From Area 25 to Area 24: Malawi women still harassing each other

Advertisement
Lilongwe

A Non-Government Organisation called Family Rights, Elderly and Child Protection (FRECHIP) has condemned violence against a woman that happened recently at Area 24 in Malawi’s capital Lilongwe.

Women in Area 24 assaulted and stripped a fellow women of her clothes because one of the women’s husband picked the victim in his car. A video of the assault has been circulating on social media.

Lilongwe
A screenshot from the video

In a press statement issued by the organisation and signed by its Executive Director Esmie Tembenu, FRECHIP says women must know that when they strip a fellow woman, they are somehow stripping themselves since women are biologically made in a similar way.

“Secondly you are discrediting your husband instead of protecting him. We are further advising married women to be protecting, upholding and defending their families when they suspect something bad from their husbands.

“Married women must further sort out their marital problems in a decent and orderly manner,” reads the statement.

FRECHIP has advised women in the statement to be finding better ways of solving such issues rather than violating other women’s rights.

The organisation says when a woman suspects a husband of messing out with another woman, she must have proper procedures of disciplining him rather than taking action which will bring a negative impact on them.

“We are further worried about the protection of children who see their mothers through social media being stripped like that and also the protection of children whose mothers behave like wild animals in this case, just because a dad offered a lift to the victim in his car.

“The barbaric way in which these women acted towards a fellow woman is condemned in its strongest terms. The law educates us not to be taking the law into our own hands. That is the reason why the Malawi Government established law enforcement offices like the police, Ombudsman, courts, human rights organizations etc where these women could have lodged their complaints and be assisted than taking the law into their hands,” reads the statement.

FRECHIP adds that striping or assaulting and insulting a woman suspected of messing around with a husband is not the best way of strengthening marital relationships.

“There are marriage advocates and other elderly people like faith leaders, chiefs etc who can discipline a cheating husband,” adds the statement.

The incident in Area 24 came days after some women at Area 25 in the same city urinated on and assaulted a fellow woman after accusing her of exposing one of the women’s HIV status.

Advertisement

183 Comments

 1. Azimayi mwalowa mkati tsopano zee word yakupundulani inuyo musanachinditseko??

 2. Mwano wa azimayi pakhomo ukumatipangitsa amunafe kukapeza chibwenzi kunja kuti mwina mkumapeza oseka naye.
  Ndiye azikaziwa akadziwa m’malo moti afufuze bvuto lawo iwo amakalimbana ndi mzawoyo.
  Shame on these bastards women. Had it been kuti mwaminayo ndinali ineyo, banja ndikanalowa naye tsiku lomwelo.

 3. To me I was very ashamed & shocked when I see the video of this innocent woman,who assaulted her fell women…What is it?A khoti ayenera apeleke chigamulo chokhwima chifukwa azimaiwa avula amai onse mMalawi muno.Pogamulw asanyengelere coz akadakhala kut wachita izi ndi mwamuna sakadamunyengelera…Mwamuna amene umavaisana nd mkaz ameneyi mokupempha mutenge basi.Akazi enawo ndi Afiti.

 4. Koma nde kupasula banja ndi manja uku sinanga kunachuluka ndi kudzifila kumati ndinu eni zinthu, makonka ndeno palinso ukonka apa? Mkazi amene Ali konka kapena mweni zinthu salonda mamuna wake!

 5. Komatu azimai manyumbamu mumamupanga dala mamuna kuti azithawa kumapita kunja kukusiyani chifukwa cha umve Wa mwano umene azimai ena mukumachitira azimunanu. Matayilira, kaya kumakhala kulizolowera banjalo nthawi yoti muthangate mamunanu, kumuchengetera inu malenga zopepera pena mkumati madzulo, madzulo akafikaso muvekere mbanda kucha. Mukatero mamawa kungobamduka pogonaso, mukuona ngati azibambo amasangalala nazo? Nalo Dziko lungokondera azimai. Awa okha asatuluke ataaaaaa. Azimuna pakhomo pao pomwe kukanika kukhalapo chifukwa chazimwano ZANU, mukonda ma WhatsApp group kuleka azimunanu. Awa akangowatulutsa za usilu ofunika kuwatentha aja awa. Zonyasa izi iyaaaa

 6. Our moral’s have completely gone down azimayi sitiyenera kuvalana ngakhale zitavuta bwanji apa ndiyekuti amayi tonse tinadzivula ana athu atilemekeza bwanji ,zikalakwika tiyeni titsate njira yabwino yothetsera mavuto athu

 7. boma laziwasopano kuti azimai ndi akhaza heavy laona kuti amunaifeo ndi abwino kwambili kuteloko azimai alindi khaza kwabas aona okha omwe amaimilila azimai koma Ali abambo chocho akulephela kumusangalasa mamuna nyumba sopano mamuna akapita out azipanga sanje mwaona aboma inu langizo azimai siyan matama akadzi achuluka omasukaso bwino kuposa zomwe mumapanga zinja

 8. Just waiting to hear the punishment desrved for these pathetic ladies. Im still surprised and shocked seeing a woman being victimised like that. I feel sorry for this poor mom. May God strengthen you.

 9. That victim lady must not be condemned here guys because she’s innocent until proven guilty. This is sad. And the law doesn’t allow to punish someone like that.

 10. This is what fools do really. She punished this young woman just like that and yet no evidence? But stupidly enough she took a video which is an evidence to punish her back. Justice must take its course.

 11. This is not the first time .Mwayamba ndinu kukhala pabanja? Muzifusa azimayi akuluakulu akuuzani ulemu umazipatsa wekha mwadzizuza.

 12. Koma sizoona mkazi ndiofusilidwa bwanji osalimbana ndi mamunayo bwanji or ngati alidolo akanagotenga chiwalo cha munakecho aziyenda nacho komanso kt muone azimayi amamunthandiza kumenyawo ndi ma hurenso zatikwiyitsa zimenezi watiyalutsa ndi nsanje yake yamanyiyo alandile chilanga mamuna ndiye onyengayo

 13. Nzomvetsa chisoni komanso nzochititsa manyazi azimai kuchita moteromo. Nditaonera koyamba sindinakhulupirile. Ndinaoneranso pomwe ndinagwidwa ndi mantha kuti Malawi a kupita kuti , Ambuye alowelele mdziko mwanthu muno siziri bwino.

 14. Nditawonera modekha ka clip kameneka ndagwidwa ndimantha kwambiri ndipo ndikupempha akhothi kuti chilungamo chiyende ngati madzi chomuzuzira mzawo mwamtundu woterewu chikhara chani???? Atakhara mayi wanu kapena mchemwari wanu olo mwana wanu kumene mungamve bwanji eeeee zandiopsa kwambiri

 15. More less like the Dark Age. Or else too much freedoms? These are the aftermath of Midoli, women have joined the bandwagon of liquor gulping.

 16. So sad killing a fellow woman because your husbands infidelity! zangoonetseratu the level of illiteracy we are having mmakwalalamu!

 17. Apandiye urusi ukudusa mmene wadusa zingano 1choipa chisata mwini 2 andione andione anakharira zakezomwe 3 tinkumbire adankanawo 4 kuno kwathukomwe adakagona kumaura 5 osayesa kutengera ramuro kumanja uzavutisa banjarako uzabvutana ndiboma 6 ukanama sikuchedwa kucha

 18. Ayenera akagebe bas…pempho langa kwa mwamunawe chonde unkwatire mkaziyu ukudziwa kale kut chikheba chakochi chamulakwira heve,,,,ndipo azimayi kumazifusa nokha mumawona ngat mwamuna anakulengerani nokha? Ngat wakukwatira kukusiya pakhomo kumayamika sikut ndinu opambana aliko anzanu okongola owoneka bwino km akusowa mabanja,,nde chikhebawe kumaseweresa banja hehehe!! Uziwona ukazeweza Maula aise……

 19. These women must b severly shaped into adesirable shape so dat they shud be alesson book to those who r also intending to do such evil things all in all these r disgrace

 20. Next is Area 23. Khalidwe lomwe akupanga azimayiwa ndi la ufaka mpweya. If women bully one another, what will men do then? Such actions give room for gender based violence to continue happening in our localities

 21. zinsezi nchifukwa choti amunafe ndife ochepa ndiye opanda amunawo akangoyesela kudya nawo zanzawo akangogwidwa akumamva kuwawa.

 22. I like the way most women have reacted to this issue. That’s what we call solidarity. Two wrongs don’t make a right. These women are indeed evil and must be punished severely…

 23. Kumenya munthu like that? These women needs a stiffer punishment. The court should give them enough punishment. This is totally inhuman.

 24. Amenewa apite kokaona mbwadza, angosonyezeratu kuti ndi olephera kumbali yochengetera mabanja awo koma nkhanza ngati zimenezi.

 25. Ineyo zandimvesa chisoni kwambiri ndipo ndi ka video kolilitsa nkhanza yomwe apanga azimai amenewo akuyenela kulandila chilango ndipo ndili ineyo ndimusiya banja kuuma mtima ngati osabeleka chinchija bwanji. Mamunayo amusiye ndi mai oipa ameneyo

 26. Za ziii,zinasalanso zokanganilana amuna,sakundifuna sakundifuna basi,pomwe anali lu labour mayi ake ndinawathandiza,ahaaa kukumana okula kula ahaaa.pa ndekha ndikhonza iyaaa,nanga mpaka ndikazipase mavuto motere,bwanji ndingomanga sanza zanga nkumapita,kaya ndi tomatoe ndizikagulitsa,moyo nkumapitilira……

 27. Nkhani izi zimakhala ovuta kumvesa basi aliyese tingoti ndiolakwa thats y azibambo ambili amapha nkazi komaso ena amazimangilira tili masiku omaliza basi timuziwe yaweh

 28. Iwoso amachindisa koma kumampyeteka mzimayi mmmmmmmmmm amalawi where are u going with ur life pls check first ur characters before doing this stupid evil otherwise u will be in stiffer life for ever.

 29. Can’t you tell that this is not something you should be sharing on a national page. It’s the image of Malawi you’re ruining here. Yes this is happening and it’s not wrong to share about it but hide the lady’s privacy and edit or hide her like what is this???

  1. How does it feel? And how do you know am not? You think all Malawians are the same or every Malawian would do this??? If you as a Malawian feel that this is right that is just you and I know a lot of Malawi oti sangapange zinthu zotele. Pa Facebook pali anthu a mitundu yosiyina oti they don’t even know what Malawi so this one act is not supposed to define what being a Malawian means becuse it is wrong and not in the pride of any country let alone an African country

  2. You have a point Gman Gasore, we are so much blinded by the grave act which someone did forgetting how much more wrong we get through our publicing of these events. You really think u become more Malawian by exposing ur own weaknessess and shaming ur own? U only expose ur lack of knowledge because whoever is going to laugh will at Malawi with u inclusive

  3. Exactly. Good example, Kenya attracts tourist and the get money from it just like Malawi or any other country. Few years ago when a terrorist attack hit their Mall they reported the story and Made if clear that this was not Common in Kenya and that it had been handled. If it was Malawi they would put caption “Vampires in Malawi” as if that’s a common thing instead of clarifying “suspicion that there is a blood sucking activity in Malawi” not reporting a story before it’s even proven. Like I looked at the photos posted on the news and it looks like they cut with hands it’s not even vampires, two that story happened before election again “nachipanti” the story seems political. But. Is every is treating the story as if we have Dracula in Malawi sucking blood every night ? please report things the way they’re don’t try to make people laugh or sad coz it will affect a mass number of innocent individuals

  4. Instead of sympathizing with the victim by simply writing a story, you further show nudity of the same victim. That’s double insult. Guys you wouldn’t want this happening to the people personally known and care, would you?

 30. To Say The Truth.. These So Called Activists,had It Been These Ladys Were Men Something Could Have Been Done!! I Tell U..They Would Have Acted Quickly!! Koma Chifukwa Choti Ndiwaakazi!

 31. Sibwino kumupanga mzawo khaza zotere ngati mwamuna wanu ndi hule ndi hule basi ndipo ndi mulungu kuti mwaziwano kuti amuna anu ndi a hule ukazamagwira wakuba ndekuti wakubayo anayambira kale kuba Mayi inu amuna anu ndi hule uyo ndi mkazi iye ndi ofusilidwa iye akanatani azimayi omwe mwamupanga khaza mzanu you hear me you must be very stupid.amabungwe mupange Kathu sangatenge chilengedwe chazawo kuchisiya poyera ndipo azimayi omwe amupanga khaza a police awamange akayakhe komaso amulipire malamulo adziko lamalawi agwire ntchito amuphere ufulu mzawo kodi azimayi onse akupanga uhule kumagona ndi azimuna ayini ndiye ekha amabungwe mupange kathu zawo amuyalutsa bwanji asakamutengera kupolice kulibe apolisi ndakwiya nazo

 32. They deserve death or life sentence or even be killed for this horrendous act.But the said part is that no matter how many life sentences they gets, that poor woman will always be torn and broken mentally, physically emotionally and spiritually and no amount of justice will ever change that. Oh!my Lord God come soon.

  1. I agree with u Mr…. the mark these women have left on a fellow lady, will remain for ever. And she will leave in no peace at all, She will be subject to ridicule and all sorts of negative things the entire of her life. I personally feel for this victimised woman. And she needs compasation despite what ever sentance the evil ladis will get…

 33. Women need to respect each other no matter what. This is behaviour shows some women are agents of the dark kingdom. Repent and let Jesus Christ save you

 34. Let them Stupid Ladies face the reality.An eye for an eye.Aone chinameta nkhanga mpala. Sangamutelo nzawo ayi.So they think they are on top of the world? Ayiwone bangwe

 35. Takhala ngati ine ndi ngangokwatila mkaziyo wamenyedwa kuthetsa winayo kuti apse mtima zenizeni …akalowe mu chitokosi basi khanza azimai amenewo

 36. Koma azimayi inu ufit zoona nzanu mungamutelo?? Munthu kupepesa konse kuja koma kuchita kumuumila mtima chonchija mmmm zandikhuza hevy koma Mamunayo Ngat ali hule ndi hule bas mawa apita kwina,iyi mwapanga apayi si solution bwanji mmasiya kulimbana ndi mamunayo?? Mwinanso akumakuthawani mmakomo mwanumo chifukwa chosowa khalidwe,koma ndili Ngat ine mamunayo ndinakamukwatila yemweyo omenyedwayo kut tione ndikusamalika kwawoko. Iyah zandinyasa hevy chikhalidwe chanji ichi? Ngat ukumuona kut mamunako sakuyenda bwino iwe osamusalila kudya kumupephelela bwanji? Kod pali chomwe chingamulake ambuye ?ana anjoka azinkhanila inu.

  1. Wamulongezela katundu wake wakasiya kwawo ati akatuluka kupolice kwakeko angoyenda streat wakwawo banja lathela pompo. Zochititsa manyaz izi aaaaa Ngat alibe umunthu zoona

  2. Ngati wamulongedzera ndi mamuna wazeru ameneyo, vuto loti msika ukatha ndikupeza banja ndilimeneli umangokaikira zilizonse.

  3. Azimayi amenewa mwina ndisataniki zomwe anachita apa munthu wa chibadidwe chaumunthu sangayaluse mzimayi mzawo mwanjira ngati yimeneyi. Akuyenela kupelela compensation. Ngati approach sunayitenge bwino olakwa amasanduka innoncent chifukwa cha approaching.

  4. Ndipo inenso zandinyansa zomwe apanga azimayi amenewa.mamunayo anamubala ndiwowo zausilu basi osakathana ndi mamunayo bwanji aaaa ine andibowa mapeto ndipo amangidwedi

 37. No chill in capital city zi azimayi zouma mtima anga phongo.
  What shocked me chomudulira nzawo mikandachooooo akuti mwina mamunayo amatsata mikandayo hahahaaaaaa chiwewe azimayi a Elazi.
  Komanso zalowa umbuli akujambula vedio yoti iwaika okha mmavuto

 38. Chikhalidwe chilikuti adzimayi,where is our country going killing each other. discusting what these ladies did to fellow woman these is not Malawi ,I now

 39. kod chmakhala chli chan azimai kuthamangra kuyalutsana like that? asawasekerere amenewo wakucell basi kmaso akakhale mucell yaabambo akaone mazangazime

 40. azimaiwa nkona amuna akumakupangani nkhaza ngati nokha nokha mukupangana izi how do u expect men to be nice to u stupids

Comments are closed.