Nduna zonse zopanga u Chaponda zinyetsedwa – APM

George Chaponda with Peter Mutharika

Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika auza nduna zonse zatsopano kuti saziteteza ngati zikhale ndi dyela pa chuma.

Polankhula ku nyumba ya boma ku Lilongwe kumene kunali mwambo olumbilitsa nduna zinayi zatsopano, a Mutharika ananena kuti iwo sakusekelela katangale.

“Nduna zonse zochita katangale ndizichotsa ndi kuzisiya kuti zithane ndi lamulo,” anatelo a Mutharika.

 Peter Mutharika
Mutharika (Kumanja) Wachenjeza nduna zake

Iye anati sakufuna nduna zokhetsa dobvu zikaona ndalama koma akufuna zolimbika ntchito ndi zokumva malangizo.

“Ine ndikufuna nduna za khama pa ntchito ndi zokumva malangizo a ena,” anatelo a Mutharika.

Mawu a Mutharika akubwera nduna yakale yoona za ulimi a George Chaponda atanjatidwa ndi Apolisi poganizilidwa kuti anachita za katangale.

Anthu ambiri anadabwa kuti kwa nthawi yoyamba, mtsogoleri anakanika kuteteza nduna yake.

Pa nduna zimene zinalumbila dzulo panali Mayi Anna Kachikho ndi a Aggrey Massi.

Advertisement

82 Comments

 1. Ndikufuna Mudiuze Mboma Alipo ASaba ? Musaname Kuti Mukupanga Zoti Muthandize Muthu OSauka Ndizonama . Muziti Tikhaulise OSauka . Mateba Tiziwasowa Kaba Ka Iwe

 2. Mablacks “muli Ngat Abwino,pamaxo Mukamalankhula,koma Mmtima Ndiachaponda”..Kutiberako Sikut Mwayamba Lero,achewa Amat;chiswe Chikaboola Chikwa Ndekuti Chayambira Patali….To My Side,coming 2019 I Will Vote 4 Nobody!..I Beta B Called A Bad Citizen Than Employing Thieves In My Poor Country…

 3. ONSE,E ngakumba palimbe wabwino. Tikamakuvoterani. Mationangati zitsiru inu ochenjera lero achaponda muimatso. Thawiyakampeni

 4. its too late for peter to cheat coz we have already lost our hope in dpp leadership and 2019 you will be like mcp,and mcp will be like dpp,,you are such uncaring leader and anthufe ukutizuza as if you are in your last term cz the wise leader should be transparent and encountable as secretly compaining for the next term,,what aselfish living organism

 5. sindimakhulupilira wa ndale wina aliyense kuno chifukwa zonsezi ndi mbuzi,agalu,anyani,akhakhakha,muzitiphimba mmaso ngati inu bwana simumadziwapo kanthu?mumamubeleka chaponda kuti sanabe lero manyazi kwainu bwana ndi nduna zanu zobweretsa manyazi dziko lathu laling’ono ngati ili

 6. Kaya Azinyetsa, Kaya Sazinyetsa, Kaya Azipindapinda, Kaya Azisinasina, Kaya Azizisekelera 2019 ndi ya MCP, Iwil Never Turn Back,

 7. Ku Malawi a Chaponda ndi onse…..inu ,awo, uyonso uyo ndichaponda….ndiye mukutinso zichani apa…dzulo lomweri iwenso waba monga ndikunama….? refute me!!!!!!!!!!

 8. Kuteleku china chakopeka nd speech yopoilayi munthu wakubelani kale apa akungofuna kuoneka ngat wabwino, mbava yaikulu ndiyowei. Osapusiska aMW … Sleep & kip 1 eye open 4 2019

 9. ZIKOMO KWAMBIRI A STATE PRESIDENT, PROF. A.P.MUTHALIKA: Ine ndimakondwela kwambiri kumva inu mukuuza onse ogwila ntchito m’boma ndi dziko la MALAWI masamalidwe abwino ndi luntha pogwila ntchito zotukula dziko lathu pa chuma ndi zina zotelezo: Maiko ndi mabungwe othandiza dziko lathu ali ndi chikhulupiliro mwa inu: ndiye akamaona UKATANGALE,KUBA komwe kukuchitika m’boma lanu amakhumudwa, ndipo chithunzi chanu amachipepusa chifukwa cha “ASINZINA-N’TOLE” omwe akuzungulirani: Posachedwapa kudali msonkhano wa G-20 ku GERMAN, ndidakhumudwa kwambiri kumva maiko ndi mabungwe a zachuma othandiza AFRICA akudandaula kuti chuma chopita ku AFRICA kuli ngati kutaya mungalande ya madzi, because they lack POLITICAL-WILL TO DEVELOPE THEIR COUNTRIES: INDEED THIS IS TO THE POLITICAL LEADERSHIP THEY INTRUST WITH THEIR FINANCES: Kaya atsogoleri amu AFRICA adamva bwanji??–sindidziwa!! A STATE PRESIDENT, ndinene chilungamo ku MALAWI UMBABVA CORRUPTION NGWAUKULU ZEDI: MUONETSE MPHAMVU POKONZA LEGACY YANU: ZIKOMO: REV.CHIBISA.

 10. 01
  02
  03
  04
  05
  06
  07
  08
  09
  10
  11
  12
  13
  14
  15
  16
  17
  18
  19
  20
  21
  22
  23
  24
  25
  26
  27
  28
  29
  30
  31
  32
  33
  34
  35
  36
  37
  38
  39
  40
  41
  42
  43
  44
  45
  46
  47
  48
  49
  50
  51
  52
  53
  54
  55
  56
  57
  58
  59
  60
  61
  62
  63
  64
  65
  66
  67
  68
  69
  70
  71
  72
  73
  74
  75
  76
  77
  78
  79
  80
  81
  82
  83
  84
  85
  86
  87
  88
  89
  90
  91
  92
  93
  94
  95
  96
  97
  98
  99
  100
  Let me start again
  01
  02
  03
  04
  05
  06
  07
  08
  09
  10
  11
  12
  13
  14
  15
  16
  17
  18
  19
  20
  Ock we’ll meet again

  1. my bro,don’t 4gt what peter said @ kamuzu international airport when he went to lay a foundation stone.He was furiouse trying to protect chaponda!

  2. We all know that this guy was being protected by the head of state himself. How come the whole President telling Malawians that “he saw nothing wrong” in the Maize purchase transaction yet the following day the commission of inquiry appointed by himself “found something wrong” and made a recommendation to investigate him further and discipline him.

 11. Tikudziwa kuti simukudziwa kuti Malawi anasintha ndipo anthu anapenya… Kazizipusitsani ndani sakudziwa kuti muli limodzi ndi a Chaponda…. Munauza mtundu wa Malawi kuti A Chapomda afufuzidwe kaye kalekale mwaona zoti anthu asiya kukukhulupirirani mwalixa belu pakuwamanga ndikuwayendetsa mmagalimoto kwa maola 20 kenaka mwawasiya… You take Malawians for fools wait n see akutembenuzirani chikwangwani mukuona Malawi uyu si amene analamulira Atcheya….

  1. Munthu kupanga zimene amalawi ambiri amayembekezela mukuti iyayi walakwitsa izi ayi nde Amalawi ndinu anthu odabwitsa kwabasi. Don’t just talk brother believe that things do change. Support your President wherever he shows good gesture.

  2. Michael Zuze.. I agree with your point to agree with the president when he has done something good… But am critical in as far as a good deed is concerned.. I dnt overlook some important factors connected to the good that is why it has been done??? and to whom it will benefit?? Thus y am saying this is just a “play it tough and bring it low” let them assume move its to.save a face bt am sure its not the.face of a suffering Malawian… I rest my case

Comments are closed.