Man Dema raps Chaponda

Advertisement
George Chaponda.
George Chaponda
Chaponda: ‘Rapped.’

You can steal from anyone and go scot-free but you cannot expect to snatch from the hands of Malawi’ street musician Ras Dema and walk away. A song will always follow you.

In a viral clip that Malawi24 has listened to, the street musician beats his drums to a song mocking Malawi agriculture minister George Chaponda over the maizegate.

“Chaponda, mwa dzina lake Chaponda, wapondeleza…waponda maize,” sings Ras Dema building on the name of the agriculture minister which is an alternative to stealing.

“Kuidzudzula Mbava imeneyi, Chaponda,” rebukes Ras Dema calling the minister alleged to be groomed as Mutharika’s successor a thief.

You can listen to the song and download it here.

Advertisement

105 Comments

 1. akangomwalila Dem tonse tiziwoilatu kuti ndizomwezi olo atamwalila ndi chamba

 2. Those of u into music.. please, Safeguard your talent, avoid Rapping on anything..! Nthawi zina zinthu zinazi ndibwino kudikira musanayikepo mlomo kapena magitala kuti nthawiyo mukamadzatero nyimboyo idzakhale yokhwima ndi yowumbika..!

  1. Ndipo inu y would someone uses his talent on sumn hez not sure of jux bcuz people are talking????be recognised with something that won’t destroy your future

  2. Phil K Kanono wat have u done so far to show u r angry???and wat have u gain??….destroying someone’s reputation sometimes jus makes that someone more famous and recognisable…

 3. Iwe usowa ndi mbava izi!! He Will Kill u so be watchful! He will send his dpp Cadets to kill u! But I love your courage, True Malawian!!

 4. a better look for the website, good move team Malawi24. you can also take advantage of these beautiful wordpress themes please.

 5. AMalawi mukafuna kupereka mawudindo muziyamba mwapeza meaning ya zina la muthu Nanga Chaponda .tawonani makolo ake anamuwona kuti ndi muthu wopondereza dat y anamupatsa zina loti chaponda

 6. Onsewa akut Zilibwino man Dema zilibwino ukasiyana nalo dzikoli palibe azapite kukapanga adopt ana ako kut aziwasamala..nthawi zina kukhala ngat opusa ndibwino ngakhale ukuchidziwa chilungamo kma kupanga pretend as if sunakhudzidweyi kuli kufuna kukhalitsa padziko lino…Freedom fight samadyerlera amuna nde samalani ndikayimbidwe kanu..

  1. iwe manganizo ako nde opwambwana opwambwa chifwakwa chake athu akuvutika ziko muno mulipo ambili onganiza mopwambwana zoti athu ena anataya myoyo yawo kuti zithu zisithe ngati achina chilembwe ndi ena koma iwe ukubwela ndi mfundo kungokhala ngati suzafa ,,tulo basi,,,more fireeeee dema am bihide u go on

  2. Nde mwati bwanji inu man #Suman ?? Dema munamuonako koma kapena mukungofuna kuyakhula kut mumatha kuyakhula ? izi ndizomwe anthu ngat iweyo #Suman..#Charles..#Felixx mumafuna anthu ena akumenyereni ufulu iwo alize miyoyo yawo inu ndikumadyelera…ngat mukudziwa kut mutha kukwanitsa kuzimenyera ufulu otereu bwaji simumayimba nyimbo kapena kuyakhulapo ngat zokwe wayakhula Demazi ??

  3. Kuyakhulatu ndikophweka koma kuchita chithucho nde kovuta..anthu omwe amamwalira kamba kolimbana ndi anthu andale munayamba mwapitako mmakomo mwao ndikukaona momwe ma farmily awo akuwadandaulira ? inu mukufuna kut wina azikuyakhulirani chonsecho inu muli ndipakamwa..mutu ndi ubongo oganizira mulinawo ndithu then u are waitng for someone kut ayakhule nde muzibwera nditima comment tanu ngat anthu opanda mantha apa chonsecho mukuyakhulira kumbuyo kwa Demayo…andale onse zawo ndizimodzi nde iwe uzitsate kumalimbana nawo mmalo molimbikira tchito u will end up fightng wth ur wife kunyumbako kamba kosowa ndio unali busy kulimbana ndiza ndale…

 7. ukatengera zaku jamaica kapena ku usa,mayiko amenew mfuti amagawa ngati zikondomu wina aliyese wafuna amankhara nazo,ndiye m bale tiyetizingopenya sungamenyere ufuru amalawi ndi anthu amatha aturo chilembwe anayesera koma ah! palibe anthu anamuthandiza.tiyeni tizingosuta ndikumwa akabanga ghetomu.

 8. Omenyera ufulu amafatu Rasta take care musiya mbili muli mmanda ana anu akuvutika mukulimbana ndi boma inu osauka dont 4get the late Matafale

 9. court failled to deal with him so lets the music deal with him …….remember he is a citizen of Malawi ndiye wina aziti chamba fuck you .

  1. Do u think court can really fail???or maybe the court knows the truth and they r jux trying to prolong the confusion on people so u shld talk anyhow…relax and hold on to the truth otherwise muzachita manyazi pasogolo

  1. Ahahaha balling!! The old man works so hard to get it ryyt…he can’t steal from no one I mean all the times he’s been around akabe lero??

 10. good view of the website, now its appealing, good css and javascript, koma i cant see the link to download or listen to song by dema, “here” is not a link

Comments are closed.