Bingu National stadium vandalism irks some Malawians

Advertisement
Bingu National Stadium

Malawians have expressed anger after football fans vandalized some parts of the Bingu National stadium during the Luso TV Bus Ipite football fiesta.

Bingu stadium vandalised during Bullets, Nomads match

Fans who went to watch the match between Nyasa Big Bullets and Mighty Wanderers which was also the first ever game at the Bingu stadium broke taps and stole toilet mirrors.

Bingu National Stadium
Bingu National Stadium vandalised already.

Commenting on news about the vandalism, many Malawians derided the football fans.

“Most of the times, when you are poor you live in poverty, you don’t like good things because you become an enemy of development. We Malawians we are enemies of development because of our poverty that is why we have vandalized the stadium,” Future Mdeza said.

“Poverty drives people crazy and a lot of Malawians are poor in mind that is why they are vandalizing their own stadium,” Cecilia Mco chipped in.

While Binny Likomwa said: “Too bad, that is why Malawi shall remain poor because its citizens are so pathetic, you cannot understand why people cannot take responsibility to protect our own hard earned resources.

“It is for the first time we are having such a stadium and we expected every Malawian to feel proud and hence protecting the stadium.”

Many commenters also advised government to tighten up security when the stadium is hosting matches so that it should be maintained.

The 40,000 capacity stadium was built using K26.6 billion kwacha from the Chinese government and it was handed over to the Malawi government last year.

Advertisement

305 Comments

 1. Uwu ndimkhalidwe aliyense ngakhale muno mwathu mu zambia anthu akuba zinthu zofunika kuleta thandizo kwa munthu aliyense.panopa boma inaleta mankhwala yophela tidoyo tikudya chimanga m’minda ena anaba kale,anali kunena izi lelo pa znbc radio1 a chabwela zulu ndi orbister mbewe aulusi.

 2. zimayamba ndi inu akulu akulu, cashgate, maize gate, low sallary to civil servants, mwala to mwala loans to civil servants, nde m’ Malawi wotereyu , wamaluziyu angatani? stupid

 3. Its the workers at the stadium who did the vandalism by taking advantage of the game.don’t think a lay man could have the guts to vandalize.probe the workers.

 4. Anthu openga mwapangabwanji? Mumafuna zabwino muzizionela pa tv zikabwela pakhomo osayamika ndikanakhala wa police ndikanakumangani mu uzimu chifukwa sindikukuziwani mwandinyasa!

 5. I man chipe, I suspect the workers at stadium played that soon be4 game day. And now good back up for incident is ppl on game day. Yes ppl can, but staff.

 6. We Wre Told Kut Kuli Apolice More Than 150 Asirikali More Than 300 Nde Amataniko Onseo,asatinamizire Ife Masapotaaaa.Takukaniraniiiiiii

 7. Education. Education. These morons need education. What is wrong with Malawi? Why don’t people understand small things as having a proper running water tap? Why can’t people understand and appreciate the importance of having a mirror in loos or bathrooms? Education…Umbuli. it’s not necessarily poverty , but a dumb mind that doesn’t seem to weigh the differences .

 8. We need to change our mindset a Malawi koma sindikudabwa chifukwa mmalawi ngati amachitsa zikwangwani zapanseu kupangira makasu umbuli too much ku Malawi anzathu amaiko ena amanyadila zinthu zabwino zomwe zilipo like southafrica ma toilet abwino zikwangwani kumapezeka ngakhale mutchile

 9. It’s only bush people country left in the world, u do want to be developed koma zomwe akufuna kwaponyela pansi adya not in plates…. Especially Ku Lilongwe m’chewa sadzatheka ndithu kuzolowela nyau basi.

 10. Bwaba ndinu nomwe a midia kaliloleyo munaika nthizikwama tanu tija mukufuna muzitinamizapo apa bwanji??? Mesa mmalowa ndizikwama ndinu nanga enafe or titaba tingabise kuti??? Bvabodzaaaaaaaaa wakuba nimwe nomweeee hayiiiiiii

 11. m’malawi ndi munthu okanika kwambiri kaya ndi umphawi nanga mpakana kuba ma mirror omsewo ndi umburi . komanso ife anthu ena ozindikila tikaiona mburi ikuononga tizithana nayo tisamasiile boma lokha chifukwa bwaloli ndi lathu ife okonda mpila tikuona kuthana naye zitha zimenezo m’malawi ndi munthu ochitisa manyazi pa ziko lomse la pansi pano

 12. if old pipo in gvt r stealing..kuba kalilole wamu stadium does count to me…if our leaderz show n lead by good example then we follow suit…we will vandalize until da gvt listen to our cries…

 13. Amalawi Tiyeni Tiyambe Kusamala Katundu Wa Dziko Lathu. Mudziwe Kuti Ma Chines Sanamangile Ife Tokha Stadium Ngati Imene Ija, Azathu Amaiko Ena Anawamangilaso. Koma Za Chisoni Iyamba Ndi Ya Malawi Kutha Chifukwa Cha Anthu Akuba Ngati Inuyo.

  1. Tiyanjane, ndizoona iwe anthu amu Mtandire suwadziwa? Zinachitikadi and i was there. Mpira watha koma anthu kumakanika kupita kwawo kungoima anachita kuthamangitsidwa

 14. Amalawi kawonani zakuba kodi munthu wachoka ku mudzi ngati kwathu ku mdika ndiye ukabe kanthu ka tap kapena galasi lakuchimbudzi udzagwiritsa ntchito chiyani SHAME simudzakozeka aliyense amene akukhudzidwa ndi mchitidwe umenewu ndi chitsiru ndanena ndine

 15. They are saying kuti kwabedwa but i haven’t seen a picture kuti apa panali mirror koma yabedwa kapena apa panali tap, but what i know is that ntchito yokomza ku ma toilet inali isanathe thats why the toilets were fitted temporary doors, in my opinion someone is playing us, ife tiziti kwabedwa ndi anthu okaonera mpira pomwe iwo akudziwa how and where the so called stolen stuff is

 16. Why a u surprised ??? We are Malawians that’s our behaviour ,we start from school until when we reach udult hood. We need to pray hard so that we can stop this bad behaviour.

 17. Malawianz ndi adani achitukuko sizodabwitsa bola anabako zochepa achayirira game ikubwerayi kuti abenso kuposa pamenepo bola inakamangidwa ku 23

 18. Amalawi kuzolowera kuba maliseche awanthu umbava unafika pokhodzokera matap mukapanga nawo chiyani? Ine changa ndichison

 19. Kkkkkkkk malawi ndimunthu ovuta anazolowela zonyela mu tchile ngati amachosa chikwangwani cha nseu what about mirror choncho tingatukule dziko ndakaika

 20. Katundu wabedwayo akapezeka ku Ndirande kotero apolice asavutike ndikufufuza mu Lilongwe angopita ku Ndirande akampeza osayambanso

 21. But dont use Malawians as thieves. ..maybe the workers at the stadium ndamene anaba and are using Malawians as a scapegoat…its not fair. .how can some remove a mirror without noticed.

 22. Its not about poor leadership;but we idiots, we don’t think when we are after to pull Government and the people including them down, Countrys now our days are after competition through infrastructures.

 23. We are the first people to complain if things are not moving.
  All we want is the thing to move and we come in and punch the tyres.
  Nowadays to be a malawian
  Zumachita Kunvetsa Manyazi

  1. Exclude yourself bro, those people are these ones who stole at stadium.
   Tomorrow they will be striking just for their own sake

 24. Esther wa amvula
  Funzy pogba prosper
  Aaron nyirenda plus ME are some of the people you undoubtedly can tell are the ones who vandalized the stadium.

  Look at our comments.
  Malawi is rotten with these people

 25. Amenewo ndiyo aMalawi , atengera kuononga zinthu ngati atsogoleri athu . Wina kuba zachimanga wina kukaba katundu ku Stadium ,, khalidwe lonyasa basi !!

 26. That’s good am sorry to say dat , akanathandiza admarc ndi ndalama zimene mwaononga kumanga stadium imeneyi we should have sing another song

  1. That stadium is a good devepment if you can think wisely my bro. but if it is a true story then those people are de facto and uncivilised

 27. You employ a garden help and he steals all the gardening utensils!!! And gives you that look he doesn’t know who took them!!! Kkkkk talk about taps!!!

 28. Mmmmmmm guys sibwino kutelo ayi, mwina anazolowela kupambukila ku ntchile nde izozo akuziwona kuti ndi za chilendo kwa iwowo.

 29. amalawi pabwino alibe.ku mzuzu paka stadium kathu ka nyuwani anthu akunyela ku shower mmalo month lowa ntoilet and yet chilichonse chili mmalo mwake.anthu akuda we got problem koma!!!

 30. Sizokuti mukaba nokha kumeneko mudziti anthu omwe amaonera mpira aba munthu angatuluke bwanji ku Stadium ndi ma mirror anthu osamuona?

 31. boma likungotithela ndalama munthu kupanga ka business kakang,ono akufuna msonkho nditizitumbuwa tomwe amvekele tipaseni tikiti ngati simpeleka tilanda beseni kungobela amphawi basi mbava zinthu zikukanikani kulongosola

 32. Kkkkkkkk koma amalawi mukhalidwe wonyasa kwambiri kuba mirror kodi amalawi mukufuna chitukuko kapena umphawi mulibe manyazi boma kuyika zisulo musewu inu kuchotsa kumanga mabridge inu kuchotsa mapolo chocho mungatukuke ayi kubwezera chitukuko kumbuyo

 33. Malawi wil remain poor forever ! Mmmmmmmmm ! Here is south africa there are alot of things in a public places but you cant even see someone tries to vendalise.

 34. Basi kuzolowela uchikumbe mwaononga, muzitinso akomze kodi mumafuna wabwino akhalendani? Dziko likutukuka mukulibwezela m,mbuye atengeso ndalama zina akonzetselenso muti palibe chomwe akupanga, mutakhala inu mungatani apa, ine ndikuti amangidwe anthuo ena titengelepo phunziro sibwino kuononga zathuzomwe ndiifemzika.

 35. Masapota A WANDERERS Ndicoco Amati Chilicoxe Cimayamba Ndi Iwowo Kutereku Ma Mirror Ndi Tap Aba Ndiwowo Ati Chipukuta Mixozi Choti Akhala Zaka 11 Osatenga League Title,,,,muzimvere Cixonii A Wanderers,,,,BOMA Latimangira Chinthu Chokongola Inu A WANDERERS MUKABAXO,,COCO DZIKO LINGATUKUKE??? NDI MASAPOTA OMWEWAXO A WANDERERS ANAPHA LEMIYAS JOSITA KU BALAKA STADIUM R I P..NDAKWIA NANU A WANDERERS.

 36. Kodi a Malawi tinakhala bwanji osafuna kuona chinthu chabwino chogwilitsa ntchito aliyense,koma zinakakhala zathu zokha.This is jealous at its best,we need Pastor Bushiri for spiritual healing.Stadium isakhale ndi ma mirror ku toilet mwaona chachilendo.God forbid.

 37. Team ya NBB ndi Beforwad ma features awo azikamenyera ku Civo stadium,Silver Stadium ndi mabwalo ena ngati tikuyikonda stadium yatsopanoyi

 38. koma abale ine zimandimvesa chisoni kwambili boma lamanga chinthu choneka koma mukubanso likati lisakuchitileni zinthu mumatukwana kodi mumafuna chan komatu kuno ku s African simuzaona anthu akuononga olo kuba katundu wa boma koma ndimadabwa nawo ku malawi anthu amaba chifukwa chani koma ine ndikuona ngati anthu a mcp ndiyamene amapanga zimenezi cholinga amuipise munthu wina bola akanaimanga ku blantyre zikanakhala bwino kwambili chifukwa anthu akumeneku ndioganiza ndipo ophunzila kwambili amaganiza kusiyana ndi awa ochewa wa ndimbuli anangozolowela ku susa zina zili zonse

 39. Ngati mbamva zikuyambira kuba ku boma ndiye anthu wamba apange bwanji? akubanso zaboma no need to worry just go and fix it akuba aberana

 40. Aliyense ndi Wakuba kuyambira President ndi Chief Marshal George Chaponda,,ndiye mukudandaulapo chani? mayesa tinamva kuti kukakhala chitetezo chambiri ndiye amaba bwa?

 41. Mtalika amanenadi za umbuli wa a Malawi pa kuba, afuna kena kalikonse kakhale kache,
  Mpaka nkukaba kalilole wa kuchinbuzi abalenu?
  Stadiumyo ilibe macamera?
  Zachisoni mtundu watha!

 42. azathu ku Zambia anayamba pakanthawi kugwiritsa ntchito,koma zonse zilindeee momwe anamangira.koma ife game yoyamba zinthu zabedwa kale? amalawi ndi chani kwenikweni? Nanga kumenyedyere magame 10 ndiye mukuba magolo tsopanotu. Chitani manyazi ndikuononga mbiri yadziko lanu uku komanso kubwezera chitukuko mmbuyo.

 43. M’malawi ndiye ameneyo alibe pabwino, uthenga wanga kwa ma Politicians ndalamazo zikapezeka zibeni m’mene mungathere coz m’malawi safuna chitukuko. anazolowera umphawi basi mxieew

 44. mmmmm Malawi ndiosauka inde koma zinazi timaonjezera ndife mbadwa coz there is no way ungabe mirror la 10 kwacha lomweli, kuba ma tap pomwe kwanu muli ndichisime at the end boma ndilolephera mmmmmmm shame on us.

 45. mmalawi ndi munthu ovuta ndakhulupira sopano.
  they cant just watch the match without touching things.
  they go to the stadium toilets with tripple missions.

  how did they carry those mirrors from the stadium(am amazed)

  there is a need of more and more security personels

 46. Malawi sidzathekayi I mean 4 real why vandalise govt property why mwakhala mukulira munvekere aMalawi tilibe stadium yabwino now stadium ija yabwera mukubanso anthu openga mwapanga bwanji

  1. its gud..they shld hv evn taken da stadium home..dis gvt does nt care,it z bizy stealin millionz n a citizen takes a mirror home n da governmnt cries foul…fuck!

 47. inamangidwa chaku mtandile ndichifukwa chake zikutelo bolani idakamangidwa pa plot yakwathu ku 18 mukuona bwa?

 48. koma akapado fc paka pamenepo, koma chosecho munawina, kapena kunali kuphya mtima mkuziwa kut bus yanu ndioonongeka nde kunali kubwezera pokuba zipangizo za stadium

  1. tiimbatu nyimbo ya malume bokosi, tionetsetse chili apachi chinathetsa nkhuku zonse pakomo, kusamba kusakupusitse anthu lero akuvulalira mkati

  2. nde iweso neba bus ija inakupusisa kunja ataipeta peta bobho iwe wati cha ndapata cha mamillion apa ankhani nkhani osaziwa kut mukati ndichoola kkkkkkkkkkkkkkkk

 49. I knew from the begging that these things will be happening. that stadium was to be built in BT not here in LL, our friends are more disciplined that us. thats just the beggining.

Comments are closed.