Vendors continue to reduce maize price in Malawi

Malawi hunger food crisis

As state grain marketer Agriculture Development and Marketing Corporation (ADMARC) continues to sell its maize at an exorbitant price, vendors in the country have further reduced the price of a 50kg bag of maize, Malawi24 has the details.

The reduction comes amid controversy over Zambia maize-gate scandal involving some top officials in the ruling Democratic Progressive Party (DPP) and Admarc officials.

It also happens when ADMARC is still selling maize at MK12,500 per 50kg bag.

According to a snap check by this publication conducted on Monday February 6, vendors in Nsanje, Chikhwawa, Blantyre and Mulanje are selling a 50kg bag of maize at K10,000 with some selling it at as low as K8,000.

Malawian-Maize
Maize price getting down.

In the past weeks the traders were selling the maize at K12,000 per 50kg bag representing a reduction of 16.7 percent.

Speaking in an interview with Malawi24, vendors at Bangula Market in Nsanje attributed the maize drop to availability of the commodity and the nearing of maize harvesting season.

But Dr Joseph Chidanti Malunga, Chairperson for Parliamentary Committee on Agriculture, attributed the drop in maize prices to prospects of good maize harvest this year.

“The drop in maize prices simply means there is a lot of food in the country this year. If you go to most maize selling points, you will not find people queuing for maize and most vendors are busy selling their consignment in order to avoid them from rotting,” said Dr Malunga from Zambia.

Meanwhile, some farmers at Tengani Trading centre in Lower Shire district of Nsanje have already started selling green maize.

Advertisement

124 Comments

 1. Koma zoona ndzakut mutsitse mtengo wachimanga abale sizabwinotu koma zmenezo mwamva

 2. AMENE MUKUSANGALALA NDI MITENGO YOTSIKA NDINU OPANDA NZERU MUKALIME CHANU NDIYE MUKAGULITSE MOTSIKA TIONE NGATI MUNGAPEZE PHINDU. ANZANU AKULIRA KUTI SAPEZA PROFIT NDIYE INU MUKUSANGALALA KUPUSA ETI. MBEU ZINA MONGA FODYA ZIKATSIKA NDINU NOMWE MUMATI BOMA LIKULEPHERA NANGA MLIMI WACHIMANGA IYEYO SAVUTIKILA KUCHIPEZA.?

 3. I wonder wy de admarc iz aiming at making profits instead of helping pipo,i really appriciate wat vendors r doing n dis iz a great improvement,lets show dem dat we can do it without dem.

 4. Tidziwe kuti nkoyamba pa mbiri ya Malawi chichokereni mmanja mwa Tsamunda sizinachitikepo mumaulamuliro onese mmbuyomu BOMA KUKWEZA CHIMAMGA KUPOSA VENDA. Zachitika mu 2016 since 1964.

 5. Nkhombo pasi ku ma venda nmuli nachitemwa na banthu banyinu ,ba boma kwawo nkhuba pala bali pa mipando,kuvivotelaso yayi Chammanja Shaba Thokozile Mike Justice Alexander Kampango Shaba Fredrick Lukhere Chrissy Shaba Kapira Jofa Shaba Jervis Shaba

 6. Chomwe tikuenela kudziwa ndichakuti Mulungu So James apo nde mundimvetse. pamene munthu akuona ngati maganizo ake atheka pompa Mulungu amaambila pathela akopo mkumapitiliza kwinako, njala ya chaka chino ena amaganiza kuti Anthu tikufa kapena kuti tivutika kwambiri ayi ndithu Mulungu simunthu wakoza njila zopulumutsila ana Ake tere chanucho chimangacho gawanani mwamva ife ayi zaumbava zanuzo mudye mwina zikukwaneni anthu osatukula dziko inu mbava

 7. If the government doesn’t have market locally, it should start looking outside the country for its market. We Malawians are comfortable with prices vendors are offering and the government is very luxurious and profit oriented with its maize. I hope to it pesticides are not expensive to maintain the quality of maize.

 8. Anthu tilibe pabwino. Chimanga chikanatsika boma likanatukanidwa kuti it’s punishing poor farmers. If vendors are getting this commodity from Malawi it means farmers are gaining.

  1. Tidziwe kuti nkoyamba pa mbiri ya Malawi chichokereni mmanja mwa Tsamunda sizinachitikepo mumaulamuliro onese mmbuyomu BOMA KUKWEZA CHIMAMGA KUPOSA VENDA. Zachitika mu 2016 since 1964.

 9. Back in the year’s we were relying on government but in these year’s its sad to the government is merciless than local business people and this is the only government that sells maize on very ixpensive rate

 10. Ku edingeni kuno kumzimba kwawo kwa mberwa dowe tidya 2weeks ikubwelao 2weeks inao basi msima yamunda admarc ibwele idzanyamule chi chawo maadmarc awo kuno ife mmmm sitiangula

 11. Price regulation, in economics describes govt deliberate actions aimed at disturbing the workings of the free market mechanism in setting prices, it involve setting minimum and maximum prices, maximum price which is also called “price ceiling” aims at protecting consumers from exploitation by black marketeers, this forces vendors to reduce prices of their commodities, i believe this makes sense, hah?

 12. ulemu wanu mavendor for saving the nation. This govt wants to kill all poor pple but when campaign comes the will need the very same poor pple bcz they are easy to be cheated during compaign.

 13. simungamuthe vendor. zikatero iye amakhwefula sikelo. that vendor is also selling at 250 only kuti mbuli zambiri sizikudziwa zomwe.vendor wapanga. akhoza kumagulitsa pa 190 or 200 per kg koma sikelo ili hokhwefula. chimanga choti chilemele 2kg chimalemela 2.5 kgs

 14. ALAMULILI WA ZAKA ZOMALIZA ADAKAKHALA OPELEKA MOYO BWENZI ANTHU AMBILI KULIBE NDITHU. TILI MUNTHAWI ZOMALIZA MULUNGU ATIKONDELA MPAKA TIKOLOLA CHAKUDYA CHATHU. MUONA IWO CHIMANGA CHOLIMA IFE AONJEZELA MASATANA AMENEWA CHIMANGA CHINA PA SALU. NDI MANYANZI OMWE ALIBETU.

 15. We As Citizen Of Malawi We Fill Better For Us Because The Goverment Of Malawi The Don’t Help Their Citizens Due To Constant Price Of Maize In ADMARK because that Venders tries to fulfill the needs of people their Area So We Thank Alot Venders To Continue To So.

 16. Ndina nena ine kuti vendor watilira chaka chino. The government should continue controlling the price of maize. Osatsisa ku admarc. Vendor samala chikuwolera chija udasunga chija….sitsa kwambiri otherwise tikagula ku admarc

 17. Government set a ceiling or maximum price….as such we always expect price fall on black market ~~~Ecomicians hope u know wat am saying….

 18. ndie kuti President amanena zoona kuti palibe angafe ndi njala,,,komanso mwina number ya anthu amene amaganiziridwa kuti akhuzidwa ndi njala inali ya bodza.

 19. Sorry ndifuseko ma brothers and sisters. Kodi chaka chino chimanga akugulitsa bwanji 50Kg, ndili kuno ku South Africa sindikuziwa azibale anga ndiudzekoni.

 20. Koma mmalawi muno munachuluka zitsiru za anthu… olo muchite report motani the bottom line is,, munthu wakumudzi wanjoya chaka chino… ndipo sazayiwala zimene boma lawachitira. Kulandira chimanga chaulere, mafuta ophikira komanso ndiwo zonse zaulere.

  In 2013 chimanga chinafika k15, 000 per bag,, kwa venda pomwe ku admarc chinali k5, 000 koma mavenda amapikulako mkumakagulitsa times 3. In 2015 /2016 season the issues repeated itself long ques all over. Now government had raised the price for whatever reasons, but for the benefit of rural masses. Lero kulibe kudya matindiri, venda akulira heavy losses after losses…
  Vuto ndi loti ambirinu ndi ana oti mungosungidwa. Mukachezacheza pa facebook mumathanga kukalongeza mbamu mmimba mwanumo chakudya chomwe u dont know komwe chachokera… kenaka mukakhuta muzitinyasa apa… stupid!

 21. nkhani yabwino mavenda asisebe mitengo ya chimanga chaka chino tinyadeko ndimitengo yabwino kuchokela kwa mavenda adimac izasise mitengo ya chimanga chaka cha mawa tikamaliza kudya chimanga cha mavendachi

 22. Mmmmmm km inu amalawi 24, kukuyenera kumawauza anthu cilungamo Vender caka cino akulila kwambili cifukwa anakonzekera ktikhaulisa pokweza cimanga, km cifukwa cakt Boma, kmanxo mabugwe akufuna kwabwino akupeleka cakudya mwa ulele ndipokt nvula ikugwabwino zapangisa mavender kutsitsa mitengo yacimanga comwe anacibisa pofuna kuzakhaulisa amalawi. Inu ocommentanu plz ndale samadya phunzirani kuyamikira zinthu zikakhalabwino osamalowesa ndale paliponse Zoona mungayamikira vender? Mmmm moyo uwu Malawi sazatukuka. Piata kmuzi mukaone mmene anthu akulandilila cakudya Boma ili caka cino layesetsa kusamalila nthu ake,

  1. vender mfiti ya munthu ingamve chisoni?pakadali pano chimanga chammunda chayamba nde vender chache alowera nacho kuti?nthawi yanjala yonseyi mabungwe akhala akupereka food donation yomwe yapangitsa kuti ma vender zawo zide kamba koti malonda akuyenda very slowly.when supply is high the demand is low,when supply is low the demand is high so ngati zili ndale muchedwa nazo izo coz njala imeneyi the governt has scored a distinction.ngakhalenso miyezi yonseyi eni ma golosale akhala akudandaula kuti sakugulitsa mafuta ophikira kaamba koti a wfp akumalandilitsanso mafuta ophikirawa.enanu zidyani ndale zanuzo chifukwa ndi mmene mumapangira survive.

  2. Ndikuziwa kt chilungamo aliyense akuciziwa ndipo nunena moopa Mulungu caka cino njala sinawawe nga caka catha ngt mumazitsata mwezi ngt uno vender wanuyo ankagulisa ndama zingati thumba la cimanga? Mau a Mulungu sananame kt ngakhale kuwala kudadza km anthu adasankha m’dima. Ena maso alinawo kma amangoonera zolephera za anzawo basi, pakamwa pawo amapagwilisira ntcito molakwika ponyoza ena, Makutu awo amakwanisa kunva zolakwika za anzawo nt zabwino za ena. Kmatu Mulungu amaona zonsezi. Kwa ine ndikuthokoza Mulungu kamba kamvula yabwino, kmanso kamba kopereka mzeru ku Boma ndi mabungwe potipulumusa ku imfa za njala.

 23. Pepani2 Abale Ndi Alongo! Tiku User Itel Ndiye Kut Titsegule Link Ikumati ” Opening Page Error”…. Ndiye Ndimat Ndifunse Kut, Ma Vendor Akugulitsa 50Kg Pa Mtengo Wa Ndala Zingat Ndi Adimac Agulitsa Pa Mtengo Wa Bwanj? Plz Tell Me

 24. the strategy was simple and unique!Admarc and goverment knew that vendors were the ones perpetrating hunger by hiding the staple grain so that they should struck poor malawians with an exorbitant price!now the game was a twist with the goverment price hence the reduction of the price!so?big up admarc keep thae grain we shall feed from these unscrupulus vendors till the next harvest!!

 25. Vendors have no silos for keeping their grains and they can’t do otherwise while government can. Admarc must not reduce the price so that next harvesting season should buy little grains to control the budget for other duties.

  1. I dont believe ur a true malawian citizen who love his own country and ur people. I hope you grew up in a rich family. if it had been that you grew up a village man like me i hope u would not insault a poor village citzen like the u have spoken. Am very sorry of you. And if your serious about your comment may God bring missfortunes in ur life and family from today and forever and evermore. Amen

  2. Your idea z gud but then the govt shud put aside other measures on hw the citizens shud survive the vendors maize, infact govt need to offer a low price comparable to the vendors considering that this z our own tax

  3. Control the budget for other duties,!! these are your ideas if the money wll be speared then it is for fuel and diner.

 26. As far as I know a vendor can’t loose I once a vendor too. We know how to adjust the scale. Believe me this if you don’t even know how the scale is? U always get crooked.

 27. Vendor sangatsitse mtengo chifukwa chomuvera chisoni fellow malawian….the fact is …as harvesting season is approaching….they have bulk of commodities and demand is coming low. Amasungira kuzagulitsa mokweza njala ikavuta and now ndizolandilazi chimanga sichikuyenda akachikakamira asowa nacho kolowera….nchifukwa akutsitsa….next its admarc…..when demand is low,suply is high,price becomes low kwa amene tinapita ku school…..sorry sinakambe za ndale

  1. Well, good observation,vendors are forced to reduce the maize price due to low demand which is the result of the relief items(maize included)distributed by this Caring Government

  2. Ndava chisoni.Zowona nawexo uri m’modzi mwawanthu amene uri pa ndandanda wa anthu omwe akurandira ndalama kt muzikhara mbari yawo?YEHOVA NDIYE M’BUSA SUDZASOWA.Pliz ganizira bwino mawuwa zinazi ndizachabe.

 28. Boma Lasauka! Kulephera Kugula Wivokill Zoona Mpaka Chimanga Kufumbwa? Osangochithira Phulusa To Preserve It Bwa? Or Atatchipitsa Nobode Can

 29. I stil dont understand how the whole APM stood on the podium to dictate the maize price, who cheated hm, does he realy knw what is happening in our mother land?

  1. Umust be very stupid. Ungofaniza anthu kunyoza. Ndiwe ndani iwe.. angangako chaka chino sanakayime pa mzere ku admarc chifukwa choti boma lamukhwefula venda ….

 30. boma lasanduka venda,mavendawo ndiye boma.malawi akuyenda opanda mutu,,akanakhala nawo mutu akanamaganizila za anthu ake komanso zamawa

 31. ADMARC osatsitsa mtengo wa chimanga ma vendor asawine zowonjeza ulendo uno atsitse ndinu inu chanu mutsitse May tikamakolora kuti zakuba zichepe mukatsitsa azigula ndiwo chanucho akhaule ndithu inu ni BOMA simungaluze.

  1. Amwene, ikukhaula pakali pano ndi admarc yanuyo. Ife tikugula cha ma vendos Ma vendor ali ndi chimanga mbwe. They don’t need chimanga cha kaloswe cho. And tikakolola tigulitsa kwa ma vendors chifukwa Admarc izakhala ilibe ndalama. Musolva. Mulungu si munthu.

  2. ADMARC Siingasauke tsibweni Vendor misonkho yake tsiku lina idzalipira ndalama za ngongole ya ADMARC kaa Chimangaso sakulira chitagulidwa Bwana Mulumbe magalimoto 12 pa pool yawo monthly kulandira kuposa nduna zawo zinayera anachapila OMO ali phee

  3. boma likamalengeza zoti kulibe njala ndiye kuti likunama,,chimanga anthu akugula kwambili kwa ma venda kuwonesa kuti kuli njala,,sopano anthu azidalila budget yaboma kapena ya mavenda?boma they’re claiming having lot of maize in their silos,are those maize for people to buy or campain?mavenda have no siloz to budget for people,,they smuggle the maize from zambia every day&night but they are cheap to people,,,loving their fellow malawians!!! its not easy to smuggle maize from zambia!!

  4. Vendor alibe mtengo the same with Minibus Operator amayendera Market Forces – Demand and Supply – ngati atsitsa its simple logic Chimanga chilimo mu dziko only that Malawi is Food insecure because we are not self sufficient as we are relying on external forces to feed us koma zotsitsa mtengo ADMARC ayi thats a control vendor atchipitse basi amaba kwa mlimi ndi masikelo omanga amenewo

 32. kumeneko ndiko kukonda abale zikomo mavendor kamonga kkamonga kulibwino kukhala amphawi bola anthu akhute

 33. IMENEYO NDIYE MPHAMVU YA MULUNGU MULUNGU AMAKONDA ALIYESE. AMALAWI TIKAGWADA MOKWANILA PAMASO PA MULUNGU MULUNGU SANGATITAYE AI. MULUNGU AMADYESA KOMASO KUKONDA ALIYESE.

 34. mulungu amatikondadi . asiyeni a admarc chimanga chawo adye okha.

Comments are closed.