Kamlepo Kalua blocks MRA

Advertisement
kamlepo-kalua

Outspoken Rumphi East Parliamentarian Kamlepo Kalua has obtained a court injunction restraining the Malawi Revenue Authority (MRA) from confiscating his two vehicles.

MRA suspects that Kamlepo brought the two vehicles into the country without paying duty.

Last week the police together with MRA officials invaded Kalua’s house in search of Land cruiser registration number KA 8966 and Mercedes Benz registration RU 5437.

The High court in Blantyre has since found that the two cars in question were bought using proper procedures since a legislator is allowed to buy a maximum of two vehicles without paying duty.

Kalua’s lawyer Wanangwa Hara has urged the police to stop investigating further on the matter.

Hara added that he has evidence that government wants Kamlepo “arrested” on the same charges.

Meanwhile the police are yet to receive the injunction document.

Advertisement

83 Comments

 1. Where Is Kamlepo’s Cleaniliness?We’re All Criminals But We Are Not Caught.I Repeat:a Ndale Mbava,a Zipembedzo Mbava, N G Os Mbava ,tonse Operewera Pa Maso Pa Mulungu.

 2. Where Is Kamlepo’s Cleaniliness?We’re All Criminals But We Are Not Caught.I Repeat:a Ndale Mbava,a Zipembedzo Mbava, N G Os Mbava ,tonse Operewera Pa Maso Pa Mulungu.

 3. I support you brother you are really a fighter. Had it been that you are corrupt you couldn’t have been looking good as you are but because you are fighting for powerless people God is with you.Keep up.

 4. Kamlepo sathana naye peter akunama ndipo akutaya nthawi yake amene uja adakanika kamuzu kuli bwanji munthu osatha kulankhula chichewa ngati uyu

 5. Hon. Kamlepo Kalua is now suffering because of Malawians regardless of tribe, religion, region, or political affiliation. Can somebody remind me here in case I have forgotten, have we heard the CSOs or anyone from opposition condemning the DPP witch hunting behaviour on behalf of Kalua? In 2005 when Lucius Banda wanted to present the impeachment procedures to impeach Bingu wa Mutharika as president, the members of the press quizzed him, why you and not other MPs? His response was, there others who are men and others who are boys. Now here we are today, Alekeni Menyani is chair for PAC in august house and Kamlepo is the deputy. The issues that PAC were working on were of national interest. Kamlepo was able to disseminate anything for public interest. Alekeni Menyani, the chairperson, could only waggle his tail. I could sense some sort of snoring and elusiveness in the chair. The “let me see” approach the chair had, was like, let the bomb blasts in Kamlepo’s hands. Kamlepo is a matured politicians. He struggled with ngwazi, ngwazi. Then Bakili. Thereafter, another ngwazi. People labelled him with all names all because he is from the north. Now you don’t want to rally behind him in difficulties. You only love him when he is fighting for your gain. He is a man and not a boy.

 6. Its useless to fight for peoples rights in malawi coz the same malawians will not support u and when u are in chains the same people who u fighting for will only watch u being prisoned,zizasntha may be and only may be 50/100 years to come when the brave young malawians will born to change things ku malawi

  1. Ukunena choncho coz history ya kamlepo sukuidziwa amene uja adakanika kamuzu banda kuthana naye kuli bwanji okanika kulankhula chichewayu?

  2. Brother it seems you did not understand me well.you support kamlepo he is genius to you but not me.ineyo I support Peter tonse sitingakonde zofanana.komanso since I don’t like kamlepo it’s not areason kuti ndimutukwane he deserve respect is an elder just like Peter Muthalika the academic.

 7. Ndale za ku malawi ndi zaumbuli,kuzunzana ndi kuphaka,kd kamlepo ndi chaponda oyenera kumalondedwa ndani?rulling government muziwe kt izafika nthawi nanu muzazunzidwanso,

  1. Wapanga zotani uyu? Awatu atumidwa ndi peter kuti athane naye koma akuchepa kamlepo adakanika kamuzu kuthana naye kuli bwanji wadzanja limodziyu

  2. Inu mukumubakila kubako umboni upezeka akawonesa makata amene akawombolela costom WO iye ndi anthu amene anamuwuza zozembawo wonse akalowa basi.

 8. Koma kunena monenetsa Enanu zinthuzi mukuzitengela molakwika kodi mukuona ngati kuti amene akukutumaniwo azakhala pamenepo mpaka liti? zinthutu zimasintha ndipo muzaona ngati kutulo inuyo mutakhalako kapolo ngati mmene mukuwanzunzila anzanuwo kwa Amene amasatila ndale za dziko lino zinthu zikamachitika ngati mmene zikuchitikila panomu kumakhala kusanzika kwa chipanicho ndikunena monenetsa ngati nzika ya Malawi komanso okhudzidwa ndikunva chisoni pazimene zikuchitika mudziko lino mukufuna aliyense azipanga yes bwana ndizolakwika zomwe? amene angamadzudzule pazomwe zikulakwika azikhala mdani wanu? Haaa nde Malawi wake siwalerotu , Nanunso A MRA mwakhalanso chida choopsezela anthu ena? koma or patavuta pangatani choti muziwe ndichakuti okudzudzulaniwo nde akanabwelabetu ndipo simunati komanso Zotsatila zake kenako mupezeka kuti mutha ndinuyo coz nthawi yanu yokhala pamene mwayesa pozunzila anzanupo ikhala itatha nde simuzakhalanso ntmdinthawi yonzunza ena, Munalimbana ndi Uladi mussa nkhani ya ziiiiii , Apa mwaona kuti sizikupindulilani last tym munalimbilana ndi Jessie kabwila Ulemu msungama ndi Ena zinapita, lero mwaona kuti koma Kamlepo Kaluwa mmmm manyazi kumakhala nawo kodi MULUNGU WAKE uti amene angalore kuti inuyo muzingozunza anthu osalakwayo inu nkumasangalalayo ? nde nda malume anutu MULUNGUYO, Inunso yanu ikubwela nthawi muzaonanso zosaona. Koma manyazi kumakhala nawo ndikukamba zanonse amene mumatengapo mbali kumatumidwa ndi kagulu kena ka anthu ndicholinga chofuna kusangalatsa wina wake Lemekezani ena kuti enanso akulemekezeni. kale tinali ndi police yabwino kwambiri koma pano mmmm nawonso ukaamba kuwaganizila nkumati kodi nchipaninso? Kale zinthu zikavuta apolice amatengapo mbali kukuthandiza koma pano mmmm zikumatengela kuti amachokela kuti nanga Ali pambuyo pandani Eish zoopsa . koma samalani zanu sizidzaendanso tsiku lina. Koma dziko ili sila anthu Awiri Kapena kagulu kadela lina lake ayi koma ndili tonse ngati Amalawi nde wina asaoneke ngatisikwawo.

  1. Zoona zake brother Michael awawa asatipusitse ndipo atikwana kwambiri. koma akapitiliza awona ngati zomwe ena anaziona kumapeto kwanthawi yawo Chabwino or atimange tonse koma chilubgamo chizalankhulidwabe ndipo zomwe akupangazi sakupusitsa ana aliyense akuona ndipo kagulu kochepa komwe kazatsale kazalankhulanso chilungamo .

  2. George cool down… osamapsya mtima ndi nkhani za anthu andale kkkkk whether we like it or not as long as we are on earth problems shall be there….

  3. My brother Eric Nkozomba,problems shall be there it’s true but we can not be watching all those problems without doing anything,JESUS said that,the poor shall we have always but it doesn’t mean that if you are poor you shouldn’t be trying to be rich prosperity belongs to the children of God,I have seen many christians distancing themselves from politics but by the end of the day we are the ones who go to vote hoping for a change ,we are also affected positively or negatively by roles taken by politicians,remember we as children of God we can change situation, mavuto sazatha but to those who pray for a change God shall not be quiet. 2Chronicles7:14

 9. Ndiye Kamlepo yemwe ndikudziwa ine ameneyo. Chonchi ndimakumbukira nthawi imeneyo pa Channel Africa , anzake anali a Shyle Khondowe, Singini ndipo a vice president awo a mdp anali George Kanyalika mwini wa Taoloka pa Zomba. Zamatikitiki enawa angopusapo awa.

 10. A MRA ndi apolice they act like they have never gone to school kamlepo akawina mulanduyu due to ur brutal aproch then mumulipira pomuyipisira mbiri komaso kumuphwanyira umfulu kodi a MRA mumaona ngati court lilibe mphavu tikuonerani zopusa basi u need to have advisers to advise u bfore u start mobalising ur pipo nonses

 11. kkkkk katangale wa ena kudana naye koma wawo akumutchinjiridza mpaka kumutengera ma injunction shame zitheka bwanji landcruser mkulembetsa vitz uyo ndie katangaleyo mumaona ngati akati katangale ndie ndidzokhunza chimamga basi?

 12. OLD CLUELESS POLITICIAN..RECYCLED..WE DONT NEED PPO LOKE KAMLEPO IN THE SPOTLIGHT..NORTHENERS,GIVE US REAL PPO..NOT THESE USELESS BRAINLESS DUMB IMBECILE

  1. THAT EXPLAINS THE MORE REASON WHY KAMUZU THE GREAT SON OF THIS LAND WANTED ALL NORTHENERS OUT OF MALAWI,GO BACK TO UR UN DEVELOPED BUSH..

 13. Kufuna Kumanga Munthu Woti Wagula Magalimoto Ndi Ndalama Zake,koma Onkhuzidwa Ndikuba Dzindalama Dzambirimbiri Komaso Kusokoneza Ma File Achimanga Alibe Mulandu Ndiye Ku Malawi Kumeneko.Eish Kubadwira Dziko Lolakwika!!!!

  1. but do you know why he is under scrutiny??? kkk shielding corruption am not a political sided but you have to know Malawi full of corruption

  2. Me2 Am Nt Apolitician Bt Sometyms It Jst Concerns Ngat Munja Amati Wakuba Nkhuku Zaka 5 Koma Wakuba Galimoto Miyezi Itatu.

 14. Using MRA trying to silence our outspoken honourable number one, if courts clears you then they are stupid but bwapini won’t stop there he will keep on pushing and incriminating you

  1. Uyu ndiye Kalua amene ndamdziwa kuyambira kale chifukwa chogulitsa Chamba ndi kunamiza anthu m’blantyre, m’zomba kukongola ndalama zosamabweza, Crook wachabechabe,

Comments are closed.