Ana aziphunzila mu Chizungu – atelo Bambo Mtumbuka

302

Pabuka chifwirimbwiti pa Facebook malinga ndi malipoti oti Bishop wa katolika wa diocese ya Karonga a Martin Mtumbuka wanena kuti ana aziphunzila mu Chizungu kuyamba adakali aang’ono.

Malipoti anena kuti a Mtumbuka atapita ku Gala ya ana a Fomu 4 pa Chaminade ananena motsindika mawu kuti ana aziphunzila mu Chizungu.

Bishop-Martin Mtumbuka

Bishop-Martin Mtumbuka wati maphunziro ndi ofunikila zedi ku Malawi kuno.

“Iwo aboma amati ana aziphunzila mu Chichewa pamene awo akuphunzira mu Chizungu mu sukulu za pulayiveti, bodzatu limeneli,” anatelo a Mtumbuka.

Iwo anaonjezelapo kuti njira imodzi yoonela kuti palibe kusiyana pakati pa olemera ndi osauka ndi yoti aziphunzila zofanana.

“Ngati awo akuyambila chizungu, anunso ayambeni mu chizungu,” anatelo a Mtumbuka.

Koma zimene ananena zautsa mapiri pa chigwa pa Facebook pamene a Malawi ayamba kusiyana Chichewa.

A Malawi ena ati akufuna ana aziphunzila mu Chichewa pomwe ena akufuna ana awo aziphunzila mu Chizungu.

Share.

302 Comments

 1. Ndiopusa amene akudana ndi chichewayo! bwanji ena aja amayankha mnchiyankhulo chakwawo chosakhalanso chingerezi! Amalawi jelous plus uchitsiru ophatikiza ndimatama amaona ngati munthu akayankhula chizungu ndiyekuti basi ndiophunzira fotseki!

 2. it’s now exactly 100years since we started using English in Malawi,but what has English benefited us? in Tanzania there are still using there own language but they are developing ndie mukakhuta osamabwera ndi mfundo zopusa

 3. Zophunzira chizungu pongofuna kukhoza mayeso, kusangatsa azungu kuti atipatse thandizo ndi kungofuna kutchuka pa dziko pano sikuthandiza. Ife ngati amalawi tikufunika tilimbikitse za chilankhulo ndinso chikhalidwe chathu. Abusa awo awerenge bwino mau a Yoswa 24:14-16.

 4. ife ndamalawi chathu mchichewa zinazu zikagwele uko mayiko azathu anakwela cz chilichose amaphunzila mchilankhulo chawo so y we panic abusawo mwina anabanda thts y amalankhula zimenezo

 5. Do u know that Africans have no languages, tribes & chiefs? Kingship & Clans for all! Ene ng’oma, miti, nguluwe & so on! Kings=>Chiefs, Clans=>Tribes. These guys don’t want to be equal to blacks! Tisa phane abale. BANDA ZAMBIA

 6. Sorry for typing error (ODL)Open distance learning teachers Ali poor ngati ine in English language zitheka bwanji apaseni nchito white people kuti afalise uthengawu

 7. Zats is the best ever planning to catch better English in our country nanga English amakayambila ku collage or university? Ngati school udasiyila high school nothing in this simply language

 8. Ndalama za ma missionary zamukomera ndie atakhala waona kuti chilankhulo cha ma missionary chili bwino kusiyana ndi chilankhulo chachimalawi. I think mkuluyinso ndi wakatangale lomanso osusuka.

 9. Thanks Rev. Bishop Martin Mtumbuka Popereka Maganizo Amenewa Kuti Ana Aziphunzira Chingerezi, Kalero Tinkaphunzira Bwanji Ndiye Tipemphe Boma Kuti Litithandize.

 10. Koma mukadadziwa mmene ana akumalepheleramo chichewa sibwezi ukukamba chonchi,,,,,, I passed English and other English subjects very well than Chichewa nde mukufuna kupheratu?

 11. Let Chitumbuka be the national language. Then we can really develop. How u expect Chewas, the majority of whom are illiterate to put their language as a medium of instruction? They don’t want education, yet we learn their language. Poor Malawi.

 12. Hehehe ngakhale aziphunzitsi aku primary wo chizungu chawo ndichotchokatchoka nde ophunzitsa anzao chizungu muatenga kuti? Akhungu okhaokha sangalondolelane njila

 13. Kodi mukati anawo azimpuzira mutchichewa kuti azimvetsa mukutathawuza chani? poti imafika nthani yina mwanayo ndikuchitika mwayi ndiku khoza bwino ? boma kapena mabungwe ndi kumutumiza kunja kuti akapitilize ma phunziro . Kodi ku njako azikapitizaso maphunzirowo mu chichewa ? Guys think twice bafore you comment we are not playing here .

 14. You can talk, you can curse, you can criticise but the most important thing is that he has expressed his ideas. It’s up to an indvidual to buy it. Remeber coins make a lot of noise but they have less value, banknotes do not make noise but the have higher value as opposed to coins. Are you a coin or a banknote? Proper hemeneutics is vital for co-existence. Please! be civilised.

 15. not english alone sir ,but it must be taken as a priolity coz if they understand it whilest young its for the good and better,we need malawi to change for the better

 16. Nthumbukayo anaphunzira chizungu chokhachokha akamphunzira musiya kuba example ma china sagwira ntchito akuyankula chinese, what we need is stop stilling create job.

 17. Mwina zomwe ukukamba ndizoona but your statement of saying tumbuka’s are stupid is very wrong because u did not choose to who u are or to born from the side u are. dont say again. Thank u

 18. Umbuli umakhala mmaganizo; Ngati tingasungunure ubongo wa achicheperewa adzakhala ndi maganizo aphindu,ntchito ya mwana si kudziwa kuthira mchere mu mphika kokha***Azipeza njira ya solution ya zinthu ,Izi zingatheke ngati anawa tikuwaphunzitsa adakali aang’ono mwa zina ndi KULANKHU CHIZUNGU

 19. kwa ine ameneyu waganixa xofoila cfukwa ziko lililonse lili ndi xiyankhulo xao kuti mumufunse agogo ache iyeyo satha chixungu tinga pange bwanji kuti tiyankhule ndi makolo athu amene aluxa ndalama kuti ife tiphunxile pomwe iwo sanaphunxile thati ixi nonsensi akagweleuko ndi nxeru xakxo

 20. Ndizotheka kutero koma ngati kholo silinaphuzire ndikovuta kuti mwana aziyakhula chingelezi chifukwa kuschool atha kumuphunzitsa koma akapita kunyumba azimuyakhulira chichewa ndiye mwana azikhala akusonezeka

 21. anawadi aziphunzira nchingerezi kmanso aziwalimbikisa kukonda ziyakhulo za mizinda nwawomo kaya chichewa, chitumbuka, chiyawo ndizina zonse amayakhula midzi mwawomo kma vuto ili apa maziphunzisi ali panowa zizungu zimavutanso penapake nde zikhala bwanji ayambe kuphunzira ndi maziphunzisiwo kapena anawo

 22. Yeah thats good news chifukwa ntchito timagwira kwazungu ndiye timavutika kuyankhula tsopano ana athu tikufuna aphuzile chizungu please my Malawi lets agree that.

 23. ,,,,,our primary and secondary xcus hav many subjects and out of the many only a single subject is taught in our mother language,,,,,so wat kind of english are u toking abt?????or is it an attack to hear wat we’ll say?? ,,,,,

 24. actually this is a good concept, coz when u always teach our children in mother language can’t improve our nation as well as child’s mentality. so let’s try to understand my fellow brothers nowaday’s kids can’t introduce themselves in english while parents r spending alot of money to educate their kids. i agree with mutumbuka that will be a crual thing that’s the point

 25. Kwathu kumpoto zili choncho kma kwa alomwe ,ayao ndi Ochewa mmmmh.still problem.but i ll thnk if it goz all over nyasa.ana ambiri ochewa ndi amafisi.moti muona kutukwana on this truly comt

 26. APPLICATION LETTER…………………… Kamphemvu Village, P.O.Box 301, Nkhwazi, Mchinji. 09/10/ 2016………….. To
  The Jeneral Manajer, Dalitso Jeneral Sapulaizi, P.O.Box 464, Namitete…………………………. Dear Bossi……………………
  APPLICATION ABOUT OF THE JOB…………………. Fest Of All I Want Work. Second Of All Am An The Yang Boy Of
  Years 37 And Am Single Becoze My Wife Runed Of Me Becoze Me Is Poverty But I Think I Was Find Another Women
  Next Weak. Am Malawi Citizenship By Born. Am Want You To Write Me A Job. I Working Hard Even If You Paying Me
  Yang Money Becoze Am Orphanage…………….. Am Was To Kanyindula FP School P.O.Box 17 Nkhwazi, Mchinji And Am
  Get My Standarde 8 Of Certifiketi In 1992 Year. Back Time I Was Worked At Maize Mill But Boss Was Difficult There So
  He Remove Me Work, But Now I Applicating To You For Job Of Me As Shopkiper, I Know Mathematics Dont Wary Big
  Man….. Last Of All, Give How Are You To Your Family. Yours Fethfuly, Maliko Gama.

 27. Pakhale magawo awiri: Sukulu za English ndi za Local Languages.
  Maphunziro azinthu a zaulimi, technical skills, ndi maluso ena ziziphunzilidwa mu local languages kuti ana azizimvetsa kutero dzikoli lidzatukuka nsanga.
  English ikhalepo koma isakhale compulsory. Ofuna English pakhale masukulu a English. Chikufunika pa Malawi ndi chitukuko. Malawi ndi dziko limodzi komwe timayankhula bwino English koma zilibe kanthu & sizikupindula

 28. Good idea Bambo Mtumbuka,,zikamatero zikanakhala bwino chifukwa choti kulibe manual book yamuchichewa,dziko lonse la pansi limagwilitsa ntchito chizungu (english) polumikizana pogwilira ntchito zimodzi, komanso pomvana-Chizungu ndiye mfungulo (key) language to communication,,maganizo apamwamba zedi,, osati kumangoganiza zomayambisa zipani za ndale,,,bullshit!

 29. I support this motion, because here in SA, more Malawians they fail to communicate with their employers because of poor quality of our English, mine I improved my English because of encouragement from my Boss, since I have been here he gave me some his books, some novels so that I can improve my English. While @home there I ended my education in standard 8, by the times of Kamuzu Banda, unfortunately my father couldn’t afford to pay my school fees, So yes when you are there @home it’s fine when you only educated in your own mother language, but is very difficult when you are out of your country, so yes that is good views I support it. As for mine I’ve seen myself how is important to know how to communicate with any body in the world. Now I’m able to work properly as a driver in the company out of my mother country!!!!

 30. I support the idea. And learners from stds 1 to 3 should be taught only english & maths so that english as a medium of instruction be given more attention

 31. I agree with Bishop Mtumbuka,because in other countries children do not learn in local languages its always english.For example in RSA.From nursery to high school

 32. He is 200% right. This is what has crippled our education since we forget that we are in a global village where knowledge is unversal and deviation or kudzikonda timachita ku Malawiko sikudzatipinduluira

  • You are free to hate him for what you are. But he has spoken what wise and inteligent brains care to hear

 33. thats true. nanga ku malawi kuno wina kuzibali kuti si ndiye yekha amene akukanika chizungu chonsecho boma la malawi limaika phunziro la chizungu kukhala lokakamiza.

 34. English is not superior. In fact its not a measure of intelligence or success, Amene munapita ku xul mundimvomereza kuti munthu wanzeru ndi wanzeru basi, kaya aphunzire mu English kaya Chichewa, kaya Chitumbuka, kaya Chisena… In situations like these, my Italian professor simply says “it’s nosense what u r saying”… I guess these r the kind of people who like this modern colonisation

 35. Ooooo political party now l,don’t and stand now ndisiye my mom language forget about tomato sauce oky nyimbo timaimbaija mulungu dali mudzinthanso et

 36. I agree with him ,kids of nowadys they r having more problems in de terms of speaking n writing english i think dat idea it will improve our kids .

 37. Those taking pride in their so called ‘mother language’ must think again. We are living in a global village. Do not be barbaric. My mother language is Nyanja…And so, any local language used in school’s apart from this is not welcom. The Learned Academician Bishop is very correct and very right.

  • Bishop Mtumbuka is not like someone who has just risen up from mice killing and arguing this way. He is a long-experienced academician who thinks and reasons well before commenting or proposing anything. Where will you go with Chichewa?

  • Thats the problem. Professors and Doctors have committed errors in reasoning before and its all plain for all of us to see. Maybe you are not in the know. So who is Mtumbuka? Anyway, thats besides the issue at hand. Maybe i should ask you this question; can you support the assertion made by him academically?

  • The most unfortunate debate of the century. Are these guys opposing the idea for real? ? I remember when I was young I use to fail in class not because I ddnt understand the question. Growing up I saw pple signing on things that will mess with their life progress ‘”big time'” asking them why? They did not understand the condition. Gud Communication using common official language help one to progress but if a man knows only mothers language that’s crazy.

   For instance Dalitso he’s a footballer asking him his dreams is to be professional, jst wonder is he gonna b using sign language incase of a chance of international club if he can be signed in other country?
   People loose good contracts gud jobs simply because they cant speak english.

  • Let me ask you a simple question, that Chichewa is not rich in vocaburary I hope is not hidden and you know this. Can the country manage to write its books in chichewa? From all the subjects? Can we translate the most impoortant theories and science books to our local vocabulary?

  • Are you only dumb? Do you really read books? Your ignorance is now making me to get mad. For starters, there is no language which is superior to the other. Any language including Chichewa or isiNgoni can be used to convey concepts and theories. And it is actually kind of misplaced to hear people like you to say Chichewa has got limited vocabulary. By the way, there are so many books that have been written in Chichewa. I am just surprised that this appears to be mystery to you. About your purported theories not being possible to be expressed in chichewa, that just shows how uninformed a person you are. There are so many books that have been written in chichewa my friend. Do you know of countries like China, Japan, Spain, Philippines, Russia and Brazil just to mention a few have all recorded tremendous progress in their developmental drives without using English as a mode of communication. You also shows lack of understanding on globalisation when you say just because we live in global village then we all have to adopt english as a means of communication. Who told you this? Which brand of globalisation is that? It looks like you read the book upside down on globalisation. There is a concept of multiculturalism in globalisation. Any form four student at your school can help you to familiarise well with this concept. As for your friend Alexius Woyamba well i dont know if you really follow your football. Nevertheless, let me refresh your mind a little bit. I hope you have heard of this player who plays for Barcelona. His name is Lionel Messi. He barely understands english and yet he is a renowned international footballer. So what are you talking about? Check your facts before you get caught in this bandwagon.

  • We are not adopting any foreign language. English is already the country’s official language. We are only saying that let schools use the official language from junior primary level.

  • There is already a policy of using Chichewa as a means of communication in junior primary schools. So to hell with your proposal. Father Mtumbuka can join you too on this journey.

  • Can you compare the financial muscle of the countries you have mentioned to your Malawi? Our Malawi… Do you still see the possibility?

  • Bakili Muluzi and his government made a very big mistake here. The introduction of the learning in Chichewa brought down completely our education system. No wonder it has produced half-baked products like you.

  • Kodi zimenezi anapanga ndi Bakili? Hahaha ada inuso koma. Am just wasting my time here. Good luck with your ignorance. I really wish you well. Another time.

  • The best way to say ”am defeated” is to do that yah. Go in peace Mr. Educationist. I will ask Dr Kamberembere to school you. I liked your arguement though. Are you a Primary school teacher maybe? Afraid of teaching in English?

  • Kkkk, so funny enough. From which angle cud u expect Lionel Messi speaking English, my brother any1 putting Messi as exhibit has to do the homework again. Have you ever heard that in Spain they use english in there schools? This thing of Dalitso is a straight forward thing.

   HE IS A MALAWIAN, FROM A COUNTRY WHICH USES ENGLISH AS OFFICIAL LANGUAGE ON CONTRARY MESSI IS FROM A COUNTRY USING SPANISH AS OFFICIAL LANGUAGE. HAD IT BEEN UR COMPARISON WAS BETWEEN SAILESI AND ANOTHER ONE FROM ENGLISH SPEAKING COUNTRY IT CUD HAV HAD A VALID POINT.

   Remember being ignorant and being proud they are 2 different.

   Am not saying we shud not be proud of our mother tongue, we hav to b. If someone like u can so that (a person that I can see that he can speak english and he is speaking chichewa) I will say he is proud of his language but the guy it was written all over his face that he is a footballer but salvage, u cant say that he is trying to acknowledge his mother tongue. He brought a very bad image he has jst set a bad example as far as football is concerned. Learn to see things from angles of truth.

  • The issue of mother tongue in primary schools is a complex one,the case of Malawi is just one in particular where multiculturalism/multilingualism, politics and religion are in juxtaposition in the implementation of such policies..Take it for instance,if u choose to teach in Chichewa in ur primary schools then how would u expect Lambia boy from Misuku hills or Nkhatabay girl get the content being taught? This has bn a bone of contantion in many parts of the world hence leading to the choice of a neutral language in most cases that of the colonizers..Little wonder we fynd English as the most appropriate language in Malawi schools..

  • The problem is that, we malawians just as african countries & many other countries arround the globe , have been mentally colonised from wayback….to the extent that we can’t figure it out to live as a country without english. Infact one is considered special only when he/she speak or act in english. It is a long time problem….even the whole system of our government is english….& yet we choose to call ourselves in-dependent yet even the dressing code in our own parliament is white man’s. Some mps even fail to contribute effectively on issues of national importance just because of the english burden . .nde choncho dziko lingatukuke..? It is the same thing with our schools. For example if I happen to fail English & pass the rest of the subjects with distinctions….I have failed the whole exam….just imagine…!! Colonisation can not be any more than that…we are actually doomed ,if I may put it that way.! ¤Why is it that anything that has got some sort of english garnished on it, considered special..¿ ¤Why is it that anything made from a white man’s Idea is somuch valued.¿ ¤Why is it that for example,when one is speaking some typical chichewa from dowa is considered primitive..than that other so called educated guy speaking foreign language(english) ¤When are we going to wake up from our slumbers & start cherishing what’s really for us , not something that actually came with someone. These are just some of the questions that we need to ask ourselves. It is high time we go to school not only to speak english…but to be equiped with skills that can help us when we grow up…to develop our country. Malawi is a cotton producing country..but we can’t even make zingwe za nsapato from that cotton . In conclusion , english as it is ; is just another language for some kind of people somewhere…..just as it is the case with chichewa. There is nothing magical with english for goodness sake. !! Let us not colonise ourselves with it..!! One can leave a beautiful life without the involvement of english. We only need to decolonise our minds people…& begin to see thing from a different angle. #MINDOFME….

  • #Bandawe, so english is all over all the national arms and sectors. I am specifically equally concerned with the part you said some Members of parliament fail to express themselves in english. Perhaps they should start learning it at a tender age so that they master it by the time they are adults and become MP’s

  • The thing is our education standards are way below par, even our chichewa is not good enough. Yes we speak it but it’s not good enough, and yes chichewa is not a rich language. We haven’t invested much in it, our bright minds don’t major in chichewa. Even at Chanco chichewa is taught in English! Most of our everyday words are also borrowed from English.

   You cannot compare Chinese, Russian, Japanese to Chichewa! Those guys have millennia of civilization and have their own scripts. Where do we get our script? From English of course.

   Our civilization is strongly attached to the British, we cannot run away from that. Yes they colonized us, bad thing, but they also brought civilization, literacy, English included!

   I would want my children to have a strong command of English just as they have a strong command of chichewa.

  • Mmmm Spanish people, Portuguese, French they don’t learn in English. Leaning English should be a personal choice then i will force you kuwecheta nachiyao then

  • #Ben_and_Masina u cant ignore the fact that English is predominantly becoming a global language and the fact that we are leaving in a global village plus the fact that even those so called civilized nations like China,Rusia an France are moving towards the inception of English as a language of communication.(ie, recently there was debate in France to introduce English as a subject in their syllabus)…Now Malawi is just a niddle in this global village and there is alot for Malawi to learn from other nations who advanced in physics and chemistry for instance,,whose documents are mostly in English..How would u expect a Chewa learnt boy search for the meaning of the word (Diagnosis) on the googlescholar search ingene which is in English…???Guyz be realistic do not pretend to be march with Giants like China,Russia or France when u dont have anything to show to the world…I love my country and wud luv if Chichewa was the global language but I bet we must wait for another 500 yrs to come….

  • Themba Mzembe & Louis Mwenda… Such wisdom in you is very, very rare. I admire you alot. Truth be told in its original form. We need English in any angle of the country. And for this I strongly maintain that Mtumbuka is very right.

 38. Ndikudabwa kuti amene akukana mfundoyi akulemba chizungu. bwanji osalemba chichewacho? this is a welcome development and the government MUST take note of it. I whole heartedly support it.

 39. pandalama yathu pali kwacha amalembedwa mu mchichewa.Kungokhala wodziwa sizokwanila kutukula dziko.Mapulani ndi luntha pantchito ndizokwana.Kudziwa chizungu kusadziwa sinkhani,bola ntchito itheke.

 40. Sure, i support u father,,,,many of us (students) r busy encouragng ourselvs 2 speak gud chichewa yet more subjects r taught in english and its only 1 subject that iz taught in chichewa,,,,,,,as 4me i hav already started learning hw 2 speak gud english!!!! try iz better dan none

 41. Dalitsi si zoti ali proud kulankhula chakwawo ingakhakhale mayankho akuyankha sakugwilizana ndi funso umbuli uwu akanakhala wina bwezi akuyankha muchichewamo koma zogwilizana ndi zofusidwazo tiyeni tizuke amalawi zochitisa manyazi izi

 42. I don’t blame bambo mtumbuka but it will take time people to understand this cos we grow up in a poor country now everything you held from other countries then you wnt t in ur country t wll never work.

 43. that’s first degree of madness Mr bishop. Everywhere n there s always local national language which children learn by compulsory and hey ***** iwe

 44. ana ake akumalawiwo,ngat amalephela aform 4 nde ana azitolapo chani?kufuna kungowakulisira ntchito maziphunzisi?nde muwonjezerenso ma salary one more thing English is just language but when u are poor its when u thought u need english to get rich but never the Chinise President cant speak gud english though

 45. I think this will help our children to understand, cause some they fail exams not because they are not doing well, no. But it is because they have been taught in our language so to translate it into English it becomes an issue.

 46. I do not agree with this, here in malawi we think speaking english is a measure of intelligence, look in tanzania thaey uss local language, the same as chinese, japanese even in zambia but they are much better than us so why botther or busy buying language instead of knowing what to do not showing off with speaking foreign tongue but not knowing what to do, why import language there is a lot of things to learn to benefit the country not english

 47. Ndinu anthu onvetsa chisoni kodi simunawonepo amzathu amaiko ena kulankhula chilankhulo chawo popangidwa interview chizungutu ndi chilankhulo ku mosambique salankhula chizungu kuti mupite ku mosambique kulibe chizungu ndinawonapo man of the match waku congo akulankhula cha kwao ife umphawi bizy chizungu kuti tiziona popemphera kudziwa chizungu kulibe ntchito kwa maiko olemera koma ife amphawi timaona ngati tafikapo kuiwala kuti chizungu si kuphuzira

 48. Ife ndi amalawi..chizungu chinachoka kwawo nkuzatipeza ife kunooo…ndye chiyankhulo chobweracho mpaka nkumachigwadiranso??? Mtundu wa amalawi ukuonongeka chifkwa cha kusadzwa

 49. Good idea! I feel ashamed to c my country men failing to communicate in English young food :akuti chakudya chochepa, father mama same akuti ndimphwanga ameneyu zirikuno kujoni kklkkkkk

 50. I second u bambo mtumbuka, izi zingapangitse ana ambiri kudziwa kulangula english yomveka bwino adakali ku primary koma zizafunika boma likhuthule ndalama zokwanira Ku ministry ya Education n aphunzitsi atawalemekeza ndi ma salaries a bwino..

 51. akuteromo tsopano english amaphunzira mu chani?? and zokopera za eni akezo sizabwino,,pali otchuka ,ma celebrity ambiri akunja koma satha kuyankhula chizungu,,’amayankhula chiyankhulo chakwaoko,,so whats wrong with malawians? timachita manyazi ndi zinthu zathu kumalimbana ndi zakunja,,’lets appriciate our mother tongue,,,BE MALAWIAN BUY MALAWIAN,SAY CHIMALAWIAN,,,,KKK

 52. why is it that tumbuka people are always stupid. these people are sp inane. tell your stupid tumbuka not all Malawians. don’t come here n say tumbuka people are intelligent. u deny that in the name of the living God. I just don’t understand these idiots, we are proud of our local language. if the whites have given u money then let it be so.. one thing if u come on my comment n write tumbuka are intelligent then here is your story ‘ when I was in standard 7 a certain tumbuka guy was writing his first MSCE. lucky enough I made it to government secondary school. in 2014 I wrote my MSCE again with this Tumbuka guy, I mean the one who wrote when MSCE when I was in standard 7. stop being stupid. all tumbuka guys I have met speak poor English. they even fail to pronounce ‘one’ n they will say ‘wanu’. if I am wrong listen to ur lecturers n secondary school teachers…. if u say am being uncivilized then consider yourself cursed. even Donald Trump defends his own people n has natural hatred towards Africans. even in football there is what we call racism. stupid Malawians will try to defend their foolishness by arguing with me. I rest my case. if u see one tumbuka just know u have seen a slave of school n white man…. the most dump people on earth who claim to be intelligent but they always spend 30 years doing their primary n secondary education. …. may the good Lord bless those wasted sperms who will be after my comment.

 53. inde zoona Mtumbuka umboni tawuwona dzulo pamene Sailesi zidamkanika kufokotokoza muchizungu.

  Ku Joni amalawi akukanika kuyankhula chizungu chomveka chifukwa chakuti chain?????

  • It’s not only sailes m’bale Erick matoho kaiser chief defender saziwa English akamafusa in English akumayankha in venda or ma players ambili satha kuyankhula chizungu u must watch soccer bra u ll see

  • Is Matoho a malawian? Komanso udzaonetsetse kuti Matoho bcoz atolankhani amadziwa kuti naye english is not his sanguage mpake amamulankhulitsa chakwao nanga waku malawi mayi uja akanatha chichewa?

  • koma amalawi umbuli ulipodi inu pomwepaja simumaona ma coach akukanika kuyakhula chizungu or CR7 amene chizungu samatha koma simudzava anthu akwawo akumunena ngati mmene mukuchitila inumu eishiiiiiiii and Game yoyamba ya Malawi ndi Tanzania bwanji waku Tanzania uja amakanika kuyakhula chizungu koma panalibe vuto koma ifeyo amalawi iiiiiiiii musamuyalutse nzanu coz ndiamalawi okha mukuseka koma anzathu ena sakuonapo vuto lilirose ai

  • Bola tinamva zomwe amafuna kufotokoza simunthu oyamba kulakhula broken English alipo ambiri Gabanso ali gulu lomweri koma sibwino kumaseka kuli bwino kuwakonza kotheka ambiri osewera mpirawa amangokhala ndi luso lampira koma ena school imakanika pazifukwa zina monganso John Maduka ankangobwereza form2 pa Commerce ku Lilongwe koma mwai wake otchuka umapitabe chitsogolo ndiye osamaseka pamene alakwisapo tiziwakonza ndi azibale athu enawa ndiazinzathu.

  • Ndiumphawi umatipangisa kupita ku joni komanso sitimaganixa mokwana pena timatengela anthu ena pomanena kuti bwanji wakuti anapita koma sanaphunxile pomwe sixabwino koma kunena xoona sichanxelu kuti ana axiphunxila chixungu chokhackha sixingakhale bwino palibe xiko lotelo pansipano iwenso abale ako ambiri satha uxixiwa ximenxo so don’t think that you are good bc u now English

 54. That’s stupidity at its best!;!!
  Kuwononga chikhalidwe!!!!!
  Every country is known by it’s culture and language is just the greatest aspect of culture!!!

  Bambo mntumbuka, mudaphunzira chizungu inuyo muli mwana?

  Kapena pempho lanuli mumalipereka kwa amalawi mnchizungu?

  This also I call shataaaaaaaap

 55. Kulakhula chizungu si school kaya ngakhale mtsogolelj was south Africa Jacob Zuma sanalowemo mukalasi koma pano ndimsogoleli aliko Ku Malawi anthu pamene sanapite Ku school koma amalakhula ndikulemba simungalembe ntchito chifukwa sanalowe mu class Vuto ndiliti limenelo

 56. akhale ndi mphamvu zophunzitsa chizunguyo ndani chidyereni mbamu/nthongo ndi lachisanu la sabata latha kamba kosowa ufa ,boma silikuwalipira??

 57. How do u feel to be a man of the match of this game Dalitso?
  — Am good madam and my country tikuthokoza Mulungu kuti ali nafe.

  Oho mukupulika waka anyamata wakuuchewa wakuvwapula chingerezi na mutu pukupuku

 58. Chizungu chake chiti…..sindikumvesa coz from std 1 mpaka form 4 English is there as a subject but check hw many Form 4 students out of 10 can write/ speak fluently this langauge

  We are not proud of country and culture including me…, Am a Lomwe koma olo moni wa chilomwe sindimatha Kkkkkk

  Instead of promoting our local langauges we busy promoting wat does not belong to us
  A good example to show that they are proud of their country is SA.. In Malawi Chichewa is taught in all schools countrywide Even a child who does not know chichewa in Katuli Mangochi is forced to learn it…
  But that is not the case in SA ..if u are in Kwazulu Natal u will learn Zulu as ur native langauge and if change take a transfer or perhaps move to the North West province u will learning Sutho as ur native langauge

 59. Inu ndiochitisa manyaz kwambir, #Sailes wakupatsan zobwebwetuka ait, kumalawi kuno xool yayamba chaka chino ngat? Mmbuyo mosemu munali kut?

 60. I don’t surport the idea that pupils shud be taught in english….
  The pupils can be taught english as a subject…and the lest of the subjects shud be taught in vernacular….
  KODI MWANA OTI AKUPHUNZIRA CHINGELEZI NDE MUKATI ZONSE AZIPHUNZIRA MU CHINGELEZI AZIMVA BWANJI…?
  The sole reason it is hard for pupils to grasp what the teacher is preaching is that chizungucho samachimvesa…nde muti geography aphunzire mu chingelezi…amva bwanji asakunvesa chingelezixho…
  Tiyeni tivomeleze english ndi yobwera…otherwise sukulu sizalongosoka…

 61. I don’t support this. For Malawi to develop tikuyenera kumaphunzira mu chichewa. Tiziphunzira kuti tizidziwa ndipo tikwanilitse zomwe taphunzirazo. Our problem in Malawi is that we learn to pads exams and not to know. That is why we have more educated salvages in our civil service and most companies in Malawi. What I know is that all the developed countries in the world lean things in their own language. Ifenso tidzachita bwino if and only if tidzasinthe mindset yathu ndikuyamba kuphunzira komanso kulemba mayeso ziyankhulo zathu. I therefore disagree with the Bishop Mtumbuka 100%

  • yankhan man #micky, akut buanj mwa commenta mu chzungu mmalo molemba chichewa ngat ndachtiramu? kkkkkkkk u must b one of the bext educated salvages indeed.

  • Iweyo unadziwa kale chizungu ufuna anzako asadziwe ? Ndi dziko liti ungapite kukapanga za tchito kapena business muchiyakgulo chachichewa .sudayende ndichifukwa ukuyakhula zimenezo .tikadakhala kuti tili ndizoziyenereza zobweretsa chuma mudziko ngati gold ,diamond ndi zina zotero mwina kapena koma 60% chuma chadziko lino timathandizidwa ndi azungu .

  • Ndi dziko liti mu Africa lidachita bwino kamba komaphuzira muchiyakhulo chawo ? Do not compare with other continents bcz even on African level we r very far intems of wealth .

  • When Billy Mayaya calls for demonstrations, and that he announces that participants should put on a certain color of clothes, be it black or white, he makes sure that he is in that color so that he is recognized as an active activist.

   Let’s hope you get me clear there,, you are very wrong.

   You like, and you enjoy English, and you speak it very well.

  • ENGLISH YOMWEYO WE ARE UNDER BRITAIN THAT’S WHY WE GOT THAT SUBJECT. Angakulembe vepi ndani if u speak yo district language mesa azungu omwewa ndiomwe akuthandiza Ku Malawi language tinvane basi kkkkkkkkkkk

  • You seem not to get me right. Tiyeni tidziwe kuti agriculture imaphunzitsidwa ku primary ija komanso ku secondary ija ndiyokwanira kutukula dziko lathu tikanakhala kuti timaiika in to practice. Sitiika into practise chifukwa anthu ambiri samaimva. Inu mukanakhala aphunzitsi mukanandivomereza kuti ana ambiri malawi muno ndi anzeru koma saoneka odziwa chifukwa samva English. Language is for communication ndiye ife timaphunzira kuti tidziwe zinthu zomwe sitimadzidziwa. Mungadziwe bwanji chinthu chomwe simukuchimva? Sindikusintha maganizo Ayi tikuyenera kumaphunzira mu chiyankhulo choti mwana azimva komanso tizilemba mayeso mu chiyankhulo chathu kupatula phunziro la English bansi. And English must be there for communication bansi. Izi ndiye ndikunenetsa ndithu. Go to China, India, Japan Tanzania and South Africa they all prioritise their mother languages. Besides English inabwera ndi anthu ozikonda amene sanafune kuti ife tiidziwe ( our colonies) Ma British….. Anzathu amene anatengedwa ndi anthu abwino ma French and Portugal ankawaphunzitsa anthu awo zimene ma British anakanika kutiphunzitsa ndiye ife tikukakamira chani?

  • #micky ku SA amaphunxra xyankhuro zao plus english,,,so let m ask u “dnt w learn chichewa frm primary-sec? i dnt c da dfference. za ana a xul xo sionse man en mwana akayamba kuzndkira english amakhala ndchdwi chochuruka than b4,,,wat kind ov a teacher are u? #amalsoimpendingteacherman.

  • Kkkkkkkkkkkk koma uyunso uyu.hey.ngati ana akulephela kumva chizungu which means vuto ndi mphuzitsiyo.si okwanila kuphunzitsa ana chizungu alibe experience.and wanena kuti south africa.limenelo ndi bodza.the first language ku south africa kuno ndi endlish and its common.ana amaphunzila mother language malinga ndi malo amwe ali.eg.ngati uli ku kalonga home language amaphunzila chitumbuka same as ku lilongw aziphunzila chewa,like that ku lilongwe sangatenge home language as chitumbuka.koma konseko ma subject onse its english.ma kwawo kwa ma kaladi amaphunzila africans. Ndipo ma province onse amaphunzilanso africans as their second home language but only in high xools.nde mukatelo kumalawiko,mukhala ndi ziphunzitso zambilimbili malingana ndi ma dela omwe muli.as chewa,tonga,tumbuka,yao,sena,nkhonde,nyachusa,lomwe,kotakota,etc.