MDF to have new cars in two weeks – APM

Advertisement
MDF

President Peter Mutharika has said motor vehicles which government has bought for Malawi Defence Force (MDF) will start arriving in the country in two weeks’ time.

Mutharika made the remarks when he toured Cobbe Barracks in the old capital city of Zomba.

Peter Mutharika
Mutharika says the men in uniform play a pivotal role in safeguarding the country.

According to the president, the men in uniform play a pivotal role in safeguarding the country hence they have to have perfect means of transport.

He said shortage of motor vehicles derails the performance of the soldiers which is bad for the country.

Speaking at the same function, MDF Commander General Griffin Supuni Phiri asked Mutharika to construct new houses for the soldiers.

Phiri said the soldiers are using old houses which are in bad condition.

He further hailed Malawi Defence Force soldiers for being disciplined. The army general said Malawian soldiers are also hailed in countries such as Democratic Republic of Congo and Ivory Coast where they go for peacekeeping mission.

Among other dignitaries who accompanied Mutharika include Malawi’s First Lady Gertrude Mutharika, the country’s Veep Saulos Chilima and Chief Secretary to Government Lloyd Muhara.

 

Advertisement

146 Comments

 1. Mr president u made the mistake,don’t look forward look the police there walking along distance bcoz they don’t have car’s buy car’s 4 police thus it

 2. Inu galimoto za chan ku MDF – dziko loopa nkhondn ngat ili, why cant u just fund them to orphans & oldones!!! Shupit zanu mwamva! Pena pake mumandikhumudwisa Mr. P moti vote yanga muiwale…….

 3. Otsawapatsa magarimoto mwalo mowagulirila ma Ambulance kuchipata a Army amagwira ntchito yanji kuMalawi kulibe khondo eaither buy police

 4. We can not work without security.Its a gud move,we should not take things for granted.Many business in mw are accompaned by police and mdf eg,mobile bank.Incase of opponents attack should mdf walk several ours to rescue its citizens?

 5. Buy more sophiscated weapons sir inclds advanced air defence systems for defensive nature incase we hav bn attacked, more attacking weapons aswl

 6. mr president ,can upls fix our roads .our roads are sub standard,our roads are dengerous to drive .the soldires can wait,we are 50 +yrs independent but our country is still one of the poorest countries in the world.if we can fix our roads and electricity am sure malawi can come out of the stuation we are in.

 7. Heey mr president are talking about these old fashioned cars? They were used in the Gulf wars some thats 25 years back.So you said as they are new in the world of military service. They are old fashioned mr president don’t cheat Malawians.They r new in Malawi to other armies they r useless. They are white elephants to us Malawians.

  1. According to world armistice our weapons my friend cant match with some Africa countries. Imagine how poor Malawi boarders are.

  2. Am with you Anthony,anthu awa sadziwa ntaaa,adzipanga check ku google zinthu ngati izi,most powerful military in the world and apeza zambiri kumeneko awone kuti nzotani,kuno ku Africa kuli maiko kaya ndi 5 amene amapanga match pang’ono zedi ndi maiko akulu akulu,maiko ngati Egypt,Kenya,SouthAfrica,Nigeria kungotchulapo chabe,ingakhale North Korea makani onse akuchitawa powopseza America iwo aja sali mu Top ten ya maiko amene ali zinthu za nkhondo, America imapanga top pa zambiri, and budget ya America pa za Millitary its almost 700 million/yr,second ndi China 100+million/yr, check the difference betwn no 1 and 2, Russia ili pa 3 ku budget za millitary ans so on. Kumafufuza anthu inu

  3. chimakhala chobuntha komanso chimakhala kuti chidachoka handle so chimavuta kugwira mmanja.End result mmanja mumapanga matuza (blisters) waiona bro so enemy akhoza kukugwira pakhosi so you can luz the fight. kkkkkkkkkkkkkkk.

 8. Bwanji magalimoto amenewo agawane pakati ndi apolice ,kupolice kuli mavuto amagalimoto kuyambira fone Ku police umva galimoto yachokapo kapena iri busy kusonyezeratu galimoto nzochepa mapolice’mu asilikaliwa mbali ina ali bwino magalimoto ali nao.

 9. Apa wakula ndi umbuli kusadziwa komanso kusaganiza. Chitetedzo chikachepa mdziko ntchito zina siziyenda bwino kupanda chitetedzo mchiyambi chamavuto even tikopa bwanji ma campany akunja kubwera kudzayambitsa ntchito muno abwera bwanji ngati mulibe chitetedzo ndizambiri zomwe zimafunika kuti mdziko mukhale chitetedzo

 10. Apa wakula ndi umbuli kusadziwa komanso kusaganiza. Chitetedzo chikachepa mdziko ntchito zina siziyenda bwino kupanda chitetedzo mchiyambi chamavuto even tikopa bwanji ma campany akunja kubwera kudzayambitsa ntchito muno abwera bwanji ngati mulibe chitetedzo ndizambiri zomwe zimafunika kuti mdziko mukhale chitetedzo

 11. hahahahahaha koma amalawi ambiri akuchita oppose nkhani yabwino ngati iyi ndi ambuli ndithu. are you sure mpaka pano simukudziwa ntchito yotamandika kwambiri yomwe atsirikali akugwira? zooti kwakhala kukupezeka ma bomba mmalire a dziko lino omwe cholinga chake ndikuphwatsula dziko lamaliwi lino simukudziwa zimenezo? ndipo ndi atsirikali omwewo anachita detect kugwiritsa ntchito zipangizo zomwe anagulilidwa ndi boma komanso mabungwe, komanso ndimagalimoto omwe boma likufuna kuonjezera pano amene anapangitsa kuti asilikaliwa akafikepo pamalopo mwachangu ndikuphwetsa mabombawo, kuteteza iwe ndiine kuphatikizilapo iwe okula mutu usakuona kufunika kwa atsirikali’we. mabumbu aamanu agalu inu. mwandikwiitsa kwabaasi, kodi mukukumbukila nthawi yomwe samora machel amafuna kuotcha dziko lathu labwinoli? ndipo ndi atsirikali omwewa mogwirizana ndi maiko ena akutifunila kwabwino, anamuonetsa chimphenene. pano mukandiuze kuti atsirikaliwa ntchito yawo siikuoneka? pamanyini paamanu ndithu.

 12. aliese amene akutsutsana nd kugula ma galimoto a silikali akuika umbuli wake poyera. osamatsutsa chifukwa cha umbuli koma muzitsutsa chifukwa choti tanthauzo kufunika komaso kuipa kwa chinthucho mukukudziwa. vuto mumasapota ndale koma muli mbuli za ndale.

 13. Koma mudziuze dzitsiru zanuzo dzimangomenya anthu osalakwa chifukwa munthu wavala kabudula wansalu yachisilikali.Kaya nkusowa nkhondo kaya dzausavegi ngati kabudura uyu nkumati wavala uniform yausilikali?

 14. Zochitsiru basi mmalo mogula ma ambulance bizy kumagula magalimoto asilikali adakuuza mndani kuti kumalawi kuli nkhondo uziyendako mzipatalamu iziona odwala mmene akuvutikira iwe ndiwe mbuzi eti

  1. Kkkkkkkkk! Shoot’n without target,road moverz what it for ,4 forest patrol to kill civillianz @ mulanje forest& Dzalanyama yet we all knowdat problem iz on de lake which conten oil&gas u were suporse to purchase speed boatz,jet fighterz & war ship to be gud’n de lake from Tanzanian

 15. Zaziii magalimoto a ntchito Chan? Akukonzekela nkhondo ya 2019 kapena akufuna azkalandila makala ku Mulanje? Ine Malawi sindikudziwa kt tnalakwanji? Mmalo mopeleka ndalamazo ku society kt anthu alembedwe ntchito ayi kma kugula magalimoto ankhondo mmmmm so shameful

 16. Chosecho boma lalikulu likupezeka ndimaambulance awili akugwila ntchito osawonjezako maambulance bwanji? mukuwapatsadi zoyenelela koma chitetezo chikutsikilatsikila.

  1. Don’t say it again my friend, one F16 figher jet was at 52 million US dollars in 2011.Thats lower class jets but as for Euro fighters and other brands eg falcons we can’t manage.They will also need insurance and maintenance. Eeeeeee Malawi can not buy, she can get poor.

  2. Fighter what? Aba nthawi yanji ndalama, jet ija anagula Bingu atagulitsa ndalama zinanka kuti? Ndiye ubava akutchuka nawowo akalole kugula denge muyiwone,chidule chawo nkumaba ndalamazo zidzilowa m’matumba mwawo

  3. Yah Anthony that’s true sitingafikeko,akulephera even ma Helocopter(sp) ena tili nawowo ndioti anachita kutipatsa group ina yake yomwe imakwanitsa izi,komanso nzakale kwabasi,or upange check ku google”Malawi Defence force ” muone zomwe tili nazo ndi mavuto ndithu koma kuba ndalama m’boma ndiye eee number one. F-16 is agood jet but I like F-22 Raptor jet,the most feared and deadly jet in the world it cost USD 200million each jet.

 17. Thanks Mr President, MDF imavetsa chisoni makamaka kuno ku Marine (Navy). kumakhala ready 4 any attack zida za nkhondo nso zikufunika zamakono nsanga, pa Lake Malawi apa.

  1. Dont rush for war we can lost what we have. We don’t know how strong the two armies r. But peace must be our number one priority.

 18. Mnyumba mopanda bambo, chitetedzo chimakhala chapenda penda, nchimodzi modzi mdziko mopanda asilikali, chitetedzo limakhala penda penda. Nkhondo sitimachita kuipempha, komanso ikayamba, msilikali amakhala pabwino chifukwa amadziwa chomwe chikuchitika. Ndi ife macivilian timangochokera pakhonde kuthawa kusiya zonse pambuyo. Anthuwa ayenela kukhala ndizonse zofunikila.
  Usilikali uli ngati team yampila,, ikapanda kupanga training, sipanga bwino tsiku la game. Maganizo anga,,,

 19. Anthu Amenewa Shaaaa Amalandila Ndalama Za Boma Amadyaso Zakudya Zaboma Mbola Za Anthu Ndithu Sagwilanso Ntchito Ai Akagwira Tsiku Limenelo Nde Kut Athamanga

  1. U think our MDF sagwira ntchito?? Work of MDF is not only pulling the triger to shot..they are many security works these pipo do….its difficult for you and I to understand these things..

 20. kupita ku kunja ku peace keeping force mkumat akugwira ntchito? mfuti za kamuzu zisanagwirepo ntchito, za bakiri zosagwirapo ntchito, za bingu ndiye chomagulira magalimoto a silikali ndichani? muzidzagula zimenezi ikadzayamba nkhondo zida za UN kunjako mesa asilikaliwa amakazipeza? mukungononga ndalama

  1. Uli munyengo ya kusazindikira masoka saitanidwa anzako akudandaula mmaiko. Momwe muli nkhondomu ngati ukuifuna nkhondoyo ungopita ukakhale komwe kuli nkhondoko

  2. Kape, Umaziwa Nkhondo Kmaso Cholinga Cha Nkhondo Iwe? Umbuliwu, Mchifukwa Chake Maiko Osogola Amaphunzisra2 Mwana Usirikali, Kupewa Unyapala Ngat Wakowu.

  1. chilichonse kumangopanga oppose….basi ndi chabwino chomwe poti mumasapota chipani cho tsutsa mmmmm malawi nsanje sizatha

  2. Zazii ma magistrate awagulile magalimoto ngati ndani?Akupindula chani mmalawi muno? Iweyo,ineyo komanso magistrate yo tikukhala motakasuka chifukwa cha asilikaliwo.

  3. Magalimoto asilikali ndiwofunika komaso adakamaganizako zomaonjezela maambulance paboma kumakhala ndiambulance imodzi yogwila ntchito mkumati ithandiza chosecho ndiboma lalikulu bolani kummwelako adaduladula timaboma.

Comments are closed.