The rivalry between Be Forward Wanderers and Nyasa Big Bullets has gottten more exciting after a Wanderers official aimed a jibe at Bullets.
Nomads Gift Mkandawire said his side will not be traveling by bus in the CAF Champions League competition.
The Nomads Chairman was taunting Bullets for traveling by bus enroute to Comoros Island in 2014 for their Champions League assignment against Fomboni FC.
“We will be traveling by air, not by bus. We are not like them, we have very good sponsors who have assured us that everything will just be fine as we are aiming to conquer Africa.
“We are ready for Africa. We have a very good squad and we are not in the competition to just compete but rather to participate,” he told the local media.
Bullets had to travel to Tanzania on their way to Comoros by bus due to financial constraints under Kondi Msungama led administration committee.
However, despite the hardships, the people’s team were able to get a result before completing the mission at Kamuzu Stadium.
In 2004, Bullets made the nation proud when they reached the group stages of the competition, where teams such as Orlando Pirates, Club SC Villa, Zanaco FC and many more were put to the sword by the Blantyre based giants.
More fire, more fire
kkkk moto kuti buuuu wanderers pachiongolelo
Inu anoma musachite mwano ndi matama ngati mwamenya kale mpira ndipo mwawina,ma team mukukambawo mwawadziwa chifukwa cha Bullets mwachidule ndingot Bullets imayamba zinthu mateam enawo amatsatira oce a BB fan always BB fan it is in our blood kalawenikoni
Komasotu akuti noma ilibe masitaz omenya bwino mpila pano tikambapa neba wabwelekamapuleya kumatimuena atulo tofanato akuti akamenye kafu kuyimila wandalazikkkkk
All de best neba as u try to make a name international like bb. good ambition kma bb not ur level
Nde Ife titani? Mxiew,,,
A Wandrers onse asanyade poti akumwa mkaka lero koma adziwe kuti tinayamba ndife kumwa mkaka umeneo kuwapatsa mwayi chisakhare chifukwa
Talawanikoni ndegeyo ife tatopanayo ,
Ingovomerezan abulets palibe nkhani yomatukwana apa ndkuzwa ndzowawisadi mtma wosayiza noma nonse mupsa mtma .zakuvutan Ingovomerezan azanu akachta chabwino alakwisa. Noma forward ever never back ward asafuna asiye akakolope nyanja kapena akasamuse mulanje mountain napite Kukaika ku chitipa. God if says yes bullets can’t say no .
Kkk…. Koma matama amenewa muona pothera ndithu
Kodi Bro Mumasapota Team Iti M’malawi Muno? Hav Gud 9t.
Kkkkkkkk koma neba ndiye ukumva kuwawa kutha zamkamwa choncho?
Inayamba ndi Bullets kuyenda m’malele, nayoso idamenyapo CAF, otherwise gud luck neba.
Mwalowa Caf cholinga chongofuna kukwela ndege or..? Caf yabooka chaka chinotu.. Nyerere yalephela kugonjetsa Nyasa BiG Bullets, Silver Strikers, Civo etc lero mkumang’amba kukamwa kuti iri ndi best squad? Kkkkkkkkk Kungolowela chipsela mtima coz Nyasa BiG Bullets imatchukanso ndi Caf? No wonder pa ulendowu mwasankha kumakalimbisana mtima ndi uyu ali #.. chani mu Super League? Zabwino zonse..!
Man ma games akuno ma player amadziwana nde kamakidwe ka mpira nkosiyana ndi faz yot sakudziwana nayo,Ichita bwino
simungatiyambanise ife tinayambana kale timawalilana ndiye caf ya 2017-18 kuno ku MALAWI kuchoka timu yolemela kwambili otsutsa akhale noma more fire!
tisakamve kuti wina anabibidwa kumene mupitako iyaaa !
Shaaa awa NDE ndi matama. NDE muikwanitsa? Kkkkkk osangogula bus ya bwino bwanji?
Tikuonani matama caf sizaphanda2
They will be wandering by air haha
Your Right Fredric Kazembe!Ooo Dont Just Think For Us Concitrate Well.Timakunyadira Neba.
For the first time…eeeish
Nthawi ndi nyengo Noma
Mau oti we will be travelling by air abwerapo chifukwa a bullets amati azatibwereka bus yawo anagula pa APL Ku kwacha kuti tiziyendera ndiye Noma imayankha. Osati chilichonse tikupanga compare ndi bullets, bulletsyo ikumenya CAF?? Pa nthawiyi tisiyeni ma size athu ndi TP Mazembe , All hiral ndi ena oterowo si za mwana kumangozungulira mMalawi ayi
Auzeee
Zikuonetsa kuti chimene mumafuna ndikukwera ndege osati kukamenye mpira koma mupemphere kuti ndegeyo isakatere chifukwa ma team achalira kukakuumbuzani
Yenda bwino ukazione wenkha
we don’t have bb at caf, so stop talking shit about them. we have the enyimbas, etoit de sahels and others of this world, you will face them out there.
Manoma yambilatuni kupanga pulakatesi chingelezi , osakapanga ngati ujayu amayankhula chichewa kujoni Uja ,akufunsidwa mu chizungu .mpaka kumanjenjemela kuti ayankhule .kaya ameneuja ndi wa timu yanji kaya ?
Ndikutha kumuona neba akusapota obwela kuti ati tibule ,koma tithananazo tokha ,pajatu noma ma champs mono munyasalande .
Mabi akale sanunkha,nenani zapano osati za makezana .ndipo noma ikuona kuchedwa kuti drow ichitike tione kuti tizakumana ndi ndani,ndipo timukonzekele mogwilizana ndi saizi yake .
maso anu ayang’ane kumene mukupita coz bb kulibe kumeneko
Zoona man am a noman
After kuika Norplant ya 13yrs mwapeza mwana mwayamba chipongwe samatero mudzatipeza
This is CAF kumakakodza ku toilet not pa goalpost!
Mukabwela mmamawa omwe!
Tauzadi Ndiye Paja Amakakamira Pa Balaka Ndiye Akapita Ku Drc Zikatani Amakana Pa Bingu Kumafuna Ka Ground Ngati Pa Chinena Kaya
Aaa ka ground ngati pa chinena kkkkkkkkkkkkkkkk
Kumatenga lig komanso kukamenya CAF kuti neba azipsa ntima
Nkhani imeneyi musamaikambe neba angakomoke
hahahaha paja mudatenga ligi munthawi ya nowa kkkkkkkk zilibwino neba umkatichititsa manyaziiiiiiiii.
Go Nomads, compete & not participate,mukundimvetsa kukoma noma 4 life. m
Kulimbana ndi BB you’re waisting time mukafa ndi ntayo ntchito usadagwire
They will travel by air only for 2 trips after those trips Kabaza will be loading
Nyerere ndi nthawi yathu neba cheteee !!!
AFTER CAF, FIFA CLUB CHAMPIONSHIP.
Am a bullets fan koma Noma iyenera kunyada paja since the introduction of WhatsApp and Facebook Nomads will grab Super Leage for first time congrats
Zaka 11 no league. Arsenal ya Ku Malawi
Pitan mukakumane nd tp mazembe nt bullets zimenezons alinazo zambr. Tamapangan za kuchipinda kwan nt bzy wth bullets
Thats our great failure lies , comparison,do they think conquering Africa is just a walk in the park, linda madzi apite tiziti tadala
Bullets won’t be shaken. Msungwana wina anabadwa wakhungu ndipo tsiku lina( at 30yrs) bambo ake anapita naye kwa abusa kokamupempherera ndipo mwachisomo adaona . Pobwerera kwao adakwera min bus koma msewu onse nkhani inali ya mitengo. Ati ankaona mitengo ikuthamanaga. Sitikudabwa nanu anoma coz mwazionera ku ukalamba, ife tinadutsamo kale
Sanje by san b
Iiiiii Kkkk Malawi Wa Nsanjetu Uyu Asaaaa
Paja CAF Imatengera Team Yomwe Ikuchita Bwino Komaso Yomwe Ndi Yandalama, Tsoka Kwa Uyo Anyoza Anzake Akachita Bwino, Neba Upsadi Mtima Sunati.
Neba uyamba kutuluka thovu kukamwa kwakoko thukuta ndi misozi itatha no more bulets
Kalaweni bas
ana wofewa..
Wa NOMA satukwana amangopsesa mtima NEBA kuti BP izikwera kwinaku akutukwana ma phuzo tsoka NEBA!
Osayamika Khala Chete Noma Ndi Noma
Kkkkkkkkk koma wina alira amene zikumuwawa.
That is a whisle from young lad…We have been in that air many times,its ur chance neba ..koma usakatichititseko manyadzi…all the best!!!
Nkhani siyamanyado imene tikufuna. Koma bringing best results bas
Manoma woyeeeeeeeeeeeeeeeee
i like noma
aapapano tione sapota woikonda #Noma izipta komweko kukaonelera team yake..hahahahahahah
BULLETS I LOVE YOU MA SWEETEST CLUB
kuyamba kukwera #Ndege chan more over sizinathekeso zaundo wa Nebayo..#Nebaso wayamba umbuli eti tikusamukilatu ohoooo kkkk
oohh zilichoncho
All the best neba.
Remember its CAF and not against bullets.
If you think bullets every time then Bullets will be your limit.
You cn do more than bullets only if you think beyond it.
Yendani bwino muzatipeza!
Zikomo poti mwavomeleza!
Munayamba mwaonapo mwana akuganiza or kukhala ndi ambition kuposa role model wake?
Kkkkkkkkkkkkkkkk osatheka @ Kipa
Mwana ndi mwana basi hahahahahahahahahahahahahahaha
Ndipo auuze everytme kupanga za bullets ayangane xa caf ka
Wise comment!
adatenga ligi munthawi yanowa kkkkk
Zisakuwaweni asiyeni its their tym
Anthu awa ndawaona amafuna zabwino zikhale zao zokha
Kakomenti kozuna
Sindidaziwone adachezera kuziona pepa neba kt sumayembekezera kt nyerere zingafike apa
Sindidaziwone adachezera kuziona pepa neba kt sumayembekezera kt nyerere zingafike apa
Coment yoveka bwino
Wise men speaks courage
nice one bro respect
Well said..
Ndege mwayamba lero ku kwera. Kkkkkkk
A Bullets sazathekaso ngati Bango,
Mmmmmm ooooo noma
Bullets once participated in this competition bt never made any noise!!!!
Wakwiya ndi mfiti.
We also have been there before many times.We played Zesco, Yanga and so many teams.
False
kod anyani agalu amenewatu mkukhara kwao kulakhura nde ndi 1 koma kukwanilisa zomwe mwalakhura zimakuvutani, osewera anu kwanamiza kt apite ku japan akasewere mpira pano akubwerako chaka chathanso chimozi mozi zimakhara bwanji neba iwe
Inu kwanu ma prayer amawanamiza kt? Bola amanamuzidwa mkukapondakoso ku japani ko nanga anu mkuti anakapondako jerous si umuna man mwava!
Mmmmm koma yah
big fat liar
anoma nonse pamtumbo pamanu mbuzi zamanu kumtumbo ukatelo wina uyankhe mmmm mavuzii amako kapado efusi
Pachintumbo pako iwe ukuyesa ngati angakuope ndani pano
Umbuzi wakuchulukila et?
nyini
Utakwana Chani Mutu Otupao
Unakazimvera chisoni ndi dzina lakolo
Paulo saimone, ndiwe mwana wa hule wamva?
Ndikudabwa, Kodi ndizampira izi?
Kumakhala Anthu oopa Mulungu ,shame on you.
Musadabwe a bullets onse ndi ana obadwira mkachaso palibe chachilendo
Whenever, mukapanga kena kake, maso amangokhala pa Bullets basi. What a shame! Bullets once participated in this competition bt made any noise. Learn to do ur own business silently. Ndi mu CAF mmenemo. Mumaterera
Eyetu bullets ndi team yowopsya kwambiri, ndi imene iwo amati akakhala samapumanayo bwino ndi team ya fuko bullets.
Mwadzindikila lelo zimenezo
Kkkkkk!! Bodza ilo ine mesa ndi aja mukati ife caf sitiidziwa? Kkkkkkkkk! Sitinati pa easy
#But_Made_Any_Noise_indeed., A Timoteyo Timu Yanu Ndiimene Ikusokosera Pa Zaulendo Wa Noma, Ife Eni Ake Tili Pheee! Nyama Yokudya #Noma Iwe Ungolimbana Ndimafupa,, Upse Mtima Zeni*2,
Sure Manoma sure
And in my time as chairman the whole was flown to mzuni to play a semi final match against Moyale and we won
??????????
First of all can u buy a bus like bullets which looks as Real Madrid then talk
This year u have not taken a single cup despite having the best side????????
Sizodabwitsa Paja Ndi Anthu Okonda Kulongolora, Asanayambe Kumenya Koma 2 Munch Talking Kod Bullets Pomwe Imapita Mu Caf Inakambako Zonyogodola Noma? Just Mind Ur Buzinez Ikubwera Thawi Mudzagwetsa Khope Pansi Mutatuluka M’mawa Womwe,,,, Ingopangani Consetrate Za Magame Omwe Mupatsidwe,,,, Bullets Sizachilendo Kusewera Mu Caf Ndikhalidwe Lathu
lig yake ya 15 mitayi?????
Am proud of boys
Bullets idayetsetsa without sponsor but kukwanitsa kupita ku CAF…… Neba anangokhala one year no sponsor koma mpaka kutsala pang’ono kukamenya BDFL….. Mwayi Japanese Zulu tel a
Mbolo zanu manoma nonse muuzane
Eeeee mulungu akukhululukire zomwezi mpakana eeee!!!!
NAWENSO AKUKHULULUKIRE WAMVA
Wina paja ankayenda pa bwato ngati nsozi wa nsomba eti?
zamanyi. nde ife zitikhunzze?
eeeeh koma awaaa ativuta!!!! panathatu 11 yrs,,,, ndipo nka number 6,,,,,,anzanu a 13 Ali pheeee
kkkkkkk komadi ativuta amenewa sankaziwa kuti angatenge league
Paja Bullets ulendo womalizira kulowa Caf anagona panja mdziko laweni
10yrs Itsnt A Joke!! Ndipake Kuyenda Mwamba, Ngakhale Mkazi Akakhala Kuti Samabeleka Kwa Zaka Zambiri Koma Ali Pa Banja Akangotenga Mimba Amanyadila Ngati Mwana Wang’ombe.
Iwe wapsa mtima zenizeni.
Kupsa Mtima Ndi Ziti? Sindisapota Team Yomatenga Ligi Mpaka Kuntha Zaka 10.
Kkkkk Auzen man, kuwina league after ten yrs its not ajoke ndpake ayende mumwamba pamene ife a Bullets tinatopanazo zimenezo komanso sitimalora kutha season popanda chikho.
Kkkkkkkk Tiyenda Mwamba Just Cuz Of Taking Superleague After 10yrs!!!! Lero Mukuzuza Linje Ndi Mzake Ku Japan Nkumati Ali Ku Ma Trials Akukaona Mitundu Ya Ma Shop Ndi Magalimoto….
Kkkkk mulira zenizeni simunati, mpaka muphulika kkkkkkkk.
Wa ku Caf basi neba usova
Palibe Kusova #Jacquline Ife Zanthu Tinachapila Sunlight Pouder, Ukuvutika Ndiwe Neba Ukuti Uyenda Mwamba Cuz Watenga Leaque!!! Ku CAF Pitani Ma Player Tikubwelekani Mwina Zikakuyendeleni Bwino.
Zaka 11 osatenga League eee koma kuli kulela ndiye Noma inatenga kalela wa zaka 11
Gd news probably the best team and club technical Pannel in malawi. warning to some Player of different club in malawi don’t hastate come and Join the plps Choice team inorder to enjoy tolgelther with our players massively.
People’s choice team???? itinso imeneyi????? Sakani dzina lina loti mube… People’s Team forever
Sakudziwa chomwe akunena uyu kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Angolemba poti 4n yake ili ndi FB basi hahahaha Zampira osakwiya Lol
A Wanderers akakhuta amasowa pogeyera muzingowayang’ana chipongwe ayambachi akaputhidwako mamawa omwe atipeza.BULLETS ili pa easy simalambira sponsorship
Tittle no 6 since 1964 kkkkk ikazakwanisa 10 anthu azasegula mumimba koopsa eeee inu not even half yamene tinawinira ife agalatiya mwaona mene imakomera ligi?kkkk anzanu timatenga osapha waudindo ayi ndemukatengaso 2018 wina apiteso eshii apalanya inu mmm
Akulu ndinu mtundu wanji wa anthu?Amati m’mimba kapena mumimba?
Akulu bola uthengawo wakufikani
Ndiye mumaganiza ligiyi ndiyanu nokha kkkkkkk zimasintha mpira muxiutsata not just supporting, kusapota noma mkokoma.
Bola mukuziwa kuti imakhala ngati yatokha mwayamba kulawako musathe mau,remember mukatero kuzatengaso its after 11 yrs again kkkk
Anthu enanu I think kuganiza kwanu mumagwirisa ntchito chobibira
Talk as a human being imfa ndiyowawa APA ndipa air multi ndiumboni ndiimfa yawaudindoyo? Kuchenjera kwina umagwa nako mmbuna simunayankhule bwino
Official Opusa Noma Ikhala Yoyamba Kutero Kno Ku Mw
Kod Mukuona Ngati Kukhala Ndindege Ndichani? Mufufuze Za Kk 11-11 after that muzapeza kvi ndi umbuli chabe.mwina simuziwa kuti BB inakapangapo ma training ku MANGALANDE.ndipo popita kumeneko amakwera ndege kkkkk MBUTUMWA za manoma
upitenso ku sukulu sizikumvema zomwe walembaz
Wapsya mtima? nde upsye mtima zenizeni iyi ndi noma ase
MUWUZENI ZOONA AMENEYO.MWINA APEZE MUNTHU KUTI AZIMULEMBELA AMENEYO
Ameneyidi tu
Ameneyidi tu
Kkkk odi uko NOMA Iduseeee
kodi ku Nigeria Tunisia Ethiopia UK bullets inkayenda pa bus? ??????
Enyimba 9 mkhumba fc 0
Bullets olo itamakwera ngolo sitisamara bolani ku wina basi
That’s nice
Chitimu mbambande.
Zonsezo zilibe kanthu chimene ife tikufuna ndiku wina basi
Ife nde bus tilibe?
Zawo izo ife tili ndi bus
Mwapsa mtima?
Bwana kupsa zomwezi?