Joseph Kamwendo targeted by thugs

Advertisement
Be Forward Wanderers

…robbers ransack his car

Be Forward Wanderers midfield maestro Joseph Kamwendo managed to escape a robbery at his residence in Blantyre last night.

However, his vehicle has had parts stolen and windows smashed.

Kamwendo’s car in bad shape.

Pictures circulating this morning show the vehicle in bad shape after the purported attack on him failed.

Reports say he managed to hide while the thieves turned to his car parked outside his house in Chigumula Township.

The thieves have gotten away with a radio, windows and other items that were in the car.

Apparently, it is reported that police have ignited a probe into the matter.

Night robberies are on the upsurge owing to lengthy power blackouts that have rocked Malawi.

Just last weekend Kamwendo extended his popularity among the Nomads family when he scored a screamer that saw Wanderers win 3-2 against a rather resilient Dwangawa United side at Balaka stadium adding to the lifeline of the Tnm super league title chase for the Lali Lubani side.

Advertisement

278 Comments

  1. umbuli ku Malawi kuno wafika pachimake, ndikudziwa kuti zinthuzi zikukambidwa chifukwa chosaphunzira kwa anthu amene mukuti ndimasapota a Bullets amene amubela kamwendo. ndikuona kuti suspect wankulu mukukhala inu amene mukunena kit

  2. #Joze where ever you are, forget about the past and focus for the future, #which_its_the_game_against_mzuni….Neba chala cha #YAWE chikaloza chaloza
    #Noma_pachiwongolero..

  3. Aliyexe ndiwakuba apa enanu ndikuxalulika ngat mukut ndi abullets pot enanu bambo anu ndi a maule nde kut amakaba nawo?my sory goes to kamwendo he is ois amalawian guy’s let s love one another

  4. Oyamba Kubeledwa Kumalawi Kuno Ndikamwendoyo Taona Anthu Akubeledwa Magalimoto Ikhale Galimoto Yolongosoka Akanangobamo Wailes Yokha Bas

  5. Koma Anthu ena zikugwilizana bwanji ndi Bullets zimenezi? Eneya Banda anakhapidwa ali Ku bullets sitinanene kt nda Noma koma poti ndi Kamwendo basi ndi Abullets apanga attack, Ma savage ndinuyo, anthu amabeledwa daily sizachilendo,

  6. Mmmmmmmmmmmm guyz zonenanena kuchuluka mvula ikagwa chilichose chikachitika ndi BB bwanji adaleka kupangidwa robb m’mbuyo mu mudzilakhula bwino kuti mawa tiinene zina shame on u ukulimbana ndi BB

  7. It’s very true we don’t buy the newspaper, we buy the news. Big headlines but shallow contents.

  8. Kkkkkkkk anthu oipa inu!!!!!
    Kwa khama kulibe anthu?
    Koma ndilande ya ana akachaso ngati imene ija,
    Ngati mumafuna kumupha,
    Mwalephera!!!!
    Noma inyamula chikho basi
    Mufune musafune
    Ng’oooooohhhh!!!!!!

  9. AAA KOMA ABALE, TIZITUKANANA TOKHA TOKHA CHONCHI? Page iyi analero lokha aaa landiopsya. Aabalee ndichani chikuchitika mpaka kuyima pachuru kumatukanizana? Nkhani ya galimoto la chekamwendo labeledwa.

  10. Makape masapota anoma,,,player azikakhala kwa KHAMA koma abale,,mmene anayendela iwowo maiko onse aja kumalephera kumanga nyumba kumakhala pa rend.Mayesa kwa Khama ndi kwa masapota anoma.

    Ku SA 3yrs ago Senzo Meyiwa anaphedwa ku chibwenzi wa Orlando pirates,,munamvapo akuti ndi ma rivals awo a Kaizer Chiefs?
    Kodi umbuliwu uzakuthelani.,,,okuba amaona nkhope?.Iye ngati amamwa mowa mwaumbuli mumati asabeledwe

  11. Umboni oyamba mumafuna kumumenyesa duka,mwatuma a Dwangwa kupanga complain nkhani ya Kamwendo.kachitatu mukutiuza kuti munthu oziwika sangakakhale kwa Akhama,mukufuna kuthandauza chani??.Anthu ena akhala kwa akhama ndioziwika kuposa kamwendo.Winanso akutukwana.muyaluka nazo zimenezi.Zinani kuti zonse mupanga tikuziwa powona polekera.Neba sazatheka ndi achule awo ali kusulom kowo.

  12. Ndikhulupira kuti amene mukunena kuti ndi abigbullets muli nawo umboni wokwanira,ndipo ndi nthawi yabwino yoti mutibweretsere umboniwo.

  13. Panthawi Ino Nkoyenera Kut Ma Player Anoma Akhale Ndichitetezo Chokwanira Chifukwa Adani Ndiambiri Kuphatikizapo Neba Wathu

  14. Mmmm a BB nd a Sulom aaaaaa mwayamba kulonda ma players athu mmm koma ngati jealous wanu anyanya aaaaaa cholinga mupweteke asakasewere game ya Mzun huuuuuuu Chauta wakana manyazi bwanji awooooo hooooooooooo

  15. Should we say ESCOM blackouts are giving robberies an opportunity to attack People?

  16. few years ago, thugs killed Meyiwa in S.Africa but I never saw comments like I’m seeing here from uncivilized Malawian supporters who always encourage their teams in Juju/ngunda and misconduct during games. Mpira wathu sudzatukuka mpaka ………………..

    1. we learn from others…with this resistance to change eeeeee mkulu keep kulimbikira kukodzera magolo, zithumwa, kunama zaka zakubadwa and the like….lol. Sorry if my comment has disturbed your peace of mind

  17. YOUR FRIEND YOUR DAD YOUR RELATIVES AMTAPANGIDWA CHIPONGWE ANALI WORKMATE WAKOYO UMADANA NAYEYO?OLO SCHOOL MATE WAKOYO?OLO NEBA WAKOYO? WATCH YOUR MOUTH NEARBOUR!

  18. It seems thugs are afraid of mob justice than anything else because Police is not there in residential areas. You get more on them along the roads. So basically a Chitetezo seem to be taking the lead

  19. Thus why l don’t support football teams,they lack discipline, love and Peace but full of backbiters pull him down, JUJU beliefs, drunkards, osuta kanundu full of woes just to mention a few, Learn to love peace and unity

  20. Aliyense wa inu amene wanena kuti a bullets mitumbo za amanu kwa zaka ziwiri kaya amako anafa watukwanitsa mafupa ndipo apanga bwino kumubela

    1. Wachamba iwe ulbe manyaz? kutukwana mpakakana kuoneselatu uchisilu wonse wako komaso wa amako coz sanakulange

  21. apa tikuwonetseratu umbuli ndipo amalawi ndifedi mbuli,chomwe a bullets angalimbanire ndi kamwendo ndi chiani? udani umakhala mground,mecium muhone adapangidwako chiwembu ku south africa,zimachitika izi kamwendo sioyamba. ndiye anoma tamayankhulani ngati anthu ozindikira pajatu mumati ndinu ophunzira.Tiyamike Mulungu Pomuteteza JK.#nbb_supporter.

  22. Kusowa nzeru kwa munthu ,wabwino bwino aganene kuti ndi a bullets? Anthu onsewa akubeledwa mu dziko munowa sianthu? Bwanj timasiyanitsa zinthu, aliyense akhoza kubeledwa osati zopusa anthu mukunenazi, Ali yense ndi wofunika chimodzi modzi ana a mulungu

  23. Mukamakhala kwanuko simukuva bwino mukava dzi loti NYASA BIG BULLETS.Bullets ilipobe kut mupsye mtima,mupwetekana mkumanamizira BB koma mbiri yathu sidzasintha.

  24. This is very bad indeed I hope Bullets fans are not behind this attack just to make sure that Jk doesn’t play in our must win game against Foolish…educated salvages called Mzuni

    1. Bwana Samuel kathewera mwalakhulatu ngat mumakhaa kunja kwadziko,ubwino awake nyumba yanu tikuidziwa tibwerako usiku uno muzatiuze momveka bwino

    2. Vuto siiweyo kma adakupatsa dzina LA Kathewerayo…. kalikose ungayankhule kazinunkha ngat thewera… Manyi Vs Nkodzo…. yaaaa

    3. Poti mwadziwa kuti ndi abullets, mungowaitanira apolisi basi athanenawo. Inu ndi amene mukuidziwa galimoto yake, mwakonza pulani yoti mumubere zakanika ndiye mukunamizirano abullets.

  25. Iwe Rhodney Mandala ndiwe chitsiru ndiye kuti mbava ndiiweyo muti tathokoza chauta kuti Kamwendo wapulumuka pa chiwembu iweyo kumalowetsa za mpira zikukhudzana chiyani

  26. Koma wa bullets ndi chigawengadi guys akufuna amuvulaze then tilephele kutenga lig inu musangalalele ng’oooooooooo muli m’madzi Mulungu akasankha wasankha ngakhale mubele ma penalty palibe chothandiza kkkkkkkk Manoma patsogoloooooooo

    1. ai paja ndimwez wa xmass2 uno achifwamba ndamen anampanga attack kmas tilibe khawa league tatopa nayo mutengek inu a kakhumba f.c

    2. Iwe Emma Gondwe ife sitingave nyunyunyu ukumva nyunyunyu ndinu ankhumba cfkwa mwakhala zaka 11 osatengako league BB kuchokera 2000 paka pano yatenga kangati 8 iwe neba 1 angave nyunyunyu ndani pamene mukamayakhula muzichita manyazi koma ntundu wanga wa mbwenu mbwenu suzathekaso

    1. Musawiringure inu, ndizo ntchito zanu zimenezi tonse tikudziwa munayambira ku Dwangwa sunday apa, mukukana chiyani? pakamwa ngati amphaka kkkkkkkkkkkiest.

    2. Let’s agree we are all salvages ignorant in football. We supporters *We are not civilised* we inspire our players with a salvage mind.. I don’t know when we will peacefully have our families and watch bullets and wanderers as our only rivals in football. Let’s peel out our and see guys

    3. Mosapita patali iweyo pamodzi ndi anthu akwanu (abale ako) mwavomereza kuti ndinu anthu otere osati ife abullets @ bwana late

      Kkkkkkkkkkkk Lol zampira

    4. mpaka kutukwanana chonchi? ife abullets tisana name ndifed okuba nanga zimenezi nzibchiyani ndipo ndikufuna kuisiya team yakatangale, yokuba,komanso chinyengnoi

    5. Much As I Respect NBB,,but I Dont Lyk It Wen They Win Thru Penalties..They Have A Good Team With Nice And Strong Playrs But That Thing Of Giving Them Penalties Were Its Not Even One Pains Me A Lot..,, I Only Wish It Ends After They Try N Win The League In Such A Way…

    6. Sibwino kumayipitsa mbiri ya anzanu mulibe umboni. inu mukuti amenewo ndi masapota a bullets munawawona akupanga zimenezi? Ndiyekuti akuba onsewa ali ntownwa ndi bullets fc? Mudziganiza mukafuna kuyankhula osamakhala ngati nkhuku kapena mbuzi ponena zinthu otherwise mutha kukaperekera umboni coz inuyo ndiyekuti mukukhudzidwa nawo pa chiwembu chimenechi.

    7. @ Jacob penalties are part of football game if you don’t know, have tyme to read FIFA rules and regulations on football otherwise don’t show your ignorance here or ngati bullets imawinira ma pernaties then go and report to FIFA simple!!

    8. @ Jacob penalties are part of football game if you don’t know, have tyme to read FIFA rules and regulations on football otherwise don’t show your ignorance here or ngati bullets imawinira ma pernaties then go and report to FIFA simple!!

    1. iwe anakulesa ndani kuti usamasute moyo wako ndi wako basi panga zosamala moyo wako posausutisa fodya bwina ungakwanise zaka 100

    1. Masapota a Nkhumba fc mukulimba ndi BB cfkwa chani kufuna kuyipitsa mbili ya BB ukunama iwe agogo ako aja ndiamene akudziwapo kanthu akusaka ya Christmas @Chiko Ben Jnr Tagawa

    2. Koma chaka chomwe noma ilipamwamba pa ligi zinthu zikuvutatu magets kulibe bill electoral reform yavutanso opopa magazi ndi amene anavuta aja bwanji kodi? Paja patha zaka khumi eti tiyeni tisatukwane paline abale

    1. Iwe tseka chikamwa chako ukundibhowa mesa ndizimbarangondo zakwanu cholinga muipitse mbili ya BB mukunama2 inu @Emma Gondwe

Comments are closed.