A Malawi apemphedwa kukhala anthu olola ndi omasuka pa nkhani za njuga. Malinga ndi wamkulu wa mu unduna wa zamalonda, a Elsie Tembo, a Malawi sakuyenela kuona njuga ngati chinthu choipa.
A Tembo ananena izi mu mzinda wa Lilongwe pamene amatsegulila malo ochitilapo njuga otchedwa Marina Casino.
“Anthu akuyenela kumvetsa kuti njuga si chinthu choipa, chinthu chilichonse chili ndi ubwino ndi kuipa kwake. Nayo njuga ili motelo,” anatelo a Tembo.
Iwo anaonjezelanso kunenapo kuti anthu akamasewela njuga akuyenela kukhala omvetsetsa ndi oleza mtima.
“Anthu azidziwa kuti awa ndi masewela, utha kupambana kapena kugonja.”
Sponsored
204 thoughts on “Boma lipempha a Malawi kuti ayambe kukonda njuga”
Comments are closed.

chenjerani anthu inu.sizonyadila izi zitchito zasatana ndizimene akuyendetsa anthuwa
Nditchimo njuga.boma lathu likupita kuti abale.owerenga akhale maso.amen.
Zaulendo uno by mwanache
Zautsilu
Dirty funny
Nde lolaninso chamba kuti chizipezeka paliponsetu kkkkk
Nonse amene mumakambirana nkhani yimeneyo ndinu mbanzi zawanthu mwava komanso nonse m’bomamo ndinu agalu awatho
Chamba koma kuba
ndezachamba suja mumaletsa viganda, mwayamba kulolezanjuga ndechambaso tiyambe kulimba
Kkkkkk Malawi waonongeka
Mbuli za anthudi zimenezieti? Kukalimbikisa khalidwe lachabe koma abale dziko lathu likunka kt makamaka! Last week amakambilana at nkhani zololeza abortion koma zooona? Lelo akubwelesaso ina akt boma lanyong’ola kt amalawi aziyenda juga, our country is damage by stupid leaders
malawi wakeyo.soon timva zoti alola anthu kuti aziba momwe angafunire
Mhhhh!!! Kukadakhala kuti kuli mwayi, osinthanitsa kutenga Wa moyo munthu nkukamuika kumanda nkukatenga wakufa kuti akhale ndimoyo chinali bola kukasiya Pitarayu nkukatenga Bigu chifukwa bolani ada ajawo ankakana za chifinezi ,osati INJA uyu/ ( Galu uyu )
Kkkkkkkkk ndinali ndisansione nkhaniyi Mwati Boma kupempha Amalawi kuti ayambe kukonda njuga? kkkkkk Mukamamva kuti uchitsilu wa Anthu akulu akulu ndiumeneu basi kufatsa nkufatsa amvekele Amalawi azikonda njuga asaaaaaaa!!! mukauze akwanu zopusazo mwamva kuganiza uku nde bolanso Mwana anganize zanzerutu Mbuzi za wathu
Komanso muloleze kut munthu akaba asamangidwe boma la alomweeee zaziiii
Pansana pake galu ameneo
Kkkk what is happening to my home country? Tell us what is wrong to reach that extent