Lucius Banda set to join MCP

Lucius Banda

Sole United Democratic Front (UDF) Member of Parliament in the August House, Lucius Banda will be joining the leading opposition party Malawi Congress Party (MCP).

Lucius Banda
Lucius Banda dishing UDF

Media reports which have been verified by independent sources have revealed that Banda will be joining ranks with the Lazarus Chakwera led party after falling out with his UDF which is in bed with the ruling DPP.

“Lucius cannot forget the humiliation he suffered under DPP, so he would rather be joining MCP,” a source said.

The source disclosed that Banda was only staying in UDF because moving to MCP fully will make him lose his seat in Parliament.

“However, he will be supporting MCP ideas and propositions in Parliament. By 2019, he will fully move to MCP,” the source said.

Media reports have revealed that Banda will be performing at a rally the MCP has organised in the Lower Shire to welcome Sidik Mia whom rumour has it that he has been promised the running mate post in the 2019 polls by MCP leader Lazarus Chakwera.

Advertisement

322 Comments

 1. Takulandilani bwana Lucius Banda Mwaganiza bwino, ambili amafuna kulowa muchipani chimene chikulamulila kamba kadyela koma inu mukutsata mfundo zachipani cha MCP, enawa zawakanika umbava wachuluka maka a dpp anthu sakuwafuna ngakhale alomwe atopa ndikugona ndi njala akuthawila ku Lilongwe akuti njala yavuta

 2. Ukasowa chochita umasowa chochita basi koma ndi chani apa ati azaponye vot yake ndindani. kkkkkkkkkk abale kupha kuli thooo!! akakhala mia ndie iiiiii amathawa ameneo sekerera kudyeretu kkkkkk ndipo azodiack ndikakukondani koma mmmmm munalowa uche!! iwe kazako wandiyenjeza wamva

 3. MCP yonweyo tione zina basi, musaiwale kuti utsogoleri wapamalawi siwakufuko ngati ufumu chonde lolani ena alamule.

 4. Well; if he wants to join MCP is his will, no one can stop him, or accuse him, because these multiparty politics are like that, anytime he can come in the party, or move out the party, so why; my fellow Malawian, you start to make noise because of Mr. Banda; is his choice if he wants to do so; “Ndizapadziko lapansi pompano kulowa, ndikusiya, chipani sitipita nazo kumanda ayi”

 5. Mutayini alibenso phindu wadziwika kamba ka UDF AND AKUTUMBWA KUIWALA KUTI TIMAPEPALATO KUTI TIFIKE WAFIKAPO NDI UDF USOVA SOLDIER KKKKK

 6. thats impossible lucius is not like other politicians he dont brow like wind he is a son of UDF and he will remain in the party l like him so much and l alwez learn something grt from him

 7. Nooooooo.he is loosing tyming.He dezev to be UDF president coz he is strong standing than Atupele.Hope he wont join another party for UDF’s sake.tho he has a choice to choose what good for him

 8. paja anayimba kale nyimbo timafuna kt tiziwe mzimu wagadama tiziwe zoona zokha mzimu wamatenje wakuba amakhala nzake wakumbanso ny wakupha nzakenso wakupha pitani amwene tikukanthinilani konko mu 2019

 9. paja anayimba kale nyimbo timafuna kt tiziwe mzimu wagadama tiziwe zoona zokha mzimu wamatenje wakuba amakhala nzake wakumbanso ny wakupha nzakenso wakupha pitani amwene tikukanthinilani konko mu 2019

 10. Sonja this will be a biggest mistake made in your life…i trust u as a strong person and plz be strong never be stupid…am at your back

  1. UDF inatha kale, palibenso za chipani apa. Atupele analowa DPP ndipo athera limodzi 2019. If Lucius has not joined, I would encourage him to do so. MCP is our only hope which can liberate us from these thieves

 11. Wanena Lucius Chiccio Banda pa page yake kuti iye monga oimba osati ngati member of parliament koma ngati Zembani Band ndeno inu atolankhani ndi bodza lanuli Iiiiiiii pepani

 12. If Lucius joins MCP that’s his conscience. Freedom of association. This is the party he lived to love since 1993. Yes, he has been hired but politically he has been used to embarrass his party UDF for aligning with DPP. Don’t just look at it that he has gone to make money but that he doesn’t care about UDF. By respecting UDF, as a UDF member of parliament, to avoid conflict of interest, he had the right to turn down the offer no matter how much they offered him.

 13. Mukamanena zankhazazo inu(nkhaza timapangidwa ndi MAKOLO ATHU)ndiye mumafuna kuti APRESIDENT ADZIKO adzingosekelera ndizofoila zomwe nkumati DZIKO LIKUYENDA BWINO???Aliyense amakhala ndi UBWINO WAKE/KUYIPA KWAKENSO

 14. Stop misleading the people Lucius Banda as a musician has a right to perform as long as he is willing to do so.
  It doesn’t mean he has joined MCP.unless we hear from him.

 15. Nsewu opanga 1969 ndi MCP panopa udakali OLIMBA,KAMUZU CENTRAL HOSPA,MZUZU CENTRAL HOSPA ndingonena kuti MCP idapanga zinthu zoti munthu WANZERU SANGAYIWALE.Nsewu omaliza mwezi wathawu omwewu ku AREA 24 KU LL KWATHU kuno WAKUMBIKA KALE PANOPA ndiye pali CHILUNGAMO???????????????

 16. Apa ndiy kut UDF komaso PP kuphatikizirapo AFORD sibasino wakumalembe?New Freedom Party ife titenga chigawo chakumpoto bas olo tizaluze koma tizakhala achitatu munyumba yamalamulo

 17. Malawi wake up muzasiyanisa liti hayala ndi offering ? We work for everybody to put food on the table but we have 1 boss Jesus.

 18. Pali ma show ena oti ngakhale ali oyimba sakuyenera kuvomera kupangidwa hire,zikuonetsa kuti ali ndi chidwi Ku chipani cha MCP!sizolakwika kulowa mchipanichi tingodikira tsiku lomwe alengeze kuti walowa

 19. apite kuchipani chokupha poti iyenso ————(-amunyenyembe) paja section 65 pitani amwene kwaokupha solobala

  1. You such a fool Joe Kamwana….problem with u fools is ur mind is programmed and you will just be following Muluzi even if he is taking you to hell.talking about “akupha” where is Matafale???

  2. Sandy is Not a Fool coz he’s not living in the past. All of you talking bout MCP being an organization of killers. What look around you now,, How many yrs has Your Country been “free” compare Malawi with her neighbors Zambia is way Ahead of Us. Yet during the same government you blaming now we were better off. When will you open your eyes and stop being the Beggars of the world cox you allow Leaders to fatten their pot bellies. That toothless fool you call President is responsible for poor people’s deaths e everyday in hospitals that have no equipment or drugs,, I’ve never Been a fan of Lucius Banda. But I know his heart is in the right place,, he loves Our People just like some of us without tribalism or whatever. Let’s stop this blind politics and help our country before it’s too late. Starting with demanding a new government.

  3. You don’t know what sense is maybe…Only fools will blame Lucius Banda for doing what he is doing now forgetting it was the President of UDF himself who went and joined DPP coz there is no MOA btwn DPP and UDF..If there was any then Lucius could be the first to know about it as he is a NEC member and Leader of UDF in the house..open ur eyes people,Muluzi played you all and it’s a waste of time supporting UDF when Muluzi hismself is a DPP supporter (member)

  4. Kd Mukamati MCP Ndiyakupha Mukutanthauza Chani Chasowa,Njaunju,matale Ndi Agalu Ajaadanena Akweni Adasowa Muulauliro Wawo Komaso Sindikuwona Chachilendo Cz De Same Pple Adali Ku MCP Andli Udf,Dpp,Pp Panoxo Aliku Dpp Eg Dausi

 20. At least you have done well in terms of publicity by hiring such musicians coz if u had hired the Joe gwaladis mmmmm u could easily count people but with soldier Banda u are safe coz people like his music

 21. Munthu samalima munda wanzake wake uli ndi thengo losayamba. Tiuzeni zowona.pafuka payatsidwa moto. Tingoti phee tione.

 22. Hahahajahaj kaliba u are lying an active politician and i follow malawian politics A to Z za Sidick Mia zo ndiye its obvious but not Lucious

 23. And when putting up pictures on Facebook please be honest, You should be saying “The crowd that came to Lucius Banda show where MCP was in attendance”.

 24. Luscious is a celebrated musician and expensive on live shows ndiye zaulele zapezeka tipita kukavina ndiye ena u will think tikamvera recorded speech ! No no no get ready Levi Spikiri Kalitsilo we are kwa gabu for Luscious

  1. Kutelokotu iye Lucius adakhoza kale nyimbo zokaimba kumeneko zosapota Mcp pamodzi ndi Chakwela komaso Mia udziwe zimenezo

 25. Lucius Chiccio Banda
  SPECIAL MESSAGE TO ALL:
  To those who fail to differentiate between Right Honorable Lucius Banda and Soldier Lucius Banda, I would like to notify all my fellow supporters in both areas that I, Soldier Lucius Banda have been hired to perform today in Ngabu at a political rally organized by Hon Sidik Mia.
  I wish to thank God for the business opportunity to advance my musical skills.
  On behalf of myself Soldier and the rest of the band, we hope you can support my musical career as much as you have supported me politically.
  God Bless you All.

  1. Moya apa mwalankhula bwino ndale ndi biziness sizimodzi munthu akatengedwa tiye ukandigwirire ganyu uku ndiye sikuti walembedwa ntchito anati ganyu

 26. Paja inu a Malawi 24 kunama too much, wakuwudzirani kuti kuti akukalowa MCP? Kumeneko akupita kukagwira ntchito yake monga woyimba pa mapeto pake amulipira. Mukufuna kunena kuti atolankhani, a police ndi ena omwe akagwire ntchito yawo kumeneko akapitako akhala kuti alowa MCP? Kuwuma mitu bwanji?

  1. Khala kaye choncho iweyo wamva? Uzindikila bwino patsogolo chisalu cha mnkachisi chitang’ambika ndipo za mkati zonse zitaonekela, ambiri adakali okutikidwa mmasamba komaso adakali mbuli pa nkhani imeneyi koma Lucius uja amaganiza ndipo akuti alibe chidwi ndi mbava zonse mdziko muno

 27. Watch the space…soja is just another power hungry failure who can celebrate death of an individual..hes satanic evil..he wont come back to parliament come 2019

  1. Mr chris mainje, ever diferenciated btwn politcs n spirituality ? Luscius as an artist bng hired to perfom at a rally, is it satanism? Do u realises how much positively Lucius has contributed to the politics of this country malawi? Are u realy Malawian? Mature brains never castigates the strength of others,rather apriciates. wait ur turn in 2019 try to stand if not get doomed in primaries ! Luscius is more than a HERO! Be ahuman being , learn to RESPECT OTHERS !

  2. i could appreciate if you could have written ur shit in chichewa,coz all this nonsense you hv written is pissing me off…turn it off

  3. Iwe umamudziwa soldier, soldier samaluza mpando komaso samasangalala loosing of life of any life of anybody.ona mbiri ya soldier yammbuyomu.

  4. Stop ur day dreaming. Even if u can take muntharika to contest against lucius banda in his constituency he can not win. Lucius game anayiponya patali

 28. UDF is gone long time ago Lucius Banda is coming to the Mighty MCP those they are opposing will open their eyes later and let them talk whatever they can

 29. Koma atolankhani sibwino kumangolemba zomwe mwaganiza kwanuko podzuka mammawa, ndikudziwa ndi ntchito, koma palibe lamulo loti muphedwa ngati musalembe kanthu, bwanawo ali ndi kukamwa atiuza ma fans awo ngati ife sangatibise, sizammutu zanuzo, Ndakwiya nanu…

 30. Wina adzimbidwa basi kwwwaaa cchhaa!! Kwacha!! Madrama ayambika mkuyamba chambe mmatienjeza kumakhala ngati dziko lanu lokha tizingovela inu basi popanda chotithandiza tax basi eish.

  1. Kuzimbidwa ndi Lucias yo kkkkk it seems Pali some sort of desperate on ur part sir.he is influential as an artist not as politician mind you he was in UDF but they have lost twice

 31. Malawi 24 now confusing people, the story is banda to perform at the rally not to join the mcp party, why u news 24 intermingling these two things to complicate mind of fresh people? Why mix utaka and nyemba to be cooked together? Why always telling lies ? Lost trust in u sorry!!

 32. Anthu ofunira dziko lathu za bwino awa,i ges he is nt joining joining DPP bcoz of poor administration nt bcoz of humiliation he suffered during moya….no permanent udani in politics as we say

 33. Pliz don’t mix two things, soldier is simply hired to perform at mcp rally at mgabu in lower Shire as a cloud puller and as artist and he will be paid for thst. Wats wrong malawians?

  1. Lucius Ali Ndi Ufulu Olowa Chipani Chomwe Akufuna Koma Nenani Nkhani Yomwe Ili Ndi U$boni Owona Walakwitsa Kupangidwa Hire Kukaimba Ku Msonkhano Wa Mcp? Malawi 24 Y U?

  2. Awa ama news paper amalakwitsa zithu, iye ndi woyimba ndipo ngati apangidwa hire palibe chifukwa choti muzinena zanu zoduka mutuzo

  3. Mmmmmm zinayamba zachitikapo zimenezi oyimba osewa osatenga wina amene siwochuka pa ndale bwanji . ziwoneka mutuwake .Just wait and see

  4. This is the beginning and as a malawian he has the right to associate any grouping in the country a s far as he doesn’t violate others rights

  5. Thanks brother for making correction on that because I had no idea that’s how it is. This platform misinform people all the time.

  6. Soja amaganiza osamangolembapo zomwe mwalota usiku mutakhuta mbatata.
   He is a celebrity that can attend any occasions as long as amuitana bkoz siulere ayi
   That one i mean Soja win or lose will stand for UDF

  1. By 2019 onsewo balala. Lower Shire inali ya Chakwamba koma palibe chomwe iye chinamupindulira. Zaboka zidyewe vote iri mkachipinda!!!!

  2. Ukakamba za kuipa ndiye ngakhale Dpp kodibe chabwino waononga dziko lino kwabasi kuba kwaonjeza koma wakubayo osamunjata moti ndithudi munthu wanzelu angasangalare ndi zimenezi?

  3. ndzoona man palibe ali perfect, koma zoona zna zinyanya,ndkayankhula ine mwna uzit ndkuonjezela uwafunse agogo ako zachpanichmenechi,kod mmangosatla makaka eeeti,ulingat tchetche kusatila chimbuz kkkkkkk

  4. chipanichi sichoipa ai oipa anali a Dausi ndi anzao amene amationgera dzina la mcp uwafunse agogo ako akuuza kut manyi akuchitika panowa kale kunalibe university kumangotseka mwachisawawa kuchipatala kusowa mankhwala mphunzitsi kupanga strike ndaonela maboma awa

  5. Hy boy, don’t forget that most senior members of DPP ar from old MCP whch was persecuting people in 90’s. Vote someone to change the situation not coz of background

 34. Palibe cholakwa nanga wekha wekha nkutani? UDF inalidzana lero ndi history.

Comments are closed.