Bullets awarded dubious penalty, says Mafco

112

The Salima based soldiers Mafco have asked Super league of Malawi (Sulom) to nullify the result of their game with Nyasa Big Bullets due to a dubious penalty awarded to Bullets.

Mafco says a Bullets player dived to get the penalty through which Bullets scored their second goal in the match that ended 2-1.

Moyale vs Mafco

Mafco have asked Sulom to nullify the result of their game with Nyasa Big Bullets.

The soldiers have also expressed concern over poor officiation on the part of referee Easter Zimba and his panel that handled the game on Sunday.

“In the second half of the game it was sad to see our player Martin Masoatheka brought down in the six yard box which was an action of denying a goal in unlawful manner but the referee allowed the game to go on.

“In less than a minute it was observed that Nyasa Bullets player deliberately handed the ball in eighteen yard box but the referee again played on the match. Painfully, in less than a minute Mafco Fc defender cleared the ball when the Bullets FC striker was attacking towards our goal and the referee awarded a penalty after the Nyasa Bullets player dived,” says the letter dated 3rd December and signed by general secretary of the team Jimmy Chisenga.

The letter also says that Mafco is suspecting something fishy between Bullets and officiating panel since all the officiating personnel did not attend the technical meeting prior to the match.

“As Mafco FC we are not satisfied with the results and ask your good office if the results be nullified and investigate the matter,” the letter says.

The game ended 2-1 in favour of Bullets through goals from Bright Munthali in the 18th minute and Fisher Kondowe from the penalty spot in second half, while Zikani Sichinga scored for Mafco.

Share.

112 Comments

 1. Amafco Musadzivute,mungotaya Nthawi Yanu Pachabe Kapena Tinene Kuti Inu Simukudziwa Kuti Sulom Yonse Ili Mmanja Mwa Bullets? Mufuse Manoma Akuwuzani.

 2. Chimene ndimadziwa bb imagula ma ref
  Kuti musewele game ndi a bb wa bullets akagwira Moira my 18 ref amakhala ngati sanaone koma team inayo olo ikhale ball to hand amaimba pyoooo malo aimfa alozedwa
  Agalu inu ma penalty fc

 3. Game tinaonelera koma zinali zikhumudwitsa bullets kuipatsa penaty pomwe panalibe penaty.mafco inapeza ma penaty awiri abwino koma ref osayimba.akanamenyedwa ref zikanakhala bwino chifukwa anthu awa akuononga mpila pa malawi pano.game ndiyifunika replay.

 4. Hooo! komatu kudali zodabwitsa, and with that kind of officiation mpira ku Malawi siudzatukuka, player wa Mafco Martin Masoatheka adagwetsedwa mu 18yard box ref osaimba akuti game on, kenako BB player kugwila mu 18 aliyense kuona koma ref osaimba amwene, kenako mpira wapita ku golo la Mafco defender anapanga clear mpira striker wa bb ndikungo diver ref akuti penalty, malodzatu, ndi Mafco idamenya mpira possesion mwina 75%, ndipo game imeneyi ikanaimbilidwa mwachilungamo BB imaluza, koma Mafco imati ikati ipite kutsogolo uona riseman wakweza kalekale iii guys mpira ku Malawi siudzapita patsogolo

 5. Ama MFCO ndi ena nonse amene mukulalatanu ngati mukuti ma penalty ayi ndiye mupange apply ku FIFA akachotse ma penalty. Otherwise ma military teams mungosiya mpira and do what is in your order, go to Ivory cost, DRC for peace keaping

 6. Penalty imapasidwa mu zifukwa za penalty ndipo 3 kick imapasidwa muzifukwa za 3 kick mwatani kod aneba mwayamba kusadziwanso malamulo amumpira?kod mumaona ngat mkophweka kukhala refu,?mukadakhalanso inuyo refu bwenzi penalty ija ili go kick ndipo conar kick ija bwenz ili off side kkkkkk

 7. Ine Ndingopepesa Kwa Mafco M’malo Mwa Sulom Kt Pepan Chifukwa Choluza Kwa Pamwamba Mwaluzaku.Ndikutha Kukumvetsetsan Dandaulo Lanu Poti Palibe Ngakhale Ndi Tsiku Limodz Lomwe Limene Anamfedwa Adasangalala Ayi Kwawo Kumakhala Kulila Ndipo Amafunitsitsa Ngati Malemuwo Atadzukaso Koma Sizimatheka.Apa Ndingopezelaposo Mwayi Okupemphani Kt Muyambe Kusiyanitsa Pakati Pa Football Ndi Rugby. Zokankhana Mufootball Chonde Ayi Koma Murugby Chieukwa Zotsatila Zake Zimakhala Zmenez Or Mutapita Ku Ulaya. ZIKOMO ASILIKALI ATHU NTCHITO YABWINO KU BARACKSKO ZIMATHA!!!!

 8. Ma Ref Mukulakwa Game Ikavuta Mukupeleka Penalty Nfinachita Kuona Pa Fisd Cup Kupeleka Penalty Sulumba Ataphonya Pagolo Malomwa Goal Kick Mukuti Penalty Kodi Akanagolesa Sulumba Mukanaimbapo Zapenalt? Nanga Chifukwachani Kumapeto Kwa Leage Mapenat Amavumba Ku Bullets? Zamanyi Basi

 9. eyadi mafco akunena zoona komaso zigoli za ziwiri za bullets zija azivomeleze cz the same ref adakanira people’s team two goals cha manyenje and kangunje so ifeso tikuti ref adakana zigoli zabwino zathu ndie mutithandiza bwanji???

 10. ICT LEVEL 1, GPS SATELLITE & IT TRAINING{6WEEKS} . BLANTYRE AND LILONGWE . COMPUTERS ARE GOING TO BE PART OF OUR FUTURE AND THAT FUTURE IS YOURS TO SHAPE . ANYBODY CAN LEAN DON’T WAIT FOR OPPORTUNITY CREATE IT . VENUE : ACCOUNTANCY TUITION COLLEGE OPPOSITE N’JAMBA SEC SCHOOL . REGISTRATION FORMS: ARE AVAILABLE AT ALL IN ONE SHOP OPPOSITE BLANTYRE METRO . COMMENCEMENT DATE : 18 DEC 2017 . TIME : 08:00-12:00 AND 2:30 TO 4:30 PM . IN LILONGWE AT LILONGWE PRIMARY SCHOOL (GOVER) OPPOSITE CALVARY FAMILY CHURCH . COMMENCEMENT DATE: 27 DEC 2017 . TIME: 8:AM TO 12:00PM . FEES : K49,000 PAYABLE IN INSTAILLMENTS REGISTATION FEE:K1000 . REGISTRATION FORMS ATTACHED WITH TIME TABLE ARE AVAILABLE AT LILONGWE PRIMARY SCHOOL (GOVER) OPPOSITE CALVARY FAMILY CHURCH . SIM-TECH IS REGISTRED UNDER TEVET AUTHORITY’S AND TRAINEES WILL BE AWARDED WITH CERTIFICATES, WORKING TOOLS SUCH AS: PROFESSIONAL HARDWARE, . SOLDERING IRON . DIGITAL MULTIMETER . OS DISC & APPLICATION SOFTWARE . CALL / WHATSAPP 0888700421 . 0996681303

 11. Kodi penalty imangobwera yokha ngati amene amazisata Zampira bwino akhoza kundi vomeleza #Mafco yaluza basi #Bullets yatenga ma points kodi ngati munthu anagwesedwa mu 18 yard box #Referee akanatani? amafuna ayimbe goal kick enawa kuvomeleza kumakuvutan

 12. mwauze asulom mukamasewela ndi nbb malef muzikatenga kwanu nbb yilibe vuto ndi super leage chifukwa siyimankhala zaka 10 yisanatenge

 13. Ndiye ngati mukuti pali chinyengo zikusonyeza kuti anyerere apeleka 600,000,00 Ku mzuni kuti akazume ,iwowa bwanji amapitiliza kusewera mpira bullets itapasidwa penalty nkuchinya kumapeto ndikumumenya referee ,amakuwa zapenatewo anali masapota awanderes,chifukwa zikumayendela neba akachinya wina akumakuwa ndiye uku ndikulira kwanyerere siakuona kuti tikuwayandikila kwambiri

 14. Koma za khofi la kuseli kwa dzanja lomwe adaphathikidwa fische mpaka magazi mmano sizili kukambidwapotu apa bwanji kweni kweni mwinatu idali yophela awemba cholinga abise kukondeledwa ndi ref

 15. Ma reff a ku Malawi ndi choncho,tiyeni tidikire mapeto a leage zitachitike ndi chiyani?Iwotu akufuna leage ipite ku BB,koma akunama Noma inatenga lale.

 16. We Already Know How How BB Behaves, I You Can Recall Last Season Pipo Nicknamed It Penalty FC Because Of This Tendency So, This Denotes That Refs Are Not Officiating Professionally, Lets See And Wait But I Believe Nothing Is Going To Happen According To Sports Governing Body Like SULOM.

 17. Zobelekedwa ndima ref siza Nyasa bb aiii, bwanji dzanadzanali pa Balaka stadium ref sanaimbe penalty mu 18 player wa Dwangwa united atagwetsedwa game ili Noma 3 Dwangwa united 2 ???. Ma team aku Blantyre nonse mumabelekedwa ndima ref anoma musalankhule zambiriapa umundimomwe ukumayendera mpira pamalawipano that’s y sitikupita chitsogolo ndimpira. Sizotukwana izi koma zampira….

 18. If it was noma mmmmm right now ,we would ve heard alot of abusive words and insults. But because today its them nothing will change, even the sulom executive can’t rules against them . If it is true then the referee should be taken to the tribunal ,go and explain what has transpired to award such penalty. Sulom and fam should wake-up from there slumbers, people ll continue complaining over the same issue if these problem won’t come to unend. Sometimes referee kill games for deliberately ,tione zomwe achite asulom nangasi lero zadza ndi mapale

 19. Ine ndinali komweko ku chitowe mapenalty achilungamo amayenera kupita ku mafco defenda wa bulesi namugwesa osewera wa mafco mu 6yad box koma ref angoti pheee kungowonesa kuti mpira uzipitirira pasanathe 2minutes difenda wakumanzere wa bullets anagwira mu 18miter box ref sanaimbe kenako game ikuoneka kuti ikupita kumapeto osewera abullets anatenga mpira nkubwiza njomba kunja ka 18 koma difenda wa mafco atamlanda anangoziponya kuti akafike mu18 koma anasalira mwina ndi 10cm kuti afike mzera wa 18, komano pamene timati bullets yapeza free cick kunja kwa 18 tinamva kuti ati ndi panalty moti olo osewera abullets amadabwa nde panali nkoke nkoke, mpaka ref anakanika penalty inamenyedwa mpira utatha ref wa mayi anayenda chothawa ngati nkhuku yoti iphendwere mlendo kkkk kk #silver_waganyu

 20. Za ziii a sulom amangoyangana ma report akuti chani basi. And panopa onse apereka ma report awo kuti game inali bwino. Which means mafco will b alone to oppose which can’t carry weight. Noma kkkkkk fighting behind mafco kuti zokhale ngati zanu ndi mzuni? Kkkkkk. Auzeni yisewere nawonso alandire 3-0 muone iyaaaa

 21. Inuu Bze Bas Ndi Bb Tnaziwatu Kungot Takuyandikilani Muthemukila Tingokuwophezan Sitikulandani Matha Ngat KHwagwala Mwina Chfukwa Chot Patha Patha 11 0saina Tnm Hhhhhhhh Kkkkkkkk Neba Matha Iiiiiiii Sha Mbuya Taupeze Mtimawo?

 22. palibe zimenezo,iwowo angodandaula momwe ref adalili,mphamvu yopanga nullify results ndiya sulom ikamva mbali zose koma sizochita kupempha,amafco asaiwale kuti adalakwitsa kale pomenya ref,mwinatu akuopa chilango.komaso tiziganiza kuti mafco idadya za noma.

 23. Olo senegal ndi southafrica game inamenyedwanso coz za ma penalty abodza zomwezi…. Hahahahaha penalty fc

 24. Fifa ikazangochotsa lamulo la penalty. Marcopolo fc izatha, team imangokhalira kubelekedwa ndi ma ref. Mapenalty amawapatsa akaona kuti zinthu zikuwathina kkjkkkkkkkkkk

 25. A Mafco ingobwezani ndalama zomwe Vandalazi fc idakupatsani musawuwewuwe apa.Ngati mukufuna mpira opanda ma penalty mulowe nawo mpikisano wa beach soccer wa mu nchenga

  • Chaka chatha anthu anakutchani kamapenalty chifukwa chogula ma ref . Inu kupanda kuthandizidwa ndi ma ref mutha kutuluka mu league. That’s why kuwina kwanu kumakhala kongogwera. Mumati timu yaikulu koma zosewela zake mbola yeniyeni. Inu or kutenga zikho kwanu ndikothandizidwa ndi ma ref plus a sulom. Taonani phala mwasewela for the past 4games .mmmmm blantyre united ili bwinoko.

  • Hahahaaaaaaa umangonziwilatu kuti sound ya ma return from Japan iyi 😂😂😂 BT untd itakumvera ingakudandauletu koopsyaaa.
   BULLETS sigula ref koma ma ref-wo ndi ma die hard a BULLETS 😂😂😂😂.Tikamati The ppoz team simumanziwa meaning yake kapena??.BULLETS is ppoz team not AKA Pigs fc kapena katu Nyerere fc hahahaaaaa zinyama xonsezi ungasakhe Nyerere yopanda bongo??? 😂😂😂😂 Neba size yako ndi Nyasa BULLETS reserve ife ndi ma Elder aise.

  • Inu Penalty mudapatsidwa ku Mzuzu ija bwa? Adaphonya Kafodya wanu Kamwendo ija was that foul worthy penalty?.Inu mpira nde mulibemo ndichifukwa mukumaliza season opanda choloza 😂😂😂😂.Mpira mwaulowetsa chiwembu kufuna 3 points ya ulele basi ana oipa kwambiri.

%d bloggers like this: