Chakwera faults Mutharika for not attending Kamuzu memorial prayers

261

Malawi Congress Party (MCP) president Lazarus Chakwera has condemned President Peter Mutharika for not attending memorial service for Malawi’s founding president, Hastings Kamuzu Banda.

On Sunday, Kamuzu’s family organised memorial prayers for the former president and the service took place in Mzuzu.

However, to the surprise of Chakwera, Mutharika neither attended the prayers nor sent top government officials to attend the ceremony.

Lazarus Chakwera and Peter Mutharika

Chakwera (L) fires shots at Mutharika (R)

According to the MCP president, the government was supposed to send some top officials and even president Mutharika was supposed to attend the prayers.

He further said it is very shameful for the government to shun such an important ceremony.

“My understanding is that they were invited just as we were invited and I remember some years ago former President Bakili Muluzi attended the ceremony at Civo stadium and articulated the importance of honouring Kamuzu knowing that he was a public figure.

“So it’s a pity that they did not attend the ceremony and we don’t know why they have done this maybe the organizers have been told the reason for their absence,” worried Chakwera.

The family of Kamuzu through its representative Ken Kandodo also expressed disappointment with the government’s absence at the event despite being invited.

He said: “All I can say is that we sent them an invitation to the event as it has been in all the last 18 years and this time all Members of Parliament were all invited regardless of which party they belong.

“So we don’t know why the government did not attend the function despite receiving an official invitation to the prayers.”

Share.

261 Comments

 1. Mesa peter adamphunziraso makalasi a kamudzu, adapita kunja kukalemera ndi banja lake, not za politics asakunamizeni gogoyo. Dzindikirani now, dzukani anyamata ndani akumwa tea wa DPP boma? We r still poor ndi boma lomweli, inuyo zinyozani, ifeyo okonda truth tikhala mukadzadzindikira muzawona nokha kupelekera umboni. Akulemeraso ndi a MCP, pm, ndi enawo KIKKKKKKKK Malawi yomweyi

 2. The DPP of Peter Mutharika is so AFRAID of Lazarus Chakwera and MCP. Ndi chifukwa chake samafuna kukhala pamodzi naye. Kaya zawo izo, MCP is forming the next government.

 3. Should I say, U, Mr Lazaro, You Didnt Know Which Party Does Pitala Belongs?Aaa! Aaa! Mesa Aliyese Akukumbukira Founder Of His Party Yekhayekha,tsono Mukudabwa Yet Munayamba Ndinu Kukhala Ku Memorial Ya Brother Wa Mzanuyo. Aaaa! Kod Okati Otsutsa Omangotsutsa Chilichonse?

 4. Chakwera Sadzamva,kkkk Pali Nkhani Apa Yonyozera Mtsogoleri Wadziko? Kachipande Kathelere Kamakoma Mkuenderana.Inu Kuchikumbutso Cha Bingu Simunapite Ndiye Mumafuna Apm Apite Kuchikumbutso Cha Kwanuko.You Are Too Selfish.Only Your Bread Should Buttered On Both Sides? Grow Up Young Man In Politics.

 5. Chakwerayu kaya mukuti chasikayu zabwino likuchita boma la DPP iyeyu sakuona ??? Kodi nthawi yakamuzu adalikuti ?? Nkuluyu ngosayamikauyu adamanga chiliza chakamuzu ndichasikayi wawiwala dzabwino zonse DPP idachitira kamuzu?? Dzoti chasikayi adalinkuluwa charichi ndakaika adangopita kukadya chopereka basi

 6. And he is always attending his brother’s memorial prayers,this guy is very stupid sometimes i think he feels himself as God,never he will leave everything & sleep behind his brother ku Thyolo ukoooooooooooo ndikumatchulidwanso malemu Peter Mutharika.

 7. This is nonsense, chakwera being the leader of opposition is part and parcel of government. His present represented government itself.

 8. KOMATU ULENDOUNOWOKHA APETER 2019YI MUONEZINAZOTIMUZICHITA CHIFUKWA UTAKHALA UPRESDENT LAZARUS CHAKWELA NDEADZALAMULE TSONO POTI WAMKULU SACHITAKUMUUZA KUTIWAKHALA KUUTSI AMADZIWAEKHA

 9. chakwela ali ndi vuto lalikulu ndipo alib mtima ngati munthu wopemphela Samantha kukhululuka ndipo zokuti adali mbusa ndimakayika kwambili olo chimodzi chomwe chabwino sanachiwonepo pa peter? apa pali vuto anthu ngati sathakumuwuza john tembo amatha kuyamikila muluzi olo bingu kumanena kuti akupangazi achita bwino anabela kwaife a mcp why chakwera?

 10. Let me remind Chakwera about Kamuzu. He sent members of youth league wing who beat up Mr Thom who was the father to peter mutharika and he died of the injuries sustained during that beating. The late Bingu was hunted by Kamuzu like an animal and he did not succeed. Do you expect in your normal senses Peter M utharika to attend the remembrance of a killer? Zipangani nokha zimenezo anthu ozikonda inu

 11. MMHHH,koma inu muli pagulu la anthu amene amayambitsa mtsogoleri kuti akhale oyipa. Uyu president Peter Muthalika ndi munthu wabwino akadati asamamvere zomwe enawa akunena.Bvuto lili lonse mdziko zikalakwika timati pulezidenti ndiye oyipa chifukwa choti ndi mtsogoleri. Ambiri timaleka mutu wankhani nkulowetsapo ndale potengela udani wathu omwe wakhazikika mdziko muno. Apa tikuti Kamuzu adaali oyipa wakupha, ozunza, wankhanza,poti adali mtsogoleri wadziko.Nanga Peter Muthalika ena samunenaso chimodzimodzi amene akuona kuti abale awo aphedwa,azunzika,achitidwa nkhanza,asowetsedwa munjira zosiyanasiyana.Chonde tisaipitse atsogoleri athu powapaka mbiri zoipa pofuna kuti tidye nawo.

 12. Who cares?, Who is kamuzu, chimunthu cha nkhanza, chinyawu cha chabechabe. Bravo APM. Pliz dont attend stupid functions. Let fools organise and attend this murder day

 13. How foolish, stupid, anyani, mbava zili muboma instead of them to honour the father and the founder of the nation busy talking shit, ask the zambians what they did on comemoration of keneth kaunda there no opposition or in the government. shame on you!!!!

 14. Yesu anati asiyeni akufa alilane akufa okha okha odziwa mau achautanu mukudziwa zimene yesu amatanthauza Achakwela asatenge anzawo ngati olakwa kwambiri ayi.

 15. Wapeza nkhani chakwela kodi ameneyu ndi munthu wa ntundu wanji? Kusiya za mpingo kufuna kumazalalatila anzako zoti uzalamulila Malawi ndi mcp yakoyo ndakaika

 16. Koma honestly DPP and its leadership didn’t do well otherwise you wonder if they are all normal, how can you politicise events like this one? I thought this was the time that Malawians could come together, leave their political differences aside and honour this founder of Malawi nation. Iwowo kuti azikhala atsogoleri kapena andale its because someone fought for them, even the state houses akuginamozo were built by the same Kamuzu whom they don’t want to recognise…is that normal? I have every belief that this group is very cursed and abnormal. That is why we are failing to develop the nation because chilichonse timachilowetsa ndale komanso kusankhana mitundu. Let God intervene and enlighten these fake politicians who are crooks, thieves and visionless

  • Kamuzu was a dictator, he chased my Mom for not having card while she carrying me ( she was pregnant). That guy doesn’t deserve a respect iyaaaaa!!!

  • John Jackson Soyah i dont think kamuzu came to ur home…know that some people did evil things in his name but he had no knowledge on many evil things that took place in his name………………can we kuba akuba a dpp akuwatuma ndi ichi chamuthalika?

  • The thing is, Muthalika’bs reign is very Ethuno-centric, racism and regionalism, that’s a concrete reason which made him abscent.

  • He is the founder of independent Malawi, Democratic Malawi emerged from independent Malawi which means he is the one who has made Malawi as it is today, only wise and gifted people intellectually can understand this. Here must be honoured. APM is therefore somehow misled, he was supposed to be there.

  • The whole professor to be misled! My foot…what qualified him to be a professor if he can dance to the tune of his subordinates instead of him making them dance to his tune? Questionable leadership and that is why we are seeing a failing government because his vision is in the Juniors so they share with him what to do instead of him sharing with them

 17. By not going he has saved our taxes because presidential trips are so expensive and Chakwera and company knows it well

  • Kkkkkkk Tell them especially in central region akuonjeza heavy & sizoona munthu wamzeru zake angasiye ubusa mkulowa ndale ndizodabwitsa kwambiri dyera mkuluyu after ataona anthu asakupereka molowa manja then anayidomoka kkkkk

 18. It takes aman to appreciate what other have done, pakuoneka mbuli zophunzira apa!, zosasiyani sa ulomwe ndi boma,kaya mwina muzabelanso.

 19. those who are saying mutharika did a right thing for not attending the ceremony are ‘idiots’.one of the duties of the president is to attend such important events .agalu inu mwava?

 20. komanso zinazi abale tikamati ndale ndiye mwaonjeza ndithu basi president sadapezeke pachinachake basi palinkhani pamenepa.kodi president sakhala ndi nkhani zina xochita manga iye munthu wamkulu chomwe mudziwe inu nomwe mudapita kumeneko basi mwakwana okay mumafuna iye akafika kumene mutani kapena chikadasintha pamenepo ndichiti mwina iye akadaukitsa kamuzu mwina ?

 21. Kwaaaaacha? Abusa AChakwera mumawerenga inu bible ndipo limanenetsa kuti “WAKUFA SAZIWA KANTHU BIIII” Palibe apa chomwe walakwitsa pitala, amene munapitanu munakwana basi. Koma ngati ukufuna u president waziko iwalani baba odala ochakwera. Coz MCP inatizunza mokwana, mumagona ndi azikazi athu, kutidyera nkhuku zathu ndi mazira kutimanga nyakula, komanso timayenda ndi makhadi mthumba kukhala ngati tili kwa eni. MCP ll be the oposition untill the end of this world. Tangopanga kachipani kanuko kakhale kampingo. Chifukwatu ndinu m’busa wabwino. And Yu Can call your church MCP= Malawian Chakwera Prophet.

  • ndiye mukukhala ngati odziwa malemba zikakhala zokhudza kumpoto ndipakati padziko lino bwanji apm anapezeka ku chilembwe day ndi la bingu day ku ndata amenewo sadafe ndi ofunika eti? amenewa malemba sawakhudza kuti ndi anthu akufa? chonde apm ali ngati tate wadziko lino palipano ngakhale ndi mtsogoleri wa dpp. akadzachoka sadzafusidwa kutero bwanji sakutchulidwa ena koma iye? musamusocheletse dziwani kuti maganizo oterewa anayipitsa kamuzu oti anthu kudandaula ena kumayankha monga mukuchitiramu

 22. Mayankhulidwe A Mkulu Ameneyu Samandisangalatsa, Amayankhula Kaya Ngati Wakunja Kaya Ati Kutengera Obama, Ndipamene Ndimaonanso Mkulu Ameneyu Azakhala Ozikonda Koophya Atati Walowa, Koma Aaah Ndakaika. Ngati Akumayankhula Ngati m’British Kuliri Akafikapo Azayankhula Chi Israel, Kkkkk

 23. tonse amalawi tikudziwa bwino kuti achakweranu ndinu otsutsa ndithu komanso anthu amakulemekezani ngati m’busa wampingo koma zomwe mukumapanga mungokhala ngati kamwana komwe sikazindikira kanthu komanso kamangodzikundikira olo utakagulira chili chonse chapadziko pano ikoko sikakhutisidwa komanso pachichewa pali mawu oti chaona nzako chapita mawa chili kwa iwe komanso ena amati maliro mkulirana mwaiwala zomwe mudapanga mbuyomu lero mkumati nzanu wakulakwirani mwatikwana nazo musamayang’ana zanu zokha ngati zakuwawani kuli bwino kufunsa nzeru kaye monga agogo Tembo mene zimakhalira ndale zanuzi nzosathandiza ndiponso mwina simukudzawa chomwe anthu okutsatiraniwo mchipani adakuyikirani pampando

 24. Akapandakutchula dzina la peter amasegula mmimba eeeee koma what surprise me its that its very rare kumva Peter akuyakha kapena kutchula dzina la Chatsika kkķ

 25. Kamuzu Stadium,Kamuzu Central Hospital,Kamuzu Road,Kamuzu Barrage,Kamuzu Statue plus Kumangaso Manda okongola aja that turn into one of the Tourist attraction in Malawi…Zonse zinatheka ndi DPP Government kukhala ine waDPP olo mtakhala zaka 10 osapanga attend palibe vuto!!

 26. Tembotu amatsutsa constructively, osati izi. Kukangokhala ku America tizaka basi nthawi yomweyo kusintha kayankhulidwe kukhala ngati m’mereka.

 27. Kungoti alomwefe tili ndi vuto.tikulemba ngati ntalikayu wachita bwino,anyway this is our country and zinthu zosonyedza kugawaniza a malawi zikamachitika nde inu nkumalankhula ngati simukuona vuto izo zanu…..Bingu memorial ijatu sanawaitane a MCP, pamene apapa Kamudzu family anawaitana onse posatengera zipani.. Inenso ndikuona kuti ntalika sanachite bwino,ngati iye anatanganidwa ngati anthu oitanidwa akatha kutumiza nthumwi….paja GS a Dpp alankhula kale kuti enawo akagwere…ndikulemekeza maganizo anu ndi momwe nanu mmene mwaonera.

  • I see people wanted APM in person,He is a celebrity leave him alone, we commemorated our grandfather HKB and it went on well i dont think someones presence would change anything. Sometimes our Chakwera is so irritating that people are losing attention, and opting for the current come 2019, he lacks self-discipline

  • Ndikuti attending or not, it won’t bring fufu on my table. Kamuzu anagwira ntchito chimodzimodzinso Bingu and his DPP. Chakwera sanapite ku Bingu Memorial, was it an issue. Chakwera akambe za mphutsi zoononga chimanga, aphunzitsi ena sakulandira malipiro, and ena trained but not employed, albinos akuphedwabe, the list is endless. Osakamba zimenezi bwanji. Ndiye pali anzawo a Chakwera omwe akuganiza kuti aliyense akukamba zabwino za APM ndiwachipani. Nkhani ili pano is national not political neither is it regional nor tribal. Kumamvetsa zinthu.

  • And this spirit of your fellow Lhomwes is putting Malawi on fire as they are there to defend all bad acts. I salute you for noting this weakness dear. This Bitter world

 28. Kamuzu anali munthu woipa wakhala akupanga zinthu zambiri monga abduction, kidinaping, komaso wazunza anthu ambiri powapaka sabola m’matako komanso kuwamwetsa chitize john tembo lero akuoneka ngati wolung koma ndi munthu woipa kwabiri ndiye mukamati kamuzu day mmmmmmm! Tingonjoyapo holiday yokhayi koma kamuzu anaali wachabe chabe

 29. Ineso sindinapiteko bwanji simukundinena? Kulephela kupita kuzochitika za zakamuzu chisakhale chifukwa mawa ndi inu a Chakwela mizalephela kubwela ku ukwati wanga

 30. Mr Chakwera Should Learn How To Control His Lips.If You Continue Doing The Same Thing I Don’t Think Malawians Will Let You Take The Highest Office.It Started With JZU He Was Busy Opposing Everything.We Know How His Journey Came To An End.They Say Give A Credate Where It Is Due.Mr Chakwera Should Know That Fighting The Govt Wont Help Him Win The Next Election.Malawians Know What Is The Best For Them So Don’t Waste Your Time Attacking The Govt Because The More You Attack It The More You Lose Your Supporters.Malawians Need A Leader Who Can Bail Them Out Of This Situation.We Need Ways Of Solving Our Problems,we Don’t Want To Be Reminded The Mistakes Under The Leadership Of Peter.Put Your House In Order Show Us That You Have That Possibility Of Developing This Nation.Oppose Constructively,apo Ai DDP Will Continue.

 31. Pepani a Chakwera zinthu zinasintha izi, osati nthawi yanu ija yoti Kamuzu ali ku Lilongwe, koma anthu aku Nsanje kusowa mtendere, ine ndinakakolora kumunda ikanakhala nthawi ija nde kuti ndikanathilidwa chitedze mmmmmm zinasintha izi

 32. when it comes to things of national importance all malawians of good will hav to gather as one, kamuz was a hed of state so was bingu, were all these invited? u hve no proof zip ur kamwa!

 33. Iwe Pasadi Katore Kape Ndi Kamuzu?Chonde Chezani Bwino Kamuzu Ndi Adah Amenewa Doro Ndindani?Kamuzutu Amatha Kulankhula Zomveka Monga Freedom Osati Furudum,ngongoliwa Osati Ngondoliwa, Ndizina Zotere Osati Tchani Tchani Komaso Nyanja Ikupita Ku Tz Kamuzu Adarepheretsa Samora Kulanda Dziko Lino

 34. If indeed the head of state did not attend the memorial service of first former head of state although I don’t know the reason why but it is a total mistake n it shows the president is. not patriotic

 35. This so called Chakwera or whatever name you may call him ali ndi vuto lalikulu.He doesn’t see anything good in President. Attending or not attending memorial ceremony doesn’t matter. After all DPP led government honoured Kamuzu already by reinstated his name on government infrastructures formerly under his name.Government built mausoleum in Lilongwe,what else would he be respected? That man was dictator and was not supposed to be remembered for.Anatikwana ngakhale tinali ana ang’ono kkkkk.What Chakwera wanted was to despise our President in front of his MCP supporters basi Ku mtima kwake mbeee!!!

 36. Kodi anamumangilila kuti pavute pasavute asapitek0? Ngati akuti sanamuyitane ndiye kuti anthu ena onse amemene anapitakoo anali oyitanidwa? Ngati chakwera akanakhala munthu yemwe amamva Ku koma ndi tsiku limenelilo bwezi atangothila mafuta mugalimoto lawo nkupitako monga mmalawi okonda dziko lake ndi ambiri yake osati kudikila kuti ayitandidwe ndiye ngati kuti iyeyo so mmalawi ayi !!! APA wangosonyeza kuti iyeyi zadzolo lathuli alone Nazi kanthi kuntima koma kutsupa koma iyeyo osaonetsa U munthu ndi chikondi chake kudziko lomwe akufuna atadzalamulila. Mmm akhodza kukhala maloto olamulila dziko ndithu

 37. Chakwera, you don’t breath well bcoz the President didn’t attended memorial ceremony?, wat matters to you?-# you’re the President too….. Say something.

 38. Nde ndimulandu? Instead of collaborating with the government basi busy opposing everything, creating unnecessary stories and so on. What has all that negative attitude to do with you? You won’t find a way with all that…

 39. Iwe Peter Kwakwara Sukudziwa Kuti Kundata Kudali Speaker Wanyumba Yamalamulo Richard Msowoya Vice President Wa Mcp?Nanga Zamseu Muthalika Wakoyo Adayamba Kugwira Ntchito Mumseu?Kodi Kumene Kuja Kudalibe Mseu?Umene Uja Ndichitukuko Cha J .B. Pitala Wakoyo Ife Watikwana Pamavote Akubwerawa Achoka Basi Umuyimbire Phone Erukuruku Wakoyo!!!!!!

 40. Wakufa saziwa kanthu & palibe kuyendelana pakati pa wakufa ndi wamoyo APA ndimadabwa kuona anthu odziwa a sukulu yao kukafunsila munthu wakufa kuononga ndalama kwa munthu amend sangayankhe kankhu abusawo kukhala ngati mau samawadziwa bwanji adathana nao poti adapeza zofuna zao

 41. Inu Blessings Ndi Muhamad Mmene Mukuti Ndikuononga Ndalama Zaboma Nanga Kundata Kuja Popeza Adapita Mudamutumizira Pa Airtel Money?Muhamad Ndiwe Mjomba Werewo Sudziwa Chikhalidwe Akadzakufera Atupere Mpamene Udzaziwe Kufunika Kotulukira Pamwambo Wotero

 42. Peter muthalika kodi enanu mumati ndi munthu wakuti amaganiza za ena? Amene uja wakhala kunja kwa dziko lino kwa zaka zaambiri kotelo kuti adaiwala za chikhalidwe cha amalawi cha umunthu weni weni

 43. Chakwera wandikwana, wamva! Did you find out why APM didn’t attend? Kodi campaign yanu ndiyonyoza APM basi? You didn’t attend Bingu memorial, munamumva APM akukunenani, or someone should remind me. You are a small mind, Lazaro; busy discussing people. Takambani zamsewu wadutsa kwanuwo! It’s time you gave us a break!

 44. Kd Munapitanu Si Anthu?Kapna Mwapo Unalepheleka Bambo Chakwela Tiyeni Tiyang’ane Pasogolo Musiyen Bg Man Osamangosata Pangan Zanu Zabwno Anthu Akutameni

 45. mmmh..i think chakwela has got nothing to say,coz to be a leader it doesn’t mean that u can present at any location..tink twice mr chakwela.

 46. kwa chilembwe kumapita boma, kwa bingu kumapita boma ku mulakho kumapita boma. colephelela ndi ciani kupita ku kamuzu day? paja wina ananena kuti alomwe mukudzikonda kwambili

  • Lekani zosankhana mitundu. So tinene kuti achewa ndiodzikonda chifukwa chosapita ku memorial ya Bingu? Nanga Asena, Atumbuka, Atonga, Ayawo, ndi mitundu ina? Tizingokamba nkhani yomwe ilipoyo basi! And zosankhana Kamuzu amadana nazo!

  • ndikukamba za boma osati mitundu. gadama. ndifotokoza mukandiuza za casowa, njaunju, kudomtoni + uja mudaphela ku zambia

 47. Wachita bwino zimenezo nzomwe zikuononga misonkho yathu kagwere uko, Chakwe wamva? umafuna akabwera azakupase ya sopo?paja si umati wakubera mavoti? Ndiye umufune lero ndi malemu wakoyo….

 48. mukati musabwere pa memorial ya bingu amakupangani blame ndani?tsono kamuzu wapambana chotani kuti president akapedzeke pa memorial yake? mutsamatikumbutse za nkhanza za kape amene uja mu zaka 31 zomwe analamulira mudzimukumbukira nokha kumeneko achipani coz simunamve naye kuwawa nafenso tizimukumbukira wathu moya a aford nso azipanga chimodzimodzi ndi chihana ziko lonse pamodzi tidzikumbukira John chilembwe basi

 49. On 06 April this year Malawians were commemorating the life of the late President Bingu Wa Mutharika and Chakwera didnt attend the ceremony so why ranting? Learn to keep quite Mr Opposition Leader. We know its your job to oppose but not on anything. Zip your mouth.

 50. u think that hell of a presdent even cares of wat goes on this country,think again. he illegaly won that throne 4 revenge and after swindling our money he will go where God knows he had been b4 his brothers death

 51. You shouldn’t praise Kamuzu today since he is dead. My memories are fresh of how he was insulted. You hypocrites! Kamuzu was not honoured in any way. Most people are praising him today to gain politcal mileage. A Malawi, learn kuyamikira munthu ali moyo.

 52. akulu akulu of what significance is remembering the dead and their works whatsoever to us? u say u honour them wat can respecting dead people do to we the alive ones??? will this stop hunger from plundering poor people??? will this open our Beloved CHANCO? stop waisting money and ur attention in the name of the dead and channel the funds and ur attention into helping we the alive ones….the dead have nothing to do with us…and we have to do likewise…# condemn him for not getting CHANCO opened up to now..

  • Akunena chilungamo chakwela dziko lina lilironse limayenela kuchitapo kanthu pa chili chonse chomwe chakhudza mtsogoleri oyamba mdzikolo mwachitsanzo ku south africa likangokwana tsiku lomwe lidakhudza Nelson Mandela president wa dzikolo amayenela kuchitapo kanthu pamodzi ndi dziko lawo

%d bloggers like this: