DPP, PP considering alliance

256

Democratic Progressive Party (DPP) and People’s Party (PP) are discussing the possibility of forming an alliance to boost their chances of beating Malawi Congress Party (MCP) in the 2019 elections.

According to the local media, the ruling DPP is keen on an alliance with opposition PP in order to stop MCP from extending its tentacles into the Southern Region.

 

Kondwani Nankhumwa

Nankhumwa: Leading the guns.

“The loss in the recent by elections is what has prompted us to start thinking ahead.

“We thought it wise to start consolidating [the grip] of the Southern Region to stem the momentum that the MCP is gathering in the region,” a DPP official told the local media.

According to reports, Minister of Local Government Kondwani Nankhumwa and former cabinet minister Ibrahim Matola are leading the DPP and PP teams respectively.

The two teams have however been meeting without the approval of exiled PP president Joyce Banda who formed the PP after she was fired from the DPP.

Some PP Members of Parliament do not also approve of the possible alliance saying DPP is a party that is in decline.

The DPP recently lost by-elections in three constituencies and one ward to main opposition MCP.

Share.

256 Comments

 1. amuthalika chenjelani chomwe akufuna anthuwa ndichakuti akunyengeleleni miziwawona ngati akukukondali ali ndicholinga choti muwasakhe kuti akhale vaisi pulezideti pamapeto pake akupheni ndi u d f imeneyo yomwe yakuuzani fundo imeneyi ikupusisani itayeni pangani zanu za dpp

 2. Tidzawakwapulira onse limodzi. When DPP turns to PP it is a clear manifestation of panic. You form a coalition with a party that has no president in the deal? … and with the fired Change Golo kkkkk

 3. guyz nanga tiziti ndale ndizinthu ..wina anayimba kuti eniakewo akuonamo phindu …billy kaunda wapanga resign last week …tiyeni tilimbikile pazathu zomwe mulungu anatigawila kaya maganyu bola kusamala mabanja anthu …pakamupeni akusokonezani akusokonezani akazawina ….muzaisova

 4. I’m not a politician’ i don’t admire to become a politician’ but one word to you so called politicians, don’t take Malawians for granted.Everyday We Are Hearing Distorted Views Of Politics.If You Have Failed To Rule Malawians It Is Good To Stop Ndale And Start Farming, May Be You Are Good At Farming.

 5. Chakwera z only one who can bring new agenda of how 2 run th Government affairs dan these so called dpp n pp coalision. It can b so stupid 2 vote 4 dpp n pp as of now as both hv failed Malawians completely 2 zero.

 6. This is false , fabricated story aimed at bolstering political mileage by the perpetrators of doom .BE CAREFUL THIS I S ERRONEOUS

 7. Nkhaniyi ndi yabodza President Peter Mutharika sangapange za manyi ngati zimene zikukambidwazi ai. chipanichi pawokha ndi champhamvu ndipo palibe kulumikidzana ndi China ai, ndipo pamene dzaka, mezi, masabata komanso matsiku akumasendera ku dzaka za masankho tidzimvera zambiri ndipo onena nenani ife pheeee kumangomvetsera ndithu.

 8. But who in his right mind can vote for DPP again. PP will be making the gravest mistake if they make an alliance with DPP. PP is a party on the decline already if it joins with DPP then it will be buried. May be if it can join with MCP may be it can be propped up.

 9. It was Bushiri who was used to announce about this Alliance on media last week, even JB aprove this, it could impossible for Bushiri to start boosting about APM and DPP after what he went through because of the same DPP, where was Bushiri all this time to say good about DPP today on Media? Have u ever seen Bushiri on MBC since DPP took the government? Was it not the same DPP that uses T/A Lundu to tanish the image of Bushiri by calling him that he is from the Kingdom of darkness?

 10. mupanga bwanji mgwilizano ndi chipani chimene mukuti aniaki ndi mbava zoba misonkho ya amalawi mesa mumati muli ndi warrant of arrest kwa mayi yemweyu mukufuna ku manga naye banjayu zamanyazi ku dppko ndinthu tionana 2019

 11. Ndiye kut MCP ikuopedwa kwambiri eti… bcz last tym ndimamva za alliance Dpp ndi UDF and now discussing za PP..
  … mmmmmm guyz apa ndiye akumpasa mpata mdyelekezi.
  Akumuopa azitukumula tsopano.

 12. Yooooo DPP+PP+UDF….osusa mukulimbabe ntima 😀 😀 😀 malawi muno muli anthu almost 17million nde pamenepo muchosepo 7 million a DPP ,5 million a UDF ,3.6 milion a PP…osusa wagwa nayo…chakwera ukakhala presdent pakhomo pa ambuyako mneneri onyenga iwe…ukafune dziko lina lot ukalamulire osat malawi… 😛

 13. Chipan chilamula mpaka kufuna china kt anthandzane kungonjetsa otsutsa? Zaonekeratu kt chipanichi chilibe phavu pachokha akuopa chan ngat akulamula bwino akudziwa kt penapake pali vuto ndnthu

 14. Chakweraaaaaa kiririri raaà.ndale zkukoma izi.its my first tym kuona APM ikutenthedwa,kuotchedwa,kunyowesedwa,kuzinguzidwa mutu nd munthu otsutsa.Walimbana nako kulimbana kwabwino chakwela.come 2019.tmuike munthuyu malo oyeneraaaa raaaa chakweraaaa

 15. Thus my boc kp it up ur estblshng us.2019 boma imeneo nde tmat kapmen and pp izingofera kusatla ife mkumalamulira thus no any prblm boc ur plan iz 100%!!!!!!! Stay there ull c in 2019 dpp’ll cm again lyk mafunyeta

 16. I suppose 50+1% is doing the trick here. DPP wants to fully grip the South despite some cracks which have been caused by the Sheikh. The North is quite unpredictable.. It may go either way especially after LC makes his decision on who to partner with.

 17. ine pamene ndikuva kukoma kuti atupere azipsa mtima,ben phiri,chapinda,nankhumwa,chilima,kaliati,henry musa,kuti akapsa mtima ndi alliance imeneyi,alowetsemo madzi a mphutsi mu dpp kenako okha okha ayambe kuzomorana,hahahha

 18. Come on DPP take all the Peace’s you can see but remember we wil beat you lyk David to Goliath thats when you wil know that MCP is back to its Root

  • then why dpp is seeking alliance with pp ? u’v udf already komansi mukufuna ena,iweyo ndye idiot osati pang’ono..kkkkkkk

 19. Nkhani Ya Bodza!! Dpp Cant Allience Wth Dead Pp… For Ur Information Mcp Can Not Win The Plesidency Perhaps High Nmbr Of Mp’s..Chakwera Alibe Nfundo Up To Now Sinnanvebe Nfundo Zotchyakuka,masomphenya Otukula Dziko Koma Kunyoza Basi Nyasi Izi Pepan Amalawi Anzanga Sizilowa M’boma…Dpp Yawina Kawiri Opanda Alliance Nde Pp Ndichan? A Mcp Ndi Zipan Zina Ndiomwe Akufunika Alliance Kut Agwetse Dpp Kupanda Apo Dpp 2024 Wooo

  • Bvuto la free data ndi limeneli…tamawelengani nkhani yonse ku link kuti mumvetsetse musanaonetse umbuli wanu pa comment.

 20. I wonder what their new political flag will look like…kkkkkkkkkk chimanga chokuba chaponda atachikiyila

 21. Mmmm! Jb Alinizolingazina. Muziwona Patsogolopano. Mgwirizano Waboza. Kapena Pot Zosendi Mbava Aziwana. Wakuba Akayenda Niosaba Wose Colled Mbava. Zawonesa Kut Mw Mavuto Adakali Mmmm! Pp + Dpp Cabwino

 22. Pp cashgate plus dpp cashgate =avery big cashgate!tulutsanitu achinalutepo,mtengeni budget director okuba uja akhalenso bdirector!muitaneni mayi anathawa ataba uja mudyele limodzi msonkho wanga!machona anthu oipa inu!mukufuna kutipha tonso,mufunse nganga mzanu ku zimbabwe,mukundiyamba dalatu apa ok!

 23. even if they can join together but they won’t beat MCP,MCP has come up with huge number of followers in all 4 corners just immagine PP how many followers they are,forget about that MCP it’s another big level you will see 2019

 24. A herbalist in Africa has been curing lots of HIV patients using natural herbs. He has on countless occasions after curing patients presented lab results both positive and negative, together with the cured person. I never knew there was a cure to HIV until my sister was cured from the virus after four years of battling the virus with ARV. She took his herbal medicine for a month and some weeks and when she went for a test and she was diagnosed to be negative. you can contact the doctor on WhatsApp or call +2348147299781

 25. Koma zovetsa chisoni kwambiri. ngati ndizowna. chikwatu anthu ena a pp alikundende kumati adaba ndalama mu ulamulilo wa pp.lero yakoma .anthuwadi ndi amodzi amafuna kungotipusitsa.basi.

 26. Chimenecho ndiye chambacho. There’s no way PP can form an alliance with DPP. Mrs JB cannot approve of this. And if this is true, it means DPP ili desperate to win in elections in 2019. And a ruling party to make an alliance with an opposition party in Malawi? Strange.

 27. MCP ndi Big party CRC amene tsamaikonda UDF pp vote yawo MCP amend tsamaikonda DPP vote MCP cashgate maize gate MCP chipani changa

 28. Kkkkkkkkk but that can be a very wisest tactic by DPP because PP with Amayi Ku eastern region can have more supporters than UDF and Amayi pano has a good political stance than enawa

 29. A nice move keep talking behind doors koma ngati zafika pa nyasha choncho ndi year kutI ku ntundako kali Vito akazitape achuluka

 30. Mind u friends that if that is going to happen,its obvious that where PP had stronpholds,people wil opt for MCP,WHY?;people have lost trust in dpp and pp will end up like curtains as udf

 31. Dreaming in colour after u exiled jb ,did u forget u arrested change golo now zakuthinani u sick for their hand mwauponda ,as far as I know pp+ MCP + aford that’s the way to go coz u DPP u will dump them as soon as u are in positione

 32. Hahahahahahahaha awatu apenga awa, si omwe akhala akuyalutsa PP kuti inaba Ndalama mmboma, lero akufuna PP yomweyo, iyi ndiye misala yeniyeni ndiye paja ndale ndi uzereza no wonder wanthu mbakufuntha koma samalanibe because alliance imeneyo siyiphula kanthu

 33. Dpp ndiye kuti chani? Pangani alliance yanuyo mukhaula 2019, ife pano mavuto ali thoo kamba ka Dpp, Malawi yachangamuka mukhaula !!!

 34. Khani apa ndipitala osati chipani ngati Peter akuyimaso or atatani MCP izawina izo tiziwe azamganu a DPP pitala amalawi ambili sanamukonde

 35. hahahaha wailora wa youth apa mpamene zadziwikano kuti mcp sidzapatsidwa mpata wolamuliranso mdziko muno kunakwana basi ife tidzavota bola pali moya muthalika basi

 36. Asiyeni ma corruptions akwatire ma cashgaters chigumula chiwagumulire limodzi poti dzanja la Yehova lalemba kale ogumula ndani

 37. i just came here to read comments but this combination it shows that a lot of people are not intrested. DPP & PP wont make it

 38. Chiyambi Cha Tsankho Ndi Chimenecho. Akummwera Kufuna Dera Lawo Lisalamulidwe Ndi Chipani Cha Mcp,mmmmmm! 2bad! Kmabe Ambuye Wazatheka Bwanji Will Never Allow Dpp And Pp To Rule This Country Aftr 2019 Elections, Again. Ok, Merge! Mume Mmene Mukagwere. God Loves Malawi!!

 39. aaaaaaaaaa, kodi? koma ngatidi zili zoona aaaa bwanji musatero, mwagwilizananji? tikukumbukila bwino zomwe zinkachitika mu 2014 a peter munanyozedwa uladi mussah analankhula Ku thyolo zonyoza atapita ndi joice ndipo mwadusa muzambili mwinanso chisomo chokha cha mulungu kufika lelo mkutenga dziko mkumalamulila, ndiye lelo m’utu chani? eeeh ngatidi mwaganiza motero aaaaa mwina mukanaimabe nokha musaope munapambana mchisomo cha yehova mungathenso kuwina koma izo mmmmmmm mungowapasa anthu kunena zambili! ine ndi kuti! musaphatikizane zaimeni panokha eeeeee muzawaina koma mukaphatikizana ndiiiiiithu muzakephela musalole aiiiii

 40. Ati ife chipani chathu chili ndi ma p awiri kenako tionjezerenso ma p ena kuti ikhale DPPPP. Mnyera mthalauza muonanso. Galu izi.

 41. if this is true, then it means that DPP has done an assessment whose result indicate that they will not beat MCP single handedly, it would also mean than DPP duped and cheated Malawians by indicating that PP and Joyce Banda were a home of cashgate. Until DPP prove to Malawians that PP in no longer a home of cashgate as they initially portrayed, DPP will only be understood as a bunch of liars and the “prince of thives” tag will make more sense. It further indicate that Malawians are taken for granted and that DPP is only interested in numbers to get a seat rather than fulfilling their promises.

 42. KODI MUMATITENGA NGATI AMALAWI NDIZITSIRU ETI…
  PALIBE TIKUONA CHAZERU APA

  KULUZA KULIPO

  #MALAWI CONGRESS PARTY KOZEKA VOTE YANGA NDIYAKO

  TIYESEKO MCP
  TIZIONERE TOKHA….
  THIS IS MALAWI WATSOPANO NOT UJA WA
  DR HASTINGS KAMUZU BANDA….

  TIONANA 2019 BASI TISAKAMBE ZAMBIRI

 43. KODI MUMATITENGA NGATI AMALAWI NDIZITSIRU ETI…
  PALIBE TIKUONA CHAZERU APA

  KULUZA KULIPO

  #MALAWI CONGRESS PARTY KOZEKA VOTE YANGA NDIYAKO

  TIYESEKO MCP
  TIZIONERE TOKHA….
  THIS IS MALAWI WATSOPANO NOT UJA WA
  DR HASTINGS KAMUZU BANDA….

  TIONANA 2019 BASI TISAKAMBE ZAMBIRI

 44. Koma Chakwera ndi MCP wazunguza anthu mitu. Mpaka chipani cholamula kumasaka alliance. …..heheheheh. Chakwera ndinyamuleee!!! Bwampini wandilephelaaa!!

 45. MCP yake itiso imene yopangila mgwilizanoyo aaaaah……. forget abt mcp kamufuseni john tembo ndi ma frenz ake anakanika enawa ndiye ndi ndaniso othawa ubusa aaaah kusiya nkhosa zili mu church mkumazathamangila kulalatila boma za ziii…..

%d bloggers like this: