Mzuni boycott Wanderers clash over safety concerns

Advertisement
Super League Malawi

In a dramatic turn of events, Mzuni FC boycotted their TNM Super League match against current leaders Be Forward Wanderers which was scheduled to be played at Balaka Stadium after some of their officials were manhandled by Nomads supporters as they entered the stadium.

According to Mzuni FC General Secretary Khumbo Kumwenda, his side decided to boycott the game because their players and officials were beaten by the home fans.

Super League Malawi
Wanderers coach Yasin Osman waiting for Mzuni

“Note that Mzuni FC has decided to boycott today’s game vs Wanderers because players and officials have been beaten whilst entering the gate at Balaka Stadium. Our team is now returning to Mzuzu. Sulom can decide on how to handle this,” he said.

And commenting on the issue, Mzuni FC Chairman Albert Mtungambera said the decision to boycott the game was also influenced by lack of security at the facility.

“The game between Be Forward Wanderers and Mzuni FC has been called off because of lack of security and violence. Nomads, who were supposed to provide security to the visiting team manhandled coaching panel and leader of delegation Mrs. Agnes Mzumara who is currently receiving treatment at Balaka Hospital,” he explained.

However, Wanderers General Secretary refuted Mzuni’s claim saying the team did not even show up at the stadium.

“I have been inside the stadium all along but I never saw Mzuni at the stadium. They never came through the gates and even the referees didn’t check their cards because there was nobody from Mzuni. Somebody wants cheap points here. This is crazy. As far as we know, Mzuni didn’t come to the match. If something happened why at least one of their officials didn’t lodge a complaint? wondered Butao.

On Mzuni FC’s claim that Wanderers were supposed to provide security for the visitors, Butao said:

“Home team doesn’t provide security. Security issues are discussed and agreed by all parties at the preparatory match meeting. In fact it’s Sulom who decides on security and that was the reason why we were turned down to have the Blantyre derby played at Balaka Stadium last week,” he said.

Efforts to hear from Sulom proved futile as treasurer Tiya Somba Banda was still with Mzuni FC officials before officially ordering referees to call off the match.

It is still not known as to whether Wanderers will be awarded three points or not as they were on the pitch when the referee was calling off the match.

Article 19 of Sulom’s rules and regulations states that a match may be replayed if it could not take place or could not be played in full for reasons other than force majeure, but due to the behavior of a team for which an association or a club is liable.

Advertisement

200 Comments

  1. kutukwanidwa kikiki! chimenechi chingakhale chifukwa chokwanila sure? mungothokaza kuti noma supporters ndioupeza mtima. chifukwa munthu asiye zintchito zake akazi ake ana ake kuti akupita ku mpira team ina ndikulephela ndizifukwa za ziii. chosecho walipilaso zolowela mu stadium. komaso ngati a police a pa Balaka sanalandile madandaulo kuti team ya mzuni yamenyedwa mufunilanji umboni wina y mukuchedwetsa ka 3 points ka nomako. vuto lalikulu pa mpila waku Malawi Ma ref samadzikhulupilira pa iwo okha they can’t make decisions own there own kapena ndikusaphunzila kaya. malamulo akuadziwa kuti ngati team sinabwele chotsatila ndi chakuti koma udzapeza akulephera kupanga chiganizo pa yekha. inu a fam kapena sulom ndinu MBUZI chilungamo mukuchidziwa mukuchedwetsa chigamulo y. apatseni 3 points Yawoyo simple. bus ya noma inagendedwa munakamba kuti inagendedwa kunja kwa ground. ndiye mukufuna mundiuze kuti ma supporters amatukwanizana ku mowa adzibwela azidzasuma kwa inu? mwayamba kuweluza za kunja kwa ground?

  2. nose mukamba nkhani ya mbuletsi ndinu vitsiru ndiye kuti timuyo muyiopa sinanga zikho zakuvutan ndemuonasokut tnm par 4mitazi ndekhawayikupezan rimbikiran musaruzeko 4poits kaya tiyenazoni magem 6nambiri kaya kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

  3. Sanalowe bwanji nkukadandaula.Komanso opanga violence akuyenera stiffer punishment osati mateam ena angopanga pofuna kuononga mbiri ndi chuma cha matimu

  4. The standing orders are loud and clear, if you think something is wrong just play under protest but Mzuni the so
    called intellectuals deliberately chose to boycott the match, what a shame, this is unprofessional and childish you would have played under protest that’s all.

  5. Amamenyedwa kuti?
    Poti anoma ndi ma supporter awo anali Ali ground
    Iwo amenyedwa kunja
    Sanalowe ground
    Ndipo atolankhani anali kumeneko amati akuti atukwanidwa
    Nanga zomenyedwazo zachoka kuti?
    Alipo akuwanamiza amenewa
    Muwafufuze bwinobwino
    Kungofuna kuipisa mbiri ya noma

  6. Thanks to Dr.momoh who saved and cured me from hepatitis B.. virus. with his herb medicine you can also reached him for similar
    *Or any other….virus…like.. Hepatitis…..C… Virus….
    You can reach him through this number…you can add him on WhatsApp believe me you will never regret it
    +2349068579672
    ​Your cure is here for you​ !!!

  7. Pamene ali manoma pano ayembekeze mayesero ndi zopinga zambiri ndicholinga choti ipeze mavuto oti ilephere kutenga ligi, adaninso atizungulira.

  8. This issue has now become the blame over game where mzuni claims to have faced fate whereas noma distances itself from the same issue . The sulom should introduce tough penaltiest to anyone found stirring violences in football.

    1. WARNING SULOM IF YOU ARE TIRED ITS BETTER TO LEAVE MUNATIBELANSO NDALAMA ZA MMAGATE CHONCHO MUMAFUNA KUTI ANTHU ADZINGOKHALA CHETE MUNALEPHELERANJI KUCHITA CONTROL PATSIKULI NANGA LIPOTI LANZUNI LINAPELEKEDWA NTHAWI YANJI KAPENA ANAFIKA KU STADIUM KAPENA AMAMENYEDWALA KUTI?

  9. Mpira wanthu kuno kumalawi sungapite pa tsogolo ndi makhalidwe ngati awa.
    Ife tose amene timasapota big bullets lets not be against our main competitor(neba)by braming him.pamasewera ampira pa makhala zinthu zambiri mwazina mwa izo nde matimu kumawowozedwa akamafika pa bwalo lomenyera mpira.
    Mosabisa timu ya mzuni ya panga zinthu zosakhala bwino and okuyenera kuti ipatsidwe chilango chonkhwima kuti matimu ena amene angadzaganize zotero atengelepo chitsazo.

  10. Mzuni was right. Am a bullets fan and some of our (bb and noma) supporters are just good to be boxers. Kb should have started this. Balaka and mdc should not be no go areas. Good those hooligans from my team have been banned but we need stiffer punishments. 2milion is nothing to bullets and nomads. Start deducting points.

    #peaceinstadiums

  11. Amene wavulala ali kuti ? ?? Balaka hospital ilipafupi, police ilipafupiso , nanga ma camera ojambula omenyedwa even ma fon anasowa????? Pezani bodza lina zotenga ma points pa window inu a mzuni mwa mbwita ( mwaphonya) Noma patsogolo basi

  12. Violence z what marring our game of football,bcoz the perpetrators of this are so called big teams they’re favored when it comes to punishment,I heard that sulom treasure was discussing with mzuni at bk hospitals,I think this should be a starting point what happened that he should follow and discuss with them at hospital?something somewhere z not adding up,if fam and sulom continue favoring these so called big teams they will regret their actions in near future.

  13. Neba kufuna 3points yaulele kumeneko tatenga league ngati mwamaliza magames onse umbulidi siwabwino chilungamo chiendepo apa ngati madzi no free 3points….

  14. Mzuni wanted to test the field of play at 11 am,according to rules governing Football set aside by FAM,stipulates that teams are allowed to test the field of play a day prior to matchday…on matchday,both teams are allowed a 15 minute warm up 45 minutes prior to kick off.Pa warm up Mzuni kunalibe.Inu a bullets ena mungokamba poti zagwera Noma mukudzinyenga ndi chala.Kumbukani kuti mzuni yi,mukakumana nayo ku mpoto kwao konko..nkutheka zipongwe zonse zikathera pa inu…dziwaninso kuti This Mzuni team is always shielded by Alfred Gunda…the FAM boss who has interests in this team.Nde anzathunu mwaterekedwa pa nkhate,akuti musalodzedwe kuvunga mwala..mkangotero,2.5 million…Apapa a FAM ayenera kuunikira zinthu zingapo..1: Mzuni siyidapezeke pa nthawi yomwe ma team amayenera kulowa ku dressing room.2: a chitetezo assigned to protect team ya Mzuni motsogozedwa ndi Time Kambalame snr officer Balaka police wakanisitsa kuti iye ndi gulu lache saadawone team ya Mzuni anywhere near Balaka stadia…3: omwe akuti atukwana/ kumwenya ma player/ official a Mzuni ndi mmodzi yemwe saakudziwika..FAM/ SULOM..athokoze kuti masapota a Nomads ali mu championship mood nde zachiwawa zikuwatalikira,kma chikhala ma team enawa,dzulo tu pa balaka pakanaphwanyidwa zinthu..anthu saangangokwera ma transport,kudula ma ticket nkulowa..kukamva kuti team ina yaulesi ikungobwera ndi ma lame excuses all the way from MZUZU..My opinion: This Mzuzu based team must not only be scrapped off the 3 points,but must severely be punished bcoz they almost put the game of futbol into disrepute…and awonetseratu kuti akumuona Gunda ngati savior.. nde they are ready to commit all sorts of mess…pomaliza,FAM thru Mr Walter Nyamilandu Must scrutinize zomwe zuchitika mumpila these days and hold a press briefing kudzudzula zoterezi…a FAM acheze ndi ma team sapotaz kuwauza kuti akamapita ku mpila,nkokachemelera basi.FAM idziwitse ma team ochepa mphamvu onse kuti ku mpila ndi ku mpila,si kokatukwanizana ndi masapota ayi,adzathudzulidwa makofi

  15. Mzuni wanted to test the field of play at 11 am,according to rules governing Football set aside by FAM,stipulates that teams are allowed to test the field of play a day prior to matchday…on matchday,both teams are allowed a 15 minute warm up 45 minutes prior to kick off.Pa warm up Mzuni kunalibe.Inu a bullets ena mungokamba poti zagwera Noma mukudzinyenga ndi chala.Kumbukani kuti mzuni yi,mukakumana nayo ku mpoto kwao konko..nkutheka zipongwe zonse zikathera pa inu…dziwaninso kuti This Mzuni team is always shielded by Alfred Gunda…the FAM boss who has interests in this team.Nde anzathunu mwaterekedwa pa nkhate,akuti musalodzedwe kuvunga mwala..mkangotero,2.5 million…Apapa a FAM ayenera kuunikira zinthu zingapo..1: Mzuni siyidapezeke pa nthawi yomwe ma team amayenera kulowa ku dressing room.2: a chitetezo assigned to protect team ya Mzuni motsogozedwa ndi Time Kambalame snr officer Balaka police wakanisitsa kuti iye ndi gulu lache saadawone team ya Mzuni anywhere near Balaka stadia…3: omwe akuti atukwana/ kumwenya ma player/ official a Mzuni ndi mmodzi yemwe saakudziwika..FAM/ SULOM..athokoze kuti masapota a Nomads ali mu championship mood nde zachiwawa zikuwatalikira,kma chikhala ma team enawa,dzulo tu pa balaka pakanaphwanyidwa zinthu..anthu saangangokwera ma transport,kudula ma ticket nkulowa..kukamva kuti team ina yaulesi ikungobwera ndi ma lame excuses all the way from MZUZU..My opinion: This Mzuzu based team must not only be scrapped off the 3 points,but must severely be punished bcoz they almost put the game of futbol into disrepute…and awonetseratu kuti akumuona Gunda ngati savior.. nde they are ready to commit all sorts of mess…pomaliza,FAM thru Mr Walter Nyamilandu Must scrutinize zomwe zuchitika mumpila these days and hold a press briefing kudzudzula zoterezi…a FAM acheze ndi ma team sapotaz kuwauza kuti akamapita ku mpila,nkokachemelera basi.FAM idziwitse ma team ochepa mphamvu onse kuti ku mpila ndi ku mpila,si kokatukwanizana ndi masapota ayi,adzathudzulidwa makofi

    1. unamvapo kuti Nyamilandu ali mu committee yowona za milandu?… kungotsogoza minyozo..kamba mfundo imodzi yotsutsana ndi zimenezi

  16. kodi mzuni inga choka ku mzuzu kupita ku balaka basi osalowa mu ground popanda chifukwa ? zinakakhala ngati chotcho kuti a mzuni sanalowe mu ground popanda chifukwa pompopompo noma imayenera kupatsidwa 3 points, bwanji oyimbira mpira sanapereke 3 points ataona kuti phindi 30 zadutsa mzuni sikupezeka pa ground ,log table sinasithe ndiyomwe ija , nanga poti mzuni inapita ku chipatala ndipo ali ndi umboni wachipatala oti iwowo amenyedwadi,,,vuto ndi zikhulupiliro kwathu kuno,masapota a noma amafuna noma ikhale yoyamba kulowa mu ground nde zinawapweteka ataona kuti mzuni yafika koyambilira pa gate,, masapota a noma anayakhula kuti ” lero pafanso munthu pano” winawe nkumati mzuni yathawa game ,shame on you

  17. Nkhani ndiyakuti anayimba kaye foni kwa Mr Nyirenda aku sulom kuti atimenya mpaka anawuza pitani ku chipatala ma report aku chipatala mubweletse ndiye apititsadi panopa akudikira chigamulo cha sulom komaso aku sulom ndi atumbukaso game ikamenyedwa ku Lilongwe.

  18. Sulom amanyengerera Bullets ndi manoma. Masapota awo amapanga match fixing pomenya team inayo mpira usanayambe. Chilango chake chosaopsanso. Pa Bullets ndi karonga anakagamula kuti ngakhale Bullets yawina,karonga united yapitilira to next round, muona masapota asiya ndeu. Apanso a sulom anakati game imenyedwanso koma no sapotazi. Mukangopereka 3 points kwa noma, masapota a bullets azapanganso chimozimozi game INA.

  19. MAFANA SANALAKWE POKANA KUSEWELA GEM CHIFUKWA NDEWU KUMPILA NDKUPHANYA MALAMULO CHILANGO CHIPELEKEDWE KWA NDEWUYO , NGAT UKUNJEMELA UNEN NBB SIKUSIYAY

  20. Blantyre derby sinaseweredwe pa Balaka stadium chifukwa cha bvuto lachitetenzo………. game iyi ipangidwa replay……. had it been Nzuni yathawa game am too sure Noma imapasidwa ma points pompopompo…..

  21. Zachamba zimenezozo! iwowo akufuna kt Manoma akhale ndi mistake panthawi yomwe tikufuna kutenga 3points from them! ife anyamata athu anali wokozeka kukankha chikopa mground koma zomwe apanga apazi ifeso nde sitingalore! becauz ku mpira kumakhala kunyozana kumene akadati azitero nde bwezi kampopi fc ndi azizake aja akumenya mpira? nde bwezi ukungolepherekatu! awawa akula ndi mantha!!!!!! akudziwa kuti Nyerere pa Den sizikagawa kamba never! azawo amalowabe mground ndikumenya mpira Mulungu akakhala mbali yawo nkuwina/ ku drowetsa,afuse anzawo team doctor anamenyedwa game nkuseweredwa koma nkuluzaso iwowo awona ngati ncha? amafuna akabwera ife tiziwagwadira? ndi angati amene avulala ndikumenyedwa anene! B4ward kuti buuuuuuuuuuu!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

  22. If this is true, then teams should be playing IN the empty stadiums. Few weeks ago it was Bullets at Chilomoni and Now Noma at Balaka. But you supporters, do you know that your teams don’t have stadiums? Even training pitches you own nothing. If you don’t change, surely you will suffer

  23. Ndikudziwa Kale Kuti Ma Game Atsalawa Sakhala Olongosoka.. Match Fixing Ili Momwemo Ati Kufuna Kutenga League Basi.. Sulom, Wake Up.!

  24. Ndikudziwa Kale Kuti Ma Game Atsalawa Sakhala Olongosoka.. Match Fixing Ili Momwemo Ati Kufuna Kutenga League Basi.. Sulom, Wake Up.!

  25. Koma A Fam & Sulom Akwimitse Malamulo , Zikapitilila Zilowetsa Pansi Mpira Wathu , Sizoona Zimenezo Bwanji A Zam Anamenyedwa Koma Anasewera Komanso A Karonga Utd ? Just Imagine Munthu Kuchoka Ku LL Kungolipila Dola Yaulele Eeeish Ku Malawi .

  26. Vuto linalipo kwa team ya Mzuni fc kumvelamvela za neba ….neba kuchita kukawachingamila a Mzuni kunjira kumakawawuza maganizo ena mpaka Mzuni kuchedwa kuti ikafike pa Balaka kkkkkk

  27. Noma on top again mwava inu azathu otsalila osati ve ve kuti chani mwayiwala zomwe mumachita Ku chilomoni ground

    1. Kalonga United inamenya game ndi bullets ku Blantyre anthu ena anamenyedwako bwanji kalonga inamenya game. Sukulu yake iti ukunenayo?

    2. a phiri ngosapenya..noma pa chiongolero basi..olo tikanawathibula panalibepo mlandu,team yathu itapita kwawo anayigenda mosakhala bwino,tinatani kuthawa? mwana ndi mwana..ma level ache akukhwepa..kkkkkk

  28. nei ndikunawo tiku muti yii imapawo malankhwa japa mano imandako kukai malakhwa pa tika pa logo so nei ndikuna kut mnizu inatachi nobwi osawalo paaa yendi malankhwa a mano thawa tontchi kkkkkk

    mako kumawila mmlampi ukutitavu

  29. Masapota amateam ambiri mmalawi muno asiya kusapotera matimu awo koma kunkhala ngati woyendetsa matimu zimenezi ndizimene zikubweretsa mabvuto mmabwalo azamasewero ambiri chifukwa sapota ndi amene a kunkhala ndi mphamvu kwambiri kamba kazinkhulupiriro, NDE mfunso mkumati ndichifukwa chani? Team imapanga training osamangodalira zinkhulupirirozo bwanji? Tiyeni tisinthe kuti mpira wanthu upite patsogolo

    1. Gift Justin you better ask Mzuni why they never disembarked from their coaster.Football si phada ayitu.Iwo anatigenda ku Mzuzu ndi zimyala anaiwala kuti adzatipezatu.Palibe wamemyedwa dzulo wa Mzuni

    1. the test the ground a day prior to the game,on matchday,no team is allowed to step a foot on the ground,except for the 15 minutes warm ups,of which both teams do 45 minutes prior to the kick off…The tym for warm ups Mzuni was nowhere to be seen.

    2. Bravo Chris!!! Nde Iwo ma warm up amakachita m’mawabo? Mwina system yasintha ndiye tiyembekeze SULOM kuweruza. Thanks guys!!!

  30. masapota akumankhala ndi mphamvu kumateam ambiri mmalawi muno zimenezi ndizimene zikulowetsa mpira wamiyendo pansi nawonso oyendetsa mateam amangovera zonena sapota

  31. mpila umaseweledwa paground a mzuni anafika pa ground nkunena kwa oyendesa masewero kuti samenya plibe chitetezo ?????? bwinotu bwino,

  32. Tatitsimikizilani a Malawi 24,ndizoona kuti maplayer amzuni anamenyedwa mpaka kuchipatala? Anthu akuwawata kwambiri kunjaku,koma ndikawafusa sakundiyankha or pang’ono

    1. kupusako osazufusa kut poyamba ma points mumathawana bwanji ndi azanuwo nanga pano mukuthawana motani…..Noma kwachuluka mbutuma hvy…mumaona ngt Mzuni isekelera zopusazo?? mudikile game imeneyo mukasewera ku Kalonga

    2. A yuzuvu inu muzanizekeze ????zonizonizo!! Vuto ndikochokela a yuzuvu, ive league tatenga inuyo mupse mtima zenzen ayuzuvu muzingopita kokoka makoka ukoo.

    3. #Hule iwee Ireen uziyakhula bwino wamva iwe opusa eti…..usilu wake umennewo mumaona ngt mslamu aliyense ndi yao bass….umbuli hvy

  33. Koma kuchoka komwe ku Kaya uko kuzangoiona Balaka nkumabwelera? Mzuni penapake sinali serious.
    Nawenso Neba zomatengera zochita za BULLETS uzavulala zakusalilatu apa.Komabe kuona kwanga Neba upatsidwapo 3 yamahala basi,Mzuni yanyika yokha

    1. palibe undivomeleza alick mzuni sidathawe m’bwalo lazamaselo ndipo asananyamuke ayamba akambilana kaye nd sulom ndye wekha ukuona malamulo ndiomveka bwino nanga ngati palibe mlandu bwanji noma sanipatse mapoits pompopompo

    2. Kodi pamenepa ngati ma officials a Mzuni anamenyedwa ndikupita kuchipatala ali ndi makalata aku polisi? What if they r feigning?.Ndiku Malawi kuno people can buy medical reports but i hope justice will prevail kma Mzuni yaganixa ngat mbuzi not intellectuals mpira akanamenya under protest osat zachamba achitazi.Ife ndie 3 ptsyo tikuifuna hiyaa..

    3. 3pts Mukuifuna bcoz amzanu anyanyala schoncho..? komatu mukanasewera mpira umenewu 3pts simunakaipeza bcoz mzuni fc imakulangani kuyambira kale.

    4. Inu munamenya team doctor wa moyale mwamenyanso a karonga utd pa chilomoni ananyanyala mpira sunamenyedwe? nanga awa amaopa chani? komanso panopa mzuni singamake pa noma

    5. ?????koma kazembe alick ! Mukuchedwa tu ife 3points and 2 goals taipakila kale coz sindikuonapo chifukwa chomveka bwino apa.mzuni inali ndimaplogram ena samabwelela mpira

    6. Amadzawona town ya Balaka amenewa Team cngalephere kumenya mpira zifukwa zake zimenez izi zmacitika ngakhale Mzuniyo kwawo imapanga. Imeney ilandile chilango, even kutulutsidwa mu lig

    7. Game iseweredwanso believe it or not, palibe zapatebulo, player sangasewere mpira ngati akumva popweteka, ndichifukwa chake Sulom inawawuza kuti atseke ma gate anthu asalowe mu stadium,sizaulere apa

    8. Mmmm hedeee a Watson Chitete kod ngakuti inu?? Mukuoneka Ngat mwangofika pompano simukudziwa chomwe chikuchitika, lekani kulota ndizotheka 3 points tatenga kale ife inu zibwebwetani pot ndichikhalidww chanu

    9. Mukumamvera sports news kapena mungolakhulapo #Ireen?.Ngati a Sulom akuti akudikira ma report from both parties including Stewarts that means there is water under the bridge udekhe Neba.Ma points mukhonza kupatsidwadi koma awunike kaye chomwe chasitsa nzaye.Muzipanga ziwembu dala? ???? League waifunitsitsadi eti?.

    10. Neba Kutnga League Komvuta Wamva Kma Ndkutha Kuvesa Coz Udatnga Kale Chinthuchi Bt Czot Angkupase Usadasewele Mayaz Mwinatu Bambo Ako Aja Ali Ku Fam Aja Atachtapo Kanthu Bt To Me Ndkut Game Imeneyi Imenyedwe Kma Masapota Asakalowe

  34. Mzuni itakhala pansi inaganiza kut bola osasewera game koz league inatha kale ife manoma tinaitenga kale kale kmaso anaopa mainjalezi zikoma a mzuni popwleka ulemu kunoma kut wa bullets azipsa mtima

Comments are closed.