Ruling Democratic Progressive Party (DPP) General Secretary Eckleni Kudontoni has died in a terrible road accident this morning, Malawi24 can report.
According to reports, he died after his Toyota Fortuner’s tyres developed a fault causing the vehicle to roll over several times.

It is said the accident happened at Bua in Kasungu. He was traveling from Kasungu to Karonga.
Sources say he died on the spot.
As this report was posted, the DPP was yet to make a statement on the matter.
MORE TO COME.
219 thoughts on “Breaking: DPP’s General Secretary Eckleni Kudontoni dead”
Comments are closed.


Umoyo wamunthu umakutilidwa ndi zinthu ziwiri: ubwino ndi kuipa. Omwe amaona ubwino pa munthuyu ndi omwe akukhetsa misonzi pomwe amene amaona kuipa kwa munthuyu ndi omwe akunena za kukhosi kwao. Posatengera ubwino kapena kuipa may i say RIP!
Ee! Koma Anthu Mumatokota Pa Network Pano, Mmmmmm…
Kodi ifayi yamupita pati petela
Mmmmmmmm ifa iwe bwanji ukanatenga Peter yu please
xry ifa ndikanyama komwe kalingat ebola akuluwa anali munthu olimba mtima
Ndilibe problem kaya wina azifa kaya adwale mkono ine ndilibe PULOBULEMU. KKKKK
mulongosi mulongosi iiiiiii
maike G jinard inuo mutu mwanu mwazaza mamina ndipo mulibe umuthu mwava maliro ndi maliro zopusa mwalembazi musazalembeso iwe ndie ndani kutuwa sanachite kufuna olo iweo lero ukhoza kufa mulungu atafuna ukumva guys mukamalata zopusa ine zimandikwana naliro omwewa paka mwapeza khani ana agalu.
R l p sec
Rest in everlasting peace bwana…We shall always miss you!
Koma achaskwera ndi mai apume kutukwanidwa
I witnes dis,so sad indeed r.i.p
We will miss u RIP
Why do u let politics ruin chikondi chapaubale,,,,,politics lacks Christ
Very good example inu a DPP Mumaiwala kuti muzafa,kulalata,kuba ndi kupha mulibe nzanu bola ngati munakumbuka sacrament la kulapa
There z no way a normal human being can rejoice over another somebody’s death. Ask urself kuti where wil u end. I dont think kuti Mulungu angakondwe nazo zimezi. Ili ndidziko. R I P. Sec
Ause muntendere
RIP hon kudontoni
Ndiye mwati chakwera ndi amene ukudziwa za imfa yaku dontoni
Nde mwati o Ekelesi Kidontoni onakwe bulu ulendu wokatembelera onthu o Mulungu o Chakwera? Ha, zoona bulu kumkwapula kuti omange kowasi osadziwa kuti pa Buwa paima mnjero ndi lipanga lokuthwa konsekonse? Balam!