Mlaka’s suit hijacks Facebook

A suit by musician and pastor Mlaka Maliro has become a Facebook sensation in Malawi.

Mlaka Maliro
Pastor Mlaka Maliro’ suit has hijacked Facebook.

In viral photos, Pastor Mlaka Maliro of the Enlightened Gathering Church whose leader is Shepherd Bushiri can be seen in Church in which in one photo he is praying for a woman lying on the floor.

However, it is not his healing powers that has the attention of Malawians. It is his style of dressing.

“Your dressing is amazing,” wrote a person on the post shared by Mlaka Maliro in which he is in the suit.

“Someone to wrap fish in that foil please,” another person said.

However some people defended the dressing.

Advertisement

100 Comments

 1. iweso ndiwe kape wamakapeet! just walk 100m from where ur uone dressing kapena sunaendepo kupita madera ena,how old are u it dosnt make any sence 2 malawians i think u must go back 2 xool ur not well matured in mind

 2. Mbuz Za 24 Ngati Mwatopa Kupeleka Tiziduswa Tankhani Zanu Mumapelekati Just Sit Down, U Will Never Receive My Complaint.Mwasowa Zolemba Eti? Mumati Aziyenda Maliseche M’lakayo?

 3. kodi mufuna mutanthawuze chani….munthu asavale bwino walakwitsa ikhale nkhani poti ku banja kwanu aliese amangovala zimajekete za magogo za chikalekale…..inuso kaguleni yanu tikuoneni pa facebook….umphawi basi ntchito kumangoweruza azanu basi….zopusaaaa!!

  1. Amene anawasankha mndani? Mulungu sanasankhe iwo,chingakhale ansembe onse muli nawowo sanawasankha,azibusa onse muli nao wo amapita ku college kukaphunzira kuti adzapanga bwanji ndalama,amalandilatu zawo iwo aja ngati simudziwa,wa mulungu bwenzi akugwira yamahala apeze china chochita tidzikumana saturday kaya sunday sizoti mpaka ku college,or poti mdala wanga ndi m’busa akandiyikira kumbuyo ndikayamba,alipo wena amene ndimayitanidwe awo koma mwai sanaupeze chiphanzi,mudzifufuza amatengera kudziwana izi sikuti mulungu anawasankha ayi koma kudya ndalkama mudzina la Mulungu. Werengani YEREMIYA 23v 9-40 especially v 16 akuti ” Yehova wa makamu atero,Musamvere mau a aneneri amene anenera kwa inu;akuphunzitsani zachabe,anena masomphenya a mtima wao(Miracle money) si am’kamwa mwa Yehova# Ndipo ma Prophets awa kudzanso azibusa kaya ansembe awa ali amodzi mwa iwo akunga opembedza amene YESAYA mneneri anawakamba pa Yesaya 29 v13 Ndipo Ambuye anati,Popeza anthu awa ayandikira ndi Ine ndi m’kamwa mwao,nandilemekeza ndi milomo yao,koma mtima wao uli kutari ndi Ine,ndi mantha ao akundiopa Ine,ndi lamulo la anthu analiphunzira# Now muone masiku awa kuyambira azibusa ndi achristu ambiri ku church akuesa ngati kunsikano,mwachizolowezi koma cholinga cheni cheni chomwe munthu amapitira ku church chinayiwalika,nchifukw chake mudzaona akuchoka ku church zochita zake ngati anali kumphwando. Read Luka 21 v5 mpaka 19.

  2. V ya Luka ndi ya ma Prophets alero wa ndi nthawi tiliyi, awa ndi atumiki a Lucifer ndi nzawo yemweyo Bushiri akuwakopawo,chuma cho chikuchoka ku Illuminat brothehood. Watch out tili mu nthawi yomwe mbuye ananenayo,Nkhondo zikuchitika,anthu akudana okha okha Xeno,Boko, mnyamar and USA anthu akudana ,miliri ku USA,kusefukira kwa madzi,nkhani za moto,maiko wena njala,madzi amene kuvuta,zambiri zikuchitika tili nthawi yo

  3. Iwe Rabson,chomwe walakwa mlaka yo ufunse iwo ayika nkhaniyo ine ndikungolongosola za aneneri amasiku anowa kuti ambiri aiwo ali achinyengo sikuti ali kupanga izi mumdzina la Yesu wamoyo koma mpongobisalira,and aneneri ake amulungu mudzawadzwa nzochitika zawo I know simungakhulupilire koma Shadreck Wame amene uja anali wamayitanidwe and pokhala iye munthu nkuthekanso amalakwa munzina akoma sanafanane nao ma Prophets atcukawa muzochita zawo mngakhale ulaliki wake unali wina ndithu

  4. Sindikukamba za mavalidwe kapena kupanga nsanje ndi Mlaka Mr Rabson,nchifukwa chake nkovuta kuti mukalowe kumwamba,mukuyang’ana zinthu za dziko ili,nchifukwa chake bukhu la Mlaliki anti zonse zachabe chabe

 4. Why not write PAC Vigil postponded today due to government well reaction on50+1 bill.
  Mwalemba za clothing ku Joni shhhaaaaah

 5. Mau akuti masiku otsiriza mulungu adzazutsa miyala kuti imutumikire chifukwa choti inu mukukana.miyala yayamba kudzuka mwayambanso kudabwa,agalatiya enieni

 6. kusowa zolemba eti,,leave mlaka alone,,asatchene? inu munayamba mwalembapo nkhani ku mwavala mavwende kut ife tidziwe?

 7. I can’t get any point from the story, infact I don’t see anything wrong with his dressing..
  Mwina anzanganu..
  I can only observe that nsanje yakula kwambiri among Malawians.. just bcz ndiwa ECG basi zonena mbwee..

  My advice is: limbikirani ntchito mwina nanu nkuzavalako mphasha zovaya ngati zimenezo anthu nkuzamasirila. Than wasting your time…

  NOTE: I’m not a fan of ECG either Mlaka as a pastor.

 8. Nde zamatsiku otsiridza zija zimenezo. Instead of kufunafuna Ufumu wakumwamba amalawi agundika kusilira suit ndi chuma cha pansi pano yoti izaola, izadibwa ndi njenjete. Wide is the gate and broad is the road that leads to destruction, and many enter through it. (Matthew 7:13) Akuchita kuyenda ndi mdidi ulundo kuchionongeko 😀 POOR SOULS kuonongeka for lack of Knowledge.

  1. Ma komenti a anthu akudziko sasowa, zokomenta zawo zimakhala zachidsikodziko eee, tiyeni kaziyendani ulendo wokakukuta manowo. Ife sitinluenda nawo ulendo waku midimawo.

  1. Iwenso Mboliyako Owen ine ndi Mfana olamula makape inutu Mulhomwe ozindikila osati Mtumbuka ngati iwe wamva nonse sindimakuopaniso muuzane

  2. Tsono olemba comment yofoira ndiotukwana mwasiyana chani apa? A fool answered in a foolish way makes the one answering a fool as well. Siine mtumbuka koma I have no reason kunyoza atumbuka.

Comments are closed.