Pastor Fletcher Kaiya’s son shot by police

Jonathan Kaiya

Police in the commercial city of Blantyre have shot dead a son of Pastor Fletcher Kaiya who escaped from a police cell when he was probed on charges of armed robbery.

The son Jonathan Kaiya 30, is reported to have stolen a Demo unit vehicle from CFAO, he was caught and later jailed at Soche Police unit where he surprisingly escaped.

He then fled to Mozambique using a Zagaf truck full of cement which he also stole.

Jonathan Kaiya
Jonathan Kaiya shot dead.

He sold the truck and cement and came back to Malawi.

Blantyre police deputy spokesperson Andrew Mayawo confirmed this Malawi24 saying they  rearrested Kaiya  on Monday and he was kept in custody pending for his court appearance.

While in custody Kaiya confessed to have had a friend with Ak47 gun and that he wanted to have the gun confiscated by the police.

Mayawo added that the police were then surprised to be attacked by Kaiya who managed to confiscate a piston from one of the officers who were on duty to get the Ak47 gun.

It is after making a couple of resistance moves that the law enforcers shot him dead.

Kaiya was pronounced dead at Queen Elizabeth Central Hospital (QECH) and the officer who got shot got admitted at the hospital for treatment.

He  hailed from Kandeu village,Traditional Authority (T.A) Ganya in Ntcheu district.

Pastor Fletcher Kaiya is a veteran broadcaster who used to present gospel programmes on Malawi Broadcasting Station.

Additional reporting by Luke Bisani.

Advertisement

283 Comments

 1. Si woyamba kukhala ndi chigawenga, alipo azibusa ambirinso omwe ana awo akuchita ntchito za mu mdima. Stop talking no sense. .

 2. Stop talking bout the pastor. Zigawenga zonsezi ndi ana amulungu so chodabwisa ndi chani pastor kukhala ndi mwana chigawenga.

 3. Anthu musatengerepo zonena poti iwo ndi abusa kodi nanga sikanakhala zinali kwa inu mukanatani poti izi zachitika kungoti pepani

 4. Anthu aMulungu nthawi zambiri kapenanso kuti okhulupilira satana akalephera kuwagwetsa amagwiritsa ntchito ana popanga makhalidwe oyipa kuti munthu wa Mulungu azioneka olephera azigwa mmayesero chifukwa chamwana dzina laMulungu lizinyozedwa azipepusidwa kuti anthu asamaone chili mwaMunthu waMulungu aziweruza molingana ndintchito zamwana kuti ambiri asapeze chipulumutso apa abusa sizikuwakhuza ndichikhulupiliro anayesesa kumuthandiza kudzera mmawu muumunthu koma satana anagonthesa makutu ake musaweruze chifukwa nanunso muzaweruzidwa

 5. Awise son brings joy to his father but foolish son grief to his mother.Prov 10 v 1.So sad I remember 2003 @Luwinga pvt xl(Mzuzu) sitting on the same desk desiring to be born in the famous pastor’s/preacher’s family but to you it was not that worthy.Not knowing u will go that way.I thought your fearlessness and tricks to the teachers was just ajoke not knowing that they were lectures for great crimes.Indeed you have brought adisgrace to your parents & whole family

 6. Ine akayiya ndiribe nawo chifukwa, ndipo ndi m’busa modzi amene nditamawavera zokamba zao ndizogwira mtima, szama prophet tikuva panozi zongofuna kulemera bax.and mwana wa m’busa si m’busa nayeso, wapita ndi ntchito zake,

 7. Mphoto ya uchimo ndi imfa.Ngati kuli kokapuma Rest in peace

  1. zoonadi ineso ndikumuziwa koma poti chankhumba mtima mulekere mmmmmmmmmm

 8. Guys tisachimwepo apa popanda chimo alekeni a abusa palibe iwo chomwe alakwa mwana wawo ndi chisakho chomwe anapanga sikuti abusawo kumbali yawo sanayesetse koma ndiye kuti anangovomeleza kuti mwana wawo ndiwotere,zikomo Yehova chifukwa cha imfa iyi mwina kuti enafe titengelepo phunziro

 9. He’s the son of a pastor, and there is nothing wrong with the pastor. Even in the Bible Judas Iscariot a friend of Jesus committed suicide yet Jesus was innocent of Judas’s death. What i want to say is that everyone will be judged by his deeds, its not a matter of who was your father or who were your friends

  1. Nkhani ili apa ndiyo kuti mwana womvera akondweretsa atate wache pamene wopusa aliritsa mayi wake. Awatu ndi mawu amubukhu la Aefeso. Taonani apa, mayi wake wa Jonathan “Indiana Jones” Kaiya wa liritsa amake pamene atate wake sanakondwe. You cannot blame the seed without looking at the tree. While negative comments to the Pastor may not be fair, they are however inevitable since the Pastor might have assisted so many young people to repent their sins, his son has died a horrible death. Tsono apa ayimbire ndi a Fellowship pamene atate ndi abusa. Apatu zalakwikwa zedi.

 10. #jungle law at best.as 4 mie i prefer #sharia coz in sharia de cops oso deserve 2 die by hit squade 2 deter other power drunken police

 11. Jonathan’s characters were questionable ever since. Even in our Primary School days at Namilango, kanfanaka kanali kovuta heavy.

 12. Pastor Kaiya siolakwa and tiyeni tiwaleka coz sikuti iwo amamutuma kwana kuti azikaba ayi Mr Kaiya ndkuwaziwa bwno ndi munthu wabwno kwmbili so kufa kwa mwana wawo kusakhale chitozo kwa iwo R I P Jonnah

 13. 2017 ambiri ayilowa ndi minyama..tisogoze mapemphero..toyeni tipemphere-Allah humaa rabanaa karim ,Allah humaa rabana Yassin

 14. I believe the police in our country should learn how to handle these case with maturity becauseor policeman our too corrupted, last of last year 2014 end ,when I was in mzuzu a non citizen from Tanzania injured my young brother because he wanted to Robb him MK 780 000, when I take the guy after I catch him myself the police when I go the following day I found that they had released him with MK15 000 and WHEN WE ASK ALL THE POLICE SAID ASK MR PAHUWA IS THE ONE DID at the same time the 2 guys from Tanzania was not having a passports. .and was working to the friends & bussiness partner ofJoyce Banda….I was living and doing business with fear until I left the country ,, when I am south Africa and Joyce Banda as she bought a house closer to us we do still feel secure because I know how corrupted she is,
  Let unite malawi

 15. mmmm Malawi police nowadays they killer’s ,don’t believe them last month a police anaombera munthu waku area 49 coz anagula galimoto ndikutsegula hardware shop atagulitsa nyumba yake Ku area 49 k35 million,

  1. ccta khani ndiyakupha anthu not zomwe mukunenazo if u wanna to the truth ndikuzani or kuwalanda hule kumowa nowadays akumakupangira mulandu

  2. Muli ndi negative attitude kwa a Police that’s why mukutero funso mkumati KODI WAKUBA NDI MFUTI MUNGAMUNGWIRE NDI MANJA??Zikuoneka kt mulibe katundu oti mungaberedwe

  3. not that esa munthuyu anali atamangidwa kale ,a police amagwiritsa ntchito hand cuff mfunso mkumati anadula hand cuff?

  4. Wonama iwe !! It seems kuti sunabeledwepo moreover okuba ndi mfuti amakhala munthu okupha so he deserve it koma poti mumadyera limodzi iam sorry kuti capital yako taduka

  5. Guys think,the person oz alrdy in cell. They jct took him out when he told them that he’l show them a friend’s house who oz keeping an AK47 gun… So,whea and how dd he get the pepper powder that he sprayed the other policeman?

 16. Despite being a hard core criminal,but I can’t be over the moon with your death….JONA will be greatly be missed especially with your cycling skills eishhhhhh…and when I remember our hay days at Lunzu…it was all about being a celebrity and now so sad that you are now the celebrity in the most horrendous manner….what else can I say……..RIP…till we meet again

 17. Zikomo apolice pomuombela ndimomwe ndalama yavutilamu basi winaa wake azingoti Bela, let me thank u once again apolice athu because ngati mwana WA m’busa amayenera kumvela kuti munthu aliyense azadya thukuta lake shame own u pastor kaiya. Nkana ochewa amanena kuti uyambe wachotsa chisoso mudiso lako before usanachotse mudiso lanzako kuli busy kukamba za Ana anzanu anuo nkumayikila kumbuyo.

 18. Mukanakhala ndi nzeru simukanaweluza chifukwa kumene kumayenda mwana wanu simuziwako musiyeni mulungu oziwa zinsisi zam,banja lamuthu azaweluze ekha

 19. Bible limati ubwana ndiunyamata ngwachabe komanso pali unthenga omwe umati Abisalomu anafera zake zomwe komano chomwe ndingakupempheni abale musaweluze musiyileni mwini wake Mulungu

 20. Mkanaombera George Chaponda chifukwa amalawi ambiri akuzuzika chifukwa chakhalidwe lake lakuba chimnthu chosakhudisidwa ndizomwe chili nazo kale

 21. koma anthu enanu have you read the story or you have started commenting.? the guy was a criminal thats it, justice yake it mukufunayo cz the guy was escaping jail while waiting for trial. He deserved it he was a criminal.

 22. turning othrs to God but failing your own kids youre also going to answer your own crime against Him shame on you pastor

  1. Kukhala m’busa sikuti ni Mulungu kapena mngelo, nayenso ndimunthu, mwana anasata mtima wake sikuti samalangidzidwa, mukamaweluza mudzidziwa kuti inuso ndinu makolo mudzakumana nazo.

  2. Frazer Mguwat usathe mau. Ili ndi dziko. Palibe Kholo lingasangalale kukhala ndi mwana chigawenga. muyankhule ngati tsikulina mudzakhala ndi ana, dziko lili ndimakutu.

  1. Ministry yanuyo ndiya satanic makape inu !! Mukapenphera bwanji ndicimbava ?? Ndakhulupilira kutino ministry imeneyo imayendesedwa ndi ndalama zokubazo . May his soul rest in hell wasala ndiweyo

 23. HEY OFFICER DONT SHOOT THEM DEAD BUT ARREST THEM NANGA WINAYI MWAMUYIWALA PATI? WABA CHIMANGA CHATHUYI. “SO SAD MALAWI”MBAVA MPAKANA UNDUNA WAKEWAKE?

 24. HEY OFFICER DONT SHOOT THEM DEAD BUT ARREST THEM NANGA WINAYI MWAMUYIWALA PATI? WABA CHIMANGA CHATHUYI. “SO SAD MALAWI”MBAVA MPAKANA UNDUNA WAKEWAKE?

 25. d police who shot thiz notorius niger,he waz right,some of u here u r blamig d police coz sanawambeleko,one by one is goig nw,ena asalawo atengelepo phunziro.we r already poor nde wina azikumbela.d way situation waz if u were u ukanapanga chan?4get nt kuti apolice-xo ndi anthu n mo ova they huv relatives.gud job here tiziwavutikila kupeza dola ife,manganyu bwa?rest in eternal peace of GEHENA.

  1. I wouldn’t give a chance to a car thief even if I walk up at night and see him driving away when my revolver is loaded

 26. Nobody derseve to dies in such way,doesn’t matter mwana wa mbusa or what or criminals ,policeman could handle him professionally.

  1. These policemen are well trained on how to handle criminals & am not blaming them hope this was the only option otherwise there life was on risk!!! Let his soul rest waiting for the last judgement

  2. #MTWELA ngati uli m’mozi mwa iwo uonekera ndani ku Malawi kuno anagwirapo chigawenga cha mfuti pomwe chikuomba live bullets?? Mwadya zambiri eti?

  3. Kumva chisoni poti Bambo ake ndiodziwika akuba akumaotchedwa ma delamu akusiyana chani nde iyeyu?? Mumafuna amunyengelele akupanga zolakwika akafike ntchito zake zamuchitila umboni basi

 27. Kunenetsa Makolo×2 Ananu muzimva kamodzi. by Pati a Big Tung’ande. osati dzana Pastor Kaiya apa, iwo anayesetsa mbali yawo koma mwana osamva.

 28. Koma ndiye anali akamuna ogona kukhomo kosatsekatu! Nanga mpaka kuba track ya cement kukagulitsa cement ndi track yomwe pamodzi? Kkkkkkk! Anangowodetsa ndiye kuti! Koma lero ndiye wagona kukhomo kotsekano. BAD NEWS!!!

 29. I hope the criminals does approved by court and the court passes judgement,where does the law say to kill a suspect?

  1. Ukungonenera kusadziwa zomwe aanachita tuesday akumugwira., anamenya apolisi awiri apa area5 mpakana apolisi ndkulira ndpo anthu ena ndiomwe anachita kuthandiza ndpo ngt amafuna kupha wapolisi ndie umafuna amunyengerere? Ukunenera kusaberedwapo iwe et

  1. Anthuwa amaonjeza amwene @Matthew, for u Beckie, truth pains and I’ve no any regret for said this, if you are the beneficially then that’s for your own gud but truth pains and will set me free

   1. mesa amathawa ku ndendeko? you do not know how painful it is kuberedwa what you have laboured for. Before i was thinking like you until atandibera kunyumba. now onwards ndidzapha ndekha ndikadzangomugwira wina akufuna kundibera. let God be the Judge.

 30. Musaloze chala abusa inunso ana anu sapanga zomwe mumapanga kumbukirani nkhani ya esau ndi yakobo anaberana madalitso ana amunthu wamulungu sikuti amakhala angero ai ngakhale atamulangiza mwanayo ngati anasankha kukhala ndimagulu achitidwe umenewu bambo sizingawankhuze aliyese akakula amasankha ekha chochita mayankhulidwe otero siabwino inuyo ana any amapanga chani? Mwinanso ndi oopsa kuposa uyu koma sitingaziwe ifeyo chifukwa inuyo si otchuka nanga inuyo mumatani osalozana chala apa ukamamuloza nzako ndichala chimodzi iwe 4 zimakhala zikukuloza iweyo bwino samalani tisamale tonse chiweluzu ndichamwini moyo

  1. Zoona makolo amayetsetsa koma anafe titsalodze chala abusa APA tinkhoza kugotenga themberero .anafe timankhala abwino pankhomo koma tikagochoka we change men’s ndikumuziwira Jonathan olo zoti bamboo ake amaziwa kuti he was a Roger ndakaika.kugoti anafe tikaona kuti Manolo akutilagiza timati ndakula ndikankhale pandenkha cholinga tizikapaga zsnthuzo bwino rest in peace JONA tizskutsowa

  1. Mwati owo Cc ndimadana ndi mbava kwabasi kungotenga chinthu chanzako mpanda kukhesera thukuta ndi tchimo yaikulu.Akanakhala dolo azikaswa mabank kubera Boma bola pamenepo

  1. he was a thief anaba galimoto plus truck ya zagaf muli cement nkugulisa. Ndiye akafika ku mudziko a police anammanga kenako wawapusitsa apolice kuti nzake ali ndi Ak47 apite akawalozere panjira anamlanda wapolice piston then the fight began. then was shot

 31. Dad …y so soon …..I was coming to c u …..I stayed away from 4 a wrong tym….but u jdt left so suddenly …….R.l.P…….I lov u

 32. Eli Analangidwa Chifukwa Cha Ana Ake Mau Amulungu Amati Ngati Munthu Akulephera Ku Langiza Ana Ake Azasunga Bwanji Nyumba Ya Mulungu

  1. munthu wamulungu amakhalanso ndi mayeselo ake.sikuti bambo ake sadamuphunzitse kuopa mulungu iyayi,koma ndi njira yomwe iye adasakha kuyendamo.dont point a finger at his dad coz we r o at liberty kusankha kuopa mulungu kapena ayi

  2. What has his father being a Pastor got to do with him being a criminal. It is so pathetic to hear such comments from a grown man like you.

  1. adali mbava yoopsa, ndipo mbuyomu adathawa ku ndende ndi azake ena, lero ndipomwe apolice adamuona ndipo pomugwila adapopela apolice tsabola mmaso, kenako atamugwila adawauza apolice kuti ali ndi mfuti ya ak47 ndipo ili kwa mzake ali mu njila adalanda mfuti wapolice mmodzi ndikumuombela pa nkono izi zidapangitsa kuti amuwombele podZiteteZa

 33. AliyenseKwayekhakwayekha,Mulungu akamuweluza monga mwantchito zake,sakaitana abusa bwerani apa mwanawanu amapangazakutizakuti AYI!. ABUSA NAWO AKAYANKHA ZAWO.

 34. Ngakhale Loti wa mu bible anali ndi ana ake awiri ozunguza kwambiri ndiye apa dzina la pastor Kaiya lisakhale likubweredzedwa kambirimbiri cholinga nawonso awoneke ngati wolakwa. Izi amapanga ndi mwana wawo osati iwowo. Mwana wa m’busa si m’busa.

Comments are closed.