga uthenga..or zomwe ziri pauthengazo zakusangalasa …. don’t say osapanga like

 3. Ooh So sorry may Her Soul Rest in peace. Ambuye odziwa kutonthoza Apukute misonzi ya Achibale onse. Timakhulupilila kuti kwa okhulupilila MULUNGU Imfa simathelo Amoyo koma chiyambi Chamoyo wonawo. Monga nyimbo imanena kuti bola tikachita bwino tikaonananso moyo winawo.

 4. Mmm Iz Ndy Zovetsa Cison Kubanja Kwa Infe Nyelere Tingoti Ause Nd Peac.By Danger P Supoter Wamkulu Wa Noma.

  1. Vuto Lili Pa Fb Zingotolera Ndimbuli Zomwe. Vuto Sukulu Ndchamba Ukasuta Chija Mmmmm Sizizimalowa Akamaphuzisa Umaganiza Chamba Bas.Kapitirize Night Xool Mwna Unakati Uzimvesa Bwno English

Comments are closed.