American Pop Star Madonna has now been given a go ahead to adopt two children in Malawi, Malawi24 has learnt.
The Lilongwe High Court today gave the pop star the approval during a session that she attended.
According to Judiciary Spokesperson Mlenga Mvula, the court has order Madonna to provide a home survey report within a space of one year.

Names of the children have not been made available yet with Mvula being quoted as saying ‘it is too early to make the names known’.
She had last week denied applying to adopt two more Malawian children while visiting the country where she runs a charity, and where she has previously been embroiled in controversy.
Madonna, 58, adopted Malawian children David Banda and Mercy James in 2006 and 2009.
Since adopting David and Mercy, Madonna has been a regular visitor of Malawi to give the two children a chance to embrace their heritage.
She had also set up children’s charity Raising Malawi in 2006.
Latest vacancies
61 thoughts on “Finally: Court in Malawi grants Madonna permission to adopt two children”
Comments are closed.









Koma pa central region slave trade sidzatha mumangoseweredwa m’ chinunu ndithu & simukudziwa kuti wina waiphuraponso pamenepo
Plz adopt Peter and Chakwera akutisokosera kwambiri
But y?
Adopt This Masikini #DPP plz!!!! Masikin ameneyu akutibela kuposa ana oyenda miseu. Waba #chimanga, K77.5 bilion, #ADD_Tractors and many more. eish!!!!
Mumafuna azipempha muziwatukwana akakhala aakazi muziwanamiza ndi ma K5 mkumawagwirira akugulisa minjhaka mtaunimu. Muzikawaika Ku ma farm mtsogolo Azizipenta makaka azipani ZANU mkumakuvoterani uKhansala kkkkkkkk. Typical of capitalism where the majority should be poor so that the rich and the corrupt should rule. Achina David kutsogolo kuno angathe kudzalamula Malawi uno. Kkkk tragedy of the Commons!!!
Kkkkk tragedy of the commons
Malawi asamukila uk
Better better
Kodi palibe sing’anga yochepesa anthu? Ndufuna ndibwelele ku umwana mwina madonna mkudipanga adopt.
I just wish the whites should take over de Malawi government as it was mwina ma cashgate,maizegate nda azinzawo mkuchepa wakuda akulephela since 1964
Amai ine mwabesaso ana enaso!!!!!? Malawi wanga one mtundu wanga ukutha
Pitani aphwanga mukawone kusintha, its so good kukuchotsa ku HOT HEART OF AFRIKA nkukutengera kumtendere, ubweresooo!!! Ziana nzosayamba pa Malawi, utopa wekha kwatsalaku mungopangana azungu kaya 4, mutigule ife osaukafe kaya uzikatipanga kanyenya its up to u, kusiyana ndi moto tikuuona pa nyasaland
KKKKKKK Koma Raphael
Aaaa man Junior nyasaland akukomera okhawo andale n omwe Ali ndi ndalama kale, ife osaukafe moto basi
EEEEH!!!! Koma ndaseka osanama ndi comment imeneyii, I like it. Kkkkkk
Kkkkkkkkkkk eeeyayi
Man zyambo, nanga dziko lanji loti ngati suganiza zakuba sizikuyendera
Osamutenga chaponda ndizake petaryo bwanji ?atikwa na kuno agalu amenewa
she must adopt Chaponda.
Mukatengatenga anawo mubwerenso muzatenge njara yavutai ikhare yanu!!!!
A malawi mwafika pakulephela kusungana nokha?
May the Lord GOD bless Madonna.
Honesty it sounds awesome without a petty this woman is marvelous
Mama ndakufira coz what you do is xo big up
Keep it up, may the God whom i save bless you a bandantly.
Ayamba kugulisa ana eti. Ambassador of Goodwin angogula ana onse basi axiwalipira kangschepe pamwezi.