A new report says Malawians will re-elect President Peter Mutharika during the 2019 elections.
The report released by United Kingdom-based Economist Intelligence Unit (EIU) says Mutharika and the Democratic Progressive Party (DPP) will get a narrow win ahead of main contender Lazarus Chakwera of Malawi Congress Party (MCP).
According to EIU, Mutharika’s popularity in the populous Southern Region will see him getting re-elected regardless of whether the electoral system used in the polls is the current one or the 50+1 percent system.
“Amending the electoral process so that the presidential candidates have to win an absolute majority may happen, but even if it does, we still expect Mr Mutharika, who has announced his intentions to stand for re-election, to win,” says the report.
However, MCP deputy spokesperson Ezekiel Ching’óma noted that the EIU report mentions a divided opposition and continued internal conflict in MCP as some of the conditions for a DPP victory.
According to Ching’oma, this shows that the opposition party will win the 2019 elections if the conflicts are resolved and DPP fails to end corruption as well as the economic hardships Malawians are facing.
But government spokesperson Nicholas Dausi agreed with the EIU saying the ruling party is working on its weaknesses.
EIU which is a member of The Economist Group has on many occasions made wrong predictions.
Before the 2014 elections, the think-tank tipped the then president Joyce Banda to win the elections but she lost.
The intelligence unit has also on several occasions failed to correctly predict election outcomes in Zambia while in America the EIU said Hillary Clinton would win the 2016 polls but she ended up losing.
No doubt about that, the opposition will remains like that because they chose to be like that.
SADZAVOTA ANTHU AKU UK AMENEO MABODZA
DPP iwinadi. Kumwera anthu ndi ambiri. Chigawo chapakati sangafikire Kumwera. Kumpoto ndi kosadalirika. Ikangotengako 30% basi yawina
tatopa ndi ma professors kuti azilamulila dziko la Malawi. ka EIU ka Dpp kanuko ku Thyolo konko osati kuno ku Mpoto
DPP singawine ndithu.Mulungu sangalole.
That is wat we are expecting from ur great leader
Vincent Wandale as running mate
Foolish
A chakwera azalamulira 2024 bc
Kkkk iai neba usathawe pajatu umati mcp ndiyomwe itazawine masankho,ndiye pano ukuti zamasankho akudziwa ndi Mulungu?kk
DPP bomaaaaa razalo wanuyo azingokhala leader of opposition basi
Kwawo kumweko ku nthyoloko simalawi monse ine panja ndinalosera kuti azamwine ndi CHAKWERA pakana lero ndi kuti CHAKWERA adzawine dzinayakhulindwa kale mu 2008 mamwene mulungu amayankhulila dziko lino
In your dream!
Chisankho chili ndi a Malawi osati nzungu mphuno ili phsyuuuu alosele za zisankho zakumalawi kuno ayi. EIU keep your UK and leave Malawi for Malawians to decide what’s good for them. Komanso inu a Malawi 27 kaya mukuti 24 mumakonda kulankhula zopanda pake, kodi mulibe chanzelu chokuti mungakambe choti chipindulile a Malawi???
#100%.FACT
Dpp ndi diluu Boma iloooo
Tiona
Ine nde mzayamba kuvota …..ndikazaona kuti presdent yemwe anasankhidwa wakwanilisa zomwe analonjeza ,,i shall vote for his next term,,,kwa ineyo presdent azakwanilise izi..1.azakhale presdent wadziko osati chigawo chadziko,2.azathese ma blackout amenewa,3.azathese katangale,4.azakwanilise green belt,5.Azaonesese kuti maphuziro akuyenda bwino pa malawi pano,6azakhale ozindikira kuti police ndi aphuzitsi ndi anthu oyenela kulandira ndalama munthawi yake
Tikamenyerana kumec komweko akazangoti DPP yawina pakana masayo azaziwa chomwe wapitira mbendera
Sazaimatu uyuuuu ndiye akawinila kuti?
Zitsiru Zonama Azidyetsa Mabanzi, Komanso Amalawi Muziwe Kuti Akufuna akazabelaso Masankho Tizizati Zadusa Mu Kafukufuku. Mcp Boma
Ngakhale adzawine koma ine singamuvotere.Olo mundinyoze ena inu amene mumatha kunyoza inu…koma ine sindingamuvoterebe basi.Eee,iyaaa.I can’t vote for him.
i cant vote for this so called dpp nomatter what,now pple hav eyes which can even see far,zakuthyolo kwanu kumeneko though akuthyoloso ambiri sakumumufuna munthu okalambayo…Kkkkkkv
Mpusitseni azigona ovota ndife !!
Ovota ndi amalawi osati ma British .
Okey!
Nde tsokatu
I agree with that report 100%,pano anthu azindikila kuti mcp ilibe utsogoleri opindulira a Malawi kwao nkusutsa basi.
Umunthu wanu uli kuti??
Dpp 2019 boma…..!!!!
Ochakwela onkati boma likunama zoti lagula ma genset,APM analetsa kuti chimanga chisatuluke ochakwela anasutsa lero siiz
DPP BOMA BASI U LIKE IT OR NOT
DPP more fire…..!!!!!
Kkkkkkk nde boma lakuthyolotu paulendo basi
Except me. I can’t vote for an 81yr granny. My foot!!!!
To be honest we don’t need ur vote at all anamalila inu tizakuvaniso mukuti akubelani
Zoberazo amakunamizirani? Ulemu Msungama simunamubere mpaka munakawotcha ma vote ku MEC pokana kuchita manyazi ndi recount. Regardless any political party affiliation Moya, ine sindingavotere nkhalamba at my Youthful age or atandithira doom nkamwa.
Zivute zitani ife a Malawi tili pambuyo pa Peter……….. DPP woooooo!!!!!!!! Malawi woooooo!!!!!! Boma iloooo!!!!!! Zamuwawa akagwele okooo!!!
True DPP idzawina,anthu ena anayambira 2009 mpaka pano amangoti DPP singawine,mukhala choncho
Stupt with Mr Black out.
Osamabisa koma kumanena chilungamo mmmmmmm kumanena zoona zokhazokha ndani asaona iiiyah
PLAS CONGRAS EIU GOOD IDEA
Eti Dpp? Ndiyekuti chani? Tatopa ndikulamulidwa ndi anthu opanda chisoni a Malawi tikuvutika, chonsecho iwo akuzilemetsa okha come 2019 Malawi will decide!!!!
EIU, TRUE STORY
Fake news
Mavuto onsewa tikumanawowa ndiye mulungu watiphwisiratu
Kwacha ndidiru osakamba zambiri MCP ndiboma wapitala uko nyasi tatopa nazo agalu inu
Mukamakamba za pitala mselu kukhosi kaya Amaudziwa mseluwo?
With the coming in of this national ID S and sim card mass registration,he will.
Pamenepa Wa Ang’ona Wa Psya Tima, Dpp Woyeeeeee!!!!
Hahahahahahajahahahahahahahahahahhahaa☺ koma sewero linali..?
Sindingavotela tambala kuopa angazandigoneke ndi njala atadya chimanga changa chomwe ndayanika pamphasa UDF izandigonesa ndi njala munda wanga yonse wachimanga muli yellow DPP is my vote osusa ipsa mtima !!!
Opposite is true
Mcp must wake up as this a wake up call!
Kuthyolo konko zimenezo
kuthyoloko nkomwe dpp imawinira ma elections. so wait and see, Henry jere. its about the developments that will count on the day. iwe you hate dpp but the masses dont.specially the rural masses who vote.
kodi kale loseri zitukukozo zidali kut? ndiye tsopano waona kuti zisankho zayandikila ndiye kumatangwanika ndi tizitukuko apa ndi apo cholinga anthu apuse ndizimenezi?
He has walked the talk seriously
AZAVOTE NDI MBC CRUEL
Votsek
Anthu amene mukumat 2019 dpp boma ndamene mukupangitsa kut mvula isagwe moenera .Mulungu sakukuoneran kukondwa.mcp woyeee
20100 neba BOMAAAAAAAAA!!!
EIU Mudzavote ndinu?ngati akudyetsani chisikono apiatalawo kuti mutipusitse izo ndiye zanu amalawi pano tinachenjela singatinamizeso,DPP yatibela mokwana,2019 ndinthawi yoti idzave kuning’ina.MBAVA IZI
I doubt the credibility of EIU cause this is a nonsensical report.
EIU always favours PETER & DPP.Do you remember last year after afrobarometer results,a week later this same group of DPP MALAWIANS based in UK also predicted this same fake DPP victory….
Owina wina awo or ena akuwuwawuwa APM bomaa 2019
mwayambapo agalu inu
Maganizo atianthu tochepa chabetu ameneo koma chilungamo cha nkhani ya zisankho akuchidziwa ndi MULUNGU
Zabodza zanuzo ayi nokha owina simukumuona?
akadati lazalo adzawina bwezi mutasangalara kwambiri
Nanga Afrobarometer Imavotanso Ku Malawi?Zamanyi!Poti Awa Anena Za Peter Mukukana?Peter Mutharika Ndi Bomaso Kale.
A peter omwewo vote yanga mwatenga basi
kupusaa
Dpp boma
Chiyambire kafukufuku wawo bungwe limene palibe chimene analosela cholondola, kuyamba ndi kwathu konkuno 2014 analosela kuti JB awina chisankho komano zamanyazi anambwita, ku America chimodzimodzi amati Hilary awina zimene sizinachitike, ku Zambia anagwa nayo. Choncho apa akamati Pitala akuwina 2019 ndi bodza lankunkhuza.
Chiyambire kafukufuku wawo bungwe limene palibe chimene analosela cholondola, kuyamba ndi kwathu konkuno 2014 analosela kuti JB awina chisankho komano zamanyazi anambwita, ku America chimodzimodzi amati Hilary awina zimene sizinachitike, ku Zambia anagwa nayo. Choncho apa akamati Pitala akuwina 2019 ndi bodza lankunkhuza.
Wait and see 2019 wina azarila.oyamba ndi iyeyo.
mwayamba akadzabela muzizathawila ku report lanulo zaziiii 2019 owina sakudziwika
Vot Ili 2019 Wayamba Kale Kunama Zot Pitala Wakoyo Watikola Ukuzidziwa Koma?
ine ayi
Maloto a chumba
mukufuna a mcp azitani mukamakamba zimenezo.tiyeni tidikile 2019 sitina fike musakhale ngati simukuziwa ife amalawi timatha kusitha maganizo thawi iliyonse or muthu kungotipasa k20 timakamuvotela.Ndiye no phuma thawi ilipo.
They lied n 2014 ,they tipped JB to win…..wul c
aparty of developmemts Dpp
It’s a shame you think this way
Ndiye ndife dzitsilu2 mpaka kuvotelaso pitala??? Hahaha shameeeeee
MCP DESERVE TO OPPOSE those 31 yrs were enough ine or atandimwetse doom sindingavotere tambala
Tilipo wo vote .dpp boma!.
Ya Chakwela Azipsa Mtima
Mmm Ndakayika Munthu Wanzeru Zake Mpaka Kuvotera Peter?
Mmm Ndakayika Munthu Wanzeru Zake Mpaka Kuvotera Peter?
Aaaa…Koma Inu Mukavota Ndinu?Tibadikira Bwaa…Osati Zanuzo.Ok Popeza Ndimaganizo Sitimaletsa.
My vote DPP
boma ilo, iwe ndiye ukhalira kutsutsa komweko.
dpp ndi boma bas
dpp ndi boma bas
Kodi a EIU amavotanso ku Malawi?? Zamanyi basi!!!!
Abodza Awa siomwewa ananena kuti joice banda adzawina 2014
Maloto achumba amenewo
Akavota NDA ambuyanu