Bullets fans have the last laugh in Bus bonanza

313

Despite being humiliated, humbled and outsmarted by their rivals in the Luso Television Bus Ipite Football fiesta where they conceded five goals in two matches, Nyasa Big Bullets supporters are not the most worried with the loss. Instead it is their rivals who have all the worries piled on them.

This follows the breakdown of the newly won bus as Wanderers were returning to Blantyre.

The 26 seater Civilian bus developed a clutch plate fault at Manjawira, forcing players to abandon the new bus on their way back to Blantyre.

Bus

Nomads bus on service, this has become their mockery from Bullets fans.

Minutes later, social network was invaded with pictures of the bus at the fault area before more pictures at Nissan Offices in Blantyre where the bus is being fixed.

“We knew it, there is no way we can lose 5-1 to Wanderers, we knew that the bus was not good,” wrote one fan on the social media.

“Nissan Civilian Year of make 1997 Original price K7 million Claimed price K25 million Tax free as it was purchased for charity first trip: breakdown at Manjawira,” another fan mocked Wanderers.

However, Gift Mkandawire, who is Wanderers’ Vice Chairman said the issue of the bus should be reported in a professional manner.

On their part, organizers of the bonanza, Luso television, through Station Manager Dick Juma said the bus is still in perfect condition despite developing the fault.

He also rubbished rumors that Luso Television has made a lot of profits from the just ended bonanza saying they spent K40 million for the event to take place but what they got is not what they expected.

The Nomads fans maintain their rival fans are only frustrated to have been reduced to a 5-1 aggregate.

Share.

313 Comments

 1. koma munali piston m’menemu kkkkkk ine kudabwa miracle scoring kkkkk. Mekha wanu Nakamora anapita kkkkkk musova wish Neba quick recovery kkkkk

 2. You can not use yesterday’s tools in todays job and expect to be in a business tomorrow, for a moment try to think what great opportunity you have missed in the past years, you can’t relax unless there is rescusitation of you dreams, reviving your lost visions! Or else were you worried that you did not move in the right path in chasing success. Don’t mind its your past, let it go, here is a risen opportunity to take you closer to the path of success with#DISTANTVISION MALAWI, you will find what you lacked for a long time in your life.We are international recognised organisation, infact a pool of donor funding, we work with young people acrossthe nation! For more information like our facebook page #Distant Vision Malawi, follow us on twitter, @vision-mw, or else email the national coordinator at symonlubanga@gmail.com, WE DON’T MISS OPPORTUNITIES whenever it comes our own ways in life!!

 3. Sponsor wanu kuchimake kwa galimoto zambiri koma osakupatsani yabwino ndithu? Ayi mumawakayikitsa akudziwa kuti sumungawapindulitse chifukwa mumalimbikira timipikisano tandalama zochepa koma superleage simulimba. Kkkkkkkkkk

 4. Name the first team that lost at Bingu Nation Stadium by 5-1 aggregate the answer will be Bullets. Name the team that won a bus at Bingu National Stadium the answer will be Nyerere hahahahahaha wakwiya ndi mfiti

 5. Sometimes you need to reason things the bus did not come from heaven for everything that is made by a man there is nothing strange unless you tell me it was bought from heaven NEBA you are mad uzithokoza a MOYALE unawabera aja unabwera chabe opanda chikho

 6. Off course we lost those two consecutive games but as for that bus of yours Neba mmmm yoyenera a Wanderers nomwenu mpake munawina sitikusilira bus imeneyo njanu

 7. Admn iwe mbuzi, khakhakha, Nkhasi, Gulukunyinda opanda nzeru, ukuyenera kuwauza anthu kuti bus sinalakwe kalikonse, inalakwa ndi Noma pothidzimula Nyasi big bullets, that’s all!

 8. Kkkkkkkoma mkangano wakula uku shiiiiii munalonga munaneta ife pyathu nkhungothaimambo. Makaniki kudyambo pyake Luso kudyambo mbondo noma kuduambo phapha pyadidi basi waaaaaa leka kulonga ba noma inatcherenga iyi na bus maningi

 9. Kodi admin ukukokomeza nkhani ya Bus , 5-1 ayi , Bus ikuyenda ndadutsana nayo pa Nyambadwe ikuyenda mseu wa Chileka lero pa 5 January 2017.

 10. I think bullets fans need to be sensitised.Iwenso neba bus iyi wagula nawo and on top of that zigoli 5 kwa 1.Amva kuwawa nda?sorry neba mutu uzitchaja

 11. guyz why not worring while your lossing ndekutnso team yanuo simumaikonda Noma nd Dilu zikumphweteka akasume! viiiimuu!! pachi Bus chathuchi a Bullets Kathamangiran

 12. Tiyen tivomereze aneba anawina koma vuto ndi aluso tv powapatsa basi yomwe ili ndi vuto. mmasewero ampira ndizotheka 5:1 tiyen tisangalare bho kut mawa tizasangalareso, neba samala tizabweza chipongwe chimene watipanga. 2017 ndi maulemaule.

 13. Ngt Radio yotchedwa tyms ndakhulupililan kt sports dest ndi ya kampopi 1. sadamalize game coz Noma idawina 2. pa mpira ku Malawi sadakambepo za game ya bus 3. zomwe adakamba ndi zonokola kwa bus. 4. etc sindizamveranso sports pa tyms

 14. Sanje a Malawi..& Wanderers is losing nothing here…pomwe inu a Bullets Munaluza 5:1..munaluza Bus & even play maker Chande tinakulandaniso hahahaha

 15. Ukanalemba nkhaniyi muchichewa chifukwa abale ako akusekawo ndakaika ngati anva zowme chizungu walembachi, moti akungokusekaso ngati m’meneakusekela breakdown, shame.

 16. Akusekera umbuli..chifukwa tikawauza kuti tulusani yanu yabwinoyo sakutulutsa,chabwino tulusani chiphapha sakutulutsa koma ukawauya tulusani zigoli akutulutsa zigoli 5 hahahahaha odi uuko..anhopemphera kwakuya mwina amasters security atha kuwapasa yawo ija

 17. Ine monga sapota wamkulu wa maule sindikudadaula ndi tax chimene ndikudaula ine tnm yokha basi chifukwa tavulidwa ufumu ndi ana ang,ono chimene ndingakabe mchakuti tiyeni ting,ane tsogolo zakale tiyiwale angakhala iwe neba ndiye unayiwala kalekale kuti anthu amatenga supel leag

 18. Za ziii,ine ndimaona ngati zaonongeka ndi zigoli,ngati ili bus simakonzedwa?inu munabwerako mchani ku LL,musova,muyankhula mutopa mpaka mabala mkamwa simunati

 19. If we can go back to history, Bullets managed to beat wanderers 5-1 in a single match and wanderers has managed to beat bullets 5-1 in two games but nomads supporters they talk as if they are lunatic pple

 20. Hahahahahahha why being worried. The best of all seasons finishing the year in style and beginning a new year in high spirit after defeating our old rivals.

 21. Bullets fans has nothing to worry …its all about the bus kapena tinene kuti minbus
  NKHOPE ndi ISUZU
  BODY ndi NISSAN
  ENGINE ndi BEDFORD ….MUSOVENGE kkkkkkk

 22. KKKKK NEBA SAZATHEKA…..KUFERA WOOD…IMENE IJA NDI BUS OR IZAKE YA BUS…BUS IPITEDI KU GARAJA…KKKKKKKKK..NAKAMULA ABWERE AZAKONZE..KKKKKKKIEST

 23. Ngakhale wonderers ikanachinya zigoli 200 ndizopanda ntchito chifukwa Bus YAFA itangoyenda ma km ochepa kuchokera pa stadium. Yafa bus,ngakhale tiyankhule zambiri bus yake yafa basi!zopanda ntchito bus yafa! Bus sinafe?

 24. Kod neba season yangothai watengako cian cogwlika ngakhale day lolandla photo zaleagu uzatengako cian?pakanakhala photo ya njiru,kaduka,nsanje ukanalandla koma palibeso pepa neba kkkkkk wagwla cito yopanda maliro kkkkk

 25. Munthu Akakhala Olemela Patsogolo Amadzakhaso Osauka Tsono Osauka Uja Amadzakhala Olemela M’kumulembaso Ntchito Uja Adali Olemela M’mbuyomu Mkumati Adali Mphawitu Uyu Koma Lelo Wandilemba Ntchito Ndiye Chikukuvuta Ndichani A Bullets Kut Mungovomeleza Kut Ma Noma Ndi Team Yaikulu Inu Ndinu Ana Basi Tavomelani Kuti Eya Ndife Anadi

 26. BB kuzolowela mach fixing mpira obera ciyambi cabe cimenec mulira zen zen sulom yakuzindklan kut match fixing yakupulumusan mu zambr neba usovenge utambka cakacino

 27. Timvane bwino lomwe ndithu
  inu ndi ife tonse ndife amphawi tokha tokha. Tilibe bus tonse apa. Tikahara ndi game bus timachita kubwereka. Ena ataona umphawi wathu anatinapatsa mwayi oti tilimbirane Bus imeneyi kuti tichepetse vuto la mayendedwe. Tisanamepo apa tonse Bus yi timayifuna poganizira za mavuto omwe timakumana nawo ikafika nthawi ya mayendedwe. Titayesana woperewera mphamvu zamuvuta ndipo wamphamvu watenga Bus. Mmene mpira umamenyedwa palibe amene amadziwa za mavuto a Bus. Lero Noma yatenga bus mukuti ndi chiphapha. kaya ndi chiphapha,kaya phokonyore koma chodziwika ndichakuti “noma lero ili ndi Bus,kusiyana ndi padzana paja tinalibe ngakhare phokonyore olo mmodzi, timachita kulipira ndalama kukabwereka phokonyore wa ena.
  Inuyo wanu ali kuti phokonyoreyo??

 28. A Luso tv so you think Malawians are still stupid and blind??That bus cannot cost MK25,000,000.00.(U$34,000.00).hahahaha kendall and your team you must be jocking.The good thing for you was that you were dealing with stupid and senseless official from both bullets and wanderers who could not forsee that you are using there clubs to make a fortune.Ok,wait a minute Luso tv,I mean Kendall and your team can you produce the documents you used to purchase the bus to the public so that this matter is put to rest?My simple advice to both bullets and wanderers next time don’t allow these thiefs to use you like they have done now.

 29. Nenani mmalize!!!Red/white, Bus belongz to B4WD the Pionners of Investments!!Nxt Bonanza,idzakhala ya L city Dabbie zikupwetekabe”SIUNATI NEBA!!!”2017P,more fre gyz!

 30. Nkhani ili apa ndi ya zigoli osati ya bus ayi. Kungoti zigoli zinachuluka ndipo zikadawawabe mpaka lero, how possible is it for you to keep on laughing at that up to date yet you lost the match and failed to get the bus? Ine sindikuonapo chinthu choseketsa, uku ndi kulira uku!

 31. Ngan sachitika kuno Ku sounth Africa anyamata ndi akanz pachire yosemba bedibuliji anthuwo awomberedwa anthu ambiri awomberedwa ochepa apulumuka ngani ikuti matilasipota akumalawi

 32. Inenso nkhani iyi yandijwana, kuyambira 2015/16 kuti muyambe kuwelengetsera zigoli ndiye kuti kuti winawe usova, nkhani ndiyoti mwapata bus ndipo a Luso alibe mulandu ulionse kamba koti akupatsani chaulele komanso kachipukuta misonzi kaja munagawana kaja muwauzenso ma player kuti abwenze mukakhonzetsere bus

 33. I dnt understand Malawi 24 wat r u trying to say!!!!! U dnt have something to ryt???? Galimoto imaonongeka ndipo imakonzedwa nothing new here. Anyway see u cha mmabullets mu………meaning cha mma 5!!

 34. Ndiye pamenepa sizingatheke kubweza? Ngati yavuta kwambiri mundindibweretsere ine ndikuguleni ngati scrap. Mopilira ndikugulani k750,000 chifukwa ma bus amenewa ndi achikalekale!

 35. Mmmm apa ndi pomwe kampopi FC yayalukira. Zoona 5-1 mu ma game awiri? Koma mpira mumaudziwa makape inu? Bwanji osamangopitiriza kuba m’tawunimu, ndikusiya kumenya mpira? Nyanga zomwe munakhwimira Noma zija zoona mwalora kuti zisuluke? Hahahaha

 36. Hahahahahaaa za bus tisiye uko koma tiyang’ane za zigoli now. Kkkkkkk 5-1 kodi team imeneyi imapanga training? Kodi ku training-ko amavalako ma pant? Kkkkkkk zamanyazi kwabasi (very shameful)

 37. Admin ndwe chitsilu, tonkhwetonkhwe , nyani ,vivi , kanyimbi weniweni mukafuna kulemba nkhani muziganiza kaye mwava , kod chikanakhala kut inapambana nd bullets mukufuna kundiuza kuti akanawapatsa bus yabho kapena yomwe ili nd vutoyo??? masapota a bb 95% mwa iwo nd mbuli samadziwa udindo weniweni wa supporter , noma 4 real, bfoward the wise pple’s choice .watch out u ignorant pple.

 38. koma Noma si anzathu, mpaka 5 : 1. ine ndinanena tisachite nawo mpikisano umenewu chifukwa Noma ndi Barcelona ya ku Mw, taonani apa yatikantha ngati dothi. Ma player athunso onse anakalamba ngati abilimankhwe.

 39. Ndikudziwa kuti zosezi ndi nsanje ndiye nsanje sikupindulilani mungoyang’ana za team kuti ili bwino kapena ayi chifukwa kumenyedwa kawiri ndizochititsa manyazi kutengera mbiri ya team yanu zigoli 5 ndi zambiri bus yangoonongeka clutch plate bt still in good condition inu mwatenga chikho chimodzi nyerere zikho ziwiri + bus bwanji osachita manyazi ndi performance ya team yanu.

 40. Khazibeki, Tateng. Fisidi Tatenga, Bus TAnyamula. Kaya Yo4ila Ife Bola Tamuonesa Neba Kut Paife Sangaime. 5-1, Ndudu Big Bullets Wasmikza Kt Kusuta Kumaononga Moyo.

 41. Kumene ife a Bullets sitikuda nkhawa ndi phokonyole wawoyo akanakhala ena anakangopita kukabweza Nakamula anayenda wapasi chi bus chitafela panjila kkkkkkkkkkkkkk Neba suzathekaso basi

 42. Its what I know about BIBI supporters, anzawo akachitabwino, ndi zoola aiwala zawo zopezeka akapereka ziphuphu kwa oimbila, musatinyasepo apa 5> 1kkkkkkk

 43. This is just nonsese mainly to you admin but to the bullets suppoter i can tell them they still needs to worry coz its not about bus but history the have to think of that if they relly love their team emagine 5 goals in two matches,ine wanoma

 44. Chifukwa Chake Masapota Noma Ndiwozindikila Anavomeleza Kuti Chitsulo Chimakhala Ndimavuto Koma Akanakhala Neba Tikanamva Kuti Mafans A Fodya Wa Bale Aphwanya Maoffice A Luso Tv Chfukwa Chabus,,

 45. amene akufuna ganyu yokankha bus please tumizani ma cv anu ku lali lubani mukakankha from ntcheu to Blantyre bangwe. onse amene akudziwa ntchito ya u mechanic chonde tumizani ma application anu ku wandalazi football club po box 1234 chichiri. Blantyre 3.ref . bus ipite vacancy.

 46. Kodi waphwanya stadium toilet ndani?.
  Bullets
  Wamenya mbama sam madula ndani?
  Bulets

  Solve the equation
  5noma : 1?
  ………………………..5marks

 47. mukagula nginga mumakayikozetsakaye musanakwele koma inu munapanga phuma akulu akulu amati mbuzi ikasangalala amalonda alipafupi mwatengelapo phuzilo musamathe mawu ife NBB tadutsa muzopinga ndiye izi zadutsa tikambe zina

 48. Nyerere zitha kukonza bus ndikumayendaso bho bho kma nanga ife a BB tingakwanitse kukonza history yachitika ija poti amati what is done is done..tiyang’ane chigotsolo basi..

 49. Ignorance at its best. So to the admin, You mean you are so very happy to see Bullets supporters laughing at their rivals because the Coaster developed a Mechanical fault?

  But who is at fault here, Players, supporters or technical or the Bus itself?

  This simply means that the admin wanted the Bus to go to the other side but sorry.

 50. Noma was not desperate kuti imafuna bus imangofuna kukuziwisa neba kuti zonse zoyambilira zimakhala zake , tikanatha kungoyiwina bus imeneyo ndi kukayipanga donet to the hospital

  • maganizo aboza amenewo usazilimbitse mtima apa chikupwetekabe mesa mumavina kutokota heavy kut mwapata bus nde mauwo akuchokeraso kut zakuvutani basi

  • Mwatikwana a bullets saname inu mungolimbikira bwanji khani yopanda pake aaaa tatengabe 5 kwa iyayi anyamata anu an go bwera ndi ukweche betta ife tabwera ndi phokonyore hiyaaaaaa

  • Kumeneko kuzilimbitsa mtima a Norma? Kuyambira mu 2015/16 takumenyani kangati ?? Nanga mutiona tikuwelengetsera zigoli? Tiyeni tipange masamu tione kuti amene achinyidwa zigoli zochuluka ndindani? Chopatsidwa samakabwezayi, mwavina vina kuti mwapata bus lero mukuti bus mulibe nayo ntchito koma zigoli shameeeee ma neba.

  • kkkkkkkk on top of dat chawonongeka ndi Gear box yokha baasi! mtengowake ndi 50,000 so lets make the ratio pazigoli zija zinali 5,mtengoso wa busyi ndi ya 25 mit. so titha kuwona kuti 5 alingati Common #kkkkkkkk.

  • Timvane bwino lomwe ndithu
   inu ndi ife tonse ndife amphawi tokha tokha. Tilibe bus tonse apa. Tikahara ndi game bus timachita kubwereka. Ena ataona umphawi wathu anatinapatsa mwayi oti tilimbirane Bus imeneyi kuti tichepetse vuto la mayendedwe. Tisanamepo apa tonse Bus yi timayifuna poganizira za mavuto omwe timakumana nawo ikafika nthawi ya mayendedwe. Titayesana woperewera mphamvu zamuvuta ndipo wamphamvu watenga Bus. Mmene mpira umamenyedwa palibe amene amadziwa za mavuto a Bus. Lero Noma yatenga bus mukuti ndi chiphapha. kaya ndi chiphapha,kaya phokonyore koma chodziwika ndichakuti “noma lero ili ndi Bus,kusiyana ndi padzana paja tinalibe ngakhare phokonyore olo mmodzi, timachita kulipira ndalama kukabwereka phokonyore wa ena.
   Inuyo wanu ali kuti phokonyoreyo??

 51. Ine ndine sapota wa NBB. Koma ngakhale tiwaseke anzathuwa kuti bus yawo ndiwonongeka, sizingapindule komwe. Tiganizire za tsogolo la timu yathu ya NBB kuti lili bwanji, osakalimbana ndi za anzathu. Kugonjetsedwa kawiri, simasewera ayi. Nkulephera kwa timu kumeneko. Bwanji osangovomereza kugonja kwathu ko? Sizingamatithandize izi zomangolimbana ndi anzathu, koma kulimbikira basi. Taganizani zigoli zonse zija, ndiye kuti team yili bwino pamenepo, moreover team yayikulu ngati imeneyi?

  • Kkkkkkkkkkk, mpaka kudyedwa juga? Imene ija si bus koma coasta. Abwere kuno ku SA, adzawone bus zimene amakwera anzawo ma players. Penapake ku Malawi kuli vuto. Si bus yomanena kuti akhazikitsa mpikitsano wa bus, kumatchula minibus. Shame!!

  • Kumbu, umafuna kuti ndinene chani? Nanga iweyo wa nzeru zambiri, ukuwona bwanji? Ndiye vuto lanu limenelo, chifukwa simufuna chilungamo.

  • amwene nkhani ndi ya bus..ngati mumayitsata Bullets mu 2016 inatenga Presidencial cup komanso inakhala pa nambala 2 mu super ligi kusonyeza kuti timu yathu siyolephera..apapa apa bus ikakhidwa bwanji kuchokera ku Ntcheu mpaka Bangwe BTs????

  • Munya simunati muli labe zose tu ndi chande bora iwo abwera ndichokakha nanga inu mwabwerako ndichani kungobwera ndi ukweche basi ha ha ha ha zikuonekera ife anthu akudyerera ku off season anu apita ndi khawa 5 lero date mwezi wa 1 chaka cha 2017 mwina mungaiware

 52. Costar imeneyo ndidaiona kubangwe akuikonza siya new wani ayi koma kungoti neba phuma sungadabwe mumbili udavapo kuti BB yaluza motero???? Kodi Driver ndi Chande chifukwa nde adatengekatu kkkkkkk

 53. its part ov the game, ngat pirates inaluza 6 _1 ndi supersport utd , man u kuluza 4nil ndi chease, nde kuli bwanji bullet’s zazii ,chaonongekabe tafanana ndebola mukanangowauza kut akupatsen ndalama , kabwezeni ndithu bus yo pasanafike pa 30January kkkkkkkk

 54. we dont care about the condition of the bus. but the most funny thing one may wonder is that how did u manege to concede dozens of goals? shame on u.

 55. Galimoto Ikagulidwa Kumene Imapangidwa Service Ndye Zangotengera Kt Admin Wa Pageyi Ali Mgulu Lokhumudwitsidwa Nd Kuwina Kwa Noma.Ndye Udziwe Kt Bola Ife Tapeza Chopititsa Pa Garage Kusiyana Ndiwe