Traveller fined for carrying Rands


Machinga

The Mwanza First Grade Magistrate court on Tuesday ordered a 38-year-old man to pay a fine of K15,000 for being found with South African Rands.

According to police files, the traveller has been identified as Innocent Chiyagwaza.

On Monday, Chiyagwaza was travelling to South Africa and when he arrived at Mwanza border post, officers searched his bag and found 6000 South African Rands.

He was asked to produce documents for possessing the said cash but he failed to do so and was arrested and taken to Mwanza First Grade Magistrate Court for hearing.

At the court, Chiyagwaza pleaded guilty to the charge of illegal possession of foreign currency which is contrary to section 25 of the Exchange Control Act.

He was then ordered to pay a fine of K15000 or in default to serve six months imprisonment.

Chiyagwaza comes from Kalonga village, Traditional Authority Mponda in Mangochi.

Latest vacancies

112 thoughts on “Traveller fined for carrying Rands”

  1. Inu akhoti muziganiza ali ana anu akupangidwa zimenezo ndi ena munganve bwanji muziganiza popanga zinthu muziziwa kuti kuli Mulungu, Namalenga mphambe akukuwonani izo mukupanga

  2. Mphutsi Government Manyaka enieni kuzolowera kuba ndalama za anthu ozipezera okha Apusi
    Mudzandipange ine ndi ka section kanuko nzakumangitsa nakoni.
    Osakamanga Chaponda anapezeka ndi over 40 thousands mnyumbayo bwanji?

  3. so which is whch ,in 2009 at mwanza anandimanga ndikundilanda ndama zanga Mk90,000 atichifukwa ndinadinditsa passport ndisanasinthe cash to foreix mpaka pa khoti anakandilipila 20,000 ati ya chindapusa pa mwamba pa ndalawa yanga ,sono uyu ali ndi sweet rands yake walakwaso,kodi ku south africa amasintha rands to kwacha ,may u dont know that malawian kwacha is a flat curruncy ,dont do that guy sweet rands ndiyovuta kupeza

  4. pa 21november ndizadutsa pa mwanza bodapo ndi madollar anga ndiye tizaone ngati muzandigwire,tikuzunzika ku RSA kugwira ntchito kuti titukule malawi,ife kuno timaitanidwa ndi maina ambiri mbiri ngati awa ;khwelekhwele,amazayizayi,mangongongo koma sitimadandaula bola tipeze chomwe tikufuna.iwe umasecha iwe ubwele kuno uzaone ,mwayamba usilu

  5. Koma Malawi Ali ndimalamulo augalu iwowo okha anauza boma la South Africa kuti tizionesa r3000 lero wina watenga yoposa imeneyo akuti kulakwa ,,,zaugalu,,,,,mwafikapo etiii ? ,,,Kusauka sikuzatha chataputa abusa mbusi ngondolo angangawenu yala wipii jamanja wawiyi etiii

  6. Umphawi tidzafa nawo aMalawi boma lathu limalimba ndizithu zoona pake mumakhala kale mukudziwa kuti ngati munthu kuchokera ku S.A. kapena kupita ndekuti akuyenera kukhala ndi ma Rand nde vuto lomupititsira ku khothi ndichiyani? A police ake amachita kudziwika kuti ndiakuba. Malawi sadzathekaso ndithu. Loma umphawi uli thooo! Shame.

  7. My question? Why do Malawians show 3000 rands in cash at every boarder unlike Zimbabweans or Zambians or any other nation in Africa?Don’t you think this puts Malawians travellers at risk of been robbed and killed.Cant you come up with something else apart from 3000 rands

    1. Malemu Bingu ndamene anatipalira moto potuma akweni kuti auze boma la RSA kuti tizionetsa R3000.anachita izo poona kuti akuononga ndlama kutumiza ma bus kudzatenga amalawi othawa xenophobia.koma it’s long gone anayenera kufewetsa lamulo limeneli

Comments are closed.

Discover more from Malawi24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading