K55,000 thief gets 10 years in jail

Mangochi

The Midima Senior Magistrate Court has sentenced a 33 year-old thief to 10 years imprisonment with hard labour.

Deputy spokesperson for Limbe police Pedzesai Zembeneko said the convict William Konyani on 16 February broke into the house of a resident in the area and stole items worth K55,000.

The thief stole assorted items such as a DVD player, two small speakers and few groceries all worth K55,000.

In court he was convicted of theft and burglary and during mitigation he said the court should consider that he is a first offender and has a family to support.

However, senior resident Magistrate Mangawa Makhalira said despite sound mitigation factors, the convict deserved a stiff sentence.

He then sentenced the thief to 10 years imprisonment with hard labour for burglary and two years for theft, both sentences will run concurrently.

The convict hails from Kalimbuka village, Traditional Authority Chimaliro in Thyolo.

Advertisement

229 Comments

 1. Judge amene wachita izi Mulungu amukhululukire K55000 ten good years in jail anthu akuba Billions and millions of money ali kunja ooooooonooo I’m speechless.Koma mukamachita izi mumadziwa kuti kuli Mulungu?

 2. Don’t worry abt him!
  At 33 he is still young.He is going to write MSCE while serving his sentence and soon he will graduate with a Degree in Law @ one of our Universities. There is no hard Labour in our prisons nowadays.
  Too many freedoms….!

 3. Pantumbo pawo ma judge wo, wht about thos thieve who steal billions of money they come out after 2 years after behave well in prison shame on you judges

 4. Lets try maths…k55,000=10….chapox cash in house $158m=life improsnment wif all hs relateves together includong de judges n hs relatives…all life imprisonment….kusata malamulo pa mphawiyu kma enawa mukuwaopa…chidiru judge ameneyo…nbuz yamu2,wandinyasa hevy

 5. Didn’t u know the justice system in Malawi works only on those who can’t buy their freedom????? If I had a billion dollars today id give a dirty slap to the one who believes himself to be leading this country n they’d let me go!!! I bet a judge would be like ” after going through the prosecutions presentation and the defense we find the accused not guilty,he was just venting out his anger kkkkk

 6. Mwanyozensa dzina la kuba inu…muba bwanji 55 pin??? if your want to still,, you better still big cifukwa ukaba zocepa nde mpaka pa nyuzi kkkkkkk ucinsilu…mukaza matuluka muzapeza 50 pin yogwilana yatuluka…

 7. apa nde zawonetsa kut our judges are after money milandu ya anthu akuluakulu imayenda bho sibho kma #Malawi unite tithese zimenezi

 8. Kukondera amphawi tizafera kundende koma anthu akumaba ndalama zoti zikhoza kuthandiza ziko palibe chimene chikuchitika

 9. aah Guyz this is not fair k55 000=10 yrs 144 milion=2 years aaah nope Guys we need to do something to help our country #Malawi Unite

 10. lets speak with no point on the bottom line k55 000 in the village is too much money and not eazy to find amene mwakulira mtauni mundisusa koma takulira ku vge mugwilizana nane so the judge is not wrong coz wamuganixira obeledwayo kuti apeze ndalama imeneyi anavutika bwanji?? Kumudzi tikulima fodya season yonse ndalama yobwera ku auction ndikukhala imenwyo nde wina akulenso

 11. This isn’t wise at -all, 10 years of free meals, housing, water, electricity at prison for stealing 55pin? Think of community service and other non custodial punishments

 12. chilungamo palibe apa zaka zachuluka sizikugwilizana ndi ndalama zomwe anabazo bwanji akasambala anapatsidwa zaka zochepa pamene nkhani yawo ndiyayikulu kodi mukamapeleka chigamulo mumaona nkhope

 13. kkkkkkk!!! kma inu malamulo akuno kd ngotani? zoona k55,000 kundende pamene K124,000,000+$58,800 ma applez kwawo? ndithu mudzafa imfa yowawa.

 14. Kumalawi kulibe ma judges, judges ndikuchuluka kwandala zomwe waba zikachepa 10year, koma ube ngat awa mr chimanga tifufuze kaye muzavaso kut amayipisila mbili apasidwe ndalama.

 15. ngati kungatheka pelekani mwayi kuti ndikubwezeleni kandalamako maniwo atuluke ndalama imeneyo Kuno ineyo ndiyamasiku 4 mpata zaka zonsezo zopusa

 16. K55,000 10 years in prison shame to his wrong doing and i have nothing to say Dzikoli limakomera olemela aumphawi ali ndi Tsoka ndithu ndi ma judge ake awatu kaya

 17. Lol the poor guy stole R1000 and he gets 10 Years in prison while politicians are stealing millions and walk out freely. There’s no justice for the poor…

 18. If 55,000 =,10 years what more this chaponda who stole billions ?the answer is chaponda deserve life in prison ,but he is not worried bcoz Malawi is a gud country u can’t steal billions & get away without facing the law

 19. Ukaba ma millions m’boma ukuyenela kulandila warrant of arrest. Ukaba timasauzande tsiku lomwelo judgement 15yrs imprisonment with had labour. Mmmm Malawi anagulitsidwa uyu.

 20. you mean 55? even trasport yopita ku south africa sikumaka taaa nanu ogamula milandu ziyamban mwaopa mulungu pozenga mlandu aibo ana ake azuzike kamba ka zaziiii mmesa waba kamba kosowa jobs mmalawimo mmat banja lake alidyetsa chan? so what about chaponda? ingomutumizan ku hell tu pot ndamene adaba za malawi yonse shame kwa amphawife

 21. Inu ma Judge ndinu zisiru munthu akabe K55000, kugamula zaka zonsezi, anthu akuba ma billions zoti zithandize anthu osaukafe mugamula motani? ??? Stupid Malawians shame on you,

 22. anthu osauka 50.000 zaka 10 anthu olemela ma billion popanda chochitika nde ikana khala 100.000 muka naika 10 wina ikhala zaka zaka mu side b mo heeei

 23. Know that most times the jailed ones are poor people.The world is always unfair to the poor.Hope unfairly judgement will be that we expect from God.

 24. Akuba azizanga pliz tiyeni tisamabele anthu azathu tiyeni tiyesese kuba za boma kaya mzipatala, mmaschool, kupolice ndikatundu ulionse waboma ndiamene tiziba. tiyeni tigwilane manja Bomalaonetsa kuzikonda zoona k55000 10yearz pamene ama billion kumangoupeza ali pheee thats very shit. now am here kulimbikitsa umbava pakatundu wa Boma

 25. Nonses thats not fair if u want ur money back hit me in my inbox l will pay back let him go back to his family mukusiya anthu akuba mamilion kumalimbana ndimunthu woba dvd playr kkkk

 26. ndende zakumalawi ndizaanthu amphawi osat olemela nchifukwa chiyani mmanga anthu osauka akaba nkhuku mmizmu koma utibela ndalama boma mukungoyang,ana ngat sumukuona. ngat pali agulu ndinuyo mukumanga zopanda mutu. ameneyo zinali zokambilana kut abweze chapondayo sanabe anasunga eti? zopusa basi osauka akaba mmanga tsiku lomwelo koma koma olemelawa mmati mufufuze. pano ndiye tatopa nanu.

 27. Uyu ndalamayo anadya wakanika kubweza, pomwe chaponda 166m ilipo more over sanabe angomupeza nazo akamufufuza ndikupezeka wolakwa amunyonga

 28. Mxiiii can I pay back the MK55,000 on his behalf and get him released and instead direct the resources to deal with cashgate and maizegate EL Chapos!! Chilungamo palibe apa

 29. Ndifukwa amati munthu asabe khuku kapena 10 000 ayi chifukwa akamugwila boma silipezapo kathu pamenepo koma ukaba ndalama za nkhaninkhani boma limapeza phundu komaso macort amapeza cholowa

 30. Ndiye Malawi ndikudziwà ine ameneyo. Mbava zikuluzikulu zilibe mlandu ku khoti koma okuba nkhuku mbuzi ndiye eni ndende.

 31. Dziko linayanja achuma iliii!55000,ten yrs,chifukwa ndiosauka.Akanakhala aja akusamila ndalama ngati mapillow aja akanangoti tifufuze kaye….mhuu7uuuu Ambuye bwerani ndithu

 32. Sha!! But Chaponda Will Serve 2 Weeks Under House Arrest If He Is Found Guilty Of Stealing Bilions Of Our Money.

 33. He gets 10 years because of 55000kwacha while people like chaponda who still billion is a free man there no trust in justice and constitutional affairs department nowadays

 34. Ngati pali njira yoti kupanga kut atuluke; kaya kubweza kandalamako imban +27643170054; tilipira, kandalama kachepa aka mpakana zoti munthu akhale 10yrz mundende, agalu akumalawi mwatan?

 35. Sinditsutsa chigamulocho koma zizikhalanso chimodzimodzi ndi omwe akuba m’bomawa. Taonni wina mamillion kutulutsidwa ati wonetsa khalidwe labwino osamusiya amalize chilango bwanji. Lero ena ndi awo palibe cha nzeru chikumveka.

  Malamulo athu ayambe kukomera a Malawi onse osauka ndi a chuma omwe. Zisaone mapezedwe kapena kudziwika kwa munthu. Mbavayi ilangidwe ndithu komano teroni ndi oba m’bomanso.

 36. This man is a thief, its just a pity that he got caught with this amount but on serious note he can do better or worse than this, on the better side he might one day walk away with millions or on the worst part he can even kill to get what he wants

  1. Cady, remember this guy is being judged against K55,000. zoti anabapo k1 million kapena atha kupha munthu ndikuba zilibe ntchito. We are only weighing the judgement that has come out from K55,000 theft. Get the point man

  2. Anyway, you guyz are right was just thinking out of the box, and you find out that this person is already having a file of which is not mentioned in this article (maybe) judgment comes in a different way don’t compare with what others did, for example the man who shot the girlfriend jailed for five years think of that.

  1. Koma okuba ndalama zochepa Ali pamavuto ndithu nanga ikanakwana 100,000 sizaka 20 mmmmmmm koma pamalawi chilungamo palibe

 37. Kkkkkk km kumalawi mmh ngati wa55,000 pini 10 yrs nanga chaponda sikufela komweko bax nanga pakhala kuneneleranso apa? Amakhoti mwatiwonjezatu amphawife km ndati chapondayo ndye ndikumunyongatu

 38. Mmakhoti mwazaza mbuli za anthu ndithu. K55, 000 nkachaninso mpaka dzaka zonsez? Ameneyo akuyenela kupasidwa chilango chosesa kuchipatala or any public places within his residence. Ana ake azunzika nthawi yaitali pomwe iyeyo ali kundende chikhalileni wina anaba misonkho ya amphawi sanamangidwe, ena anapasidwa dzaka zitatu. Chaponda ali phee! kumwa m’pweya ku parliament uko chikhalileni ndi mbava yaikulu, mpaka ndalama kukasunga mnyumba kuli kuzaza kwa ma accounts ake mmabank. This world is so unfair. Magistrate ameneyo Mulungu amuone ndithu. Limenelo likhala pemphelo langa iyaaa!

 39. Oba Nkhuku Life Imprison Koma Oba Ma Billion Kwacha Pa Bell. Uchitsiru Sudzatha, Thats Malawi Will Remain Poor Until Judgement Day.

 40. Mmmm why malawi? k55,000 i use only one day for beer and kanyenya wankhumba ndiye mpaka 10yrs in jail?come on judges what about big big cashgaters?shame pon you judges

 41. Malamulo a mMalawi adawaika kukhaulitsira anthu osauka, musamadabwe. Nanga mudaonapo osauka amakapanga nawo malamulo? Ndi olemera okhatu amakachita izi, ayenera ndithu zaka 10, pamene olemerera muva zaka 3. Ndiye ku Malawi kumeneko, kkkkkkk.

 42. APA mwalakwisa uyuyo amayenera kukhala zaka xiwiri zokha osat zachambazi why aximalume amene akumaba xen zen mukungowasiya

 43. koma judge yemwe wapeleka chilango chimenechi adzaweluzeso mulandu wa chaponda akadzamupeza olakwa tiwone kuti adzamupatsa zaka zingati 55000/1660 00000

 44. Kkkkkkkkkkkkk mmmmmmm guys magistrate amayenda ndi akazako? Khani yake ya 10 years ma magistrate enawaso ofunika retire akalamba 10 yrs k55000 basi nanga a k124 million anja

 45. Why don’t they penalise Cashgate convicts to such a period of time? MK 55,000 is just a small amount of money, why don’t the court make him pay? Kukondelatu uku

 46. Why don’t they penalise Cashgate convicts to such a period of time? MK 55,000 is just a small amount of money, why don’t the court make him pay? Kukondelatu uku

 47. poti siwose wolakwa womwe amalandila chilango uzipephera kwambili sikulako lili kubwera ( thanks mlaka your word is meaningful ) i still remember this song like yesterday

 48. This life is in favour of rich people. Prisons are for the people without names, without Id’s only poor people.

 49. Chaponda yemwe waba ma million ali pheee. koma ine ndimadabwa ndi a ma khothiwa, malemu mayi namathanga senzani a cashgate aja anaba ndalama zambirimbiri, koma anakaseweza ukaidi kwa zaka zitatu zomwe anawachoseraponso, koma uyuyu wa K 50,000 mpaka zaka 10 mmmm that’s unfair.

 50. uyu nde wangotenga ka k55 000 basi ten years in jail with hard labour koma ena aja ma million with no prison or hard labour come on the flames

  1. koma inuyo simukuona kuti achaponda anabera osauka kumene panopa munthu ukapita hospa mankhwala akumakuuza kuti ukagule ku pharmacy chikhalilenicho msonkho tikudula pa chinthu chomwe tingagule why dont they take that other money from tax and buy medicines for the poor dont think kuti ndalama anabazo ndi za munthu kapena boma ndi ndalama zathu zoyenera kuti zizitithandiza mavuto akatigwera nde onani pano akuba ndalama zimenezo pa mawa azidzati chakuti mulibe mdziko muno chonsecho msonkho tikudula tsiku ndi tsiku

 51. stupit why dont thy jail chaponda abig theif stored k569.000.00.00 but he is free but someone k55.000 is jailled fot, 10years thay we call corruption

  1. K55.000 Ten Years Mmmm This Is So Sad Indeed, Ndakhulupilila Osaukadi Alibe Mau Alot Of Malawians Are Waiting To See What Kind Of Punishemement Are U Going To Give Chaponda Lets Wait And See.

Comments are closed.