Mawa ndiye kuli Moyale ija inawagweba ndi kuwapilikitsa mu chikho cha FISD.
Lero ndiye Chitipa ndi iyi yaliza nyerere.
Sizili bwino ku manoma pamene lero alephela kuikamo olo chimodzi chenicheni pa masewelo amene amakumana ndi timu yomwe ili pansi penipeni pa ligi ya Chitipa United.
Pa masewelo amene anachitikila pa bwalo la Karonga limene alitsegula kumene, manoma akhumudwitsa owatsatila atasowa mwayi obooleza kuti atolele ma pointi atatu.
Zimaoneka ngati nyerere sizivutika potengela kuti Chitipa ili pansi penipeni pa ligi ndipo ulendo wawo otuluka ukukhala ngati ndi okonza kale.
Koma nyerere ayi ndithu zinakanika kuluma ndi kumangochinya pambali kapena pa mwamba kupitiliza kupsetsa mtima owakonda.
Anyamata a nyerere amene akhala akuonetsa mbwadza anzawo akuoneka kuti lero analibe ukali.
Mawa lamulungu, nyerere zikhala zikuphana maso ndi maso ndi Moyale imene inawakhoma mu chikho cha FISD.
Usadanene Ulinde kaye madzi apite ndipamene uziti ndadala
Ulipo
Yaona mbwaza ndi silver nanunso muli mmalawi koma?
Sorry neba
Lembaninso nkhani ya moyale kkkkk mphenzi siibwereza kawiri
Anthu aku chitipa chimene amadziwa ndi Ku khwima vuto palibe zinayambira kwa ng’ono wathu pa Mzuzu stadium bolani anthu athuwo abwera bwino moti ndikunena pano abwerera Ku BT ndi 4 points atayimenya Moyale pa HOME
Uyoooooo watilira
Pelekan uthenga momveka, osat monyoza. Uko sikutumikira aMalawi.
Lero agwebedwatu!!
Kkkkk NDE lero yawinatu NDE ukuti bwa? Ndikunena iweyo umalemba post ineneyi haaa wakhaula
Wachita manyazi iwe simulungu ayi
Kodi anews Noma imakumvetsaniso kuwawa eti nde talembanitu za moyalezo panopa
Adm Khalani ozisata 0_0 ndikuona mbwaza ngati inalowa mu super lg imeneyo ndiyayikuluso so thats beta result we are moving forward noma 4life
Zitsilu nose anyani agalu mbuzi a24 kuyambila bwana wanu kutelo pa mbuzinu
lero ndiye amubilibinya
Hahahaha wakhaulatu iwe
Kkkkkk Nancy tikubilibinya tokha
Kkkkk kumbukira KT mamuna nzako MPA chulu
Koma za ife ukuziwa kale kuti game yagona kkkkkk
Kkkkk lindani madzi apite NDE muziti mwadala
Hahaha Bullets ndi second round tikuzingaso kachitatu
mbwadza drawyo iwe mbuzi et
Galu wachabechabe iwe
waganyu iwe panga zako
Kodi aganyu mukadachulukirabe koma ganyu yanuyo izakuphetsani kupanga drow ndiye chifukwa mutawonere lero tikunkhazulani muwona mawule wamkamka basi a bb pano angonjenjemera ngati mavu pa chisa chake kuti akumaneso ndi akulu akuluso
24 mzeru mulibe,,Mbuzi
admin osavinidwa iwe kkkk
Malawi 24,,,ndinu makape simuziwa za mpira ntchito kulimbana ndi Noma matimu ena apanga draw muli ziii koma Nomanoma (stupid )
This week silver yiwalani kuti muwina guyz, you must know that your going 2 loose
Admin achoke saonetsa mbali pa group ngati ukufuna udzimuthandiza danger pa times muchuruke ansanje& noma bwanji
iwe 24 panyini pamako umakhara ndi bali bwanji
Kagweleni uko a 24
Kkkkkkkkkk ooodiii ukooo lelo moyale ikudyaso mwa neba kkkkk usova neba!!!!!
NDE wakhaulatu kkjkkkkk
Nde yadya?
mapazi ake azikang’a ameneyo always Noma osamakamba za Embassy fc bwanji? silver yapanga draw ndi blantyre united koma sukukamba kathu koma always Noma why?
Ukati wamkulu waonesedwa mbwaza ndiye kuti taluza game bullets inapangapo draw zikusiyana pati
kkkkkkkkokoo Neba amunyula cheya kkkkkkkkokoo akumatumbwa amenewa ndpo sanafike kkkk
Paja Galu Amawuwa Galimoto Loyenda…Loyima Kumakhala Ziii….
empty tin make noise ngati mbuzi dza bullets
Noma 4 life
Lelo manoma kuwina basi
Apopedwa mag mako moti iweyo timu yako sinaluzepo mamina mmutu
Nothing has changed on log table though its a draw ndiye mukuti chani apa
atumbuka muzkomenta zom veka APA!
ukungoona za manoma zokha, ndeye kuti sugona nayo tu kape iwe tidakali pa top zikuwawabe
Kkkkk
Kkkkkkkkkkkkk kumwa wothra soda
Lero ndiye Moyale…abwerako ndi 1 point
Silver yapanga draw koma muli busy ndi Manoma Hahahahah team iyi imakumvesani kuwawa Manoma the wise people’s choice
Nkhani sikutimvetsa kuwawa mayazi nkhani ndiyakuti inuyo mukamapita koyenda kaya muli pa home mumatokota kwambili ndizomwe zikupangitsa kuti anthu akutsatileni ndi mulomo wanuwo.Pajatu amati ukayenda siya phazi ukasiya mulomo udzakutsa.
Hahahahah man mawu mumatipasa ndi inu
Asiyeni Man,chirichonse cha noma chimawamvetsa kuwawa…
chitsiru ichiiii
Ndimamva kukoma noma ikamaludza
Taonera Ena Amvera Mpira Wa Athakati. Ena Nkumat Ngongoliwa Fc Ena Akuti Ayi Koma Akhale Namapopa Fc Poti Zonse Nzamasenga.
Manoma chaka chino ndi chathu mufune musafune
Chitsilu chachikulu ndi iweyo Sonia Wa A Chemwa
Collins Samalan zampira izi osatukwanana
Silver ku mwera yabwerako ndi 1 pamene Manoma ku mpoto 4
koma noma ayayaaya
Palibanso pano opikisana nafe
mmmmmmmmmmmmmm. Hwooooooooo ine nseru
Kkkkkkk sanza
Yaona mbwaza ndi team ya amako ase, kaya akutuma unyaaaaa .NOMA 4 EVER
Zayenda kwa ife
Malawi24=Mbuzi mind
Munathamau Bullets itadrawetsa ngat inuyo mumadoda kuposa bullets. muonanso lero ndimoyale aphwathuuuuu…saizi yayamba kuthina pang’onopang’ono ndipo simunat ithinad zenizeni mpaka mutayambiranso kumakodzera pagolo mwina.
NDE wakhaulatu kkkkkkkkk
Noma 4 ever
Iliko lero. Kkkk
paja timuyi idayamba ndikulira isadapite ku mpoto. wanderous ngw’engw’engw’e-ngw’engw’engw’e!!!!
Kkkkkkkkkkkkkk kuwapitikisa haha kd anatuluka at ndiona ngat ikumana ndi mabagalaz2 kkkkkkkk silver
muli pachiyopsezo ma man
Za ziii. ..don’t you know that it’s a game of football? ?mapazi ako ndithu
Azioona achilephera chikhoci angosogola nawo chikwa achilaweko,
admin MBUZI…
Anyanawo eeeershiiii munthu Wamkulu kwambiri kkkkkk
Inutu wanu ulipo lero nde linda mazi apite kumatokota bwino Nebour.
I can see admin wa pano z against noma ndithu…zolemba zakuthera sungamakambeko nkhani zina koma uzingokamba za noma bas?? Shame on u ndithu noma stl on position udziluma ku msana kwako komwe tsopano
Hahahaha
Zanu izo muthana
ndiye ganyu ameneyu wakuva neba ubwebweta zenizeni mawa tikutenga 3points ndie neba minibus yakoyo ikugwa kudzenje iyo mabwebweta uziona chaka chake ndichino ndie usaiwale neba mulandu uja waliripila ?
Ikanaluza nde mwano ukanageyedwa weniwenitu .
mawa moyale inyika n it is a must: Noma 2-0 Moyale
Mwazolowela kuķodza pa golo afiti inu!
U will be suppress when wanderers carry day tomorrow. No doubt iwina
Amafuna akasewerere pa Balaka ground kuti awine
So bad..
admin wa Malawi 24 amakhala chitseka khomo ndaphunzira naye ku primary ine. Mmutu mulibe kalikonse. Anapopedwa magazi ali mmimba mwa make.
Eeee kuyankhulatu! Kkkkk
Ife tikuthokoza cozi 1 yo tinalibe ndipo watikankhalaso kwakuya
Mbwaza????! nde ikanakhala kuti yaluza ikanaona chani? Haha admin mfundo zikusowatu apa! Noma 4 lyf!
kodi watha bwanji??
Akuti Ndiwe Namapopa?
.mwat …aigweba….kkkkkk kkkkkk ok
mbwadza zake ziti mukuzinena apazi @ Malawi24. Noma yaluza???
Koma galu imeneyi. Tiona mawa tikawina kuti udzanena chani. Poti ndiwe galu umayiwala msanga eti.Moyale tayichinya kangati ife.Kulibe timu ingasewere ma game anayi muma ola ochita kuwerengeka.Ngakhale ku England kumene Conte ndiyomwe amadandaula atasewera champions league tuesday kenaka saturday ndikukumana ndi City.Ngati umautsata mpira galu iwe ukudziwa zimwe Conte amadandaula. Nanga kulibwanji kusewera ma game anayi mosatidzana.Ubwino wake tiludze kaya kuwina sitiyendera zamaganizo ako nyani iwe wamva.Tidzakondabe Manoma mbuzi iwe wamva
Unafa Maso Imeneyo Nditimu Muthu Wamamuna Umangasate Team Imeney Pot Mwana Ndi Mwana Zomwe Amachit Samaziwa
Hahahaha koma ndiye mwapsa mtimatu Hahahaha koma sulila.
Nde Sudati,nanga Lero.
ķkkk #Collins akumapsena mtima zomaposita anthu enawa
Lolest,,,BULLETS Still Remain The Favourites To Win The 2017 Tnm Premier League Championship..
Saturday(21-10-17)
MADRID – Barcelona will offer Lionel Messi a lifetime contract at the club, CEO Oscar Grau said on Saturday.
Messi, 30, agreed a four-year deal with Barcelona in July, although has not officially signed it yet.
Grau, speaking at the club’s annual general meeting, said the Argentine forward would be offered a similar deal to the one Barca’s Spanish midfielder Andres Iniesta signed this month.
Following
pakhosi green green ngati jersey yachitipa.Noma 4 lyf
Admin iwe ndiye wanama ngat ife anoma taona mbwaza bwanji tidakali pa chiongolero mu ligimo 51 points zimenezo iwe sukuziziwa
Pachiongolero Nthawi zonse
Chokani apa mwazolowela zomamwana magazi basi ku Karonga nakoso ndi chimodzimodzi. Mwaluza vomelezani kuti ana akukunthani asa, kukhalira minyozo basi Voetsek zano
Watsala kumbuyo ngati matako iwe game inathera 0~0 ndiye waluza ndi ndani?
Kutha kwa 0:0 yoluza ndi team tayikuluyo
Haaaa sudziwa kuti mukafanana mphamvu ndi draw lero udziwe
Mesa mumati yina ndi team yayikulu, nde mphamvu zingafanane bwanji
Draw kumati mbwaza?umazidziwa mbwaza iwe kape?
Nyerere zapopedwa MAGA. . . . . Nena Malizitsa wekha lol
Pephero langa ndilakuti Moyale isanyike mawa
nothing strange coz samatha mpira ndipo league sangatenge moti abwelerako ndi 1 point kumpotoko ngati DPP kupeza 1 kkkkkkkkkk noma sizampira mumangodziwa kupelekeza yotenga ndi BB zikavutitsitsa Silver winawe iwalako
Eeee BB ndi Chitipa yomweyo I nabwerako ndi 6 points eti? Osamaiwala neba. Anakukhaliliraninsotu musstumbwe apo bii simukidziwa cox simuzitsata.
wachepa aixe ine ndiye ozitsatayo mmesa mumkatiseka titadrawer ndi chitipa kenako mkuluza ndi moyale inuso mudutsa momo mubwelera ndi 1 point
Wait for 90 minutes. Mpira sitisewera pakamwa.
Kk Neba
Kkkkkkkkkkkkkkk
Tawamenya Kangati Caka Cino?Kut Mpaka Muime Paculu Mkumat aja anawagweba aja aaaa!!
hahahahahaha kaya!
Draw ndikuona mbwadza? Admin be serious
kayatu, umbuli bac
che bulesi nawoso mesa anabwera atapanga draw ndi chitipa yomweyi,koma lero mau phee poti ndi noma.
Kape ameneyo bwadza amazdziwa neba yamuwawa ameneyo
Amfuna tiluze ukunama
Alindi mbali ameneyu
Yaona mbwadza noma? yagonja ndizingati sindinatsatire magame ose lero
Zimvere mutolo uthanenso ndianamapopa ndi zikhulupililo zakozo
aziwona amenewo
Chokani APA asaaah! ni team wuli yambula kwendela juju pala yikusewera bola??
Use whatever you can afford in order to get the results.
wakambwe imwe!!!!
Kkkkkkkk wakambwe?
kambwe munywamu yowe,,lihenga uwe,,kuyoba sha bushutano mutu
Sizimveka
Even man u ku england yaonaso mbwadza.
Hahahah
Drama pa Karonga Stadium. Zinayamba mateam akuchokera kopumira. Ma official a Chitipa amayenda ndi kamwana ka zaka 12 kuchokera ku dressing room. Chodabwisa chinali choti mwanayu amamupasa ulemmu komanso chitetezo chachikulu. Izi zinadabwisa achina Yona Malunga, butao ndi mabaunsa ena a noma omwe anafunitsitsa kuti mwanayu asatuluke ku dressing room. Anafunisisa kukamenya kamwanaka koma zinatengera apolisi about 12kukapulumusa kamwanaka. Bata linabwerera. Chamma 60 minutes, mpira unatuluka pafupi ndi mzere wapakati, panthawiyo nkut golly wa Cp utd anavulala. Ted sumani anasekesa anthu atatola mpira nkuthamanga nawo mmanja ngat rugby kukauponya mu net ya Cp utd. Abel mwakirama ataona izi anautola mpira uja nkuthamanga nao kukapanga chimodzmodz pagolo la noma. Apa nkut ref ali busy ndi golly wa Cp utd.. Chinanso nchoti Chipuwa anadabwisa anthu pomwe amakakamira mpira umodz wokha pa mipira 8 yomwe imagwiritsidwa ncthito. Bolera akamupatsa mipira inayo iye amaikana mpaka wakewo ubwere. Ref anampatsa yellow pachifukwachi.. Ndathira pano *_Lenokisi_*
Koma ndiye zinalikotu kumeneko
Kkkkkkkkkkk Juju Vs Juju!!!!!!
KKKKKKKK KOMA YAA AMAMWELA PAMOZI ANAWA KKKKK
Mwanayo is 14 yrs old anali pa beach there nothing wrong with dat noma ndiye aini ache a juju.apa anakumana ndi okwima zake kkkk
chule iwe,anatenga mpira ndi player wachitipa ngat nkhan simukuyidziwa kumangokhala chete,,,mpira unali live pa zodiak nde ngat wakhuta kwambiri kuli bwino kugona stop using your unus wen spkng
Iweee omvera pa radio ndi owonera pa stadium ungamvere ndani.. ine nnali pompo kuona ndimaso… siza Zodiak zaakozo apa
KKKKKK KMA KUMENEKO
Mmene munakwiila inumo radio mungavetsetse bwino?
Kamwana Kadoko Kawatondeka Kukatima So Kasi Na Moyale Waluzenge Nadi Muhanya Uno.Haahakkk Kumva Kukoma Pamkana Tachiyowowa Cha Kukaya.
Sidzikuveka ukut chani