Man arrested for killing impalas

Advertisement
impala-entelopes

Police in Machinga district have arrested a 23 year-old man for killing three impala antelopes at Liwonde National Park.

The suspect has been identified as Jonasi Sada.

impala-entelopesAccording to Machinga police spokesperson Davie Sulumba, on Thursday police officers received information that Sada and his friend who is currently at large were selling game meat in Kaudzu village in the district.

Police officers and park assistants from Liwonde National Park rushed to the area and managed to arrest the suspect. They also seized three Impalas and three muzzle loader rifles.

According to Sulumba, the muzzle loaders were buried in an uncompleted house few metres away from the house of Sada’s friend.

The suspect will soon be brought to book to answer charges of illegal entry into protected area, conveying weapons in protected area, and killing protected species which are contrary to sections 32, 33, and 35 of National Park and Wildlife Act as well as illegal possession of firearms contrary to section 12 of Fire Arm Act.

Sada comes from Sadamwana Village, Traditional Authority Phambala in Ntcheu district.

His arrest has come a few days after three other men were also arrested for killing Kudu Antelope valued at 2.5 million kwacha.

Advertisement

112 Comments

 1. But when an animal kills a man, what happens? stupid are we not suppose to rule over animals and…are these not the same animals we are suppose to kill and eat…when are we going to exploit the nature that God has given us when. people are controlling it as if it’s artificial…..

 2. Amalawi tikuyenera kudziwa zaumphawi wathu kodi munthu nyama azidya kamodzi pachaka ndie kuti zikuyenda palibe chalakwa munthuyu ntengo wankhuku ukuposa ndowa ya chimanga ndie nyama yongogwira ndikupha akuiona inu mukuti atani musiyeni akadye nyamayo ndi ana ake

 3. Oba ndalama zaku admarc ndie muti timfufuze kaye opha alubino alibe mlundu ntulutseni opha nyama yakuthengo mukuti kundende zomwe zikuonetseratu kuti umbuli ulipo kumalawiko nyama mulungu adailengera kuphedwa ndikudyedwa osati munthu akapha nzake nkumati palibe umboni koma chikhalirenicho mwampeza ndi ziwalo mmanja

 4. We’re also animals if elephant kills a man let the police arest the elephant imediatly if not lets all kill that elephant. Akuluakulu moyo wamunthu siuwerengedwa poerekeza ndi nyama yakutchire anthu okupha anzawo amaenda free and okuba ndalama ali afulunso panopa ngakhale pa jonzi pano ukupha nzake amamusiya koma akangokuona kut wapha njiwa or nkhunda ziri mbweezi iiiii upita bas

 5. asaliji are you telling us that the police entered in the park and arrested apoacher?if it so,where were the game ragers?

 6. Tiyeni tisamale za chilengedwe tisaphe nyama mwachisawawa and ngati kuli kususuka muyaluka nazo coz chilinchonse chimafunaso moyo and kukhala mokondwa ngati iwe amene, so plz plz guys coz to tilibe nyama zambiri kwathu kuno and anatsala ndi afisi okha okha bas komaso awanthu osati a original ngati ndikunama

 7. Iwe #Damiano usamalankhule mwamatama mesa inu aGame ndiamene mumakhuzidwa ndi kumpha Njovu inu siku likubwela muzamuziwa Mulungu unyolo uli manja mwanumo

 8. Chomwe mungaziwe ufumu wanuwu uzathela pasi pompano mukaonjeza malamulo anu mutaya nthawi yanu mulibe agogo anu anabelekepo nyama kuti mukamangile anthu ndalama mwaba.iye pokhapo amafuna thandizo mukufuna mumuuze za bero aboma manyazi mulibe ndalama zosezo mukufuna mudyele osauka tiuzeni ndi ndani wamangidwa mutamupeza ndi ndalama ya cash gate? Chomwe mungaziwe mulungu simuthu agalu inu mwangokula mitu koma mulibe nzeru mulibe ubongo muli ma tress sindimaopa muthu olengedwa ndi mulungu ndimaopa mulungu mutuluseni akayakha mulandu kwa mwini ziweto

 9. Aboma minyero yanu mwandikwana mukusiya kugwira akupha ma alubino wa ndikumanga akuba ndalama muboma mukalimbane ndi okupha somba okupha nyama mitu yanu sikugwira

  1. Alipo amadandaula ifa ya nyama or chiweto amadya koma last week amanga okupha somba pano okupha nyama ndalama adya okha akuganiza kuti anthu azitani?

 10. Hajira saliji zonse ukukambazo sizikumve what do you mean coz nkhani ukukambayo achita ndi a police Iwo alindi ntchito yayo Ife a game tilindi ntchito yathu yoteteza nyama zantchire ndi ndinkhalangoyo so don’t mix OK.delete your msg yo.inu nomwe ndiamene mukuwatuma kuti adzikapha nyama then akagwira nkumamvutika ndi kusaver ndende simukhalako choncho sibwino.but we the DNPW officers we are going to deal with them atill chilungamo adzachidziwe thnx

  1. Iwe Bande what do u mean when u say ndikuwatuma anthu aphe nyama? Umandidziwa ndiwope kulankhula coz ndiwe wagame lol .don’t make me Lough neh

  2. Sokuopseza as such but kukufotolozera udziwe coz iwe sukuyidziwa ntchitoyi kuti imakhala bwanji and ineso sindikudziwa ntchito yako kuti imakhala bwanji so tiyeni tilemekezaneni.tamugwira iyeyo potengera ndi malamulo athu Ife ndiye whatever munyoze Ife tankamatabe basi khothi ikaweruze basi motengera ndi malamulo athu ok

  3. Ndie vuto lako chani pa comment yanga kuti mpaka bp yako ikwere ndipo agame alipo ambiri, but kubwera poyera utchuke kuti umagwira ku game? Ndakuuza kale aliense amalemba comment ndimene waganira.

  4. Whatever ukhoza kulamvula zakukhosi kwako konse but palibe chomwe chingandi sunthe ine olo kutekeseka am just lookin forward thnx bless you lord

  5. Malo mongokambirana naye ngati mmalawi nzanu ndiye mwakondwela kuti akamangidwe. Si onse akuwaziwa malamulo a nkhalango ayi. Ndiye nthawi imene anali kupha nyamayo inu a game munali kuti?

  6. Kkkkkkk uli mvuto losatha mulungu adzikukhulukira iwe sudziwa izo ukuchita dziwa kuti sikupambana ndi kutsogola koma ku

 11. Opha mbawala ndye khamani khamani kumugwira ndicholinga chofunako nyama ya mbawalayo zinachitikanso kuno ku Salima apolisi kumenyanirana nyama ya njobvu,,,,,,koma anthu opha albino ali zunguri zunguri mtown ndi mmizindamu,,,agalu achabechabe inu ndakwiya nanu

  1. Eti eti mmalo mowamanga agalu anaba ndalama za boma aja mukulimbana ndi okupha mbalawa Eish! Malawi wanga akupita kt abale inu dzko la mkaka ndi uchi lija lero lasandukadi Dziko la Malawi lokomela anthu andalama ili osati amphawife ayi Only God knows

  2. Nkhuku bwino .aa ine anthu awa kundibowa.wina ndie ali busy kuwabakira.enanso dzulo kundiphera my brother coz kokakumbusa ngongole sanathe kumvesesana koma kupha ngati galu, polemba aziti anaba mfuti .Ndalama dziko zingobedwa anthu akuvuti ndi uphawi but osayisa kuba.

  3. Iwee! Nkhani ndiyopha nyama, tsopano zikhudzana bwanji ndi za cashgate? Popeza uyu mulandu wake ndiwakupha, zinthu zachilengedwe zimene ndizotetezedwa. Tsopano mulandu, wa cashgate awusinthe ukhale wopha Impala zigwirizana ndiye utsangalalano?

  4. Iwenso Tambala ndakuona kut ndwe tambaladi eti,,,Mulungu analamula zoti zolengedwa zidyedwe,,,anthu achi albino akhala akuphedwa muno apolisi samajijilika nazo lero wina kupha mbawala pompopompo kumuthira unyolo ndye ukufuna kutanthauza kuti moyo wa munthu ndi mbawala ofunika ndi utiwo????

 12. Ndekut ndiamene amaphaso njovu zija ameneyo lyf in prissone basi anthu tidzitisakumva kut boma ndi ma non govermantal akut nyama zakutchire zikuchepa kamba kanchitidwe umenewu

 13. Achita bwino kumunjata nyapapi ameneyu,boma lizinena chotani kuti tisiye kupha nyamazi,eeeeeeh! Nanu ma Game Rangers bwanji simunangomuombera gothi ameneyu.

 14. Mukumanga muthu coz siwapolice? Bwanji wapolice wapha muthu wamisala osamumanga? Komanso wapolice wabwinobwino kukabwerwka Ndalama munthu wamisala kupita kukakumbusa ngongole kulakwa? Munakhala bwanji Malawi

  1. Mmmmmh iwe utiyakhulitsa pambari ndithu!Zikuonetseratu kuti nkhani ya wa polisiyu sunaimvetse sinanga muli ku Jonz.Komaso sizikugwirizana tisieni a Malawi tizipanga zathu ku Malawi kuno.

 15. Lock them up. azikakumba mbewa ngati nkhuli yawavuta osati nyama zotetezedwazo ai.

Comments are closed.