Gaba first Malawian footballer to have clothing line

Malawi international striker Gabadinho Mhango has ventured into fashion as he now has his own clothing brand.

Gaba : Confirmed of the news.

Mhango, whose brand’s products are bearing the label “Gaba”, is the first Malawian football player to run a clothing brand.

In an interview during the program ‘Made on Monday’ on Radio 2, Mhango disclosed that cups and T-shirts with the label Gaba are on the market.

“We are having plans to introduce more designs, not only cups and T-shirts, more products are coming and currently we are making. The products are found at Kaunjika shop in Pacific Mall and Devorarge shop in Blantyre,” he said.

Mhango who comes from Rumphi and is now in South Africa where he plays for Bidvest Wits in the Premier Soccer League (PSL) further said plans are underway to send some products to the northern region since people in the region are proud of him and his achievements.

The Bidvest Wits striker also disclosed that he is planning to launch a website.

Other African players who have own brands include former Chelsea striker Didier Drogba, Cameroon’s Samuel Eto’o, South African footballer Teko Modise and Ghanaian Asamoah Gyan.

Advertisement

171 Comments

 1. Kusaimikira wina akachita chabwino pa chifirika ndiye chikhalidwe chathu akadafe sitidzatheka yemwe wa Mlungu wamudalitsa palibenso angatembelele Gaba amatiimilira kuti Ku Malawinso madolo odziwa mpira alipo.

 2. Most billionaires in the world dropped our from school and they employ anthu opita ku sukulu omweo kuti adziwagwirira ntchito. Palibe chachilendo apa. Mmalo mukupanga support nzanu mpanene mukumupezera zifukwa. Ameneyo nde m Malawi ndimudziwa ine. Like pulling others down…. come on guys get a life

 3. Malawi24 penapake tamabweretsani nkhani zabwino zoti tkawerenga tiphunzrapo kenakake,nanga nkhani ya Gabah ipindulanji pamiyoyo yathu ? bolanso mukadati a #Escom alengeza kut kuyambra lero pa 4 magetsi sadzathimanso.

 4. That’s why anthu ambiri akusaukirabe ku Malawi kamba koti amaona ngati sukulu ndiye kuti kulowa mkalasi kokha, anthu ambiri pano akusangalala ndipo amachita kuoneka kuti zawo zinayera koma sanapite ku sukulu, Gaba zake zinayera ndipo kwa iye anachivomeleza kuti za sukulu zakanika koma apeze chinthu China chake chomwe chizipangitsa moyo wake kukhala osangalala

 5. Business imeneyi siiyenda yes gaba got money anakayesa business ina I saw tht from Tay grin ndi label yake de likes of Martse too getto too cutter.amalawi ndiokonda zinthu zabwino koma umphawi ndiomwe umatipangisa osamagula kumangosilira basi

 6. Even christiano ronaldo siwophunzila, that’s why chuma chake akuyendetsa brother wake, koma he’s the richest footballer. The guy was expelled from school at the age of 13

 7. Check his earnings poor malawians enanu mwakakamira ti nchito ta hundred thousand.Bussiness pple makes that a day whle u stay a whole month on a desk think big

 8. The reason Malawi is not developing is because we all think school is the only way to success. People have talent in different areas and the world has changed now. This is why Malawi is not changing as much because we r so stupid to just dwell on school and we can’t open our eyes. We r a pathetic nation

 9. Mfana umakwana, umatiimira ife amalawi okhala kuno ku south africa, zoonadi school simathero and ma proffessor enawa chuma chawo ndi ndevu

 10. Yanjilu nkhuku simaswa mazira! Enanu mukhalira yomweyo yongonyozayo kwinaku mukutuwa. Ine ndiye ndili pambuyo pa mwana ameneyu Gaba ndipo chilichose chokhudza iyeyu ndigula basi. Ambuye amudalitse!!

 11. Soka onyozayo maphunziro mkachani ena amaphunzila kuti azakaone lilongwe kapena blantyre koma apa nzathu watola chikwama chifukwa cha miyendo amaponya mpila wa MAPAZI kkkkkkkkkk apa bola Mulungu apitirize kudalitsa anthu akumalawi osati boma ayi ndalama zaboma zimangobedwa chonde ambuye!!!!!!

 12. kulimbikira xul ndkophweka kusiyana ndimpira cz chinacho ndiluxo lamun2 jst like a gift from God pamene xul timayamba tili ana ndetimazolowera thats y we say xul z a key n t helps n all sorts of activities.Gaba mukunenayo amaexera english kuxul anapitako n chabe sanafike nayo pamene inuyo munakanda kut afike.so dnt compare xul ndiluso lamun2.the probability of hving more educated ppo n a country z more than that of hving e talented onez

 13. tlipo ambli tinapta ku xool bt we r jst stayng n tliposo ambli amene ctinaphuzle tli pa bwno, we hav some amene dey evn dont knw God bt dey r enjoyng dis lyf pamene amene amamudzwa mulungu ndpo ndiwokhuluplika bt akuzuzka moyo uno,bt chopambana chenicheni pazosezi ndmulunguyo coz umakhala ndchyembekezo.

 14. Sukulu simathelo Gabadinho Mhango is a senior player for Bidvest Vits and check how senior players earn their wages some of you degree holders even you combine what ever you get including pension you will never reach that point of Gaba

 15. Osamafananisa xul ndi zachamba zomwe….anthu amakalembesa maina pa malaya ku malawi konkuno imakhala nkhani yaikulu? Ndiangat angakane atauxidwa kut apasidwa malo ku malawi university of science n technology mukamakamba kt xul z jxt nothn..ur overgeneralisin

  1. Only fools could think school is not important. That my teacher does not have a bicycle and I have many cars doesn’t mean school is not helping him. School ndi deal. U have asked a good question who can say no if chance be given that he goes for masters degree?mpaka kuyilinganiza ndi mpira?

  2. Bodza inu gaba atafuna atha kumagula ma quantum mini bus mwezi uli wonse amakhala man of the match three tyms in a row ndalama basi iwe upite kusukulu zaka four uzalandile pa mwezi 100pin kkkkkkkkkkk bolaniso was garden Ku jozi

  3. Jx look at christiano ronaldo ,messi ,pogba ,Rooney do u think those PhD Ali ndi dolla yofanana nawo a peter anuwo anali kunja anangobwerako osamanga olo kanyumba Mwai ndale kupezako tindalama mpira ndi deal

 16. Kwa amene mumathamangila kukamba za satanic tiyeni timugendenso miyala ameneyu..
  Sipaja munthu akayamba kuchita bwino inu ma judgenu mumat ndi satanism?….mxiiiii shame on u En see his rising in 3years cming he wll never b the same

 17. Ndilibe ndalama zosegulira link yi ena andithandizeko akuti Gaba watani? ali ndi kampani yopanga zovala kapena wapangisa nkhope pa zovala zake? help me plz?

  1. The definition of the concept of success is very subjective. School has two values, firstly..it has instrumental value. This is the one you are talking about whereby one uses education as an instrumental to attain other things of value like jobs (money) or anything else and the second value of education is intrinsic value whereby knowledge that you learn at school is on it’s own of value. Others by just attaining that knowledge through school is success on it’s own regardless that they will get rich out of it. Most people will respect people with a PhD than a rich football player while others will respect a rich football player. It’s all subject and there’s not only perspective to look at things

  2. You think its not but it is,all because we come from a poor country so the only way we can earn a living is by working after school!!!

  1. Idear yanga ndiyoti iwe OFATSA ulindimoyo odzikonda ukudziona ngati wafikapo chifukwa choti mwina Gaba ma t shit wapangisira ku jones komwe iwe umakudziwa mzeru palibe AMWENE Chifukwa Munthu utchuka chilichonse angapange dziko limadziwa Rooney Ronaldo Messi or kungogura Toy yamwana wawo dziko lonse limadziwa zosiya Iwe ndi Ine tilibe mbiri

  2. @friday, nkhani si imeneyo ndilibe nthawi yomupangila nsanje Gaba chifukwa zake si zanga ndipo zanga si zake, mwayi wanga si wake ndipo mwayi wake siwanga koma kwa amene angandimvetse pa zomwe ine ndalembazi mwina ndi okhawo omwe ali ozindikila kwambiri chifukwa ku south africa ngakhale iweyo ukhoza kugula ma t- shirt 30 osewo ndikupita nawo kumene amapanga print zovala kuti akaikepo m’mene iweyo umaonekera m’musimu mkulembamo dzina laka ndi zotheka komaso motchipa kwambiri ngakhale kukukhozela nickles kapena ring yolembapo dzina lako amapanga ku south africa zimenezi ngakhale ma key ngati pakhomo mulipo anthu asanu 5 ndiye mukufuna kuti aliyense akhale ndi key wake mumatha kukapangitsa. Koma nanga sikwathu kuno zikufika kumene mchifukwa chake zikukhala ngati zinthu zotsogola kwambiri

  3. Tapitauko iwe kudzindikira kwake kuti? Ukuona ngati kumalawi sagulira key padera c Iwe ndiopanda mbiri or utapanga print ma t shit ako 1000 pic yake ndikuyika pafb palibe angapange like ndipo

  4. munthuyutu sananyoze wangonena kuti kupangitsa print zovala nkochipa en ndugwirizana naye coz alipo nzanga wina wake ntchito yake ndimeneyo sikut nzinthu zot zingaononge ndalama zambiri ku S.A. kuno

  5. @ Boy- jay, pa malawi pachuluka makape mchifukwa chake amangoombera mmanja zili zonse ineyo sindiye kuti ndili ndi chifukwa ndi Gaba ayi more over amene uja ndi friend wanga pa fb kotelo kuti akakhala ndi game ndimamutumizila mafuno abwino komaso chilimbikitso, kuti apitilize kuchita bwino. Koma anthu enanu muli ndivuto chifukwa simuli kundibvetsa. Kupanga print chovala ku south africa sichinthu chakuti munthu ungaime nacho pachulu mkumati ndiwe katakwe ayi chifukwa zimatenga tindalama tochepa ndiye ine ndikuti kwa munthu amene akufuna kuti apangitse ndizotheka kutero kaya angofuna nkhope yake yokha, kaya dzina lake lokha amapanga zimenezo ndiye ena sandikundivetsa ali ndivuto kwambiri akuona ngati kuti ineyo ndikulimbana naye Gaba chifukwa chakui anachokera ku Bullets ayi nkhani simeneyo

  6. kkkkkk inenso ndikudabwa nawotu coz akulimbikira kutsutsa asanamvetse point yako. ngat anabwerako of coz zoona koma sanayambe apitako komwe amapanga print-ko even mtengo sakuudziwa. kubwera kuno sikut ukudziwa chilichonseyi coz dzikoli lili nzochitika zambiri en sungadzithe kuzidziwa zonse

 18. Mwanayu alindi umuthu komanso ndiodzichepetsa ndiye paja odzichepetsa mulungu amamukwedza tipemphe mulungu kuti Luso laGABA lipitepatari

  1. iwe ku nyini kwa mako wava mpila umautsata iweyo gaba mesa anamutengela ali ku bullets ku pita ku certick kenako ndipamene pano ali ku vets nde iwe apa ukut anachokela kut ku nyini kwa mako kapena ? ngati sumukudziwa ndi bwino kumango yang ana kapena ndi bwino udzikango yamwa nyini ya makoyo wava zandinyasa zoko zonyoza bullets zo fack u ,and u pusy

  2. iwe arex mboli yabamboako yokula mutuwo,,,mbuli yamunthu uyu stupid kungosatila mpila osaziwa,,,ngat sanchez anachoka ku Barcelona kupita ku england ku arsenal sikut Barcelona inganene kut player uyu ndiwathu…coz anagulisa chimodzimodzi inu nyini za bullets munagulisa nde musamabwelepano ndi 5-1 yodula machendeyo yomwe yafinya nyini zamanu nkumat gaba player wa bullets….zachamba bas,,,uwauzenso amako ndi nyini yao yonyenyekayo nditha kudula nyembayo,,,stupid sinafune zotukwana koma iweyo wandiyambisa,,,panali fundo yot umutukwanile mzakoapa? stupid kankhope konyenyekako arex danken

 19. Chuma simaphunziro koma mwayi ndi nzeru zamunthu akapeza ndalama tikukamba pano ena akugwira ntchito zapamwamba koma chinthu choti angachiloze kuti ndapangapo ichi palibe

 20. Man musanenne za school when the Almighty want to bless someone he does not look at things like that.people just ned to work hard and believe in God that they can do it.

  1. Ndipo uku ndiye kupusa! Why waisting time talking za munthu wins yet you have your own problems which you are failing to overcome them? Opita Ku school nu you are beggers!

 21. look school simathelo… tikuzuzika ndi mbava kuno zungotibera makobiri m’bomamu koma akuti ndi anthu ophunzira… bwanji osatenga chitsazo chakatakwe wachikopayu

 22. Mulungu simunthudi…..munthu ananyozeka uyu atalephera JC…people mocked hm as if tsogolo ndi xu yokha….i thnk its high time malawians have to change mindsets…..congrats for your succes and may God continue blessing ths young guy oyipa achite manyazi.

  1. Kkkkkkkkk, guys ndi zomvetsa chisoni ndithu. Enanu mudaphunzira bwinobwino, koma chuma mulibe. Chuma si school ayi. Ndi mwayi wake Gaba. Ena timawawona kuti anaphunzira bwino, koma akabwera ku joni, amakagwira ntchito zosiyana siyana munyumba za azungu e.g garden boy. Komano munthu wophunzira bwino. Mwayi wa wina, ndi tsoka la wina. Tiphunzirepo ichi.

Comments are closed.