Inu amene mukumadzuka usiku ndi kumakolezera moto pa nkhani zopopa magazi, samalani chifukwa Apolisi ayamba kunjata anthu a mkhalidwe onunkhawu.
Mkulu wina wa mu boma la Zomba walamulidwa kukakhala ku ndende kwa miyezi itatu chifukwa chonama kuti kuli anthu opopa magazi.
Malinga ndi Apolisi, a Bambo Stanford Bamusi a zaka 49 anadzuka pakati pa usiku pa 16 Okotobala ndikuyamba kukuwa kuti mmudzi mwawo mwabwela opopa magazi.
Anthu adathawa m’nyumba mwawo ndi kukagona kutchire ati poopa kupopedwa magazi ngakhale kuti mderalo munalibe zimenezo.
Apolisi atamva izi, adamunjata mkuluyo ndi kumutsekela mu chitolokosi.
Atapita naye ku bwalo, iye anapezeka olakwa pa mlandu ofuna kudzetsa chisokonezo ndipo walamulidwa kukhala ku ndende kwa miyezi itatu.
Ngakhale mlandu otele munthu amaloledwa kupeleka chindapusa, bwalo linakana.
Latest vacancies
163 thoughts on “Amunjata chifukwa chonama za ‘anamapopa’”
Comments are closed.











it’s true that there is blood succer and believe it but now it is going to ended by sinio tchief ngolongoliwa in thyolo.
Fuk da so-called police
PLZ BOMA LIKANACHITAPO KANTHU KUCHEPESA /Kutheselatu nchitidwe uteleu ,chifukwa Iwo aliphe muzinyumba zawo ,akuvutika ndi anthu akumidzi ,
Kuzibitsa kumeneko!
Apopedwa ambili upite m’mlanjemu. Ena mpaka Kumwalira ndhye iwe ngat abaleako Sanakhudzidwe ay wadala
Dilussionnal
the police and local peopl in areas where remours are spreading on the issue should work hand in hand to findout the truth otherwise more innocent people will lose lives for nothing;our MP,do ur job professionaly
Tithokoze aboma mwayamba bwino amangeni amenewo zitsiru za anthu zikuphetsa anthu osalakwa
Gyz enanu mlindimzimu koma?Nkhan yopasa chison ngat imeneyi mungamat ikukukwanan ena mpaka kukupasan mselu akupanga zmenezi mkwadziwa inuyo yet?Osanapanga coment yopusa apa ngat mlibe mawu just read and pas dont coment those no ncence here
Asiyeni azitizunza choncho tionana 2019 wina adzagwapampando chifukwa cha nkhani imeneyi. Ifeyo amalawi tikudziwa anthuwa akudziwapokanthundithu bwanji asakubwerapoyerandikulongo solazamavuto amenewa anthutu sitikugona tikukhalangatianthuothawa nkhondo. Malawi watiipilakwambiri asatiopsyezeakuphqufuluwathu olankhula pazovuta zomwe zikutisautsa. Koma 2019 tidzagwila ntchito yotsitsapampandowina amalawi siopenga zikutinyansa ubwino wake ayambakalekuluza 2019 tizatsitsa Nyanimuntengo magazi athuwo awasiye.
eshi mzungu mpaka zammusiza apolis?
Mmmmmh
Kodi opapa magaziwa bwanji sakumapita kwa akuluakulu andale komanso achibale a apolisi ndi asilikali nkumakaazunza mesa akufuna evidence pamenepo mpomwe adadaipeza mwachangu osati kumangoazunza amphawi coz zayamba kutembenuka sopano.. instead of helping the victims..u r now arresting them..why??
Guys I think it’s miracle money that causes blood sucker in Malawi
Last days indeed.
Amangidwe amenewa, they are bringing confusion
Amunjatlanj Pamene Nkhaniy Ndiyowona? Akufuna Aiphiphilise Anthu Azipopedwabe Mwakachibisila. Akuziwapo Kanthu
good idea police arrest them, kudzolowela ndiwawa basi, why keeping govmnt restless since 1994, bakili mbuli mbuli, bingu arogant, joyce cashgater, pitala nde chilichonse chamugwela, Pano Tayamba Kujiya Ya Chakwela 2019 yinyamuke naye tidzamusautse kkk. nyumba yikupsa, usi wudzioneka.
Kodi ndizoona kuti mpaka pano umboni siunapezeke? Ngati zili nchochi nkofunika kuti apolisi atengepo action pa hearsay imeneyi, mbiri ya dziko isamangoipa pa zinthu zopanda umboni.
If it is not true how come that it was in mulanje now Blantyre that means anthuwa ndi amisala? Ok president amakatani ku mulanje amakayendera anthu okhuzidwa