No blood suckers in Malawi – Police insist

Advertisement
Malawi

Police in the Southern Region have insisted that there are no blood suckers in Malawi despite claims by people in the region.

Commissioner of Police in the Southern Region Demister Chigwenembe made the claim during a Healthy Football Fiesta organised by Dignitas International (DI) aimed at encouraging people to go for HIV testing.

Malawi PoliceChigwenembe took advantage of the event to comment on reports of blood sucking in Mulanje and Phalombe.

In his speech, Chigwenembe said people from the two districts should not panic since this is just a rumour and nothing of such kind has happened. He added that the origin of the rumour is not yet known.

“Please people from Phalombe you shouldn’t be living in fear, there are no blood suckers. But if you suspect someone that is doing such a thing please don’t take laws into your hands, bring him to the Police,” said the commissioner.

Chigwenembe’s advice has come following reports that three innocent people suspected to be blood suckers were killed by an angry mob in the tea growing district of Mulanje.

The reports have also affected people in Nsanje where villagers recently killed a chief after accusing him of working with blood suckers.

 

Advertisement

161 Comments

 1. zikuwoneka zophweka kwa ongomva,kwa okhuzidwa izi ndizovuta,munthu wina sangakayikile ntchito za mzake atamudziwa zochita zake,zobisika zija zilipoyela…zabwino zikuvumbulutsa zoyipa,anthu kulusilana,amantha akungokuwa,owumamtima kuletsa anzawo asamauweuwe,wopondeleza akungopatabe… zikuwoneka kuti aliyense wapenga, kuwoneka zonama pamene ena akwililidwa,ganizani bwino utsi uwu wafuka bwanji…

 2. UKAKHALA PABWINO UMATI KULIBE MAVUTO KOMA UKASAUKA NDIPAMENE UMAZIWA ZAMBIRI, MUKUTI KULIBE OPOPA MAGAZI CHIFUKWA MULI KUTAUNI MUBWELE KUMUDZI KUNO MUZAONE TIKUGONA PANJA IFE KUOPA M ‘NYUMBA MOKHALA MWATHU .

 3. So why osamanga zigawenga zomwe zimapha anthu osalakwa Ku Mulanje uku???? Zama albino zinayambira komweko izinso komweka vuto ndi chani umbuli kapena chani???

 4. Iam tired of this DPP government,kuba,kupha albino,lero awa opopa magazi.Akana bwanji kuti kulibe opopa magazi anthu oti samakhala kumeneko?Munthu waku Lilongwe ndi Blantyre kungodzuka ndikupita kukawauza anthu kumeneko kuti kulibe opopa magazi zoona?anthuwo ndi openga?#mfundoless#

 5. Kulankhula kopusaku ndie anthu aphedwadi nd2 bcoz ur sayin az if anthu akunena zot mchitidwewu uliko they are brainless

 6. Vuto corruption yavuta pamalawi koma ndikanakhala mfiti ndikanakuphani nonse amene mukulankhula zanonsesi,mupindula chani anganya inu

 7. The problem is that the blood suckers are using magic in their process. However government does not recognise the existence of magic or witchcraft, so it is difficult for it to admit to blood suckers existence.

 8. ur saying that, becoz those blood they haven’t come to ur house but when they came to ur house u I’ll agree that there’s blood suckers

 9. Even they were insisting the assuming of graveyards believed to be for albinism at the beginning in machinga TA nyambi but later they accepted l hope they have a problem

 10. Kodi Mesa Kuli Atola Nkhani? Bwanji Akuleka Kupita Kukalankhula Ndi Munthu Yemwe Wapopedwa Magaziwo Kut Anthu Tidziwe Zenizeni?

 11. only if either one of the police or relative has been blood sucked they could be convinced otherwise the police depend on their own findings | evidence

 12. with such statement 4rm our police their is no guarantee that we have security in the country. this an insult to those parents, brothers & sisters of those victims. may God The Almighty interven.

 13. Pliz amene mbale wake wapopedwa magazi andiuze ndidzamuone bcoz ndinayamba kumva zimenezi ndili mwana koma up to now sindinamuonepo munthu opopedwa magazi.Pliz guys help me

 14. Hummmmmmmmmm mere talks.Police are the very first Law breakers.I just wonder where people are still getting the energy to trust police men.Police men are best friends of thieves and all kind of law breakers.If they will reach the extent of taking someone to court, it means he was either cought publicly by a mob or He has failed to pay them a little bribe.But if they have cought someone privately, they’ll just ask Him to give them a little money and then they will free him.Blood sukers are Just everywhere now and No country is exceptional. Have you forgotten how people with albinism were being killed by malawians? Are those killers different from blood sukers? Blood sukers are everywhere.

 15. No blood suckers ok anthu tigwirane manja tiziphabe mtundu umene ukupopa magaziwu with aim yozawauza a police kuti akamafufuza amene wa pha anthu amenewa tizitinso kulibe amene akupha anthu

 16. Nkhani iyi kwa munthu amene amaitsatila ndiyopatsa chidwi. Ndiliwachichepele ndipamene ndinayamba kumva nkhani imeneyi ndikapita kumudzi kwathu ku Mulanje, nthawi imeneyo ndimkafusa & pano ndimafusabe kuti mwina mpovuta kuwagwira mkupezeka ndi umboni anamapopawa. Koma sindinawoneko mu nthawi yoseyi munthu atabwera poyela mkunena kuti ine kapena uyu amupopa magazi usiku. Nkhani iyi imandikumbutsa nkhani ya mphutsi. Mma 90’s kunaatchuka nkhani yoti kwayamba matenda amphutsi ikumadya chiwindi boma linawononga ndalama zambiri kufufuza za nkhaniyi mapeto ake inapezeka kuti ndiyabodza.Munzinda wa Lilongwe munatchuka nkhani yoti office inayake akulemba ntchito azimuna oti apite ku DRC kukabeleka ana, kufufuza zinapezeka kuti ndizabodza. Ine ndimalakalaka tsiku lina atazapezeka munthu yemwe wapopedwa magazi. Lero lino pakachitika ngozi yapansewu anthu amathamangila kujambula ovulalawo ngakhale asanawathandize nanga bwanj zithuzi za anthu omwe apopedwawo sizikuwoneka?

  1. Simunawonepo munthu atabwela poyela kuti wapopedwa magazi?Osadandawula Man Chawona mzako chapita mawa chili kwa iwe,moto umapita kwatsala tchire,tchire lotsalalo ndi inuyo amene sanakupopeni akadzakupopani or wachibale wanu akadzapopedwa mudzadziwa koma nkhwangwa itakugwelani kale mmutu.Zanachipanti pachiyambi anthu amati chani?

 17. But why r you not doing something with those who are responsible for killing innocent people, you’re just coming and telling people about this,you want all visitors to be killed?

 18. Malawi kuchuluka zitopotopo kobasi wapha albino nthawi yayitali wapha adazi wadula ziwalo lelo ukupopa magazi kodi ukufuna chini kwemikweni? Shit mw onunkha iwe fork

 19. A police akumalawi achitsilu inu agalu anakugwidwa kwambwiyanu inu mwahongedwa ndindrama aunt aine apopedwa magazine dzana lomweli ndie mukuti kulibe opopa magazine pacahkuti panu mwamva kaya kukhuta ndramazo zitsilu zanu sindimakuopaninso nonse pamodzi ndi msogoleli wanuyo dziko lauve ngat limeneli lokhomelela sindinalionepo

 20. Boma nkhani izi savomeleza ayi.ku mulanje kuyambira 1988 kuli Congress amandifunsa kuti wamuona bwanji.unali ndindani .ukapitiliza kunena bodza tikumana kapena usowa. Nkhaniyi siyachilendo ayi wapolice akudziwapo kanthu.

 21. I Wonder Wether We Have Police In The Country.They Have Poor Investigation Techniques They Wil Rather Asks Chief A Paramount And A Senior Chief What They Get Are The Same Answers We Hate To Hear. Ine Nalema Navyo Mwee Check This Out!!!!

 22. I Wonder Wether We Have Police In The Country.They Have Poor Investigation Techniques They Wil Rather Asks Chief A Paramount And A Senior Chief What They Get Are The Same Answers We Hate To Hear. Ine Nalema Navyo Mwee Check This Out!!!!

 23. Amalawife eish,kusonyeza kuti achipatala,apolice atolankhani ndi ena onse ofufuza onse akunama zoti kulibe opopa magazi koma anthuwo ndi omwe akukhoza? Amene akuti opapa magazi alipo,chonde tamaperekani umboni wakuti munthu wakuti wafa amupopa ,wakuti amugoneka kuchipatala amupopa atolankhani bwerani mudzaone.Tisamangonena zomwe ena akunena ayi

  1. Ndi zimenezotu atolankhani ndi ena ofufuza a Blessings Phiri akuti mukaone ku zipatala za Phalombe,Mulanje Thyolo ndi Chilazulo akuti kumeneko akuti alipo hmmmm Malawi ndi anthu ake

 24. It’s magical & pple r not mad to keep on claiming about this issue , thumbs up to the killers no need to take suspects to police akapereka ndalama nkutulutsidwako azitsogola basi osawanyengerera .

 25. Wapolisiyo alive uboni okwanila iye amakhala muofisi anthu amaboma a Nsanje ,Phalombe ndi Mulanje aziona ndi maso ,bwanji sanapange Chaka chatha izi zikuchithika bambo bwanji adazi so .chomwe ndingaphepe kwa anthu onse akapenzeka anthu otere olo mafumu aphedwe basi

 26. despite all the talk the beating the killing , the badmouthing on the authorities, not even a single person, repeat a single person has come forward kuti wapopedwa magazi, or auje apopedwa magazi, olo mmodzi…….whats going on?

  1. MIJ yinapita kuphalombe ndikumulanje palibe mumodzi anatchula kuti wapopedwa kudziwa umboni sizitengela kukhala konko braz.

  2. Bwera Kuno Ku Phalombe, Ufike Pa Holy Family Mission Hospital, uwafunse a ward attendant kuti mwapanga admit anthu angat opopedwa magaz akuwuza. guyz blood sucking iriko and its true pliz musamalese mwamva

  3. koma inuyo mwamuona olo mmodzi kuti ndi uyu wapopedwa magazi? olo ndizongouzidwa zimwezi…..am saying this coz kuntenga munthu magazi is a process, without kuchita kusakasaka nkuupeza nsempha its impossible, one needs to cooperate when giving out blood, i stand collected koma zikundivuta kumvetsa honestly

  4. kodi Albino amaphedwa aja inu munamvapo kuti akut Nsika wake uli kwakuti? Amalawi makani ngati ofula agalu bwanji?tiziti nonsenu ndi amzeru kuponsa anthu omwe akugona panjawo?ngati ndiza bonza bwanji boma osapitisako asilikali kuti azikayenda yendako usiku bwanji?

 27. The more they are dismissing the more they are losing interest to follow the issue and the more people are punishing the blood suckers by themselves. our police are useless, and its becoming usual.

  1. The more they will accept the baseless rumours the more the panic, the more the fear,the more innocent people suspected for that will die . Bedtime stories, stories we used to hear during our primary school.

  2. Ooh what you are saying means the police are afraid, because to me if they accept they’ll act but if they dont people will be panic and afraid as you are saying.

  1. up to now the police are falling to tell us why people are being killed in mulanje as the are dismissing that they are not blood suckers, then who are they?

  2. Stupid police,kodi mesa anthu ozachita zinthu zoyipa mmudzi amayamba awonana ndi inu kaye.nde ndindani angayembekezere uthenga odana ndi mchitidwe oyipawu?mbuyomu ku blantyre(ndilande)kunalinso nkhani monga yomweyi,koma police inatenga nthawi kuti itengepo gawo.nde izi zinthu nza usatana,zimabwera ngati za bodza komanso sizichitika mmadera ambiri.

  1. Munthu akapopedwa, apolisi akumamuwuza kut asamanene, blood suckng iripo and apolisio akudziwa koma safuna kuvomereza. inetu ndimboni wazimenezi. neba wathu anapopedwa ndpo tinathamangisa nao wopopayo, musamalese mwamva

  2. Moti inu muli ndiumboni ndithu onena kuti munawaona anthu achiwembuwo? Nanga kwa anthu amene akuphedwawo ndiangati amene akumapezeka ndimagaziwo ngati mukudziwapo kanthu tiuzeni ndithu

 28. How do u know that there is no blood sucker’s those cops they mustn’t lie to us if ther is no enough evedince @be petience the trueth it wil come out!! wonder shall never end

 29. POLICE OR GOVERNMRNT CANT SAVE MALAWIANS COZ THEY ALSO BLEED BUT GOD WILL VINDICATE US SOME DAY. IF THEY SAY THERE ARENT BLOOD SUCKERS HOW CAN THEY PROTECT THEM? VILLEGERS CAN MAKE BEST POLICE.

 30. ndikhulupira izi ndi zamathenga nde police ndiya zamalamulo.tsono ndikhulupira kut police ikukana izi kamba zot sikumapeza umboni ooneka kuti munthu apopedwadi magaz panja amakhulupira umboni.thats y ndikunena kut izi zikumapangika mwa masenga choncho nde masenga ndi zamalamuro sizinhagwile.pafunika matsenga kwa matsenga kut zikhale ndi umboni kut anthu akupopedwadi magaz.kuina kwanga ndikumeneko.

 31. Existence of Blood sackers’ are difficult to justify and it’s absurd for police to quickly make such a statement without elaborating the opposite side of it. Remember in the 80s Kamuzu was haunted by bees( Njuchi) at Nkando because spirits were not happy with forced Msonkho and Party cards on its people. Napolo in Phalombe most perished. During campaign of by-elections in Rumphi central where Enock emerged a winner, Bingu was welcomed by strong Kamvuluvullu( whirlwind) that he failed to hold a rally at one centre. I strongly rule out completely police public statement.

  1. Ngakhale ine mene ndimayamba ntchito people suspected me being a bloodsucker, pakufunika civic education ku community komanso anthu azikhala ndima umboni okwanila when reporting issues chifukwa ngati zili za matsenga police officers can’t explain accordingly

  1. Ant police!!! What about the Media MIJ FM went there through zilipati program and concluded that there was no evidence.Unamva ndani akunena kuti ine pano ndimapopedwa?

  2. #BEN_THOMBOZI yes they did investigate..and concluded that there no blood suckers.. Now the problem is that instead of goin to the affected areas to tell the pple the outcome,angotisokosa pa wailesi basi.nde u expect kut akumudziwo adziwa bwanji zakafukufuku wao?

  3. Chimene chikuoneka apa ndiumbuli waanthu akumudzi kumene kukuchitika zimenezizi,funso mkumati wagonekedwa mchipatala ndani kt wapopedwa magazi?wapezeka atafa ndani kt wapopedwa magazi?ndinali ku chiradzulu pa 27 chama 4 am mnangova zidebe kulira kufunsa ndichani akt paja kuno kwatchukanso mkupopa magazi,zoonetseratu kt anthu akuphedwawa ngosalakwa,malawi watani malawi

  4. Pajatu ananena kale.kuti akufuna Boma dziko lawokha.koma makani.ngati sutha kulankhula chilomwe usayelekeze kuyenda usiku uphedwako

 32. Join this international whatsapp group. we do
  encourage one another the word of God. many
  have testified thru this group. Jesus will touch
  u in a special way. halla me on
  +260953234122. Shalom!

  1. amalawi mundikhumudwitsa mutengeka za ziiiii just because wakuwuzani people are testifing za ziiii ndili pa app but cngapereke my digit

 33. That’s why people are panishing anthu oganizilidwao ndipo akapitiliza kukana many will lost their lives.Maybe they know something yet anthu akufa?nonsense!!!!

 34. That’s why people are panishing anthu oganizilidwao ndipo akapitiliza kukana many will lost their lives.Maybe they know something yet anthu akufa?nonsense!!!!

 35. there’s no smoke without fire,u knw its true bt what can u say when ur bosses are saying the same en ur nat going thru wat we are goin na sleepin

 36. the question is what are you, the police, doing about it? it’s clear this whole “blood suckers” thing is a belief to those in Mulanje and surrounding areas, which means “civic education” will hardly work. It’s like trying to convince a christian that God doesn’t exist. What a golden opportunity to put the competency and professionalism of the Malawi Police Service to test.

  1. HOW CAN THEY CIVIC EDUCATE US? MMMMMMMM? WE ARE THE ONES WHO CAN CIVIC EDUCATE THEM. DOES THE GOVERNMENT OR POLICE SLEEP WITH US DURING NIGHT? IF NOT SO WHY DO SAY THERE ARE NO BLOOD SUCKERS. CHULE ANADABWA MMADZI MULI MWAKE.

  1. There is sense in your nonsense, komano funso mkumati usi ungafuke popanda moto?,abale Ku MULANJE, thyolo and phalombe tskupeza tulo chfukwa cha akanganya amenewa

  1. Ndiuzeni mmodzi wapopedwa magazi ku mudzi kuja ndikufuna akandiuze zomwe zimachitika bcoz ndinayamba kumva ndili mwana koma mpaka lero sindinamuoneko ngakhale mmodzi.

  2. Ndekut gulu lonse limene mwaotchalo ndilopopa magaz ??? Ndipo so mumaliza liti ?kupha anthu osalakwa ndipo so mukumaotcha anthu chinthu chot mulibe umboni why zinthu zomvetsa chisoni kwambiri

  1. Since the birth of these rumours, is there anyone who has been sucked blood and there is evidence
   I remember well that even when I was young, these rumours were there during the early winter but non had come on the open and say ‘they have sacked my blood’
   I personally don’t believe it.

Comments are closed.