Atatu atuluka super league, imodzi m’chigawo chilichonse
Matimu atatu omwe amasewera mu Tnm super league atuluka mu mpikisanowo omwe ndi waukulu m'dziko muno. Izi zatsimikizika kumathero a sabata latha. Malawi24 itha kutsikimiza kuti matimu atatu, imodzi imodzi kuchokera muzigawo zikulu zikulu zamdziko… ...