Traveller fined for carrying Rands

Advertisement
Machinga

The Mwanza First Grade Magistrate court on Tuesday ordered a 38-year-old man to pay a fine of K15,000 for being found with South African Rands.

According to police files, the traveller has been identified as Innocent Chiyagwaza.

On Monday, Chiyagwaza was travelling to South Africa and when he arrived at Mwanza border post, officers searched his bag and found 6000 South African Rands.

He was asked to produce documents for possessing the said cash but he failed to do so and was arrested and taken to Mwanza First Grade Magistrate Court for hearing.

At the court, Chiyagwaza pleaded guilty to the charge of illegal possession of foreign currency which is contrary to section 25 of the Exchange Control Act.

He was then ordered to pay a fine of K15000 or in default to serve six months imprisonment.

Chiyagwaza comes from Kalonga village, Traditional Authority Mponda in Mangochi.

Advertisement

113 Comments

  1. Dziko lathu ine sindilivetsa,moti kupezeka ndima Rands ndichifukwa, mpaka munthu kumangidwilapo zoona.Mulungu akuone basi.

  2. KOMA NA KUMALAWI KUM’BELA MUNTHU AKUONAMASO. KOMA INE WINA NDIYE NDIDZAM’DULA DZANJA NDITHU. ANZANU KU ZIMU NDIYE ZM DOLER ANACHOTSATU AMAYENDELA US DOLER NDI RAND MUKUINENAYO NDIYE MUDZAYELEZE ENAFE. MPAKA DZIKOLOSE LAPASI LIDZADZIWASO.

  3. Inu akhoti muziganiza ali ana anu akupangidwa zimenezo ndi ena munganve bwanji muziganiza popanga zinthu muziziwa kuti kuli Mulungu, Namalenga mphambe akukuwonani izo mukupanga

  4. Mphutsi Government Manyaka enieni kuzolowera kuba ndalama za anthu ozipezera okha Apusi
    Mudzandipange ine ndi ka section kanuko nzakumangitsa nakoni.
    Osakamanga Chaponda anapezeka ndi over 40 thousands mnyumbayo bwanji?

  5. so which is whch ,in 2009 at mwanza anandimanga ndikundilanda ndama zanga Mk90,000 atichifukwa ndinadinditsa passport ndisanasinthe cash to foreix mpaka pa khoti anakandilipila 20,000 ati ya chindapusa pa mwamba pa ndalawa yanga ,sono uyu ali ndi sweet rands yake walakwaso,kodi ku south africa amasintha rands to kwacha ,may u dont know that malawian kwacha is a flat curruncy ,dont do that guy sweet rands ndiyovuta kupeza

  6. pa 21november ndizadutsa pa mwanza bodapo ndi madollar anga ndiye tizaone ngati muzandigwire,tikuzunzika ku RSA kugwira ntchito kuti titukule malawi,ife kuno timaitanidwa ndi maina ambiri mbiri ngati awa ;khwelekhwele,amazayizayi,mangongongo koma sitimadandaula bola tipeze chomwe tikufuna.iwe umasecha iwe ubwele kuno uzaone ,mwayamba usilu

  7. Koma Malawi Ali ndimalamulo augalu iwowo okha anauza boma la South Africa kuti tizionesa r3000 lero wina watenga yoposa imeneyo akuti kulakwa ,,,zaugalu,,,,,mwafikapo etiii ? ,,,Kusauka sikuzatha chataputa abusa mbusi ngondolo angangawenu yala wipii jamanja wawiyi etiii

  8. Umphawi tidzafa nawo aMalawi boma lathu limalimba ndizithu zoona pake mumakhala kale mukudziwa kuti ngati munthu kuchokera ku S.A. kapena kupita ndekuti akuyenera kukhala ndi ma Rand nde vuto lomupititsira ku khothi ndichiyani? A police ake amachita kudziwika kuti ndiakuba. Malawi sadzathekaso ndithu. Loma umphawi uli thooo! Shame.

  9. My question? Why do Malawians show 3000 rands in cash at every boarder unlike Zimbabweans or Zambians or any other nation in Africa?Don’t you think this puts Malawians travellers at risk of been robbed and killed.Cant you come up with something else apart from 3000 rands

    1. Malemu Bingu ndamene anatipalira moto potuma akweni kuti auze boma la RSA kuti tizionetsa R3000.anachita izo poona kuti akuononga ndlama kutumiza ma bus kudzatenga amalawi othawa xenophobia.koma it’s long gone anayenera kufewetsa lamulo limeneli

  10. Malamulo opusawa achotsedwe ndithu, malamulo amakezana alipobe. Ndiye nditatulutsa ma dollars anga ndimasungawa mundimangatu.?? Anthu openga mwapanga bwanji.?

  11. Guys, pena pake tisamangotukwana. Ngati sitikudziwa malamulo ndibwino kufunsa bwino bwino. Dziko Lili lonse lili ndi limit ya foreign currency.

    Eg, here in Mozambique, it is 3000MZN yomwe ili eligal pa boarder. Ngati timalowa ndindarama zoposera pamenepa zimangokhala kuti lamuloli samalikokomeza especially mmaulendo a pansewu. Koma kwa amene amakwera ndege ndikupita dziko lina atha kundivomereza.

    Tiyeni tichipetse kunyozetsa dziko lathu. Of course silikuyenda bwino koma kwanu ndi Kwanu. Enafe tilikwa eni coz kwathu zinthu sizilibwino. Koma sometimes I cry for my mother land.

    God bless our Malawi. Proudly Malawian in the foreign land.

    1. Man malamulo amalawi amawona mbali amagwira ntchito kwathu wosaka ngati athu akutukwana achiita bwıno nduna idapezeka ndindalama zakunja koma kopanda chotika.

    2. Kuno ku South Africa anthu ali ndi Botwana Pula, Malawi kwacha ,Zambia Kwacha, Nigeria naila, Mozambique Metico Palibe wamangidwa

    3. Simukundimvetsa big. Sikuti anthu samakhala nazo. Koma ndimulandu. I am not defending kumangidwa kwa munthiyo, koma zonyoza Malawi ngati kuti sindife akumeneko it’s total bullshit.

    4. Kwathu ndikumwanza ine anyamata amasintha ndalama pamwanza boarder alindindalama zakunja mtundu uliwonse koma samangidwa chifukwa amakomana kumowa mwinanso ndiamene anamuwulura

    5. Athu wose amene akunyozawo ndiye kuti zikuwawa mumtima dzikolathu lilimanja mwasatana chifukwa muthu amene wamangidwayo ndimuthu wamba ndiyekuti kandalamako amulandaso. Ndiye ndiuphawi wadzawoneni. Man chisale alekeni athu atukwane.

  12. Hello everyone am happy sharing this with you, am not suppose to be doing this but i can’t hold back my joy so i have to share with you, you too can be help just as i was helped by Dr Odudu who cured me the HIV virus after suffering from it for some years and CD4 count was very low i was depressed, i was desperately in need of getting rid of it, but the ARVs were not helping so i was eager to contact Dr Odudu who gave me his herbal medicine, today as am posting this i am HIV negative, don’t hide your sickness or else your sickness will hide you, contact Dr Odudu today so that you see a reason to back through the years of your depression and smile to yourself, you can call or whatsap him with his number (+2349067902914)or call +2349066604928 , pardon me i offend you with this post, but i must share this good news

  13. So unfair…chaponda anapezeka ndindalama za kunja… zokuba but you did nathing…but this poor person mpaka kukhoti pandala yoipeza movutikira eish…there is no justice in malawi….munatipweteketsa kale ndi ma3000rands owonetsa munjira pomwe anazathu amangodutsa mosavutika bkla they gat valid passport…amalawi munakhala bwanji kodi….nde munthu wadutsa bobho from beilt bridge …zimbabwe boarders…mozambique boarders ndi ma rands mosavutika…zoona mukamugwire pa mwanza atafika kwawo….like sereously….eish

  14. Bcz is a black Malawian he deserves to be fined? Yet Indian s carry ahuge amount of other countries currency and cross our borders even at airports not being fined.Mr magistrate here in RSA kulibe Makwacha. So mukungoyenera kuwamvetsa anthu kuti akamabwera or kuchokera ku RSA akuyenera kukhala ndi ma Rands

  15. What nonsense is this? So I can’t travel with my own money to another country and it was 6000 Rands going to a Rand country was that wrong?

  16. Ine ndili kuno kuvutika,ndayesa kusunga kanga kuti mwina mwana wanga tsiku lina adzaone bwino,tima Rand tangato ndamanga tsono mundipeze ndi za thukuta langalo inu a Boma mufuna mudye nawo ngati tinkathandizana ukapolo uli kunowu? Mulodzedwa

  17. Kuno a SAPS akakusecha mmatumba mkukupeza ndi makwacha amakusiyila ndipo ndichizindikilo choti uyu ndi mmalawi ngakhale passport utayisiya . Kotsalako amangokutiza kuti ndalama yadziko imeneyi mpaka ma zero onsewa??? Umoyo mkumapitilila patheba. Ine ndikubwera ndi R250 000.Cash. Khalani okonzeka ndilamulo lanu labodzalo ndidzakwela Munorurama ya Lilongwe pa 20 December. Zikomo ndatha ine wanu. Mwadziwe Ayao Abisamanga.

  18. Malawi amadana ndikuti mbadwa itukuke. Boma lakuba potiwopseza ndi lamulo labodza. Nafe amalawi tidanyanya kugona tulo. Dziko lathu ndilogona kothelatu. Ndimkana wapolisi amayenda ndi ndodo chigawenga kuyenda ndi mfuti. Munthu adali kudziko la south Africa moti kubwerela kumudzi asapezeke ndi ma Rands.? Kupezeka ndi ma Rands moti ndi mulandu? Amalawi tidalakwanji????

  19. Malawi 24. penapake muzilemba nkhani ndikuimaliza kuti tikawelenga tisamakhale ndi mafuso opanda mayankho. mwamulipilisa chindapusa cha k15000 , naga ndalama zake mwamupasa? naga bwanji mwamulipilisa ma kwacha pomwe iye wapezeka ndi Rand? mukamava kuba ndiye zomwe mwapangazi? wa police adamugwilayo, judge, ndiyemwe akukupasani mphavuzo nose ndinu …… what is R6000 after all. ine ndiye muzandisekelaso chifukwa ma Rand anga sindigalole kuwasintha then after ndikamabwelaso muzandigulise mondibela.

  20. How can you charge aperson coz he carries a foreign currency? Did he steal the money from MALAWI BANKS? To change money through BLACK MARKETS is legal in Malawi while carrying foreign currencies is ILLEGAL, shit yooooo

  21. Eish pa Malawi ,malamulo a boma amagwira ntchito kwa amphawi basi ,okuba ma billion ali phee akumwa coffee uku akuseka chikhakhali akamawerenga nkhani ngati izi

  22. Cockroaches! kuba basi! and you can’t escape from the punishment prepared for you, I mean you, the oppressors!! Sanabe nzake ndalama anagwira yekha ntchito. You don’t know how hard is to find those Rands here in RSA

  23. mmmmh, are you saying that, in Malawi you can’t convert your money to other currency…kkkk you are still living in 60s

  24. Kkkkk mesa adapita ku joeni kukasokola chuma ndicholinga chakuti akachidyele dziko la kwawo ndiye wapezeka olakwa bwanji pa ndalama zake zomwe?

  25. How does this work if you’re visiting SA and have Rands? BTW this is a BS law, all money is just IOUs and fake + exchange control is communism.

Comments are closed.