Wanderers fined K1 million

Be Forward Wanderers

Malawi’s Super League leaders Mighty Beforward Wanderers have been fined K1 million kwacha for misconduct.

The Nomads have been punished for incidents that occurred during their game against Chitipa United at Karonga Stadium on 21 October this year.

Be Forward
The Nomads: Punished

According to Super League disciplinary commitee, the Nomads have been fined on two counts of failing to control actions of supporters and officials and for assaulting officials contrary to article 21(2) and 21(7) of SULOM rules and regurations respectively.

A letter released by SULOM dated 28 November which has been signed by General secretary Williams Banda states that Wanderers official Vales Kamzere delayed the game by obstructing Chitipa football club players and officials from entering the pitch.

“Beforward FC official names Vales Kamzere obstructed Chitipa FC players and officials from entering the pitch and grabbed keys for accessing the ground from the steward responsible thereby creating tension and causing the kickoff of second half of the second half to be delayed by eight minutes,” reads the letter.
Kamzere has been warned for his conduct.

The commitee has also warned Nomads second official Chulu Makanga for attacking the duty referee Misheck Juba after the final whistle.

Sulom has also banned Wanderers supporter Tyson Bonongwe from watching any TNM Super League match for the rest of the season for slapping assistant referee Jonazio Luiz as officials were heading into their dressing room.

The committee has fined Wanderers K500,000 for each of the two counts and has given the club right to appeal within 48 hours on payment of the requisite appeal fees.

This fine is coming just recently after the log table leaders appealed on the verdict that Sulom punched over the match that was not played at Balaka stadium against Mzuni on 4th November.

Advertisement

73 Comments

 1. Kodi kumalawi kuli FAM n sulom? Ndalama za mabungwe amenewa zimalowera KT? Mbuz zimenez mulungu azilange musalekeza ndma devils opanda umunthu

 2. EYA nanga si adyeretu tikamazawachosa azakhale atalemera,,,kma or atero noma ndiwankanka bas,,,,,, propaganda bas aaaa

 3. Akanangonena Kut Akufuna Ndalama Zmene Titenge Ku League Zithere Kulipila Milandu Yopusa Imene Akuyipanga Create Iwowo.Kablander Kakang’onong’ono,koma Mpaka Million.Mpiratu Sumaseweledwa Mutchalitchi,ndye Supporter Kumpira Samakhala Ndwiii Ngat Wadya Mgonelo.Inu A Sulom Mwatitopetsa Tsopano.Tsiku Lina Tidza…………Mumalizitse Nokha A Sulom.

 4. Zikomo kwambiri nonse wakomenta pakhaniyi ngakhale ena mwatukwana mwangoonetselatu kut ndinu ana ajoka olamuliridwa ndi lucifa mumudziwe YESU Kukubwera gahena

 5. Please anyone making comment should make it short, so we professional comment readers (PCR) will be able to Read all comments. Thanks for making our work easier!!

 6. Uko ndiye kukolola posalima, ma team onsewo ndalama kuchuluka chonchi?. Kma pomadzafika chaka chikudzachi ndithudi, tidzamva kti ma sponsors ena akana kuthandiza kamba ka umbabva wa mabungwe oyendetsa mpila.

 7. Koma nde ngati simumanga manyumba ndikupezela azibale anu ppkhala pa bwino ndindalama xochokeka Ku wanderers Ku Sulomu ko ayi ndithu mudadwa aminyama kwanu, kodi nkhani yake nde itiyo? Aaaaa mukuonjezatu cholinga noma isatenge League mmmmm ayi Guyz yagwilani ntchito zina

 8. Sulom i think that u are against noma mitima yanu sikumva kukoma ngati mkuona akukakamira pamwamba while ma team anu ali under thats bustard u are full of nonsese. Let me tell u now inu mumazicha asulom watchout 9mm yili pambuyo panu ana amahure inu.

 9. sulom ndibungwe laumbamva limalephera kuthetsa mchitidwe obandalama zama gate kuti ma team azipeza kanthu, koma Ali busy kutchera misampha ma team kt aziwabela ndalama mudzina la fine, : pali nkhani ya noma ndi mzuni mpaka pano chigamulo chikungoyenda mthumba kulemphera kugamula akuopa chani? koma dziwani kt pamene mukutseka khomo lina yehova amatsekula ena: likadakhala ngati kale a sulom nonse tikadakuponyani mudziwe la ng’ona mulibe ntchito

 10. Ku Sulom ku kuli achule awiri omwe asakuifunira Noma zabwino.Akuyesesa kuti Noma isatenge Leage.Muzipemphera chisankho sisabwere.Nonse Ku Sulom komanso Fam.Tizakuonesani.

 11. Kod Mateam Amene apatsidwa Fine Ya 3milliyon,1miliyon…Ndiakumozambiki?Osalemba Za Fine Ya 3mitawobwanj?Why Alwez Nomads!!!

 12. N.B ma team’wa aphwanya gawo 21 (2), 21 (3) ndi 17 (6) a Super League of Malawi (Sulom).

  1. Silver Strikers…ma fine onse pa milandu iwiri K3.2 million
  2. Nyasa Big Bullets… nayo pa milandu iwiri… K1 million
  3. Be Forward Wanderers nayo pa milandu iwiri…K1 million
  4. Mzuni FC nayo pa milandu iwiri K1 million
  5.Moyale Barracks nayo pa milandu iwiri K1.84 million
  6. Red Lions iyo nde sanaipweteke kwambiri, K30 000
  7. Kamuzu Barracks iyo ipereke K130 000
  8. Blue Eagles… akuti ipereke K500 000

  1. Ma fineo achajila limodzi ndi mati ena ambiri ,apa sakanaika ya noma yokha. Ndie ma postiwo mpaka akwane 7 . Timu ilionse post yakeyake . Ndie uchitsiruo.

  2. Hahahaaaaa kalatazo zatuluka nthawi zosiyana apart from that team iliyonse ili ndi milandu yake.Nkhani ya Noma deserves its own post coz there is lots to be explained so admin didn’t want to sammurise the story.
   Nkhani ndiyoti #Yussuf unaika comment b4 viewing other posts.

 13. Heheheeee koma league ikamatha ma team atsala chimanjamanja.
  Neba upeleke 1 mita after misconduct on game against Chitipa ya Mzuni chigamulo sichinatuluketu kkkkkkk zaulendo unoooo

Comments are closed.