Atuluka ngati Maule mu Airtel Top 8: Malawi ikubwera chimanjamanja ku COSAFA

Malawi

Angopata ma pointi awiri okha, chigoli olo chimodzi sanamwetse.

Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino lero yatuluka mu chikho cha mpikisano wa COSAFA umene ukuchitikila mu dziko la South Africa.

Malawi
Yatuluka mu Cosafa osagoletsako olo chigoli chimodzi.

Malawi yatuluka itakanikana ndi timu ya anyamata a chichepele a Angola.

Mu masewero oyamba, timu ya dziko lino idakumana ndi anyamata a Magufuli amene anagoleka zigoli ziwiri kuwasiya a Malawi kukamwa pululu atalephela kumwetsa olo chimodzi.

Masewero a Malawi achiwiri adasewela ndi timu ya Mauritius ndipo mbali zonse ziwiri palibe anaona golo la mzake.

Mu masewero ake otsiliza, Malawi inakumana ndi Angola koma golo osaliona. Nawo a Angola chimodzimodzi.

Malawi imafunika kugonjetsa Angola ndinso Mauritius igonjetse Tanzania kuti timu ya dziko linoyi ipitilile.

Padakali pano anyamata amenewa akuyembekezeka kubwela kumudzi.

Advertisement

123 Comments

 1. Even if they brought something,do you think kuti ungapezepo chani,am just proud with my all niggaz how they play their games,carry on guys ,we all knows the situation is to build the team .RVG!you,re the good coach ,keep it up,Mpira pansi

 2. I wonder why we blame these innocent souls, the problem starter even before they were born, the issue is our players are not well nourished, most of them are short for their age, and stunting starts in utero, and if not collected within 2yrs, then it’s irreversible, and the consequences many which include among other things failure to score, so stunting is caused by various factors in which prevention involves several sectors, so no need to blame them, they just suffer the consequences, take good care of pregnant moms, and children below two years, if you’re short marry someone tall to improve the variety, just look at international ,take a good look of your favourite teams, compare them with Malawians you will understand me, just passing by

 3. Nomwenu mumati RVG wasankha bwino potenga ambiri kwa neba. Lero wakuluzitsani nebayo mukukapanga claim MAPALE. Muli shit kwambiri, atola nkhani a ku Malawi. Kubanja kwa BULLETS kulibe problem.

 4. Zandiwawatu kwambiri coz maule ndi team yanga yokondedwa zikugwikizana bwanji atolankhani opusa kobasi osapita kusukulu kungopeza nchito chifukwa cha azibale anu mbuli iyaaa

 5. Am a Zambian suprisingly if Malawi is playing any team i always support them. Worse when they lose i feel bad. Now coming up with the title ‘Atula ngati maule…’ doesn’t settle well with me.

  1. Maule in this scenario it’s not as in hule wa prostitute but one team we have here it’s called big bullets. .bullets it’s maule..they exited the airtel Top 8 competition without scoring a goal having played 2 matches in succession, both home and away.

  2. I put the blames to Unlucky Mr. O.G Malata for contributing to the TZ goals. he’s so stupid n the Coach decided to rest him that’s when we didn’t conceed. we put our trust in SASAMBA chester(Mr. Shonongo) he perfomed badly. for Mulimbika(Kachamba) I think his time to play for flames is over! Jabulos Linje! hehehe @ striker Mbuzi yamunu kusi!!!!!

 6. Muli ndimabvuto,leave bb alone dis is national team combination of different clubs naaeirs,lets support national team.

  1. Too provocative. As if team yomwe idatuluka ndi bullets yokha . Worse still competition inatha kalekale, Ku Malawi kumeneko bro

 7. Zitsiru za atolankhani ngati izi mukufuna kundiuza kuti zingatukule dziko?yaaa tinatuluka inde koma we r the best and tizakhalabe abwino mpaka kalekale,Sailes man of the match,Kankhobwe man of the match osaiwala Mr captain Lanjesi atatu basi koma aiuza dziko kut ku malawi kuli bullets.amene akutumayo ukamuuze kuti azakuvulalitsa.

 8. mpamene mungadziwile Kuti mpila uli mmanja mwa BB. BB ikamapanda kuchita bwino national teamso imavutikilatu. ndye ndizosadabwitsa kuchitika zimenezi. bullets ikakoza mavuto ake muina national team ikubwelela mma 90mu

 9. Kod mumaputa dala anthu bwanji???mukat atuluka ngt maule ndye kut chan??? mwinatu lelo simunadalisidwe et???patundu pako ndkut ngt watumidwa pa muzi pako ukasowa zolemba kumangosewelesa kusiko wava pomaliza ndngot pazikit pako..

 10. Vuto a Malawi timazinyozetsa tokha timatenga Team ya Malawi kukhala ngati si team yathu kumaikaikila nthawi zonse choncho sibwino APA mukulemba za mkutu mkumati team ya Malawi yatuluka ngati bullets Ku top 8 ya airtel zikugwirizana bwanji?

 11. flames yaonjeza mpaka chimanjamanja, vutoli likuchoka patali zonse ndi tsogoleli ngati presdent ali chitsilu kumangokhala kudandaulidwa ananso palibe kuchitila mwina kumangophonyanso basi

 12. Football tourist from Nyasaland overawed by Mpumalanga infrastructure.Lets build malawi to the standards of our neighbors,so we shouldn’t go for scene viewing instead of competition.

Comments are closed.