Lucius Banda attacks abortion bill, homosexuality in new song

Advertisement
Lucius Banda

Musician and lawmaker Lucius Banda has released a song that is condemning abortion and same sex marriages in the country.

In the song, Banda faults Malawi government for attempting to adopt western culture that will likely devalue Malawian culture.

Banda in the song claims that if the country wants to adopt such immoral acts because of poverty then that is against God’s wishes since Malawi is a God fearing nation.

Lucius Banda
Lucius Banda: Talsk tough on trending abortion and homosexuality bills.

The Balaka Parliamentarian adds that God did not create James for Adam in Eden since God knew that Eve deserved him because they were of opposite sex.

On Tuesday, Malawians held demonstrations led by Episcopal Conference of Malawi and Evangelical Association of Malawi to show strong rejection of the proposed abortion bill and to oppose the legalisation homosexuality in the country.

The demonstrations brought together all Malawians disregarding their religious backgrounds.

Advertisement

187 Comments

  1. Always Lucius samawopa munthu or Boma enanu ndi a DPP mumadana Nate komachoti muziwe Lucius never discouraged with people or gvt of to day ndipo chomwe wafuna chimatheka enanu
    mumalimbana ndi Lucius zake zimayenda ndipo mukhoza kukhala mmodzi wa antchito ake,wins aliyese anamunyozapo Lucius amachita retreat chofukwa at the end womunyozawo amazachita manyazi ndipo amazayamba kumusilira . Amalawi tiziyamika kukhala ndi anthu ngati Lucius…. Bigup !! Sir Banda ndimakunyadilani continue to teach Malawian . Ndizasuporter Lucius all the way!!!!!

  2. People tend to forget that we live die once, then live (after which our own deeds now will determine the after fate)

  3. what i have seen here is 90% of people ur against Gods power by bringing the same sex marriage but one word for you the Lord is watching you one day u go cry for ur stupid

  4. Ndizoona enafe ndiwokuba, enafe timatamba, enafe ndiwokupha enafe timachita zinthu zambiri zomuchimwira Mulungu. Koma balibe gulu la mbava lomwe linabwera poyela mkunena kuti akufuna ufulu wawo woti akamaba asamathamangitsidwe. Inu tchimo lanuli lapambana chotani kuti mpaka pakhale lamulo? Osamangochita bwanj uchitsiru wanuwo?

  5. Pa nzeru zake komaso pa maganizo ake waimbabe nyimbo basi! Enanu mmafuna apange ma demo inu osapanga bwanji? Demo amapanga munthu mmodzi? Akayambitsa inu mumuthawe atsale nazo yekha basi! Za ziii!

  6. Let him sing and speak out about what he sees,,, no matter some of us we don’t like him. But in other areas this guy doesn’t fear anything and he has done a lot

  7. Muthu wina aliyese amene amadana nacho chilunqamo ali ndi tchinga,koma iye mwini samaona,pamene dziko likupita kumapeto satana watilanda nzelu za chibadwidwe,pitiliza kuwuza mtundu wa amalawi mwina anqadziwe choonadi.

  8. Am ANTI-abortion bill… why bring an innocent child into the world if u r too poor to take care of it or if u r nt gonna love it and take care or it?
    Unless the government is gonna take/adopt the babies that were to be aborted and take care of them… but like we knw… the government can’t even feed/provide for the people right now…
    and also, women should be given the right to choose what should be done on their bodies…
    babies change everything…
    if u knw u dnt wnt the baby, or cnt take care of it, abort it…. period…

    1. Abort it? Really? If u knew that ur poor n u can’t manage to take care the child why can’t prevent kutenga mimba than killing

  9. I dnt see why people should be against same sex marriage… if someone is gay, how does that negatively affect ur life? Let them be. Let them love…. it’s really none of ur business if someone loves and sleeps with the same-sex like seriously… Malawians should stop wasting their time on useless issues… focus on combating poverty instead or something like that…

    1. Remember Whatever happens around you brings either positive or negative effects.with your mind can u advise someone to do rightious things,bcoz in everythn happens u wil be sayin;non of ur bznes.ur there to guide and teach hahaha!

    2. Firstly, what makes u think it’s a malpractice? It is coz the society or religion says so? Secondly, either way, that’s; legalizing homosexual marriage or not will nt affect issues like poverty in anyway… so it’s kinda useless to focus our energy on such …

    3. @reginald, not everyone is religious… we all don’t believe in God so the concept of righteousness does not apply to all. Seriously people If it doesn’t directly affect u either positively or negatively, u shouldn’t focus on it… that’s wat wrong with the Malawian society, we tend to magnify futile issues and ignore issues that matter the most… that’s y we r stagnant development-wise

  10. He speaks without fear ask late bingu on section 65 bill antil they arrested him he compose songs as a memories so that people should not forget solider wa amphawi komaso amalankhula mu parliament ameneyo let us enjoy the composition

  11. Munthu akamapanga za homesexuality amakhala kut akumulakwila ndani?…kapena akuphwanya ufulu wa ndani…?lets not jst generalise thingz,akamati abortion sikuti anthu azingotaya mimba chisawawa zimayendela ndi ma conditions ake,abortion ikuchitika/imachitika,alipo yemwe saziwa kapena?dis is in ada wayz kuthandiza kut atsikana azi user njira za bwino zochosela mimba ena amafa,ena amakhala osabeleka.

  12. Tikumudziwa kut boma livomeleza zimenezi koma plz Pakhale chitetezo chokwanira kwa anthu amene azipanga zopusazi……… Chifuwa nde kukhala kuzipha zitsiru zimenezi ……… Tizipha ngat agalu achiwewe…..ife takhonzeka kugwira ntchito yotamandikayi. Tikungodikira kut ayambe utsiruwo chifukwa Mulungu siopusa polenga munthu wa mkazi ndi wamwamuna. Ngat mumaopa kuchimwa ……… Sodomu and Gomola chinachitika ndichani? And zinachitika chifukwa chiyani?? Welcome to death to those who prepare Homosexual

  13. To #Mordicaih. We are not saying nzeru alibe. NO! What we are saying is he is a low maker. He can stand in parliament and say something that can change things. Not by composing a song out of parliament. Zinali zomveka kale lija asanalowe mu parliament tinkaona ngati ndiolimba mtima akhonzadi kusintha zinthu koma ai

    1. You need to know that message in a song will last for a longtime than just a day deliberation and its good that this big man like Banda is open about his position on this Matter.

    2. Nop! We don’t need to talk about this for a long time. Once speak, once change. That is parliament. Bwanji nkhani za ma salaries awo samadziimba. Amalawi nde amatcha kamodzi dzikoso lamva

  14. Guys NDITHANDIZENI,ndiinagwetsa foniyi.Moti yaphwanyikiratu screen…sikuonekanso bho bho.Panopa ndi pa facebook or pa whatsapp.?

  15. Aaa wofoira uyu Lucius alibeso nthawi yopanga ndale za mu nyimbo pano. Ali Mu parliament wakanika kutsutsa pano adziimba nyimbo chifukwa anthu adziyankhulira okha popanga ma Demo. Why didn’t he sing a song before demo? zikakanika azizipopa kuti ndiiyeyo? shupit

  16. Limenero ndie dziko komaso mukuyenera amalawi azanga kudziwa ndale, akuphimbani maso kuti muzikamba nkhani zimenezii ndicholinga choti musakambe mavuto aNjala omwe agwa dziko muno changamukani amalawiii jacapuu

  17. Lucius Banda ndi munthu amene amawona mavuto omwe amalawi akukumana nawo. Sanayambe lero kapena dzuro kuyimba nyimbo zodzudzula boma mukati muwonetsetse nyimbo zake zakale monga muchimbale chake choyamba anamunapo Dr K Banda muzimbale zambiri wa khala kunena za mavuto omwe ali dziko lanthu lino ndiye mukati alibe nzeru kapena mfundo ndi bodza kungoti nyimbo zake simumvela..

    1. kkkkkkkk koma!!!!! nthawi ya Bingu ija munalikuti wawa?

  18. Mayi mayi mayi ndamva kurira kurira anan kurira ana kurira umuyo wa muthu umayambira pomwe mayi wayima ungatheso kuchura dzina lamwana amene atazabadwe moyo wa muthu urinapo pake poyambira ukampha poyambira osazinamize ndithu mwampha muthu osaganidza kuchosa pa thupi chonde Malawi takanisisa lamulo lolawula kodi mayi wanga akadachosa mimba ineyo!!!!! Kadakharapo nono nyimozi sikadayimba nyimboyi ndithokoze mayi wanga pondisunga ndi moyo, tisamayambe zithuzi lamulo loterori takana takana tosefe takana veser 2 galu wamphongo adakana kugwadira mphongo dzake mamama nanga bwanji muthu akupangiranji tilemekeze ukwati wamamuna ndi kazi tiyang’ane komwe tachoka adarenga Adam sadapase James mamanewo oooooo hhhhh kaya ndimakobiri maringa ndi umphawiwu kotonewo oomh oooooo tisamatengere zithuzi ndi kutari komwe tisamamuyambe mulungu ooo ndimitima yachikondi tigwirirane manja kukanisisa lamuro lowononga zikoli tosefe takana takana tititiiitititii titititi ndimitima yachikondi tigwirirane manja kukanisisi malamulo lowononga zikori tosef takana takana takana totsefe takana tataka tosefe takana takana

    Lucius banda new song against orbotion

  19. Nanenso Ndkudabwa Kut Akulimba Mtima Ndichiyan? Chzungu Mutu Mulibe Kapena Akungot Ndisazafe Ndsanacheze Ndi Mzungu Kkkkk!! Azingolima Mphanje Ngat Akusowa Chochta!

  20. GOD fearing country my foot, Anthu inu mumatamba usiku. Lesbians and Gays are human too. Just because you sin differently from others doesn’t make you saint. God is the one that is going to judge all of us.✌leave it all to him

    1. I’m no gay bro but it’s unfair to treat them like this. Who are we to judge? Dont you sin? Come on its 2016. Passing the bill won’t affect your lives. You will still live and do what you do.

    2. Please respond to the argument he has made and not jumping into conclusions. Buy the way, inu simunachimwepo? Ngati mumakhulupiradi mulungu, I hope u understand that sin is sin and u r not holy. So if we had to kill omwe achimwa Bwezi inu muli ndi moyo?

    3. we r not judging but rather rebuking the sin i hope we as Christians we r bind doing so rebuking the sin so that the sinful pple should turn their ways n follow Jesus we not judging but condeming the sin

    4. people of Sodom and Gomorrah were sinning differently but God punished these cities because of this particular sin mwina ndiwe homo broz.

    5. I’m no gay bro but if you really read the Bible, it says these things will happen and it’s a sign that the son of God is near. So if you are really holy, stop focusing on trying to stop the bill rather pray harder kuti mukalowe ufumu wakumwamba.

    6. Guyz be serious……… Mulungu siopusa polenga munthu wa mkazi ndi wamwamuna……… Eish ngat mumakhulupilira Mulungu and ngat mumaopa kuchimwa … Kod ku Sodom and Gomora zinachitika zotani? And zinachitika chifukwa chiyani??

    7. Hahaha kulakhula ngati wamxelu koma mmmmmh zamanyi zen xen,,,,,,,guy????????,,,,,,ndiye kut chan???????,,,,,,,,,,,,,xoputsa etii!??????,,,,,,,,,

    8. #CHIMWEMWE,Palibe kusekerera,bible likuti nkwiyo umadza kwa ana osamvera.Werengani Aroma 1 v18~32 “KUIPITSITSA KWA ANTHU[especially v26] chifukwa cha ichi Mulungu anawapereka iwo ku zilakolako zamanyazi;Pakuti angakhale akazi ao anasandutsa machitidwe ao achibadwidwe akhale machitidwe osalingana ndi chibadwidwe[ LESBIAN] v27) Ndipo chimodzimodzinso amuna anasiya machitidwe achibadwidwe cha akazi,natenthetsana ndi cholakalaka chao wina ndi mnzache,amuna okha okha anachitirana chamanyazi[HOMOSEXULLY]ndipo analandira mwa iwo okha mphoto yakuyenera kulakwa kwao(v28] Ndipo monga iwo anakana kukhala naye Mulungu m’chidziwitso chao,anawapereka Mulungu kumtima wokanika,kukachita zinthu zosayenera;[v29]Anadzala ndi zosalungama zonse,kuipa,kusilira,dumbo,odzala ndi kaduka,mbanda,ndeu,chinyengo,udani[v30]Akazitape,osinjirira,akumuda Mulungu,achipongwe,odzitama,amatukutuku,oyamba zoipa,osamvera akulu awo,[v31]Opanda nzeru,osasunga mapangano,opanda chikondi cha chibadwidwe,opanda chifundo[v32]Amene ngakhale adziwa kuweruza kwache kwa Mulungu,kuti iwo amene achita zotere ayenera IMFA,azichita iwo okha ndiponso abvomerezana ndi iwo akuzichita## mau a Mulungu sadzanama,anthu anchitidweu akuyenera imfa period.

    9. may b u dont have kids or sunakumaneko ndi ma gay zopusa amapanga zobhowa pofuna ukhale mwa modzi mwa iwo God hate sins

  21. Parliament ndi nyumba ya satana aliyense akalowa mmenemo ziwanda zimawagwilitsa ntchito moyenelera jst imagine the whole parliament MP yemwe akukambako zanzeru ndi mmodzi bax………KAMLEPO!!

  22. we busy talkin’ about abortion n same sex marriages instead of developin the country .. wtf is abortion bill, how zt gonna change our lives for the betterment… we got lots of problems :electricity,water,hunger,roads, drugs in hospitals,.. why not these things

  23. Zoti ndi soja wa amphawi amadziwa ndiiyeyo soja wanji wamantha oimba nonse mukalowa ku parliament ndi style yanu mumangoti ziiii siinu oyamba baba tilibenso ndalama yogulira nyimbo zanuzosimukutimvela cisoni anthu inu kodi

  24. Musakhale ngati business simuidziwa guys.

    Mfundo ayimba munyimbozo kuti akazinene ku parliament nyimbo yakeyo adzagulitsanso ngati ?

    Palibe asafuna Ndalama.

  25. Ku parliament amawopa he is quite and samalankhulapo kalikonse ,,even kupempha zitukuko sindinamumvepo basi ukukayimba nyimbo yomwenso iweyo ndi amene uyenela kutipatsa mayankho…..I see fear in u now

    1. nde luso limenelo.akuyitha,we speak in different ways bro,poyamba paja munamumanga coz ankatokota,nde musiyeni apange chomwe amatha.kukhala chete sikupusa koma kuganiza bho.

    2. kodi kuyankhula kupose apa? how many people listen to parliament delibarations and get views clearly in malawi and how many pple wil listen the song and get the information?tamaganizani chemwali kkkkk!!

    3. He has been singing a lot of songs but nothing happened….the place where he can talk and change things is in Parliament or doing demons like what Winiko did….well said Sister…

    4. Mmmmmm Phunzilani Kuyamikila Anzanu, Zomwezi Nsanje, Koma M’nyasaland Tsadzatheka Mpaka Yesu Adzabwela Ndithu,,,

  26. Amalawi tiyeni tipemphere kolimba, kuti Mulungu atimenyere nkhondoyi. Akuluakuluwa asagwiritse ntchito Umphawi wathu kuti atibweretsere mchitidwe oipawu. Amene akusangalasidwa ndi mchitidwewu, apite ku Western komko. Ife takana.

Comments are closed.