Area 24 women sentenced to four years

102

The Lilongwe Senior Resident Magistrate court has sentenced three Area 24 women to four years in jail each.

Lilongwe Area 24

Jailed

The three women, Flora Chinguwo, Nora Chatsika and Gertrude Banda were convicted on Monday of committing an act intended to cause grievous harm and insulting the modesty of a woman.

They were arrested in October this year for assaulting another woman whom they accused of being in an affair with one of the women’s husband.
The women were captured beating up the victim.

The shocking video clip which went viral on social media attracted people`s attention and concerned Malawians called on police to quickly intervene.

Senior Resident Magistrate Paul Chiotcha was initially expected to deliver his judgment on Tuesday but sentencing was adjourned to Thursday due to power outages as the ruling was not ready by the time the magistrate was supposed to read it.

Share.

102 Comments

 1. man geor mwafotokoza bho ,ndiye akt ma banja awoso atha? ndingodikila 4 yo akazatuluka ndizasakhepo modzi ihope kt azakhala atasitha mwakhalidwe coz ndende sinamayi

 2. Zaka zachepa,mmene ananzuzira nzawo kulephera kupepesa mfiti zimenezi,zinakakhala 10 ,enawo nde afera zaeni kkkkkk,pali inepa nzikamenya chibwenzi cha mwamunake wamzanga??? Kuzunzitsa ana zaziiii..boarding yabwino azimayi oyipa inu ,,,,,

 3. Ambuye Apanga Njira Kugolimbika Kupephera,mavuto Ena Amabwera Kut Tizankhale Mboni Yeniyeni Koma Pephero Ndi Chida, Zimafuna Osalira Mulungu Amava Ndipephero Nanga Bwanj? Paulo Ndi Sillah Anapephera Ndipo Zinseko Zandende Zinaseguka.#YESAYA,61vs1 pali mau.

 4. Kwa amene munaonapo ka video ka dzigawenga dzimenedzi 4yrs dzachepa kwambiri ndikanakonda ndzikanakhara 8 kuti ena omwe ali ndimchitidwe onunkhawu atengerepo phunziro

 5. Chgamulo Chachepa Ichi, Awawa Amafunika 10 Years kupta mtsogolo, anthu anj osava kupepesa kwanzao? mzmai nzao adamuzuza koooooopsya . ndpo ndakaika ngat azmaiwa ali ndi uzimu

 6. Ndadandaula kwambiri zaka zo zachepa kwambiri …..if u look what those women did to her fellow woman was very disgusting and inhuman……6 yrs could have bin a good lesson …not talk of punishment… coz those ladies punished the woman…..u could have heard the vidio how the woman humbled her self ….asking for mercy to her fellow Malawians… but Na…. they are threat to the society ….they deserve 7 yrs …..With hard labour!

 7. Four years is too mach related nd mulanduwu,,,,nanga bank robbery nde ampasa life sentence,,,,,sinthan malamulo constitution ikonzen we are living in a different world now plis osangolimbana nd chinthu chimodz modz ku Parliament mukayamba section 65 ikhale yomweo pano electoral reforms tivina yomweo mpaka kutopa akat land bill osaganiza zina ayi,,,,,I feel bad for my malaw nkana oba njinga ndiwagalimoto zilango sizimasiyana malamulo ankalamba ngat ma judge akumalawi

 8. Apolisi ndamene adapereka chilango chabwino, bkz if those women tortured and strip naked somebody and posted the video, they also have to experience the test of their own medicine

 9. Enanu ndiye mwafera chinzanu. Nanga kunyenga kwa mwamuna wanzanu inu zimakukuzani zichani kut mpakana mukalowerere kuthandiza kumumenya winayo. Taonani mukuika ana anu pamavutono kamba kofuna kudziwika. Mmmmmm tamafunsan azimuna anu pa nkhani zinazi kut akuunikireni.

 10. kwa ineyo ndikuona ngati judge yemwe wagamula mulandu umenewu wadyapo kena kake mene munthu uja anamuzunzila nzimai nzao uja kuyetsetsa kupepetsa osamumvela chonchija chigamulo chake kukakhala chimenechi?

 11. Choipa sitigonjetsa ndichoipa, apapa zaonekelatu kuti munthu umakolola zomwe udafesa, komanso ndigwilizane ndakulu ena ake my comment yawo kuti Satana samasangalala akamaona uli pa Mtendele, nde pamenepa mwapindulanji? Ndikumva nanu chisoni kwambiri chifukwa nkhani yomwe mwalowela sinkhani yokuti mpaka zikanafika pamenepo ndizonthu zokuti mukanakambilana ndimmene ankaonekela mmai nzanu uja amaoneka kuti ankakupepesani kumene kuja kunali kufuna Mtendele koma inu munkafuna kuonesa Ngati madolo, nde vuto limakhala lakuti anthu munafuna kuoneka otchuka muzinthu zosaenela, apa mwabesa Ndalama kwa Lawyer plus kupitanso kundende ayi ndithu zosakhala bwino, munthu usanalakwe umakhala pawekha koma tangoelekeza kuchita xosemphana ndimalamulo eeeeeh umakumana nalo lamulo. Nkhani yaikulu apa tingoti ena atengelepo phunzilo.

 12. kodi ndimayesa sentencing idachitika kale? anapanga appeal?? 4 years azimuna awo adzawapeza atakwatira..kkkkk..anya basi

 13. Hihihi kukasaver MG2 muzamupeza walowelatu pa 4 years ana atatu kkkkkkkk nanuso mukakozeledweko anyapala ali kumaula ndi nkhani zinaa,,kuwaona ma mg1 akeo mbirinya zen zen kkkk tiyeni kaloweni mamunayo adye momasuka ana anjoka
  Inuu kkk

 14. Azimayi amudzi bwanji maka maka mmene kachasu amakomera muja aaaaaaaaa very story to u guyz mc u maphuzo any aja kkkkkkkkkkk ndikubweretselani vemta komweko

 15. Good news.Nde akuti Chaponda amupatsa nzaka zingatino? Tatopa ndikudikira tikufuna kumva Nkhani yoteleyi kwa iyenso?

 16. Mphatso za nzimu woyera ndi kudekha, kuzichepetsa, kuona mtima… Abale anga satana tikuenera kumuzindikira machita chita ake… Apa satana wasangalala poti wakuikani mmavuto ambuye akuyendereni mumudziwe Yesu..

 17. ndie mabanja kutha kukakhalaso kundende,,,, akulu akulu tiyeni tikapanga chiganizo tisanapange action tizilingalilaso kuti kodi zimenezi nkapanga zosatila zikhala zotani

%d bloggers like this: