Nkhani ya ma kondomu achikazi ivuta: amayi akuwakana ati amaononga chisangalalo

Advertisement
female-condoms

Akatswiri pa nkhani ya uchembele wabwino adandaula  kuti ma kondomu achikazi sakugwilitsidwa ntchito pamene zikuoneka kuti anthu achizimayi akuchita chowazemba.

Izi zaululika pa msonkhano wina omwe unachitika mu boma la Mzimba.

female-condoms
Makondomu amayi akukanidwa.

Poyankhula pa msonkhano umenewu, mkulu othandizila pa nkhani ya ubeeleki wabwino a John Msiska anati makondomu achikazi sakugwiliitsidwa ntchito.

“Angotikhalilatu mu zipatala umu makondomu amenewa, mpaka akuchita fumbi,” anatelo Msiska.

Iye anapempha amayi kuti akuyenela kuyamba kugwilitsa ntchito makondomu amenewa kuti aziteteze ku matenda komanso ngati njira imodzi yolela.

Koma amayiwo atatenga bwalo kunaphulika nkhani. Mayi wina anaima ndi kunena kuti makondomu achikazi si abwino chifukwa amasokoneza ntchito ya ku chipinda.

“Makondomu amenewa si dhilu ayi, munthu ukatchena ntchito yak u chipinda ija osalongosokanso ayi,” anatelo mayi wina.

Anzake anagwilizana naye.

Mayi wina anaonjezela kuti iwo amachita manyazi kukatenga ku chipatala.

Advertisement

76 Comments

  1. the one who improvised female condoms is a fool..woman are shy during sexual intercourse they only ask men please use a condom but i’ve never heard that someone brought hers?..so don’t worry about the use just keep on promoting the male condoms..

  2. Kodi gyz ndizimene zikuchitika mdzikolathuzi simungathe kukambilanako zoti mphavu ya satanayi tingayigonjetse bwanji?ndichifukwachake panopa ngakhale anthu akunja akutilowelela zinazilizose tikumaziyamba tokha mpake akuwuzani kut kakwatilanani amunb&akazi okhaokha komaso lamulo loti azichotsa mimba kusonyeza kt tikakhala pagulu timaoneka ngati sitingachite koma m’mitimamwathu tiliwovomeleza,malingana ndim’mene ndikumvera makambidwe bwanji,amalawi,anzanga tiyeni tilimbikitsane nkhani yakulimbana ndiziwanda zimene atsogoleliathu akukatenga akapita kunjaku nangachinemwme amati dzikathu ndidziko lowopa,Mulungu kuwopakoso kulipati tisamutenge Mulungu,ngati osewelanaye dziko lotayika osamatinamiza bwanji mukakhale kunjakomweko muzikakwatilana amunanokhanokha, ziwanda mdzikolathu zachuluka nkhani zisamangokhala zachiwelewele,kod Mulungu,amtichani pankhani yachigololo tiyeni tisanyengedwe a Malawi,tiganizile Zaktsogolo,kapena ndinthawiija sodom mgomola?dziwani kuti nthawi ikubwela alise adzlandila monga mwantchizak

  3. Mzimba ndi boma limodzi lomwe azibambo ambiri ndi oyenda ku south Africa ndiye makondom avala nthawi yanji ? Poti akukhala yekha mubambo amabwera mwana atakula ndibwino apange wina and mzimai amadalira kuti ndili ndi amuna anga abwera azandinjoyesa kodi mukufuna amwalire ndi matenda ?chifukwa apoo mukulimbikitsa kuti azikhala ndi zibwezi asiyeni eni ake akuzisunga sapezana ndi Hiv

  4. Zopanda ntchito izi siti panga nawo zausatanazo ife ai muzaese le kugula sweet ndiku mabulu munya ali nkapepala mudzawone ngati mudzamu malize

  5. Ndye wina kaya kudzimva sukulu kaya kupenga aziti apange pass ku parliament abortion bill kupanga support kupha pomwe anthu azitaya mimbazo ati sakufuna kuziziteteza kuti asatenga .Musasandutse dziko lathu kukhala sodom nd gomola poti chauta akakwiya nafe kwambiri mavuto akhalanso mbwee kuposa mmene zilili pano.God save Malawi

  6. vuto limakhala malo komwe kumapezeka ma condom,kungotenga imodzi umva bwera uzasayine apa kenaka apo,mpakana anthu dziko lonse adziwe,ndibwino azingosiyidwa mmalo oti munthu azingotenga.

  7. Pomchitila Munthu Chinthu Uziyamba Wamufusa Maganizo Ake.Makondomu Amai Amawapanga Osawafunsa Eni Ovalao,cous Azimaiwa Sakuwagwilisa Ntchito.

  8. Some of the comments here, leave one wondering if some Malawians have beard or breasts just for fun. Grow up folks, be sober minded please! Aids is real, STIs are real, we need proactive minds and prompt action, not mediocrity and retrogression!

  9. amalawi penapake amalakwisadi izi zili pachiopsezo kutenga matenda opasirana pogonana mopweka khaya niye akumachiyiranji zimenezi

  10. kondom ndi yonwe timaveka #mbolo,so plz iyii ipatseni dzina lina,kaya mwina ndowa ya amayi,kapena mphika wa adona,mutatero,ayamba kuwakonda,apo biii don’t waste your time,mungoyamba kupanga ma panti !!!

    1. Kumayenda Ndi Nthawi.Atumbukawo Akwatira Abale Anu.Nanga Ana Obadwawo Ndi Amtundu Wanji?Zonyozana Mitundu Zinatha Kalekale.Ziyendani Muziwona Mmene Mitundu Yosiyanasiyana Ikukhalira Limozi.

    2. Anawo azakhala makaladi komanso poyendapo pasiye usaziwana ndiwachabe ineyo sindikuziwa kuti iweyo wayenda mayikoanji ndipo iweyo siwukuziwakuti ineyo ndinabadwila zikolanji nangandili zikolanji nanga ndayendamotani zisiyeni zimenezo

    3. Chawera ndiwe mbuzi, zikuonetsa kuti ku church unangodusako sunalowemo, if u dn’t comment jst ”like!” rathan ma commnt opusa

    4. Gift iweyo ndi galu bwanjinangati coment yanga wawonakuti siyilibwino osango khalachetebwanji? Ifeyo ndimlonda wama coment munomo ngatindine mbuzi iweyo ndi nkhumba zoona maiako kumangila mimba miyezi 9 kumayesa azabala munthu ilinkhumba yachabechabe tiwonana ndilinawetnchito boy ukonza kundithawa koma siwungandibisale

    1. ubwino wake atumbuka tili open kukamba zinthu & timamasuka kunena pakakhala vuto sitivomeleza chilichonse,, kusiyana ndi mtundu wako..salani ndikusanena kwanu you will your profit later zopusa inu pitani mukasukusule kuti nanunso mzinena musavomeleze chinachilichonse.

    2. @davie bt iz ma home iweo umaenda kumafunasa azimayi onse kut mwagula kapena ai@khwima haha dont talk abt zoganiza baba cuz i do think more dan u nanga bwanj amtchula mzimba ndie anakati azimayi malaw monse sanakatchula dzina la boma so yambe kaye waganiza iweo kunoke kut uli ndi ntchito yaikulu hala zikuonekaso ambir mwakwiya nazo kkk ndipo kwiyani kwambir

    3. @dango ndie kut chani kaya ukunena zosamveka ungolemba ngat nyimbo alipo mtumbuka osukusula usandisekese nawe kwada bwanj kod ndipo mwana ngat iweo instead of b sleepin utsokosa

    4. azimayi akavala chi condom chimakhalisamo mukati nde akuopa cancer,kavalidwe kake akuti ndikovuta,akuopaso kuti ingalowe yonse mkati & lastly akuti samanena za kuipa kwake poti chilichose chili ndi ubwino ndikuipa..ndizime ife azimayi to be kuno kudera kwathu sitigwirisa macondom achizimayi..ndine mtumbuka wamva rashid kabichi

    5. Dango Kasimba Zimene ukunenazo ndi zoona inafe lisani lathu ndilotalikilapo , Nde timaipititsa kutali condom ija after nso kugwetsera mvula nde nzimayi akamaichotsa imamuopsa ati amakhala ngati amabereka.

    6. @dango ndie tabwera ku inbox undiuze bwino bwino komaso kambirane zambir basi zaoneka iwe ndi ine funa kambirana modekha@haneef nanu muti chan musokosa # dango wanena zomveka basi

    7. Dango Kasimba wawina chitenje kwaine ur comments r very nice, wina akuchuluka nzeru ngati kwao amagwiritsa ntchito macondom bwanji akuchulukana ngat njuchi?

    8. @prince nanu machedzatu sizinali za mpikisano munena ziti mbalame ya munthu ngat iwe udzwa chan panalibe ofuna ku wina or ku looser nanu kod andstanding imakuvutani eti sapeza chochita bwanj ana otoleza ngat inu

Comments are closed.