Chande’s poison : Lungu, Rahim Ishmael fired at Bullets

Advertisement
Rahimm Ishmael

Their humiliating 3-nil loss to rivals Be Forward Wanderers was just too much to bear for Nyasa Big Bullets as they have fired assistant coach Mabvuto Lungu and team manager Rahim Ishmael, Malawi24 can reveal.

Rahimm Ishmael
Ishmael : Fired!

The duo have been replaced by Eliya Kananji and James Chilapondwa respectively.

According to media reports, the decision to have the duo fired follows a string of unconvincing perfomances, which has seen the team struggling to defend their Super League title.

The peoples team failed to reach far in the Carlsberg Cup as well as the inaugural FISD Challenge Cup and as it is, they are on the verge of losing Luso Television Bus Ipite Football Fiesta to rivals Wanderers following Monday’s demolition.

The defending league champions are still clinging to hope for TNM Super League championship with just a game to go as they lie second on the log with 57 points, a point below leaders Kamuzu Barracks.

Advertisement

125 Comments

 1. Atanena kut chfukwa cha Karonga untd mpomvka;
  Noma inabala manyasa bullets, ndpo tayamwtsa tokha. #askausman.com ndponso zikho zkulzkulu oyamba ndfe a noma kutenga. Y don’t they beliv, kapena2 ndi #usi…

 2. kkkkkkkkkkkkkk iiiiiiiiiiiiiiii inemonsemu umu kukoma kokhakokha maule tazandithandizeni ine kkkkkkkkkkkkkkkk langizo kwa dimitri,nyengo yafodya ndi ino tengani yamikani fodya wakunazare bola fisher asakazule asanakhwime sankhani akhale kapitawo.chiukepo azikaokera,sulumba pachithekitale,kkkkkkkkkkkk itipuleni timu yonse estate basi iya sizampira

 3. umenewu timati ndi uchitsiru!!,kupanda zeru! coach wakuthandizani tym yoseyi mpaka kufika pa no 2,pano mukumchotsa?.kuchotsa coach sikuthana ndi mavuto,koma kuonjezera mavuto.ndiye lolemba mukaluzaso muchotsa ndani? nanga mukaluza ndi blue eegles ena satsika maudindo?

 4. Bullets is a confused camp now. I do not know what will happen if they lose Saturday’s game to Blue Eagles. Are they going to fire the entire coaching panel? Neighbour mutu sukugwila!

 5. Zichotsanani anthu olephera ndi choncho mitu simagwira. Second leg mukuluzanso , so may be from there team izachitidwe dissolve and pamenepo mpomwe sido harzad mjathu azasinthe team kkkk

 6. Vuto si coach kapena team manager koma munalephera kugula referee kuti mupezeko ma penault awiri zikakuyenderani. Ndiri ndi nkawa kuti ku Lilongwe Referee sagulidwa ndi akanganya amewa mm…. KAYA tiona pa 2 monday. Ma NOMA chonde mpofunika kusamalitsa chifukwa ku LL mukukasewera ndi oyimbira + NYASA

 7. Kkkkkkk koma BB yapenga ndithu! Ndiye funso langa ndi loti,kod nanga BB mukakaluzanso Ku LL , muzawachotsatso omwe mutawasankhe panowo? Why osangovomeleza kulephela kwanu? Mukazichepetsa mulungu alowelelapo. Simungakhale always kumawina game ili yonse.

 8. That’s the worst decision ,the guys are good and they produce results ,sucking them coz of losing one game is a mistake,even world best coaches also lose games,why not NBB?rethink your decision

 9. Team ili pa number 2 mu leaque ndipo ili ndi mwayi wotetezanso ligi ndiye mukuti sikusewera bwino? Phuma bwanji? Mumafuna muzingotimenya tisamakubwezereni. Kuluza game imozi mpaka kuchosa ma coach kkkkkkkkkkkk

 10. Wa yamba neba mwateromo mwazi patsa minyama monga kananji asamare apapa zingavute bwanji azukuluza zithumwa nkhani ya bus bus murinayo kutali maule mkumanzulo nde 3 mukunama mazi achinta katondo basi ku maule ngat muzawine bus 0993 178 718. Muzayimbe no, imeneyno.

 11. Ine monga mpalestina weniweni,ndimalangika kwambiri ndikaluza ndi ana ayaya kusiyana ndi timu iliyonse muno mmalawi,pempho kwamakochi:pangani chilichonse chotheka kuti tisamaze ndi noma

 12. Kodi munakhazikisa kuti BB isamaluze? Kungot yaluza basis firing the coach .learn to accept the defeat osati kunalembrdwa kut muzingowina ayi ,mpira ndimmene kwachela

 13. Plz ntchito yatha koma ndikupempheni mwachosedwa ntchito inu kuti paja kwathuko tili ndichizolowezi chofuna kuthana ndi amene wakuchosesani ntchito osada nkhawa musiyeni ndizomwe anamuuza coach kuti akatenga mpira uzipita komwe kuli golo boyi wa team inayo kukamwesa chigoli kkkkkkkkkk

 14. I knew Rahim would be fired i was once dissappointed with him when Big Bullets was playing with Karonga United at Kamuzu Stadium oooh! It was a mess.

 15. Ishmael Rahim is a good Maneger, I should say that the whole technical pennel is good, but we have a big problem with our players, especially our defenders and strikers are now becoming poor, we only have good wingers now, you can even imagine the opportunities our strikers had the game we played with Civo, out of 6 chances we had we olny used one opportunity through Chiukepo but the rest went in vain, we could have won almost 3:0 that game, and even our soccer wasn’t as good as we usually play. Players are the ones to blame not the technical panel, firing coaches won’t solve the problems, you should ask players what exctly is really happening with them because that 3:0 was really too much to the team like NBB!

 16. My team NBB has good defenders and midfielders but is lacking excellent strikers osati zomwe mwapangazo. To say the fact, potengera ndi mmene mpira ukuyendera pano, Chiukepo and Sulumba are not good strikers. Always NBB fan

 17. If it’s true then this is not the end but rather the beginning of the end of Noma Team B, and the end is coming on Monday. Kkkkkkki amayenda m’mbali.

 18. Mmm bt how izt posible to fire 2nd coach & team manager ndikusiya first coach… It dosnt make sense at all coz wat i know the first coach is responsible for team perfomance & he z the manager… it seem like ftball politics is involved @ first it was Tewesa & now the two.. With this kind of behaviour sitingatukule mpira ku Makawi kuno… Viva Maule

  1. Despite kuluza panalinso mavuto anga omwe this two guys brought. Appearing fee amati omwe alandire ndi okhawo onwe anayamba game komanso amati amawaudza player kuti achotsedwa akamandelera

 19. u made a very good mistake by firing those guys let’s accept team is not in gud shape let’s find the way forward#thepipozteamfan

 20. Pamene A Manoma Akukondwa, Posamba Mkaka Ndikumwa Ndalama,mapalestina Mpamene Akudandaula Ndi Mabala Mzinda Wa Gaza!

  Ndipo Dzina La CHANDE Likatchulidwa Ku Camp Kwawo, Limatha Kuthetsa Ntchito Anthu Ambiri.Chitsanzo, Werengani Post Above, U Will Confirm Ma Words!

  Koma Ulendo Uno, Boko Halaam, Amos Bello Wanenetsa Kut AKACHITA KUMULETSA KUGOLETSA ANZAKE AMANOMA…Ndi Time Ya Manoma Kuthetsa Kuweweta Ku Bullets. Ndipo VALENS KAMZERE Wakonzeka Kukatseka Golo La Manoma.Mziona,

 21. Firing coaches , team managers and the like won’t be an answer to team’s shameful loss. Actually you are just making things to get worse than before. ok should you lose on monday , are going to fire the newly appointed coach? hahaaa! #kuli_Nyerere_ku_LaliLubani!

 22. kkkk kutimvetsa kukoma kwambiri nyerere.mpira umaenda motero tonse sitingapambane tsiku limodzi. kumavomereza kuluza inu afodya.ngati karonga imakupamanthani 3 goals tsono kuli bwanji manoma?zigoli zinai zija tinangomvelani chisoni tinkafuna 10 goals.koma ndiyetu mukhalira kuchotsa anthu pa maudindo coz noma idzingokuthyolani mapiko kkkk

 23. Kugwila tchito ku NBB usanyadile kuti wapeza tchito…Kelvin Moyoakuziwa bwino. Ine ndingopepesa ku banja Lofedwa kuti pepani. kuluza #3_Kwa_chilowele chisakhale chifukwa chozichosela moyo. Tikufuna chaka chamawa tizayendenso limozi

 24. Vuto losavomereza Noma inavomereza mavuto awo imakakhoza koma ife timafuna kulikana nokha simugawone kt tikawina inakhara 1 : 0 nde azathu aNoma amawina ma 8 bcz adakhoza mavuto awo bwino bwino

 25. that is nonsese coz mwatelomo mwawonjela mavuto ena,ndikukhulupilira kuti,mujapita ku civo stadium teamyi ikathelatu.

  NOMADS MORE FIREEE BUU!!!

 26. that is nonsese coz mwatelomo mwawonjela mavuto ena,ndikukhulupilira kuti,mujapita ku civo stadium teamyi ikathelatu.

  NOMADS MORE FIREEE BUU!!!

 27. Vuto Lomaganiza Zoti Sitingaluze. If Karonga Inakwanitsa Kulowetsa Zigoli Zitatu Mu Ukonde Wa Bb Chingavute Wanderers Ndi Chani? Ndiponso Zitatu Is Not A True Reflection, Zimafunika 6. Taikonzani Team Pano Silibwino. Rahim, Lungu Ndi Sanudi Sindikuona Chimene Alakwa.

Comments are closed.